Ku Chikangawa zili motele mwambo oyatsa makendulo moti ayaka kale

Пікірлер: 48

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson14435 күн бұрын

    SKC MWAZ WANU NDILINDICHIKHULUPILILO CHOTHELATU KUT NDIOMWE UTAOMBOLE MALAWI

  • @user-ig9ip8jq7v
    @user-ig9ip8jq7v5 күн бұрын

    He was indeed man of people skc watching from Port Elizabeth south africa muzimu wanu uuse mutendele. I Salute u

  • @OliverChimsewu
    @OliverChimsewu5 күн бұрын

    Watching from Capetown,we are together brethren.chilim is one of the best freedom fighter ever in the history of our country.he will be remembered in the country history.

  • @simplexkasimba903

    @simplexkasimba903

    5 күн бұрын

    MHSRIP

  • @EnipherMussa
    @EnipherMussa5 күн бұрын

    WATCHING FROM SOUTH AFRICA RIP OUR VICE PRESIDENT MR SKC 4EVER YOU ARE IN OUR HEARTS 😢😢😢😢

  • @spargomw

    @spargomw

    5 күн бұрын

    Amen😭😭

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti5 күн бұрын

    Mzimu Wanu a Vice president Saulos Chilima Uwuse mu mtendere, Malawi will never forget you Bwana 😢😢😢😢😢😢

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh5 күн бұрын

    Mwaonatu ngati ndi munthu obadwa mwa munthu yemwe unachita zimenezi,uchite manyazi ndipo usiku wa lero tulo sutinunkha 😅😅 unapha thupi,koma nzimu is still alive rest well SKC

  • @JowasiMasina-fy8ji
    @JowasiMasina-fy8ji5 күн бұрын

    Mzimu wa chilima uli paliponse mu Malawi Mphakana wana apenga misara ndithu aziwona

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y5 күн бұрын

    Athakati notse mukuva bwanji amene munapha chilima kapena mukuziwona Chochi 😢 mitima mwanu mukuva bwanji? Mwapha anthu koma mizimu ya anthu 9 awa ikukhundani ndithu ndipo ikusowesani mtendele pano pa dziko lapasi 😢

  • @spargomw
    @spargomw5 күн бұрын

    Kufa ngat chiweto Chilima 😭😭😭 Ambuye atonthoze mitima ya a Malawi, sitidzaiwala za imfa iyi mpaka chimaliziro cha dziko😭😭😭

  • @Nomsa77
    @Nomsa775 күн бұрын

    Watching from south Africa johannesburg

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw5 күн бұрын

    Yehova tiululireni,komaso mizimu yawo ipitilize kuwusa mu mtendete.

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d5 күн бұрын

    Nose munatenga gawo pa ifa zimezi mudzausowa m,tendele nose muyambe kuzimangila m,mozimozi pephelani mosalekeza aonekele pambalambanda😢😢

  • @gilbertdamba7344
    @gilbertdamba73445 күн бұрын

    SKC Malawi will never forget you. RIP 😭

  • @SandraIssa-lo8il
    @SandraIssa-lo8il5 күн бұрын

    Pemphero ndi chida choopsa kwambiri. Kuteroko kuletsa mapempheroko ndi mantha komanso kusautsika. Ichi ndichizindikiro choti anthu omwe adakhersa mwazi umenewu sakugona tulo, akusowa mtendere. The good thing is that the spirit of SKC is still with us, and he will not rest until justice for his death and the other 9 shall prevail. Rest in peace all the departed souls of 10th june 2024.

  • @AbigailMilanzi
    @AbigailMilanzi5 күн бұрын

    Muzimu wake ukause mutendele

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b5 күн бұрын

    Watching from capetown continue rest in peace our SKC kumupha ngati chinyama munthu Ambuye Mulungu wina aliyense anatenga po gawo pa imfa imeneyi apenge misala

  • @EdsonKampango-y7d
    @EdsonKampango-y7d5 күн бұрын

    May the soul of the legend skc continue resting in peace 😢😢😢😢

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b5 күн бұрын

    Mmmmm abale inu SKC ngati ali moyo ndithu yhoooo zombvesa chisoni ndithu may your soul rest in peace😭😭😭😭

  • @NearBanda
    @NearBanda5 күн бұрын

    Chilima sazayiwalika in this country 😢😢 Rest well skc

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef5 күн бұрын

    We are together l watching from cape town

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson5 күн бұрын

    Kwayenela kutelo chifukwa anali dolo hvy ❤

  • @MustapherLino
    @MustapherLino5 күн бұрын

    Chakwera sakumva chisoni

  • @Hopenandola-zg6kz
    @Hopenandola-zg6kz5 күн бұрын

    Zovesa chison kwambili wapita ngat masewela

  • @happymumba2261
    @happymumba22615 күн бұрын

    I'm watching from south Africa

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka5 күн бұрын

    Mulungu salakwitsa kalikose nximu wanu uuse mumtendere bwana chilima

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py5 күн бұрын

    MCP IDALAKWITSA KWAMBILI KUPHA CHILIMA MUDAPANGIRANJI AMFITI INU AGALU INU ANYANI ANA AMAGUNDWANI INU AMFITI

  • @user-il8cn7ko9m
    @user-il8cn7ko9m3 күн бұрын

    Ngt ali moyo chilima 😭😭

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka5 күн бұрын

    Chifunga awone pochika mulungu pasanapita masiku 60 kuchokera tsiku langozi ndukhulupilira xichitika mudxina layesu wamoyo

  • @MussaZimba
    @MussaZimba5 күн бұрын

    Zilibwino kwambili ❤❤

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda87115 күн бұрын

    Umu nde amene mwatsonyedza umulunga pomwe abutsa kaya ma shehe mafumu apita kwa CHAKWELA APITILA AKUDZIWA KUTI APATSA NDALAMA ZA MAGADZI NDOTSE AMENE MWATENGA GAWO LOLALIKILA PAMANSO PA. CHAKWELA ULALIKI WABODZA CHILUNGAMO MUKUCHIDZIWA KUTI CHAKWELA ANAPHA CHILIMA KOMA CHIFUKWA NDALAMA MUKULALIKA MOMUTSANGATSA MULUNGU ACHITE NANU A

  • @SellinahDyman
    @SellinahDyman5 күн бұрын

    Allah munaloreranji 😭😭😭😭

  • @Lee-lee-w1r
    @Lee-lee-w1r5 күн бұрын

    Hmmm basi pano ndi malemu 😭😭😭😭

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka5 күн бұрын

    Xovuta kuyiwara kwake koma mulungu yekha bas palibeso china adziwa pomuyika chifungayo ameni

  • @rosekumbangarose3535
    @rosekumbangarose35355 күн бұрын

    Keep resting the Legend 🙏🙏🙏

  • @user-ro9tr8xi5c
    @user-ro9tr8xi5c5 күн бұрын

    Zomvesa chisoni mwe

  • @feranjifeza6802
    @feranjifeza68025 күн бұрын

    Rest well SKC❤🎉

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx5 күн бұрын

    Mzimu yawo I use mu mtendere mulungu analandira mzimu yawo

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr5 күн бұрын

    Chilima anafinya Colona wake inuyo achakwela. Mudzafinya chani. Muzilingalile kwambili nonse amene mumapanga zokambilana zongwetsa ndenge ya vaice president matembelelo pamoyo wanu nonse

  • @Hopenandola-zg6kz
    @Hopenandola-zg6kz5 күн бұрын

    Zosayenda bwanji

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w5 күн бұрын

    😭😭😭😭😭 imfa yosaiwalika iyi

  • @user-oy6dl1pv9e
    @user-oy6dl1pv9e5 күн бұрын

    Ndipotuuu mzimu wa Achakwela MULUNGU awusunge malo abwino 😢a ulemelelo

  • @TressLuka
    @TressLuka5 күн бұрын

    🎉🎉🎉

  • @SellinahDyman
    @SellinahDyman5 күн бұрын

    Rest in peace sir 😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @ZaccheousPetrol
    @ZaccheousPetrol5 күн бұрын

    Ntchito iyi ilimmanja mwachauta.....koma munthu amene ayesa alinako kanthu azamulanda ndikamene ayesa alinako

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v5 күн бұрын

    Eeeee ayi taa dziko lapansi lovuta kwambiri