LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
Ойын-сауық
Banja la a Banda likukumana ndi mavuto pamene anthu angapo akudwala. Lucius Banda wakhala akudwala matenda a impsyo kuyambila December 2020 ndipo wagonekedwa ku chipatala kuno ku Malawi komanso ku South Africa kwa masabata 6. Pano akulandira chilandiro cha dialysis ku Mwaiwathu Hospital. Mchimwene wake Sir Paul Banda naye akudwala matenda a impsyo omwewo ndipo akufunika akalandire impsyo ina ku India. Izi zikufunika ndalama zosachepela 30 million kwacha. Mu banja momwemo, Francis, mkulu wake wa Lucius (mng'ono wa Paul) akudwala cancer yotchedwa leukemia ndipo akulandira chemotherapy. Izi zapangitsa banjali kugwilitsa ntchito ndalama zochuluka ndipo anthu akufuna kwabwino akhala akusonkha ndalama kuti awathandize.
Пікірлер: 21
Pawer solder❤ndiwe ngwazi pamaimbidwe
Good to hear how strong your faith is....God is so faithful 🙏AMEN we are with you in prayers.
Mlaka ndi more❤❤❤❤❤❤❤
Get well soon Soldier and your fellow brothers, we love you
Za bwino zonse Lucius
May God heal them
May the healing hand of our Lord Jesus touch you and your brother's.
Uremuwanu mau aphavu
Get well soon farmilly
May God Almighty help them all in this hard time they are in.
I wish u all fast recovery, you brought me some inspirations thru music
We love you🙏
Keep it up big
Zikomo mumatimilila
Makhazi
Sorry for that my brother god please I’ll them in Blood off Jesus
But am proud of you soldier, ndinu otchuka koma munakamanga maziko kumudzi kobadwa(Balaka)
@victoriasanyila178
2 жыл бұрын
May God heal you
Pawer solder❤ndiwe ngwazi pamaimbidwe
Mlaka ndi more❤❤❤❤❤❤❤
Pawer solder❤ndiwe ngwazi pamaimbidwe