Waxy Kay kufotokoza mokupsya mtima chifukwa chimene wasiila Kuimba komanso akuti musamamujaile

Пікірлер: 78

  • @chifundonkhoma3642
    @chifundonkhoma3642 Жыл бұрын

    Organise yourself and move on, you started the career when you had no any fan.... They started loving you after you introduced your music career to them, so sometimes it's good to be patient rather than responding to each and every thing from your fans

  • @nevermindmatemba9310
    @nevermindmatemba9310 Жыл бұрын

    Amfana kuimba kulingati kugwa mchikondi Pena ukhumudwitsidwe Pena zibebe that's the lyf so there's no need kt ukakhumudwitse Fanz yonse chfkw cha anthu anakuthokera after kudya chambao mayaz..Tie nazon ife tikufunabe nyimbo zako Kod siwe uja unkati #pena zimaenda Pena kugwera kupompho...... ?.

  • @fridayphale4082
    @fridayphale4082 Жыл бұрын

    Bruh don't mind them , you know people likes to talk if you do a good thing they will talk when you do a bad thing they always talk so let them talk bruh! And please don't drop your career because of anyone that's what you was born for so please bring it to us , don't allow people to send you to your earlier grave because of their problems. Once again don't mind them who ever is talking rubbish about you if they want akakolope nyanja mpaka ikaume # your my hubby's favorite 🔥🔥🔥❤️

  • @gracemalisawo1068
    @gracemalisawo1068 Жыл бұрын

    Waxy tilipo ma true fan Ako pliz don't let them win continue with your career

  • @user-ri8dw1ob7d
    @user-ri8dw1ob7dАй бұрын

    Muchatijoina kumbanje uku

  • @esthermalekezo
    @esthermalekezo Жыл бұрын

    Iam on ur side

  • @PreciousMaonga
    @PreciousMaongaАй бұрын

    Hi waxy I just heard your warrys And I am sorry about what your funs have done to heart your feeling sorry about that

  • @dkayoza7434
    @dkayoza7434 Жыл бұрын

    Sizoti ufetu iwe mene ukuyakhuliramo......... Mapeto ake tribute titayimbe ndfeyo 😂😂😂😂😂

  • @ronzotv8728
    @ronzotv8728 Жыл бұрын

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @vukanifracksonchinkonde7324
    @vukanifracksonchinkonde7324 Жыл бұрын

    Downfall starts with pride......be humble aise

  • @Amoslibuda3rdson
    @Amoslibuda3rdson6 ай бұрын

    Kkkkkkkkk athu akudelela luso lako osafoka waxy k

  • @upendomwambije5807
    @upendomwambije5807 Жыл бұрын

    Mmmm bwanjis

  • @nyadumaduh1355
    @nyadumaduh1355 Жыл бұрын

    Asiyeni mn mupitilize kuimbako mumatha munthu ndkomvuta mn amamukonda munthu akavaya nde asiyeni amenewo

  • @user-ug8ey3pl8z
    @user-ug8ey3pl8z3 ай бұрын

    Chamba

  • @BritonPhiri
    @BritonPhiri3 ай бұрын

    Utengane ndi phyzoo ukamasiya kuyimbako ife tikuvela ndikuvina ma piano pano aise :

  • @user-gc4hq5xm1f
    @user-gc4hq5xm1f11 ай бұрын

    Kawalala samulekela munda,woi

  • @niggaluxyller581
    @niggaluxyller581 Жыл бұрын

    Don't worry bro let dem talk but you continue doing well

  • @petermakawa3416
    @petermakawa3416 Жыл бұрын

    Mwayankhula mozipopatu Kwambiri.... anyway sindinapangeko download nyimbo yako chiyambire

  • @user-lj7lm6ly7z

    @user-lj7lm6ly7z

    6 күн бұрын

    Olo ine samandiwaza olo pang,ono

  • @maxwellmustaffaalickalick1745
    @maxwellmustaffaalickalick1745 Жыл бұрын

    Munthu ndiwovuta man asiye

  • @jacobmpochela8698
    @jacobmpochela8698 Жыл бұрын

    Nsena wa kwanthu alibe zibwana 😅😅😅

  • @user-gc4hq5xm1f
    @user-gc4hq5xm1f11 ай бұрын

    Kawalala samulekela munda,woi❤❤❤❤❤ 8:27

  • @user-yi6xo9kh2r
    @user-yi6xo9kh2r7 күн бұрын

    😢😢😢😢

  • @amazingbrave6938
    @amazingbrave6938 Жыл бұрын

    Iwe ndimwanadi eti, nde achina skeffa chimoto aja bwezi atasiya kalekale kuyimbatu.. Grow up aisee

  • @shukranalex8580
    @shukranalex8580 Жыл бұрын

    Real talk bra 🙌

  • @kingbutao2023

    @kingbutao2023

    Жыл бұрын

    This is childish grow up.bro, you don't need to act based on people's opinions. Zitaye move on with your music career bro. Amenewo ndiye anthuwo. Apapa ukupanga zomwe anthu akufuna Kaya, ndizomwe anthu akufuna kuti ukwiye ubwelere mmbuyo usawagonjere zitaye.

  • @franciskameko2586

    @franciskameko2586

    Жыл бұрын

    Aaaah ndikape uyuu! Panopa anatha ma plan &nso Malawi amadana nd mafana odzipopa chonchi aaaah! Kukhala mfana woyamba ku blower nde uzitikumba??? Humble yoslf bro pamsana pako, kupanda management ko mkomwe kunakubwezeretsa m'mbuyo coz ulibe yemwe amakupanga control nde chrichonse chomwe umapanga umangodzifila ngat nzolondola... Uzitolele koma

  • @niggazmbirah145
    @niggazmbirah145 Жыл бұрын

    Katelele ching'oma ,,, Thomas chibade ,,,, Moses makawa anatchuka bfo iweyo ,,,, tachokapa iwe azakusowa ndani nyimbo zake ziti ,,, album yakoyo uzimvera kuchipinda kwako palibe uzimutchula mafanz ako ,,, zausilu basi

  • @user-jx5kb8pt1m

    @user-jx5kb8pt1m

    3 ай бұрын

    Iwe nd kapa udapangapo chani iwe amene amakudziwa ndani wax timafila ife iwe udapangapo chiyani uchedwa wax nd athu iwe uzipanga zako muthu nd wovuta muthu ali ngat galu uyu aukunyuza nd galu

  • @user-gc4hq5xm1f
    @user-gc4hq5xm1f11 ай бұрын

    Move on waxy,lets them tolk,

  • @ChristopherBanda-sr9hc
    @ChristopherBanda-sr9hc8 ай бұрын

    Kkkkk

  • @phiniasstanford430
    @phiniasstanford430 Жыл бұрын

    Kkkkkkk Waxy 🤣😂

  • @cassandramacjessie8913
    @cassandramacjessie8913 Жыл бұрын

    😂😂

  • @saidiomary7397
    @saidiomary7397 Жыл бұрын

    Kodi vuto ndi chani man😭😭😭

  • @HAWAHANDRWE
    @HAWAHANDRWE Жыл бұрын

    Mmmm wakuva wava osava ndiwosava bas guys vuto ndichan ineso ndakhumudwa kwambili chifukwa waxy Kay ndimwana sanafike posiya kuimba anthu obhowa inu tayimbani inuyo tivere inu kumangoziwa kuyakhula ngat mumantha kaimbidwe ka nyimbo 😶😶

  • @t-boymw3650

    @t-boymw3650

    Жыл бұрын

    Perfect word

  • @cassandramacjessie8913
    @cassandramacjessie8913 Жыл бұрын

    Dramatic 😂💔

  • @stevinmuhone877
    @stevinmuhone877 Жыл бұрын

    Siya ndibwino mwina ndimwayi wako dziko pamene lafikapa mmmmmmmm sizili bwino

  • @isaacjali8606
    @isaacjali8606 Жыл бұрын

    tigaile kowawa wadyako axe

  • @malawianson7223
    @malawianson7223 Жыл бұрын

    Osawatengera man

  • @robertgbanda3825
    @robertgbanda3825 Жыл бұрын

    Ine ndee ndimamvera Gospel zanuzo za my foot sinpanga nawo

  • @user-jx5kb8pt1m

    @user-jx5kb8pt1m

    3 ай бұрын

    Makhal apa kulibana nd azanu muchedwa nd kulimban nd azanu musiyeni waxy nd luso lake inu ndni ali waluso ngt waxy

  • @chatonoel4140
    @chatonoel4140 Жыл бұрын

    Mbuzi

  • @wilsongabla6340
    @wilsongabla6340 Жыл бұрын

    Siya ase uona ngati tidandaula, mo over ulibeso style yabho Chizmo anabwera moopsa osati iweyo usazipope abulm yakoyo uzivera wekha basi

  • @alinafesalima5597

    @alinafesalima5597

    Жыл бұрын

    Kkkkkkkk tamuuze kape ameneyu

  • @ministercalebsambo
    @ministercalebsambo Жыл бұрын

    Wonderful Kapenga 😢

  • @preciousnyadan8973
    @preciousnyadan8973 Жыл бұрын

    Kuyakhula ngati tikapanda kumvera Album yo sitakadya nsimatu😅😅😅🤣🤣🤣

  • @alinafesalima5597

    @alinafesalima5597

    Жыл бұрын

    Ndipo inu olo asatuluse Album yo zili ndi ntchito,matama thoo ngatinso unatha kuimba apa,ukoo kagwere

  • @user-dn9kb5ie1n
    @user-dn9kb5ie1n6 ай бұрын

    Tulutsani bg MN makwanila

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Жыл бұрын

    Ine olo awa atasiya kuimbako sasanvalatsa nkomwe zongogweramo basi asiileni anthu odziwa kuimbawo matama thoo

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Жыл бұрын

    Kkkkkkk za ziiiii

  • @edinamithi3899
    @edinamithi3899 Жыл бұрын

    Mwana oyambirila anali chatama osati iwe vuto lake uanali pikinini nthawi yomwe ankaimba chatama Kusuta kumaononga moyo apa ndiye zasintha ndi kusuta kumaononga Tsogolo 🤣😂🤣😂 wapanga apazi ndiye ndi za Ziiii iiiiiiii

  • @NelsonTawakali
    @NelsonTawakali Жыл бұрын

    Vuto mmamvera zonena za anthu ena. Focus on what you do adha. Zinazo zikuchedwetsani. Haaaa

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 Жыл бұрын

    Wamisala iwe olo utasiya kuyimba ndiye angakudandawule ndani ?

  • @hamdanmasuku4800

    @hamdanmasuku4800

    Жыл бұрын

    Agogo ako

  • @ernestchiwini2673
    @ernestchiwini2673 Жыл бұрын

    Chatama anali star

  • @tituskhuminer6539
    @tituskhuminer6539 Жыл бұрын

    Kamwana iwe ndiwezoba wava

  • @memorymailosi3676
    @memorymailosi3676 Жыл бұрын

    Uzatulusa anthu akasiya kukusata

  • @francismbewe153
    @francismbewe153 Жыл бұрын

    Weed

  • @fortunemwanza8011
    @fortunemwanza8011 Жыл бұрын

    Aise this is your career ndiye you can't leave your career because of fanz ndiye ngati wapeza zochita China kapena ngati uli ndi chochita China u can leave it but this is not the way to handle your issue unless if its dramatic 😂

  • @macfordmuwa1754
    @macfordmuwa1754 Жыл бұрын

    Iwepati

  • @danieljulius2522
    @danieljulius2522 Жыл бұрын

    Chavuta ndi chuyan man ?

  • @andrewpaul1315
    @andrewpaul1315 Жыл бұрын

    nosense zamowa basi,umayankhula izi utakhuta m'tonjani iwe

  • @gclimbanichiutira3462
    @gclimbanichiutira3462 Жыл бұрын

    amalawi kuyakhula kwambili mmmmm

  • @samsonrasiyon1030

    @samsonrasiyon1030

    Жыл бұрын

    Kuganiza mopepela munthu umalemekeza pamene ukupeza chomwe ukupeza komaso your age you can't compare with matafale adali kamuna ukasiya kuimba usawuka wekha

  • @shadrecknamvula4381
    @shadrecknamvula4381 Жыл бұрын

    Uthenga wachifanafana ee

  • @bandafatima5330

    @bandafatima5330

    Жыл бұрын

    Ungosiyadi akupha ayamba kale kukupezela zifukwa

  • @gluesaimala7448
    @gluesaimala7448 Жыл бұрын

    You are like a president so you need to calm down, osayankha zimenezo munthu ndiovuta aise just keep your mouth shut.

  • @mr_puwa
    @mr_puwa Жыл бұрын

    Artist yemwe akuyankhula osaganiza Yr fanbaz sunga iyankhe ngati zisilu ayi, mafanzi amayankhula momwe akufunira , nanga utani olo utasiyakuyi k Barton alipo ayimba Henry Czar alipo ayimba Usazapangeso mistake ngati imeneyo, asiye ma followers ako ayankule super star azikala ngati sakuziwa udindowake Achina #gwamba anthu ama munena koma sizimakuza ayi alipee akupanga zake, bwanji iweyo uziyankhula zopusazakozo Tosefe ndima Artist koma usamakale ndipuma Lemekeza fanz yakoyo yakufikisa patali kale osainyozaso ayi Fanz ikakutuluka ndimbola kwabasi ngati sukuyifuna Delete yr page facebook Delete all accounts zako za social media Uone zoyera

  • @ali123akaraji5
    @ali123akaraji5 Жыл бұрын

    Afana 😒😒

  • @jenojames3813
    @jenojames3813 Жыл бұрын

    chamba si fodya eti, wayankhula za nonsense boy, siyani sitiganiza zaiwe boy.

  • @alexmorgan8138

    @alexmorgan8138

    Жыл бұрын

    Za ziiii siya watopa iweeee hiyaaaaaa

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 Жыл бұрын

    Nonsense ma celeb amanthongo, osasamba

  • @hucklyrajabu7137

    @hucklyrajabu7137

    Жыл бұрын

    Ndipo inu or atati asiye kuimba anganyenyeke ndani malawi muli oimba ambiri mbiri osafana ndi iyeyu oimba ngati achi skeffa chimoto that juming machine atati asiye kuimba ndingadandaule osakhala kape aneneyu osamunyengelera guys khala ngati iyeyu akamaimba mapindura ndiinuyo mesa amapindura yes nonsense

  • @chifundo6911
    @chifundo6911 Жыл бұрын

    🤣🤣🤣🤣🍆zako izo iwe olo usatuluse ase

  • @hucklyrajabu7137

    @hucklyrajabu7137

    Жыл бұрын

    Kuli anyamata ambiri mbiri oimba achana JJ c ndi ena otero sikut iyeyu akasiya kuimba ndiye music imfa mmmmm