Mwalowa kolakwika, ndiwe galu mbuzi chitsiru.... Kape manganya ndi munthu wabwino kwambiri ngati nfikusintha, asintha pano koma we have hope kuti he will continue with chilima vision
@alicksonmakata75447 күн бұрын
Inu muyenera kudziwa kuti M U ndi vice president wa Malawi China Mulungu ali mbali yake mbili yake mukhoza kukamba ife tilibe nayo ntchito ife tingokupemphani kuti mudzipempherera kuti Mulungu apitilize kutidalitsa ndi kutiteteza tilifunire dziko lathu zabwino osati zaumphawi zosauka chifukwa ndi ziwanda.
@MemoryMbalat
7 күн бұрын
Ndiponso
@EdythGloryNamponya8 күн бұрын
Komatu mungoona kumutsutsa uyu...manganya ndi birimankhwe ohoooo
@TaitasMakombe-ql4rr8 күн бұрын
Umafuna asankhe iweyo mbuli ngati iwe kumangoipitsa azanu bas
@AlinafePililani8 күн бұрын
Zanzi Mwayamba nsanjetu tikutulukani..
@JustinLipipa
8 күн бұрын
Ndiyakale angoibweleza😂😂😂😂😂
@harrispheleni22057 күн бұрын
Ineyo l always say akuluwa amatenga ndalama Kwa APM and target yake ndi campaign ya DPP check all his videos palibe chomwe anakambako Cha DPP choipa as if a DPP ndima saints. Pakatipa wanyoza chilima atamwalira kuyamba kuyamikira, lero waipa manganya. Za ndalama anagawana a DPP za COVID sakamba, za chisale sakamba, mombera university sakamba uona akujama ya nankhumwa hater uyu mxiew😮
@AlufeyoBanda-cv2we7 күн бұрын
Kkkk koma ma reporter ena kubwera ati mbiri koma kuli kudzayalutsana kkk
@user-ol1hf7ru1v7 күн бұрын
Nkhaniyi ndi ntchito wapatsidwa munthuyu sizikugwilizana ata pan'ono kulakwa kumeneko aaa kale simumanena bwanji
Manganya uja waipa lero??? Lol umbuli basi a malawi. Nkona amalawi ali osauka. Why didn’t you bring all this bs when he was appointed by Chilima to be his vice president?? Education/civic education is very important.
@FrankKadangwe7 күн бұрын
This voice ikundikaikitsa
@user-hc9hc3dk5oКүн бұрын
Koma guys kung'alula kwa bwanji uku😂
@PatriciaemilyMpokwe8 күн бұрын
Ndipo izi mukuti titani nazo mmm wasowa chonena iwe
@user-dx4zu1wv4q8 күн бұрын
Timakunyadila man kwambiri
@CatherineDesire7 күн бұрын
Mmmmmh mmmmh!🤔🤣🤣🤣🤣🤣oyamwidwa chokodzera ooo akhare president lero 🤣🤣🤣🤣☠️😷
@user-xi7bo8jx8h8 күн бұрын
Best TV
@blessingkamanga17818 күн бұрын
Greatest liar I have ever seen is Bakili Muluzi tv .
@AmulatDenis6 күн бұрын
Enanu ndi alendo pa Chanel chimenechi ndiye u uth wanuwo musatinyase ife timapanga follow
@AleksaWilliams-qc6cn8 күн бұрын
Lero ndie mapolopangada osusa bakili tv ndie achulukatu lero iiiii,tv iyi simanamatu samatumiza nkhani zopanda umboni uyu
@EstherKamphale-yq8dm8 күн бұрын
Za ziiii kuti zimveke bwanji. Still ndi vice president wa dziko LA Malawi basi. Muchira koma mochedwa
@RodwellLayford
7 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@ChisomoNyimbo7 күн бұрын
Inu ndi osokoneza ndthu palipose kubweretsa negative altitude mxiew
@estherkambewa77918 күн бұрын
Nsanje a Malawi uyu amangidwe Sizisintha kanthu he is still the VP Dziko likamva kuti litani?
@chitenjepatriq3338
8 күн бұрын
Video ndiya kalekale
@user-lr2wx5xd9dКүн бұрын
Following
@AmulatDenis6 күн бұрын
Manganya ndi wamdede
@WatsonAmon7 күн бұрын
Ndangowona kuti akulu awawa amadana ndi manganya
@KennyMathank8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 koma nkhani zili umu eeeeeh bakili muluzi tv ndi wakulu
@sandramkaligida11636 күн бұрын
Enafe tikamati uyu wa bakili muluzi tv ndi chitsiru mumati tsutsa Nanga zoona akanenene za chokodzela cha munthu pano
Everyone has a dark side of history but we don't need to start digging such as if the woman has chosen to bring it to the public.. Nkhani zanutu pango'nopang'ono zayamba kumamveka ngati zija za m;maboma pa MBC.
@alicechigamba17517 күн бұрын
Mbili yonyasa anthu a seventhday ndiachisawawa I can tell
@RABSONSIKELO7 күн бұрын
Inunso tiuzen mbili yanu ...
@mollymasangano4736 күн бұрын
Bakili Muluzi channel adayotulutsa video some years back go and check Bakili muluzi platform you may realised he produced this video two to three-years ago l started watch some years ago so don't be upset.
@davidjames6795 күн бұрын
nonse imakubhowan tulukan ndipo musamamvele
@HusseinMachemba6 күн бұрын
Guyz vedio iyi ndi yakale kwambili nde chonde musaluse ayi
@AlexKaunda-ny2eg8 күн бұрын
😂😂😂😂 chakwera ndi wamisala kusiya nsonda kusiya dausi kusiya uladi Musa
Izi adayakhura kale kumene silero ai iwe nde oduka mawaya sukudziwa kathu
@TheresaKuluwemba
8 күн бұрын
Video ndiyakalekaletu iyi, mwina inuyo bakili muluzi tv simumamutsatayi mmbuyomu, koma ndiyakale kwambiri
@Omwale8 күн бұрын
kkkkkk koma manga
@MrsMachewere8 күн бұрын
Mbuzi ya Munthu Amangidwe basi
@ZIONEAMILU-oo6og7 күн бұрын
Zapakathawi 😂😂😂😂
@timothyntonga82567 күн бұрын
Kkkkkk
@user-uc1pd1tc2x8 күн бұрын
😂😂Koma malawi 😂😂😂😂 president etii😂😂😂
@MasterJailos-kv5sd7 күн бұрын
Usafooka
@user-rh3un3hv3j8 күн бұрын
Kkkkkkkkk km ukooooo
@CharlesMateya7 күн бұрын
Kkkkkkkk zamalisechezez
@RhodneyBwa38 күн бұрын
Mmmmmmmmm km abale.
@ancientnkhata11376 күн бұрын
Awa abakili Muluzi tawatulukira kuti ndi aDPP
@HusseinMachemba
6 күн бұрын
Koma akulu muzifufuza kayetu video iyi ndi three years ago
@adzonzicomedy
6 күн бұрын
video iyi ndiyakalekale
@adzonzicomedy
6 күн бұрын
we love bakili muluzi TV
@gamammwenye7 күн бұрын
malawians we have to accept that in every person there is a dark side, aliyense ali ndi mbiri.... Bakili muluzi tv has just narrated what happened, but that does not imply kuti the current Manganya is a bad person. kutukwana mkozi ndi mwini wa channel chimenechi, sizingathandize.
Пікірлер: 130
Izi zilibe ntchito musiyeni nzanu pano ndi VP wa dziko lathu la malawi ❤❤❤❤
Akuluakulu izi sizabodza zinachitikadi ndithu izi sizalelo zinaulusidwa kalekale
Mwalowa kolakwika, ndiwe galu mbuzi chitsiru.... Kape manganya ndi munthu wabwino kwambiri ngati nfikusintha, asintha pano koma we have hope kuti he will continue with chilima vision
Inu muyenera kudziwa kuti M U ndi vice president wa Malawi China Mulungu ali mbali yake mbili yake mukhoza kukamba ife tilibe nayo ntchito ife tingokupemphani kuti mudzipempherera kuti Mulungu apitilize kutidalitsa ndi kutiteteza tilifunire dziko lathu zabwino osati zaumphawi zosauka chifukwa ndi ziwanda.
@MemoryMbalat
7 күн бұрын
Ndiponso
Komatu mungoona kumutsutsa uyu...manganya ndi birimankhwe ohoooo
Umafuna asankhe iweyo mbuli ngati iwe kumangoipitsa azanu bas
Zanzi Mwayamba nsanjetu tikutulukani..
@JustinLipipa
8 күн бұрын
Ndiyakale angoibweleza😂😂😂😂😂
Ineyo l always say akuluwa amatenga ndalama Kwa APM and target yake ndi campaign ya DPP check all his videos palibe chomwe anakambako Cha DPP choipa as if a DPP ndima saints. Pakatipa wanyoza chilima atamwalira kuyamba kuyamikira, lero waipa manganya. Za ndalama anagawana a DPP za COVID sakamba, za chisale sakamba, mombera university sakamba uona akujama ya nankhumwa hater uyu mxiew😮
Kkkk koma ma reporter ena kubwera ati mbiri koma kuli kudzayalutsana kkk
Nkhaniyi ndi ntchito wapatsidwa munthuyu sizikugwilizana ata pan'ono kulakwa kumeneko aaa kale simumanena bwanji
@kingzack8999
4 күн бұрын
Nkhani ndi yale iyi
Komaso iwe usamakhale ndisanje pola moto wava wawonjezano ndale zako ".. zinthu zina muziyamikilako eeee mwatani bambo inu ayi chitani manyazi😂😂😂
Best TV ever
Zabodza zimenezo Zinali kuti kale lonse zaziii
Wazidziwa lero tinaonaona kale 3 years ago
Kma ndy atigazazira ma sisterz athutu kkkk
Video iyi ndi yakale zediii ndipo tinayiwalanso zoti kunali video imeneyi
Ada awawa amatha continue bro kkkkkkk
Maphuzilowo sanakwane
Chitsiru garu usamatisokoneze wava
Koma iweyo ndi katundu bale ❤😂
Aaaaah iwe uzipanga zako wamva ife tonse tima mpanga follow
Tingoti kudziko lapansi kulibe wagwilo aliyense alindidzake
Ife timakukondan uncle,,🎉🎉🎉
Nkhani anayangura asanasangidwe ndiye inu chikukupweteka chani
Izi tinazivela kale kale boss
Ing'alule😂😅
Akut aone ngat kometa bwino😂😂😂
Mukapsa
Guy's tizimuopa mulungu
Iyiyi mbiri ya manganya kapna mulandu wa manganya?😅... Ndimayembekeza kumva nkhan zilongosokatu kuti ndimudziwe kut ndindan iyeyu
Komatu ya Gladys Phiri yi ndi yoona, koma poti enanu munali ana, basi ziletsani.
Lero ndi vice president
Zakalekale mzanu wapita zilibe ntchito zimenezo ngati ndi umphawi zakuvutani bambo
Manganya uja waipa lero??? Lol umbuli basi a malawi. Nkona amalawi ali osauka. Why didn’t you bring all this bs when he was appointed by Chilima to be his vice president?? Education/civic education is very important.
This voice ikundikaikitsa
Koma guys kung'alula kwa bwanji uku😂
Ndipo izi mukuti titani nazo mmm wasowa chonena iwe
Timakunyadila man kwambiri
Mmmmmh mmmmh!🤔🤣🤣🤣🤣🤣oyamwidwa chokodzera ooo akhare president lero 🤣🤣🤣🤣☠️😷
Best TV
Greatest liar I have ever seen is Bakili Muluzi tv .
Enanu ndi alendo pa Chanel chimenechi ndiye u uth wanuwo musatinyase ife timapanga follow
Lero ndie mapolopangada osusa bakili tv ndie achulukatu lero iiiii,tv iyi simanamatu samatumiza nkhani zopanda umboni uyu
Za ziiii kuti zimveke bwanji. Still ndi vice president wa dziko LA Malawi basi. Muchira koma mochedwa
@RodwellLayford
7 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
Inu ndi osokoneza ndthu palipose kubweretsa negative altitude mxiew
Nsanje a Malawi uyu amangidwe Sizisintha kanthu he is still the VP Dziko likamva kuti litani?
@chitenjepatriq3338
8 күн бұрын
Video ndiya kalekale
Following
Manganya ndi wamdede
Ndangowona kuti akulu awawa amadana ndi manganya
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 koma nkhani zili umu eeeeeh bakili muluzi tv ndi wakulu
Enafe tikamati uyu wa bakili muluzi tv ndi chitsiru mumati tsutsa Nanga zoona akanenene za chokodzela cha munthu pano
Mumafukula nkhan
😂😂😂😂 Ndizakale izi uyu ndiamene bwela nazo lero mobgokumbutsana
Izi ndizakalekale worakwa ndi wotuzayo
Everyone has a dark side of history but we don't need to start digging such as if the woman has chosen to bring it to the public.. Nkhani zanutu pango'nopang'ono zayamba kumamveka ngati zija za m;maboma pa MBC.
Mbili yonyasa anthu a seventhday ndiachisawawa I can tell
Inunso tiuzen mbili yanu ...
Bakili Muluzi channel adayotulutsa video some years back go and check Bakili muluzi platform you may realised he produced this video two to three-years ago l started watch some years ago so don't be upset.
nonse imakubhowan tulukan ndipo musamamvele
Guyz vedio iyi ndi yakale kwambili nde chonde musaluse ayi
😂😂😂😂 chakwera ndi wamisala kusiya nsonda kusiya dausi kusiya uladi Musa
@masterkachingwe7448
8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@EstherZintambira-sq3yy
8 күн бұрын
Aaaah oduka mutu achna uladi kuononga chani
Perekani mbiri yabwinobwino ngati munthu woti mumatiuza nkhani pano. Zinazo ndi zosafunikira
@jumbradoone4164
8 күн бұрын
Ndi mbiri ya Munthu-tu iyi, palibe cholakwika.
@TheresaKuluwemba
8 күн бұрын
Izinso ndizofunika
Nonse amene mukhulupilila izi ndinu opusa
@user-cb5me8wp1k
6 күн бұрын
Iweyo nd opusa cos iz anatulutsa kare kare ndipo ndizoona iwe umangomudziwa manganese lero fuse athu akhala naye
tatiuzani za south africa mavoti aribwanji?
Manganya uhule ankapanga pomwe anali mphawi sono ndi u vice aupedzawo
@CatherineDesire
7 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣akupangabe wachake tsasiya komaso d,zoti angakonze dzinthu ndakaika bola Bon kalindo kkkk
Pamtumbopako galu wa munthu lwe satana ukutipatsa mbili kapena zoyipa za manga nya..
@YoungKhakhizo
8 күн бұрын
Naweso panyero pako garu
Kkkkkkk koma akulu inu bodza simudzasiya
Uyu amangokamba zomwe akuganiza niwabodza
@ancientnkhata1137
6 күн бұрын
Ndipo nchabodza osati masewera .
Nthawi yomwe waipa ?
Utsilu basi a chimanganya Kuyaluks basi A K A 47
Ukufusa kuti titani?
Does this Bakili Muluzi T V have anything good to say in Malawi? Or they only see the wrongs
@MovableSoundSquad
2 күн бұрын
What about you do you have anything good to say?
Koma nde mmakamba zabodza mkazi wamanganya nanga ndiameneyo mm
@TheresaKuluwemba
8 күн бұрын
Mkazi wake ndindani nanga? Ndinuyo kapena???😅
Eish
Akulu mwatani kodi
Nenani zanu tinve
Auzen mn
Ayi zikomo
Zauchitsimluzi izi mukadayankhula mmbuyomo pano mwachedwa mzanuyu mumuvule msamuvule pano ndi presedent basiiiiii wapitaaa!
@GladysMasasa
8 күн бұрын
Tisamatero Anthufe tiziopa mulungu.
@user-nr6po2cp4r
8 күн бұрын
Izi adayakhura kale kumene silero ai iwe nde oduka mawaya sukudziwa kathu
@TheresaKuluwemba
8 күн бұрын
Video ndiyakalekaletu iyi, mwina inuyo bakili muluzi tv simumamutsatayi mmbuyomu, koma ndiyakale kwambiri
kkkkkk koma manga
Mbuzi ya Munthu Amangidwe basi
Zapakathawi 😂😂😂😂
Kkkkkk
😂😂Koma malawi 😂😂😂😂 president etii😂😂😂
Usafooka
Kkkkkkkkk km ukooooo
Kkkkkkkk zamalisechezez
Mmmmmmmmm km abale.
Awa abakili Muluzi tawatulukira kuti ndi aDPP
@HusseinMachemba
6 күн бұрын
Koma akulu muzifufuza kayetu video iyi ndi three years ago
@adzonzicomedy
6 күн бұрын
video iyi ndiyakalekale
@adzonzicomedy
6 күн бұрын
we love bakili muluzi TV
malawians we have to accept that in every person there is a dark side, aliyense ali ndi mbiri.... Bakili muluzi tv has just narrated what happened, but that does not imply kuti the current Manganya is a bad person. kutukwana mkozi ndi mwini wa channel chimenechi, sizingathandize.
@modestamhango611
7 күн бұрын
Zoona
Zaziiiii
Kkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkk koma
Kt zimveke bwa
@Hudhayf
7 күн бұрын
Kaya naonso awa
Uyu ndi bakili muluzi TV wa fake
@shukranhabibuh9928
6 күн бұрын
Ndipo live sakumveka zenizeni
Zakale kale izi lol
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Nonsense
A crook in deed