@chenkope01 Iyiyi yokha Nancy wabwera mwaulemu koma ikubwerayi kuli kung'alura koopsa.
Mmmmm nzachibwana, ndinamva mophudzulira, izi ndi ndale izi mmmm😭😭😭😭😭
Welcome ndinatopa ku searcher kuti ndimve za impi biyeni😢
😅😅😅Zikuonakadi kuti Nancy apatsa chituwitsa😂😂😂
Mumakwana inuyo big man,,,,,,,! Don't fear in democracy time mumatiimilira inuyo ✊✊✊
Eti enawa to call them malemu sizawakhala😢😢
Ikuyamba bwino , kuononga, kusokoneza, mmmm ndakutulukani Alla mwana wa nzanu wayenda ndi miyendo zopusa
Mpakana Pepe Kale komatu Nancy umangidwatu iwe😂😂😂
Koma ndipovuta kuyiwara skc😭😭😭
Koma chenkope akumati akaluma ndi kuzilila ngati khoswe
Apepe kale kkkkkkk koma Nancy usandikomole😊😊😊😊😊koma yah
Welcome back Nancy...MHSRIP 🙏
Rest in eternal peace Dr saulos Chilima and others 😢😢😢😢only God knows what happened to you people
Osamaseweretsa Maliro, Anthu akulira ataya Abale Inu mukupangira mchezero chisoni chanzanu mawa ndinu,samalani popanga zinthu.Ife tikulira and palibe chobisika papita Mzimu wa munthu .
Munasowatu Nancy kkk
Dakutulukani mwayamba za chibwana kwambiri
go well
Ndiye kuyankhula kotani umalemu umamukhala munthu apa pokha ndiye mwayankhula zofoyila kwambiri
True....
😂😂😂😂😂😂😂😂 kma Chenkope Munabwera inuyo😊
Kkkkkkkkl mpaka mamama aunt eeti kubeleka ngati mbewa
Koma Nancy iiii kkkk
Nancy I love you so much
2 weeks ago mwantukwana lero mukuti anali wa dongosolo
Zamanyitu mwayambazi mwadya zingati chemkope?
Big up atumwi😂😂
Ndipa ndimakukonda koma na izi ndakutuluka
Kkkk 😂😂 chenkope nsanje
ndiye ngati imatelo iyeyo sakanatha kubeleka 6 amati alibe ndalama
Mwadzilowetsa chibwana, amalawitu siwoputsa inu che nkope. Mufuna akutameni aboma?
Matako ako Nancy
Koma ndiye umalemu osamukhala Impi Biyeni
Umalemu osawakhala😅
Rest in peace legend skc
❤❤❤❤❤❤❤ Hello guys
Mumatiyimilira❤
Nancy ngopoira kkkk
Ngati mcp yakupatsa ndalama ndibwino kupita ku mcp komweko wamva, anthu ambiri mumatulutsa tima video or audio ndicholinga kuti boma lizikupatsani ndalama lero ndi izi che nkope mwayamba kupepera
Che Mkope, mbambande
Koma Nancy
Bwanji akupasani ndalama ????
Galu uyuyu chintuwisa chimenechi wadya
Timakuchitani follow chifukwa simumapanga za ndale km zomwe mwayambazi mmmmm ai
Wabwera iweyo😂😂😂
Suit ya KwaZulu-Natal
Haiboo
Awapatsa ndalama awa ayamba kuyamikira Boma ndalama anakozatu
❤❤❤❤❤
MHSRIP 😢
😂😂😂😂 Nancy upole moto
Akatelelo a mcp akupasani ndalama
😂😂😂 kma nacy
Ena umalemu suwayenera.
Nancy
Mwadya bazi
Km nasy .... Unasowa2
Mwadya banzi ndipo ndinu a MCP ,okupha eti
😂😂😂umatha ase
Nancy amupasa chithumba uyu.........iziziso zaziwika kale kuti mcp yapha anthu
ati ena umalemu suwankhala,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,kkkkkkkk
Rip SKC
Koma Nacy
Kkk umalemunso imakhala munthu?😊
Nancy girl umaitha
Nancy, pamaliro unaonapo mc? Ma hope? Koma iweeee kk
Nacy wayamba misara wamva
Zanziiiiiii🤧🤧🤧🤧🤧
Zenizeni-zo ndee zili kut??
Unbelievable
Chilima Rest in peace always, u left for us questions without answers😢😢😢😢😢
Koma Nancy abusa analalikira chani?
Skc RIP
Kkkkkkk
Пікірлер: 73

@chauncychauncy1683
9 күн бұрын
go well
Ndiye kuyankhula kotani umalemu umamukhala munthu apa pokha ndiye mwayankhula zofoyila kwambiri
@mzeewandembonyirongo2972
9 күн бұрын
True....
😂😂😂😂😂😂😂😂 kma Chenkope Munabwera inuyo😊
Kkkkkkkkl mpaka mamama aunt eeti kubeleka ngati mbewa
Koma Nancy iiii kkkk
Nancy I love you so much
2 weeks ago mwantukwana lero mukuti anali wa dongosolo
Zamanyitu mwayambazi mwadya zingati chemkope?
Big up atumwi😂😂
Ndipa ndimakukonda koma na izi ndakutuluka
Kkkk 😂😂 chenkope nsanje
ndiye ngati imatelo iyeyo sakanatha kubeleka 6 amati alibe ndalama
Mwadzilowetsa chibwana, amalawitu siwoputsa inu che nkope. Mufuna akutameni aboma?
Matako ako Nancy
Koma ndiye umalemu osamukhala Impi Biyeni
Umalemu osawakhala😅
Rest in peace legend skc
❤❤❤❤❤❤❤ Hello guys
Mumatiyimilira❤
Nancy ngopoira kkkk
Ngati mcp yakupatsa ndalama ndibwino kupita ku mcp komweko wamva, anthu ambiri mumatulutsa tima video or audio ndicholinga kuti boma lizikupatsani ndalama lero ndi izi che nkope mwayamba kupepera
Che Mkope, mbambande
Koma Nancy
Bwanji akupasani ndalama ????
@sedicmuzammil8530
7 күн бұрын
Galu uyuyu chintuwisa chimenechi wadya
Timakuchitani follow chifukwa simumapanga za ndale km zomwe mwayambazi mmmmm ai
Wabwera iweyo😂😂😂
Suit ya KwaZulu-Natal
@naBEthA
8 күн бұрын
Haiboo
Awapatsa ndalama awa ayamba kuyamikira Boma ndalama anakozatu
❤❤❤❤❤
MHSRIP 😢
😂😂😂😂 Nancy upole moto
Akatelelo a mcp akupasani ndalama
😂😂😂 kma nacy
Ena umalemu suwayenera.
Nancy
Mwadya bazi
Km nasy .... Unasowa2
Mwadya banzi ndipo ndinu a MCP ,okupha eti
😂😂😂umatha ase
Nancy amupasa chithumba uyu.........iziziso zaziwika kale kuti mcp yapha anthu
ati ena umalemu suwankhala,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,,kkkkkkkk
Rip SKC
Koma Nacy
Kkk umalemunso imakhala munthu?😊
Nancy girl umaitha
Nancy, pamaliro unaonapo mc? Ma hope? Koma iweeee kk
Nacy wayamba misara wamva
Zanziiiiiii🤧🤧🤧🤧🤧
@user-dq9oe8sp8k
5 күн бұрын