wina waphedwa chifukwa cha pakamwa pake, kuyankhula kwambiri akamwa mowa.

Пікірлер: 66

  • @user-ju8qf1li9j
    @user-ju8qf1li9j6 ай бұрын

    Apatu sizinayende, koma Bala nco mumatimvetsa kukoma koma nyimbo za nyamata uyo God sizi tingazipeze bwanji, watching from mzuzu the green city of malawi

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Thanks

  • @joaoluis9876
    @joaoluis98766 ай бұрын

    Koma yeeee zoopsa

  • @user-xu5nn2gx6e
    @user-xu5nn2gx6e4 ай бұрын

    Ntchito mukuigwira Anyamata.Watching from America.

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    3 ай бұрын

    Zikomo, tikumana kumeneko nex year

  • @user-yh7yo2gi5o
    @user-yh7yo2gi5o6 ай бұрын

    Good advice from great chief.

  • @austinvincent1264
    @austinvincent12646 ай бұрын

    Koma tinene zoona mr Gova improvement ilipo ndithu continue this amazing job

  • @KascrinjondaChannel

    @KascrinjondaChannel

    6 ай бұрын

    Zoona awa ndi A katundutu

  • @anamariasilverionicolau9637
    @anamariasilverionicolau96376 ай бұрын

    Oyenda ndi lupanga adzafa ndi lupanga lomwelo

  • @mackgozambia
    @mackgozambia6 ай бұрын

    Watching from Katete Zambia

  • @alicehananiya
    @alicehananiya6 ай бұрын

    Watching live from south Africa springs geto esh zovuta kumvesatu eeeee

  • @pioireneuvictorpio1391
    @pioireneuvictorpio13916 ай бұрын

    Moz wathu akuwonongeka thawi zose kuphana basi aaaaa 😢meus sentimentos .mumakwana achina gova ulemu wanuuu

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland92416 ай бұрын

    Zomvetsa chisoni kwambiri..kuwelunza ndi kwa Mulungu tinkhale ndi mtima okhululukilana..mwina amangoyankhula kamba ka mowa sibwino kumpha simudasove vuto..Mwapatsa ana ndi adzukulu udani..ndi zovuta kuti ana otsala adzagwilizane..Ambuye atinthandize...

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599Ай бұрын

    Zosakhala bwino konse ayi

  • @ChrisChumba-zh7nu
    @ChrisChumba-zh7nu6 ай бұрын

    Ilike you guyz fromalawi but knw am south Africa keep it up

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Thanks

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland92416 ай бұрын

    Angoni Mayankhula bwino kwabansi..za ntchitidwe umene ukuchitika pa mudzipo

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr6 ай бұрын

    Munatha kulondoloza nkhani a BS ndimakunyadilani, zina ukamva kambanga mwala, mwana analakwa chani 😢 mzimu wake uuse mumtendere,

  • @user-bp8ff6iz2r
    @user-bp8ff6iz2r6 ай бұрын

    Koma olo munthu atatukwana nde kumupha simukuchita bwino ena akulira chitsirutu chili ndi mwini aaaaa

  • @ChrisjuniorBoyce-si4yw
    @ChrisjuniorBoyce-si4yw6 ай бұрын

    Watching live from Capetown

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Thanks

  • @user-ul5wx6kb4f
    @user-ul5wx6kb4f6 ай бұрын

    zikomo kwambiri mumatiziwisa koma ndizovesa chisoni😭😭😭😭pepan pepan 😭😭😭

  • @Uncle-joe_moses-
    @Uncle-joe_moses-6 ай бұрын

    Ndimakutsatirani from Pretoria South Africa

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Zikomo kwambiri

  • @mavutojackson9264
    @mavutojackson92646 ай бұрын

    Live from Mozambique Zambezia boma la molumbo

  • @user-rc9jz1gk7n
    @user-rc9jz1gk7n6 ай бұрын

    Why ku Mozambique ntchitidwe uphanawu unka nachulukidwa????

  • @austinvincent1264
    @austinvincent12646 ай бұрын

    Watching live from Capital city of malawi.. Lilongwe

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Thanks

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo6 ай бұрын

    Agovate ulemu wanu 👍

  • @Uncle-joe_moses-
    @Uncle-joe_moses-6 ай бұрын

    Mr Gova mwandikumbutsa nyimbo imene ndimaikonda Chonde tandikumbutsani anaimba ndindani

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Yakumayambiriro kapena kumapeto kwa vídeo ??

  • @user-tw2zf7bj3e
    @user-tw2zf7bj3e6 ай бұрын

    Koma kwa Angonia mmmmmmmm ai masikando a ifa zophana zanyanya

  • @MilikaKilion-tn1bn
    @MilikaKilion-tn1bn6 ай бұрын

    Watching live from Malawi Lilongwe capital city pitilizani timakutsatilani

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Zikomo

  • @HurryBeston
    @HurryBeston6 ай бұрын

    Pitilizani akulu akulu mukugwira ntchito yabwino zikomo kwambiri Kuchokera ku phalombe malawi

  • @KascrinjondaChannel
    @KascrinjondaChannel6 ай бұрын

    Muito triste este cenário, de facto o feitiço existe mesmo, mas é dificel perceber este cenário

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Pura verdade

  • @tchanganiskitsmalawi5067
    @tchanganiskitsmalawi50676 ай бұрын

    Ku Mozambique anthu amayankhula chichewa?

  • @gracekankuzi8671

    @gracekankuzi8671

    4 ай бұрын

    Eya. Kwambirinso

  • @user-yc4qq7qk5j
    @user-yc4qq7qk5j6 ай бұрын

    Yoooo zomvetsa chisoni kwambili

  • @user-bw7oc4ht5p
    @user-bw7oc4ht5p6 ай бұрын

    Zoona pakamwa ndi poyizoni ,malakhulidwe amamanga ndiponso amamasula

  • @Ndakonderedwa
    @Ndakonderedwa6 ай бұрын

    Oyenda ndi lupanga adzafa ndilomwelo

  • @user-nq7rh9pv5s
    @user-nq7rh9pv5s6 ай бұрын

    Koma kwavutatu komeneko😂😂😂😂😂😢😢😢😢

  • @GeraldTausi
    @GeraldTausi6 ай бұрын

    Angonia province inayenera kukhala mbali ya dziko la Malawi osati Mozambique ayi

  • @gracekankuzi8671

    @gracekankuzi8671

    4 ай бұрын

    Zoona zake

  • @user-bp8ff6iz2r
    @user-bp8ff6iz2r6 ай бұрын

    Koma ku tsangano nkuphana iiii

  • @Christophermapira
    @Christophermapira6 ай бұрын

    Mumaitha guys koma akumwanu mukalenzera osamaona amzanu kupusa ayi kuyakhula kwambir

  • @langsonmndalanga
    @langsonmndalanga6 ай бұрын

    Eish zikoli

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn6 ай бұрын

    Zosakhala bwino pepani nonse olira

  • @user-cm8nk1nu2l
    @user-cm8nk1nu2l6 ай бұрын

    Uku NDE zimaonjeza eeeee

  • @GeraldTausi
    @GeraldTausi6 ай бұрын

    Tikamati anthu akumozambiki ndiankhaza

  • @user-nx7yz4qo8f
    @user-nx7yz4qo8f6 ай бұрын

    Mmmmh koma zoopsatu

  • @mustafahaji2599
    @mustafahaji25996 ай бұрын

    Pepani ofedwa ndithu

  • @zindikilanivutitsani2311
    @zindikilanivutitsani23114 ай бұрын

    😢😢😢

  • @nickjalifu3287
    @nickjalifu32876 ай бұрын

    Eeeeee😢😢

  • @AnjelinaKasowanjete-fo8it
    @AnjelinaKasowanjete-fo8it6 ай бұрын

    ayi mumatha inuyo pitiridzani kutipasira nkhani zosiyana siyana

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Zikomo

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri85176 ай бұрын

    Eeeeee bzobvuta

  • @MateusbentoJose
    @MateusbentoJose6 ай бұрын

    más esiste mesmo as pessoas mataom😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @clementenhatnelesson7191
    @clementenhatnelesson719124 күн бұрын

    😢😮😮🎉❤😂😅

  • @MarcoJoao-lw6tz
    @MarcoJoao-lw6tz6 ай бұрын

    Ii

  • @MarcoJoao-lw6tz
    @MarcoJoao-lw6tz6 ай бұрын

    Bodo

  • @EvanceWatson-lz8ek
    @EvanceWatson-lz8ek6 ай бұрын

    Timamva zambiri kuchokera kwa inu from Mpumalanga SA

  • @zaithwachiwaya8885
    @zaithwachiwaya88856 ай бұрын

    Mulomo wamutengela kumanda esh kumayakhula bwino kuopa pa mawa mautu amalenga mmm

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    Zoona Zeni Zeni

  • @ojsimze-px3kw

    @ojsimze-px3kw

    6 ай бұрын

    Zambia is watching