tsikana wina wabeleka khanda la galu ndipo khandalo lasanduka ntengo

Пікірлер: 80

  • @julianokhoza7065
    @julianokhoza7065 Жыл бұрын

    Ndiye Tsangano Imeneyo, Zikomo kwambili tikudziwa zithu zakumudzi mwasanga kudzela kwa inu Balanço Semanal. From Maputo

  • @davidmaulana9277
    @davidmaulana9277 Жыл бұрын

    Zikomo tikuziwa nawo mmene moyo wa abale athu okuyendera madera ena pa dziko pano one love from malawi

  • @harrietlujere4686
    @harrietlujere4686 Жыл бұрын

    Keep up the good work proud of you guys,mmatidziwitsa zambiri watching you here from South Africa Durban.

  • @lamackbanda6869
    @lamackbanda6869 Жыл бұрын

    Koma dela ili mumachitika ma story ambiri. Koma good job guys. Love here in MALAWI

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    thanks

  • @mavuschitseko7757
    @mavuschitseko7757 Жыл бұрын

    Zokumva zimapweteketsa mutu , program iyi ili boh, tikumanva ndikuona mmene zikukhalira , here Durban love you guys pitilizani

  • @michaelsportslossi9337
    @michaelsportslossi9337 Жыл бұрын

    Koma mayi amenewo saanabe malo ena ake ?komanso kumeneko kwa angonia nkutheka kuti aanthu aufiti akupanga izi pofuna kutchuka komaso kuyesa matsenga kuti aone kuti zikutheka.Nkhani Ina aanthu akumeneko bwanji sakutchuka ndi ulaliki? nkuti aanthu akumeneko sakonda kupemphera chifukwa izi zikuchulukira kwambiri.May almighty God show powerful below this

  • @zainabchikakuda6297
    @zainabchikakuda629711 ай бұрын

    This Chanel is working .thanks

  • @arthurmadzedze5365
    @arthurmadzedze5365 Жыл бұрын

    A sing’anga Amati amachokera ku Mozambique aja mwati samachokera ku dera limeneli?

  • @lydiaamos4214
    @lydiaamos4214 Жыл бұрын

    Zochitika mmasiku otsiriza, love this channel

  • @edommustafa2132
    @edommustafa2132 Жыл бұрын

    Keep it up good work I like this channel

  • @promise3693
    @promise3693 Жыл бұрын

    Keep it up guys.... watching from Durban

  • @chifundoalfred14
    @chifundoalfred14 Жыл бұрын

    Very very sad news Mmmm dzikoli ndithu langotsala pakaphindi chabe mwini wake akubwela atenge ake oyera m'tima

  • @ririvilla1423
    @ririvilla1423 Жыл бұрын

    Keep up the good work guys informing us what's going on there

  • @user-op7ji6hw6e
    @user-op7ji6hw6e7 ай бұрын

    iiii mulungu amusungolele nsikanai 🙏Kuno ku guruwe Zambézia ine dakumudwa Izi zamasiku osiliza 🙏chomfunika tilimbike kumpepera usiku ndiusana🙏

  • @HastingsChilima
    @HastingsChilima2 ай бұрын

    Ineso poganiza pa ine ndikuona ngati ndi mkazi nzakeyo olo amacheza ndi pamaso zamumtima ndi za wenkha eyetu

  • @edenngoma8214
    @edenngoma8214 Жыл бұрын

    Zovetsa chisoni . Koma akuyenera apite ku chipatala kuti akawapange check . I love your Chanel. From 🇲🇼

  • @oliviaolivia4979
    @oliviaolivia4979 Жыл бұрын

    OMG 😳 what plz anthun mudziweni yesu komazoona nkumuika nzanu chinthu Ngati in cho mmimba .Koma Choti mudziwe mfiti yozafaso

  • @patrickgrey1511
    @patrickgrey1511 Жыл бұрын

    Mmm mulungu sizoti wangokhala chete ayi

  • @gsmmalawi1741
    @gsmmalawi1741 Жыл бұрын

    Life yaku Mudzi ndiyovuta eeesh

  • @simangodickson1794
    @simangodickson1794 Жыл бұрын

    Kwa Angonia ni koipa , kuli nfiti olo atafuna ukussandutsa Ka mbalame ni mpompo , hmmmmm

  • @floramtiwa211
    @floramtiwa211 Жыл бұрын

    Eeee😱 koma dziko abale anthu saopa kumwamba hmm ayi Ambuye aweruzepo ndithu.

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Жыл бұрын

    Eshiiiii but govati u're trying the best really appreciate u

  • @hopcharlie3646
    @hopcharlie3646 Жыл бұрын

    Ine Friday kuno ku South Africa a Malawi chepesan uthakati schupit

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 Жыл бұрын

    zomvetsa chisoni mutengeleni ku chpatala please..komanso upeze wako mamuna mitala ndi umfiti...

  • @victoriawilliam4490
    @victoriawilliam4490 Жыл бұрын

    Mmmmhhh pitani naye kuchipatala please before is too late Mmhhh koma zoopsya

  • @carlosadelinoamor3189
    @carlosadelinoamor3189 Жыл бұрын

    malodza nkhani yovetsa chison ambuye alowerelepo kuti zoyipazi zisamachitike

  • @theheritagesoundsmonekera
    @theheritagesoundsmonekera Жыл бұрын

    Muzimayiyo wataya mwana kapena analibe mimba amanama

  • @frasernamaona2205
    @frasernamaona2205 Жыл бұрын

    Is this moshiko?, mumakwana guys

  • @promise3693
    @promise3693 Жыл бұрын

    Kulakwirana uku 😭😭 munthu kutenga mimba nukachira mtengo Mmmh shame

  • @user-yc4qq7qk5j
    @user-yc4qq7qk5j4 ай бұрын

    Very sad

  • @edwardedwards3577
    @edwardedwards3577 Жыл бұрын

    Pepani mai wanga mulungu akudziwa zonse imani Pamanso ake komanso ndimayamika kwa inu amene mumatipatsira nkhani zonse ambuye azikudalitsani nthawi zonse

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    zikomo

  • @EBBOY-nl7gr
    @EBBOY-nl7gr Жыл бұрын

    Koma kuli anthu omudziwa mulungu ukuuuu kumango chitika zinthu zopanda umunthu ukuuuuu

  • @estherdumbo
    @estherdumbo Жыл бұрын

    Dziko lafikapo ambuye bweraniiii

  • @user-gk3lw9nh6g
    @user-gk3lw9nh6g10 ай бұрын

    Keep it up

  • @hopcharlie3646
    @hopcharlie3646 Жыл бұрын

    & tikuthokoza channel iy ikumatiziwisa zambri

  • @dangerkondwanjames319
    @dangerkondwanjames319 Жыл бұрын

    pepani

  • @bonifaciosimao8620
    @bonifaciosimao8620 Жыл бұрын

    Koma ndiye

  • @JayKuzemba
    @JayKuzemba Жыл бұрын

    Munthuyu anachira bwinobwino koma mwanayo amafunika kukangaroo coz of kuchepa weight koma poti mkumudzi asowetsa mwanayo nkulenga nkhani yoti wachira mtengo nde poti mumakhulupirira changu mwavomereza mukafufuza mkhaniyo muzingonva kuti aliyense ananva

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 Жыл бұрын

    Ayi ndithu zoopsya kwambiri.Malodza saposa apa.

  • @zaithwachiwaya8885
    @zaithwachiwaya8885 Жыл бұрын

    Mmm kom zoopsa apite kuchipatala kma mmm

  • @Ndakonderedwa
    @Ndakonderedwa6 ай бұрын

    Sim boca ,essas mulheres

  • @aaronmagombo2523
    @aaronmagombo2523 Жыл бұрын

    Mmm this is very sad eish

  • @saukophiri4535
    @saukophiri4535 Жыл бұрын

    Nkuthekaso kuti mwina zikuchokera pakhomo pompo komaso mwina ndinkazi nzakeyo amangomukonda pamaso koma muntima sasangala naye awo anali maganizo anga chabe

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    zoona

  • @rosebonongwe8994
    @rosebonongwe8994 Жыл бұрын

    Mmm koma abale kkkkkkk koma zoopsya

  • @eladmaster5724
    @eladmaster5724 Жыл бұрын

    Very sad.matsiku osiliza

  • @xavierfabiao9038
    @xavierfabiao9038 Жыл бұрын

    Zosakhala bwino

  • @shammimmhangoh

    @shammimmhangoh

    Жыл бұрын

    Zosakhala bo

  • @chippiephiri4505
    @chippiephiri4505 Жыл бұрын

    Kulakwatu uku

  • @user-lv9ou1gp2k
    @user-lv9ou1gp2k Жыл бұрын

    Maloza awa eish

  • @lucysimbani3971
    @lucysimbani3971 Жыл бұрын

    Apite kuchipatala akamuone mmimbamo

  • @VincentKawonga-fg1mq
    @VincentKawonga-fg1mq9 ай бұрын

    😂😂😂

  • @hopcharlie3646
    @hopcharlie3646 Жыл бұрын

    Zoona zake ufiti ulipo

  • @thamandohtonny7778
    @thamandohtonny7778 Жыл бұрын

    Mmmm soo sad.

  • @miloslundu6366
    @miloslundu6366 Жыл бұрын

    mmm zovuta zoopsya

  • @lilianchisiza4579
    @lilianchisiza4579 Жыл бұрын

    Eeeeeeeeish koma anthu mmmm

  • @joshuamtenje1900
    @joshuamtenje1900 Жыл бұрын

    Nde mwati mtsikana osati mzimayi

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    Dzaka 17

  • @victorsmbewe4816
    @victorsmbewe4816 Жыл бұрын

    Eish 🤔

  • @rosebonongwe8994
    @rosebonongwe8994 Жыл бұрын

    Komatu anthu amuziwe yesu Mmmm ayenjeza

  • @confidencebanda109
    @confidencebanda109 Жыл бұрын

    Kusatira mwachete chete

  • @iziletmwachidule3374
    @iziletmwachidule3374 Жыл бұрын

    Mmmm zoopsa ndithu koma apite kuchipatala akamuone mzimayi ameneyi

  • @rogeriojose542
    @rogeriojose542 Жыл бұрын

    Uuuuuuhhhh very sad may God bless her life in the name of Jesus Christ.

  • @agostinhogofarsimonesimone5352
    @agostinhogofarsimonesimone5352 Жыл бұрын

    zilibwino malume

  • @kuangzhao5350
    @kuangzhao5350 Жыл бұрын

    Ufiti

  • @shammimmhangoh
    @shammimmhangoh Жыл бұрын

    No good

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 Жыл бұрын

    Thawizina mitalayiso siyabhoo.

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    zoona zeni zeni

  • @johanessphili-ano788
    @johanessphili-ano788 Жыл бұрын

    Koma !!!

  • @user-lu3ll6nh3f
    @user-lu3ll6nh3f6 ай бұрын

    zochttsa matha

  • @helderdias5523
    @helderdias5523 Жыл бұрын

    Angónia assusta hiii

  • @shammimmhangoh

    @shammimmhangoh

    Жыл бұрын

    Mm zosakhala bwino mmmm

  • @vincentmathews9143
    @vincentmathews9143 Жыл бұрын

    Mmmmmm km ufiti uliko mmmmm

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    yaaa

  • @arthurmadzedze5365
    @arthurmadzedze5365 Жыл бұрын

    A sing’anga Amati amachokera ku Mozambique aja mwati samachokera ku dera limeneli?

  • @ellenfumuyiliko1390
    @ellenfumuyiliko1390 Жыл бұрын

    Zosakhala bwino

  • @josuahkachali1489
    @josuahkachali1489 Жыл бұрын

    Very sad

Келесі