Kumene MCP ikukafela ndipo maliro andale awa adzakhala opanda asilikali zafotokozedwa

Пікірлер: 15

  • @samchibenene4458
    @samchibenene445823 күн бұрын

    Uyo kamajeketi ngwankhaza chomene thus why tinamuthamangisa Ku mzimba Kuno

  • @user-ev4or2kg4z
    @user-ev4or2kg4z22 күн бұрын

    Amalawi ngati gwirizano watha ndiye kuti BOMA lonse latha ofunika zisankho chifukwa lidali losonkherana Amalawi sadavotere mcp yokha Amalawi tatiyeni tidzuke

  • @user-wd9yd1bg9n

    @user-wd9yd1bg9n

    21 күн бұрын

    Chilungamo chake 100%

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o22 күн бұрын

    Matenda ku MCP 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp21 күн бұрын

    Tikuyenla Kuvota mwachangu

  • @OssmanAbubaker-l5s
    @OssmanAbubaker-l5s23 күн бұрын

    Ulemu wanu mr Lyara Samuel osaopa osafooka freedom fighter

  • @ChawasoMlotha-ys6bf
    @ChawasoMlotha-ys6bf23 күн бұрын

    😂😂😂Chilungamo

  • @MikeMerecah
    @MikeMerecah23 күн бұрын

    Koma anthu amangidwa ku mzimba kuno why Sam lwara your quite,

  • @user-mv1wg2qd6i
    @user-mv1wg2qd6i23 күн бұрын

    ❤❤❤❤

  • @sukiemapemba4094
    @sukiemapemba409423 күн бұрын

    ❤❤❤❤❤

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona23 күн бұрын

    Zikhale ng'oma simunthu wa bwino ayi ndipo sadzakhalaso wa bwino ayi olo kungomuona kokha ndi maso ndimunthu oti alibwe chisoni ongofuna chimene wa nena chichitike chomwecho basi zangogwirizana ndi president chakwela anthu oipa kwambiri.

  • @PatricknathanMambiya
    @PatricknathanMambiya23 күн бұрын

    Greedy.. aliyense akufuna kudya pabwino

  • @user-ev4or2kg4z
    @user-ev4or2kg4z22 күн бұрын

    Amabungwe muli kuti

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga23 күн бұрын

    Mmmmm.inu phokoso iyaaaaa

  • @bisweckchimphamba8497

    @bisweckchimphamba8497

    23 күн бұрын

    Palibe wakutuma kuti uzimvesera