phuzitsi wina wa school yosula aphuzitsi wapeza nkazi emwenso ndi phuzitsi akupanga zadama.

Пікірлер: 64

  • @Envanceabwinobamusieli-sf9tt
    @Envanceabwinobamusieli-sf9tt11 ай бұрын

    Koma atolakhan ku Mozambique mukugwira ntchito yotamandika mpaka kutiwonesa stadium 😂😂😂😂

  • @kelvinskada5619
    @kelvinskada56193 ай бұрын

    Two bad, watching from malawi

  • @AndrewPilliotmw
    @AndrewPilliotmw Жыл бұрын

    Vuto ndi mamunayo........ Anyway watching from Maputo (koma ndine mmalawi ndithu)

  • @helderdias5523

    @helderdias5523

    Жыл бұрын

    Me too

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri10 күн бұрын

    Akacheza amamwa eti kkkkk

  • @fineenemy2045
    @fineenemy2045 Жыл бұрын

    Language is clear komano zudabwisa mainawo koma mwat ndiku malawi uku?

  • @kairaruphan2639

    @kairaruphan2639

    Жыл бұрын

    Akuti Mozambique osati malawiyi

  • @confidencebanda109
    @confidencebanda109 Жыл бұрын

    Mayi uyo ndiwolakwa bola akanathesa banja za uhule wake akanapangila pa nkhomo pa makolo ake fro malawi

  • @zainabchikakuda8764
    @zainabchikakuda8764 Жыл бұрын

    Komatu. Kulakwa chommenyera mwamuna wako nchiyani nzimayi oipa ukupha mwana waeni 😭😭😭

  • @LimitedMolotali
    @LimitedMolotali2 ай бұрын

    Nkaziyo ndihule aphesa amuna

  • @mayeserokaponya5196
    @mayeserokaponya5196 Жыл бұрын

    Man banja losagwirizira ili nawenso ndiwachibwezi basi zatherana Malo ndi awana

  • @chippiephiri4505
    @chippiephiri4505 Жыл бұрын

    Mamunayi ndiwopoyila

  • @grantmachira9668
    @grantmachira9668 Жыл бұрын

    Mayiyo ndiwosalakwa amadzilimbikira ekha abambowa angothetsa banja basi but it seems mkaziyo ndi bread winner mkazi malo anagula yekha

  • @Xtar_deadlol1
    @Xtar_deadlol126 күн бұрын

    Za ziii kusowa zotola nkhani Chan

  • @lamackbanda6869
    @lamackbanda6869 Жыл бұрын

    Olakwitsa ndi mamunayi zinthu zonsezo zimachitikazo opanda action kuonesa. Nkhani yamalilo inaliso yayikulu olo sanayithambasule. Komaso zimayiyu sanatenge ndalama ku bank koma zimuna akewo ndi amene amamanga nyumbayo. Naye mamunayo ofafusa kuti ndalama akuzithenga kuti zomangila nyumba kumangoyang'ana zimamutsangalasa

  • @zakeyophiri4308
    @zakeyophiri4308 Жыл бұрын

    Pls inuyo nkhani zina muziysa Kubisa nkhope kapena azalankhula atayang.ana kumbali chitsazo nkhani ya mnyamata akuti anapeleka mimba kwa mtsikana kapena mtsikana uja amene chifukwa media imapita patali tidzalephela kumufusila kapena kukwatiwa adzati ena anampatsa kale mimba

  • @chicco2294
    @chicco2294 Жыл бұрын

    Mainawa akuti bwanji?? I didnt know ku mosco mumalankhula Chichewa choncho

  • @user-ez7th2rv7g
    @user-ez7th2rv7g6 ай бұрын

    Thanks for the update

  • @westonnsulupi4056
    @westonnsulupi4056 Жыл бұрын

    From Malawi

  • @ernestbwanalisauteni3483
    @ernestbwanalisauteni3483 Жыл бұрын

    Kkkkkkkkkk zosokonezeka kkkk

  • @victorsmbewe4816
    @victorsmbewe4816 Жыл бұрын

    Emotional damage 🤕🥴😜

  • @DelcidioDiogoPedro-ir9ni
    @DelcidioDiogoPedro-ir9ni Жыл бұрын

    Nkazio ntanbuali

  • @chembachilemba7623
    @chembachilemba7623 Жыл бұрын

    Tsono wamenyedwanso mkazi ali wake kumenyedwa ndi mkazi aaaah this is not true guys😂😂😂😂nde mkazi amamangitsa nyumba inu osapezekako olo amfumu sakukudziwani zovutatu izi

  • @ndazionaanastasiaannaphiri4843
    @ndazionaanastasiaannaphiri4843 Жыл бұрын

    Palibe chabwino zonse zolakwika mkazi yo nde worsen

  • @josuahkachali1489
    @josuahkachali1489 Жыл бұрын

    From Malawi but am stay in Kuwait

  • @jamesselemani1003

    @jamesselemani1003

    Жыл бұрын

    Oky

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 Жыл бұрын

    In a true sense the man is wrong, because he was never be involved with the woman if it is true where was the men the time when the woman started to build the house?

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    of cause

  • @chifundoalfred14

    @chifundoalfred14

    Жыл бұрын

    Mozambique

  • @peterbanda7003
    @peterbanda7003 Жыл бұрын

    Osamusiya bwanji

  • @lamackbanda6869
    @lamackbanda6869 Жыл бұрын

    Ntchito yapamwamba guys mumayitha♨♨♨♨

  • @ngendahayososthene1398
    @ngendahayososthene1398 Жыл бұрын

    bambo inu ndi inu opoyira zedi.

  • @floramtiwa211
    @floramtiwa211 Жыл бұрын

    Koma ma statement akusiyana mwamunayu akuyankhula mosiyana ndiazimayi aja

  • @smithelectro-plumb2994
    @smithelectro-plumb2994 Жыл бұрын

    Kodi akulankhula chilankhulo chanji guys

  • @chancyutekakayala2445
    @chancyutekakayala2445 Жыл бұрын

    May someone assist me Kodi zikuchitika ku dziko lanji izii komanso nchiyankhulo chanji

  • @Envanceabwinobamusieli-sf9tt

    @Envanceabwinobamusieli-sf9tt

    11 ай бұрын

    It's chichewa in Mozambique 🙄

  • @zaithwachiwaya8885
    @zaithwachiwaya8885 Жыл бұрын

    Kom nkhaniyo mamunai zikuoneka kut malo sanagule nao.Komaso zimaiyo ndi uhule lothelatu zochitisa manyanzi zed

  • @zaithwachiwaya8885

    @zaithwachiwaya8885

    Жыл бұрын

    Kom saname nkhaniyi kadakonda mukanamuonesa mzimai wa chigololo yo timuone kkkkkkk

  • @simangodickson1794

    @simangodickson1794

    Жыл бұрын

    Mahule , Mabanja oyambila mvitsamba

  • @promise3693
    @promise3693 Жыл бұрын

    Kulakwa🤔

  • @bosconthandala9905

    @bosconthandala9905

    Жыл бұрын

    👀 from malawi

  • @zecamariosandifolo8535

    @zecamariosandifolo8535

    Жыл бұрын

    Malowo ngakhale atakhala kuti nyumbayo anagula ndi iwowo komabe ali pa banja nyumbayo ndiyawose basi

  • @paulmgombebanda-mr19sate
    @paulmgombebanda-mr19sate Жыл бұрын

    Zovuta izi

  • @luciajames604
    @luciajames604 Жыл бұрын

    It's Mozambique

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    Yes

  • @tadalaimwa394
    @tadalaimwa394 Жыл бұрын

    Ndemwati ndinu amalawi? I really wish to visit and learn more about this place

  • @zexndaomba3011

    @zexndaomba3011

    3 ай бұрын

    Samalawi this is angonia

  • @lucysimbani3971
    @lucysimbani3971 Жыл бұрын

    Zosankhala bwino ayi

  • @nemamoleni3041

    @nemamoleni3041

    Жыл бұрын

    Ati agulitse malo ndalama agawane?? Zosakhala bho

  • @memorymalikita3628
    @memorymalikita3628 Жыл бұрын

    Where exactly is this sad news happened

  • @mtimbasonjojailos5106

    @mtimbasonjojailos5106

    Жыл бұрын

    Mozambique iyi

  • @jessienkhoma2492
    @jessienkhoma2492 Жыл бұрын

    Koma ndi ku Malawi kapena Mozambique?

  • @kalimawandale7161

    @kalimawandale7161

    Жыл бұрын

    Mozambique

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 Жыл бұрын

    Mabanja akenso ndendi achi'chainatu

  • @eliasfaunteni6849

    @eliasfaunteni6849

    Жыл бұрын

    Mchifukwa chake timanena kuti akaziwa tikawamphunzitsa amachuluca mzelu zovetsa chisoni kwambiri

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 Жыл бұрын

    So you people the way you speak the language don't you like each other like Malawian people? Aren't you the same people, tell me what is the different there between you and Malawian?

  • @joegibsonzulu2599

    @joegibsonzulu2599

    Жыл бұрын

    It's true that the language that is being spoken in this video is exactly the same that is spoken in Malawi.We are one people, with one language, one culture , same values and similar traditions.We were only divided by colonial boundaries.Its a great pity that sometimes we seem to perpetuate these colonial divisions.

  • @shariffalick796
    @shariffalick796 Жыл бұрын

    Kodi mayina akuchulidawa ndi ku malawi ?

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    Жыл бұрын

    ayi, koma kalipentalayo

  • @chifundoalfred14

    @chifundoalfred14

    Жыл бұрын

    Mozambique

  • @chifundoalfred14

    @chifundoalfred14

    Жыл бұрын

    Mozambique

  • @user-gu4kk2bt4h
    @user-gu4kk2bt4h8 ай бұрын

    Penço nr d BS de Whatsapp

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    6 ай бұрын

    865112269