Mitima yathu ndiyosweka kwambiri ndi infa ya chilima. Palibe amene angavotere nkhope ya chakwera ndi mcp
@ernestphiri29342 күн бұрын
Kutiunikira ndiye mukuyesesa koma pa ground pali zii mpaka pano
@user-xi2jz8ru1w2 күн бұрын
Boss mmm chakwela ndi wakupha
@FridayMpanga2 күн бұрын
Kupweteka kwa mtima ndizomwe akupanga achilima
@YabwataКүн бұрын
Vuto ndiloti amalawi ndi opusa kwambili .. kanakhala ziko lina aa zikana vuta mademo mbwee koma malawi kulilila nyumba vazii uzeleza pela
@user-rl9je6on3iКүн бұрын
Bakili muluzi tv 🔥🔥🔥🔥
@MaminaDelifaКүн бұрын
Please be strong we don't want those pple to hack your page,and we don't want to miss you! We want to know the truth from you, other's of cause They're on our side but school and experience, we're all brethren bt dis banqueters akupanga nkhanza kwa a Malawi,
Ndiwomwewa anatiphelaso Gilbert Pondeponde Bakili Muluzi TV umaziwa
@ibrahimalfred6539Күн бұрын
But why bakili maluzi TV he tuned this video off? That people's we can't comment
@mcdonaldmuyombe43802 күн бұрын
Dzulo mwalankhula nkhani yomweyi mosiyana, lero mwasinthanso. Kodi simutisocheretsa? Anthu omwe mumati akutumidwa ndi boma, Pomwe lero mukuti anthu wo akumenyedwa ndi aboma😂
@jackchabwela5442
2 күн бұрын
Try to understand the issue bro sizikutathauza kut muthu otumidwa ndi chakwera ndekut aliyese wa mcp angasangalale naye no chifukwa Oro mchipanimo athu asiya kucheza zachisisi chifukwa akudziwa kut zionekela ng'amba
@MaxwellNkupira
2 күн бұрын
Muzimvesesa
@AnthonyMhango-e9qКүн бұрын
Ur the best
@user-xx4jb9se3z2 күн бұрын
Mamja mwa bakili tv ndipo musasiye mcp mudapha chilima.chilima adachita kuphedwa chipani cha kupha
@ManblesserPeter2 күн бұрын
Musamasowe bakili muluzi tv
@jackmambo2638Күн бұрын
Preach sir preach ❤
@VincentFrank-y1o2 күн бұрын
We love 🇲🇼 Bakili Muluzi tv
@eddiemafaitijr3952 күн бұрын
Our people are suffering because of greedy leaders. As small as malawi Country is, it should have been a better place for all. History will judge them its sad that people are suffering because of the ignorance of the leadership who are there to serve themselves. May God bless Malawi.
@EstherShaba-fh8ibКүн бұрын
I hope mwayivera kare apule
@HopefulCoralReef-tx4vx2 күн бұрын
Ulemu wanu big God bless you timakunyadilani
@PatrickBondo-ur2pl2 күн бұрын
Amen Tiwonana September pano mwazi
@Uncle_B2652 күн бұрын
Time will come bola kufa kusiyana ndizuzika mu dziko ilii ya chakwera
@KhumboRobo2 күн бұрын
Continue osaopa
@BlessingShabalala-py7fl2 күн бұрын
That's true chakwela mbuzi
@user-bq8gb7tb1l2 күн бұрын
Zooona big keepitup
@user-uk6xv3xe4p2 күн бұрын
Iwey ndi dolo kumalawi kuno kulibe sise yanu yamayankhulidwe
@MisheckAselo2 күн бұрын
Chakwera wakephera uyu galu kwabasi, tionana mu September 2025 munthu opanda chisoni
@aubs43212 күн бұрын
This one is powerful and spot on
@moseskavalo33042 күн бұрын
Malawians must learn to do some research before voting people into power, The case of Pastor Chakwera and Pastor Chapola
Пікірлер: 219
From you we discover all the hidden secrets, keep it up sir, we are proud of you 👏
Bakili muluzi unabwela kudzatitsekula maso❤ we are happy with you mr boss
This is fact video ever and ever God bless and protect bakili muluzi tv
Ukhalise umatha kucheza you're the African icon.
Yoyo Yoyo!!! I like you brother big up ang, alureni basi
This tv palibeso, ulemu wanu Mr bakili muluzi tv❤❤
Umakwana bakili muluzi tv
Uvale zilimbe asakupange hark bro here listening you all time
@davidjames679
7 сағат бұрын
awa ndi machine asanaganize zomupanga hack amakhala iyeyo wapanga kaletu
Bakili TV ulemu wanu brother mumakamba zowona zake wamkulu
Iweyo ndikatundu big umatha, keep it up as a man ndikupatsa daughter big umukwatire❤❤❤❤❤❤😂😂😂
Ngat anapha Muthu wamulungu dzake kulibwanj vice president wake mfit iyi sitikuifunaso mudziko muno
My everything Bakili muluzi tv ❤ watching from Israel
Apite kwa mery bro anaake aja ndiye ofedwa osati chakwera wa kuphayi bakili tv God is with you always
You are truly appreciated keep up the good work. No fear for speaking the truth. May God bless you and keep you safe always .
The best TV in southern Africa.
Chimkaka nkhopeyo ngati chikufuna kusanduka mfiti ya muthu
Mmmmmm abale chilima 😢😢😢😢😢 chakwera chakwera nyini yamako 😢😢😢😢😢
Tiyeninawoni achimwene ❤❤❤
Very good big we are behind you ❤
Always with you big man
My wish ndiyoti MCP ichoke Boma .ife anthu a business sizikuenda ndalama angogwetsa .tikukanika even kugula ma dollars
Imwe muli wakali we love you br
Uyu ku Malawi size kulibeko Bakili Muluzi tv ndikatundu ndipo tisakoreyi guys mademo pa 10 mwezi wammawa azavute koopsa
Ndipo bakili muluzi tv the nomber one
Koma Bakili Muluzi TV ndiwe Shasha Big. More life more Blessings. Let's boot out this useless Chakwera. Mfiti ya munthu iyi kupha Chilima
Izo zokha zoti tikangona tikumaona ngat wangochoka mawa abwera SKC ndye zoona zinazo ndne mwana
This is so sad we will not forget about this 😢😢
Nthank you bakili muluzi tv
Chakwela si munthu passport kulibe ku immigration kuri manyi komaso immigration yikuba mowopsa
Umakwana mr bakili milusi tv
Bakili mukukamba zoona ndithu ndiposo mulungu akupaseni moyo wautali kwambili and chakwela alibe zelu
kuswa kuswa 🔥🔥🔥🔥 osaopa
Mitima yathu ndiyosweka kwambiri ndi infa ya chilima. Palibe amene angavotere nkhope ya chakwera ndi mcp
Kutiunikira ndiye mukuyesesa koma pa ground pali zii mpaka pano
Boss mmm chakwela ndi wakupha
Kupweteka kwa mtima ndizomwe akupanga achilima
Vuto ndiloti amalawi ndi opusa kwambili .. kanakhala ziko lina aa zikana vuta mademo mbwee koma malawi kulilila nyumba vazii uzeleza pela
Bakili muluzi tv 🔥🔥🔥🔥
Please be strong we don't want those pple to hack your page,and we don't want to miss you! We want to know the truth from you, other's of cause They're on our side but school and experience, we're all brethren bt dis banqueters akupanga nkhanza kwa a Malawi,
1983 MCP inapha agadama ,amatenje, komaso achiwanga kugwiritsa ntchito ngozi ya galimoto
Kkkk bakili tv ndiwe dolo kutvetsa kukoma
Home of history bakili muluzi tv😊😊😊😊😊😊
Ndiwomwewa anatiphelaso Gilbert Pondeponde Bakili Muluzi TV umaziwa
But why bakili maluzi TV he tuned this video off? That people's we can't comment
Dzulo mwalankhula nkhani yomweyi mosiyana, lero mwasinthanso. Kodi simutisocheretsa? Anthu omwe mumati akutumidwa ndi boma, Pomwe lero mukuti anthu wo akumenyedwa ndi aboma😂
@jackchabwela5442
2 күн бұрын
Try to understand the issue bro sizikutathauza kut muthu otumidwa ndi chakwera ndekut aliyese wa mcp angasangalale naye no chifukwa Oro mchipanimo athu asiya kucheza zachisisi chifukwa akudziwa kut zionekela ng'amba
@MaxwellNkupira
2 күн бұрын
Muzimvesesa
Ur the best
Mamja mwa bakili tv ndipo musasiye mcp mudapha chilima.chilima adachita kuphedwa chipani cha kupha
Musamasowe bakili muluzi tv
Preach sir preach ❤
We love 🇲🇼 Bakili Muluzi tv
Our people are suffering because of greedy leaders. As small as malawi Country is, it should have been a better place for all. History will judge them its sad that people are suffering because of the ignorance of the leadership who are there to serve themselves. May God bless Malawi.
I hope mwayivera kare apule
Ulemu wanu big God bless you timakunyadilani
Amen Tiwonana September pano mwazi
Time will come bola kufa kusiyana ndizuzika mu dziko ilii ya chakwera
Continue osaopa
That's true chakwela mbuzi
Zooona big keepitup
Iwey ndi dolo kumalawi kuno kulibe sise yanu yamayankhulidwe
Chakwera wakephera uyu galu kwabasi, tionana mu September 2025 munthu opanda chisoni
This one is powerful and spot on
Malawians must learn to do some research before voting people into power, The case of Pastor Chakwera and Pastor Chapola
Panyapawo achakwera alibe manyazi anapha chilima chifukwa chansanje Kodi awa analidi abusa awa achakwera akumwa magazi anthu
Koma awawa atopesadi bwanji apa ndiza Kenya Kenya basi ah
Mumaima pa chilungamo
Iweyo unabwera ase 😂😂
Ayi Chakwera si butsa ndamuyankhira mafutso enawo
Inu ndi mooooreeee bingu adatisiya Ali pa mpando izo sindinazionepo zomakapepesazi
Umakwana iweyo more fire
Munasowatu ankolo , ndimaona ngati akupasan bazi😂
Big up biggy waife
Mazifumu akumalawikuno ndizitsiru bwanji, zikapita kukapepetsa Chakwera bwanji chonsecho ndiyemwe anapha, nanga kodi Chilima alibeyi azibale ake ofuna kupepetsedwa? Chakwera ndi Chilima pali ubale wanji kuti azipita kumakati tikuzapepetsa then chi mfiti cho chika Chakweracho kumawapatsa misonkho yathu? Amalawi tiyeni tidzuke pls, mademo apa 10 tisautse koopsa kuzakaotchanso state house komanso parliament. Ufulu wathu palibe yemwe angatigulire nditokha amene tikudzudzikafe
@KimJime-d9k
2 күн бұрын
Akufunako nchere agaru
@user-uc1pd1tc2x
2 күн бұрын
@@KimJime-d9k Ndipo koopsa Mwazi wa Chilima ayamba kuupangira business mmmm
Evil 😈 president ever Malawi hv
Number one bakili tv
Lero kwayakatu Moto big
zoona kwambiri Boss we don't believe Kuti Anapitadi penapake timaonadi ngati kuti mwina wangochokapo 😭😭😭
Atate Mwana ndi Mzimu Oyera
Chakwera mbuzi mcp mbuzi
@JackMvura-ik2td
2 күн бұрын
@@Edson-sj8vn pitala gwape DPP a gwape onse ndanena ineyo mosaopa
Lero president wathu wachilungamo wakwiya2 eee😂😂
Mmakwana big mudzi bwera bwera
Dpp machinery at its best
Have missed bakili muluzi tv,
Chaka cha mawa kwatalika bwanji
Very good
Iwe ndiwe kutyeka Bakili tv
Zomvesa chisoni kwambiri koma Mulungu azaweluza
2025 zisinthe mbuzi iyi ichoke ndi fiti iyi yiwoneni magalasi angosala makatani
And the truth will be revealed sooner or later continue resting SKC 😔 😢 😢 😢
Amen
AMagwilisila tchito chikangawa
Chakwela mmmmmmmmh (mulungu) azakulanga
Koma yah❤
That's true mr putin is ver rich person ok earth 🌎
Zikhale ng'oma kusukulu sanapiteko udutu ndiwumene anamusakhila 😂😂 osati sukulu anapita acadamy yiti atiwuze
Zikhale n'goma wamvela kale Namachende iwe
Chakwera is not a pastor period
Ng'alulan bwana😂😂
Chakwela ayambepo kuyimba nyimbo ya 371
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
2 күн бұрын
Chakwera must go we're tired with him
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
2 күн бұрын
Advice should go to the police officers who take part for nonsense president Chakwera one day the law of arm will visit you 2025 is coming
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
2 күн бұрын
I crying Dr. Saulos Klaus Chilima why chilima killed RIP CHILIMA
Umati imilila amalawi
Ndi jolly bro uyuu