Ulaliki wa Father Ntharika muli zinthu umu aboma apuma nawo befu ndithu kuchita kubaya

Пікірлер: 129

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif95566 күн бұрын

    Mau ogwira moyo muchowona MTSRIP 🌹 ndipoo imfa iyi yatikhudza tonse Malawi,and SKC his words shall always echoi in our hearts,ambuye athangate ma banja anzathu amene abalewa atisiya, ameeen

  • @user-pe2tu1ip3v

    @user-pe2tu1ip3v

    6 күн бұрын

    Hi my dear can I talk with you please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want you to be my girlfriend that all please dear I want

  • @OwamThoko
    @OwamThoko6 күн бұрын

    Thanx for your strong message God bless n protect you from chakwela the killer amen

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa6 күн бұрын

    Amen GOD bless you abundantly keep it up

  • @johnchikhanda3551
    @johnchikhanda35513 күн бұрын

    Very powerfull massage dzivere muntolo...wanzeru wanva apa

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z6 күн бұрын

    AMEN AMEN powerful ndipo zoonadi ndipo umunthu mulibemo apapa ulipo ndi ufiti.akatolika mmmhhh pempherani mpaka titadziwa ZA imfa imeneyo kkķkk akugawana nsalu.chakangazitsa ndi chani .mau mau mau.mcp yatha basi

  • @augustMag
    @augustMag6 күн бұрын

    Thank you father Elizeyo Nthalika you are rise us you give us powerful words Amen dziko lokoma lija la Malawi lafika powawa popweteka Ambuye atimenyere nkhondoyi

  • @davieabel5631
    @davieabel56314 күн бұрын

    Powerful message ndipo samve kt mwatola simukuchedwa paja

  • @ElphinaChirwa-qk3cy
    @ElphinaChirwa-qk3cy4 күн бұрын

    Eeeee Komatu powerful msg mmmmm ambuye titonthozeni Ife ana anu osiidwa

  • @flourencejamu6455
    @flourencejamu64556 күн бұрын

    Amen Mzimu wa mtumiki wanu Dr.Saulos Klaus Chilima pamodzi ndi mizimu ya wanthu omwe anafa nawo pangoziyi Mizimu yawo iwuse mumtendere wosatha

  • @GospelSoldiers-sr7np

    @GospelSoldiers-sr7np

    6 күн бұрын

    Amen

  • @eunicesaiti

    @eunicesaiti

    6 күн бұрын

    Amen 👏

  • @NatashaBema

    @NatashaBema

    5 күн бұрын

    Amen abusa ulaliki wabwino

  • @GroliaKafumbwa
    @GroliaKafumbwa4 күн бұрын

    Amen my priest Poweful words

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w6 күн бұрын

    Amen mau abale inu imfa yomvesa chisoni ngati imeneyi..umunthu wasowadi

  • @EstherAmadu-md3et
    @EstherAmadu-md3et6 күн бұрын

    Powerful teaching words of God amen and amen

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm5 күн бұрын

    Powerful and amen, uthenga wabwno ambuye akudalisen brother elizeyo ntharika😢😢😢😢

  • @francisntonya171
    @francisntonya1716 күн бұрын

    Amen, man of God,,,,, but we can't forget it, mmmmmm lord help us

  • @PatrickMaluwaphiri
    @PatrickMaluwaphiri6 күн бұрын

    Amen, Chilungamo chiyende ngati madzi.

  • @paulinekayuni1621
    @paulinekayuni16214 күн бұрын

    Zoona ndithu malamulo ngati amenewa siabwino malamulo ena ose amasinthidwa ili osasintha bwanji. 21 days of mourning siikumveka olo pang'ono. We need strong preachers like these.

  • @KingsleeKandiadoh
    @KingsleeKandiadoh5 күн бұрын

    Ambuye akutetezeleni father, chifukwa nkutheka kuti uthenga uwu ukubweletselani mavuto. Ambuye samalilani mzimu wa SKC uziusa mu mtendele

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon6 күн бұрын

    Amen koma ife sitiyiwalayi akunama

  • @PeterThomas-lw3io
    @PeterThomas-lw3io6 күн бұрын

    Paster mwalaluka bwino Komano mukumbukiretso kuti Malemu Bingu atamwarila maliro alinyumba Madam Joyce Banda ndiamene adalumbiritsidwa u president nde sizachilendo mukumbukile Ichi😢😅

  • @MillyKachepa
    @MillyKachepa6 күн бұрын

    Amen fr ... ndpo kuipa mtima chipani cha mcp aaaa malawi tiyeni tidzuke anthuwa aonjeza tikhala chete mpaka liti ... Ambuye tithandizeni😢

  • @GroliaKafumbwa

    @GroliaKafumbwa

    4 күн бұрын

    Ulaliki ndi chipani osaphatikiza apa .imvani mau Amulungu ndikuwangwiritsa ntchito moyenera Mateyu 26 :35 ndi mpingo anthu musawatape mkamwa

  • @eliasnyilongo4865
    @eliasnyilongo48655 күн бұрын

    Father muntharika mulungu akudariseni kaya mudari ku muthawila parichi munandi phuzisapo pa mthawila God bless you

  • @eliasnyilongo4865

    @eliasnyilongo4865

    5 күн бұрын

    God bless

  • @user-lb6ek3ee6d
    @user-lb6ek3ee6d6 күн бұрын

    Thank you so much for your message Amen man of God for prenching and directly to the point

  • @annembepula
    @annembepula4 күн бұрын

    Amen zowona zake dzinvele Ntolo

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda87115 күн бұрын

    Amen uthenga wamveka wakwiya ndiye ochita ntchimolo

  • @user-ne7rn4ki3c
    @user-ne7rn4ki3c6 күн бұрын

    Koma iwe Chakwela unalidi m'busa kumaphwanya malamulo amulungu ndi kumasunga malamulo adziko AAA! Ndichifukwa unalola kusiya moyo osatha ndikuyanja moyo wadziko lapasi imene uli wakutha abusa a Chakwela its not too late lapani tsiku ili lomwe wakumana nalo chilima lisanakupezeni khalani ngati mwana uja akafuna gawo lachuma chamakolo Ake ndikukadya kenako amabwelela kwa makolo Ake ndikukapepesa.mulungu ndiwabwino adzakukhululukilani

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y6 күн бұрын

    Amen koma Chakwela watikwana u mast go satana

  • @terezazakeyo2285
    @terezazakeyo22855 күн бұрын

    Thank you father for the revelation 😊

  • @user-yc3ik9dq3x
    @user-yc3ik9dq3x6 күн бұрын

    Zoona zokhazokha! May their souls rest in eternal peace 🙏🏽

  • @charlesmbewe4001
    @charlesmbewe40014 күн бұрын

    Oh! God , father Nthalika my God keep blessing you.

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati31666 күн бұрын

    Ambuye akudalitseni Mtumiki mmmm akudziwapo kanthu kufuna kwao kuchitidwe koma Mwazi wa Chilima udzalakhura ndipo udakali okwiya 😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @christophergibson72
    @christophergibson725 күн бұрын

    I'm a catholic member koma mchifukwa chake amtinena kuti mpingo wathu umalowelela zandale

  • @robertnkuliza5718
    @robertnkuliza57186 күн бұрын

    Zoonadi Akuziwa ndi Yehova

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd6 күн бұрын

    Ameeeen !!!!❤❤❤❤ i hear you man of God....

  • @AdamLano-sj1gv
    @AdamLano-sj1gv6 күн бұрын

    Amen amen ause mu mtendere Dr skc ndi ena onse

  • @user-zl9eq8jw1q
    @user-zl9eq8jw1qКүн бұрын

    Amen and amen

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera72716 күн бұрын

    Powerful massage ❤.

  • @user-ft9dr6dr3k
    @user-ft9dr6dr3k4 күн бұрын

    Powerfull...

  • @user-ym8zj1zl1e
    @user-ym8zj1zl1e5 күн бұрын

    Father mukunena zoona. Mulungu apitilize kuikiza zinthu pa inu.

  • @AwaliBlack
    @AwaliBlack6 күн бұрын

    Ulaliki wabwino kwambili emen abusa

  • @NearBanda
    @NearBanda6 күн бұрын

    Amen imfa yimeney yinapweka aliyense

  • @KabiluAnthoni
    @KabiluAnthoni2 күн бұрын

    Mau aphavu. RIP SKC

  • @AvrelChirwa-ho9wf
    @AvrelChirwa-ho9wf6 күн бұрын

    Very powerful message

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole6 күн бұрын

    Uthenga olamitsa olasa mtima amen father

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk4 күн бұрын

    Powerful message

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of6 күн бұрын

    Malamulo ndichikhalidwe ndizosiyana paja inu ndalomwe ndiye sitikudabwa ai

  • @user-il8cn7ko9m
    @user-il8cn7ko9m5 күн бұрын

    Amen and amen 🙏

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon34296 күн бұрын

    Amen powerful words

  • @FrankMulela-qt1wi
    @FrankMulela-qt1wi6 күн бұрын

    Katundu uyu aaaa amen amen galu wamkota sakanda Popanda nyama

  • @RosemaryMagwira
    @RosemaryMagwira6 күн бұрын

    Let Love Lead Amen

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o6 күн бұрын

    When you shed innocent blood this is what happens

  • @PeterSonga-ji8nf
    @PeterSonga-ji8nf4 күн бұрын

    Amen

  • @TapiwaMwanjah
    @TapiwaMwanjah6 күн бұрын

    Amen very powerful

  • @JohnFrank-cg1yh
    @JohnFrank-cg1yh6 күн бұрын

    That's true, amen

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma6 күн бұрын

    Amen father, ineso ndinali ozaza ndimafuso kuti zamtundu wanji maliro week sinathe ife misonzi ili mmaso ena akulumbila ndikumavina zoona

  • @isaacchirwa9518

    @isaacchirwa9518

    6 күн бұрын

    Mvuto ndimalamulo a dziko lathu, akanaika atleast one month koma analemba kuti within 7 days, nde inu mkubulema ndani? President, vice president kapena malamulo?

  • @isaacchirwa9518

    @isaacchirwa9518

    6 күн бұрын

    Mvuto ndimalamulo a dziko lathu, akanaika atleast one month koma analemba kuti within 7 days, nde inu mkubulema ndani? President, vice president kapena malamulo?

  • @joicemumba3608
    @joicemumba36084 күн бұрын

    Amen koma imfa iyi 😢😢😢😢

  • @davidkayangemakala7957
    @davidkayangemakala79576 күн бұрын

    God is speaking with Malawi

  • @user-pf5hu2pd2b
    @user-pf5hu2pd2b6 күн бұрын

    Amen 🙏🙏 God bless you.

  • @ruthsimwawa1612
    @ruthsimwawa16124 күн бұрын

    Amen 🙏

  • @RhodneyBwa3
    @RhodneyBwa36 күн бұрын

    Amen and amen pastor.

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti6 күн бұрын

    Amen 👏

  • @OssmanAbubaker-xu7ql
    @OssmanAbubaker-xu7ql6 күн бұрын

    These is true something it's wrong in the city of Malawi

  • @user-wp9js5vu6s
    @user-wp9js5vu6s6 күн бұрын

    Powerful msg

  • @GloryShera
    @GloryShera6 күн бұрын

    Mwayowoya asembe wali namakutu wapulike

  • @eliasnyilongo4865

    @eliasnyilongo4865

    5 күн бұрын

    Hi

  • @MemoryChiwanga
    @MemoryChiwanga6 күн бұрын

    Amen 🙏 my father

  • @user-lb5gt4uv3s
    @user-lb5gt4uv3s6 күн бұрын

    Pajatu mcp akumamanga anthuwa akalankhula mumangesotu uyu ndi uchisiru wanuwo

  • @user-mm9ox2pz7p
    @user-mm9ox2pz7p6 күн бұрын

    Powerful words

  • @user-hc6sr9eu4k
    @user-hc6sr9eu4k6 күн бұрын

    Uthenga wambuye amen

  • @user-sy3fz5nz3v
    @user-sy3fz5nz3v6 күн бұрын

    Amen Father E.

  • @ReginaNyilenda-ug1lf
    @ReginaNyilenda-ug1lf6 күн бұрын

    That is true...ameeen

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman22506 күн бұрын

    Ameeeeen abusa

  • @user-sm6pr9cg2q
    @user-sm6pr9cg2q6 күн бұрын

    God is in control

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa6 күн бұрын

    Yes Mulungu wayenda mulaliki uwu

  • @user-lb6ek3ee6d
    @user-lb6ek3ee6d6 күн бұрын

    Something is loten in Chakwela's and his stupite part

  • @KnowledgecGodwin-xo4pw
    @KnowledgecGodwin-xo4pw6 күн бұрын

    Amen munthu wamulengi

  • @HappyAutumnTrees-cd9ye
    @HappyAutumnTrees-cd9ye6 күн бұрын

    Amen brother,

  • @coollife-is7ir
    @coollife-is7ir6 күн бұрын

    Akutitu masiku 40 ohoooo

  • @user-xx4jb9se3z

    @user-xx4jb9se3z

    6 күн бұрын

    Mau awawa eshhhh week yomweyo ayambapo kugawana zinthu mmmmhhhhh AMEN muli uthenga tu umu ineyo ndinaona kut mzimu wa chilima suusa mpaka zoonadi zitadziwika soon

  • @user-xu9rh1lm8o
    @user-xu9rh1lm8o6 күн бұрын

    Amen 🙏 🙏 😢😢😢

  • @GraciousGIbbu
    @GraciousGIbbu6 күн бұрын

    Ati ndi malamulo angati dzuwa liri nde amene mwakanika kuwasunga

  • @PephoMungomo
    @PephoMungomo6 күн бұрын

    Anagawanadi zovala zake ndipo Malaya ake anawachita mayele

  • @deborahngwira724
    @deborahngwira7246 күн бұрын

    Kodi za novena simunakambilanebe? Inetu zundiwawa nsanameyi. I want to see something. 😢

  • @HlupekileMazunda
    @HlupekileMazunda6 күн бұрын

    Ine simmene ntima unandiwawila dzulo mpaka ndinazimitsa tv nkupita ku church ntima ukundiwawa ndinapephela pephelo lowawidwa ntima

  • @PaulMwachande
    @PaulMwachande6 күн бұрын

    Mwalalika zonveka wakunva wanva bolaso asakumangeni anthuwa ndioipa bambo

  • @DicksonMeleka
    @DicksonMeleka6 күн бұрын

    Amen ❤

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI6 күн бұрын

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zache

  • @SteveChirwa-ne9nt
    @SteveChirwa-ne9nt6 күн бұрын

    Amen !!!!!

  • @user-ke5gk8zh1o
    @user-ke5gk8zh1o6 күн бұрын

    Amen.

  • @nessiemfunie
    @nessiemfunie6 күн бұрын

    🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @JoshuaJumbo-mp3ze
    @JoshuaJumbo-mp3ze6 күн бұрын

    Ndi zoona amen abusa

  • @user-qb2lt6qj1p
    @user-qb2lt6qj1p6 күн бұрын

    Amen ntumik wamulungu

  • @staffordchibambo6439
    @staffordchibambo64396 күн бұрын

    😭😭💯 amen and amen

  • @SemuKachoma-i7o
    @SemuKachoma-i7o6 күн бұрын

    My father.

  • @user-hi2rh8ks3r
    @user-hi2rh8ks3r6 күн бұрын

    Ulaliki mbambande

  • @DesmondOzuzu
    @DesmondOzuzu6 күн бұрын

    😢😢😢😢

  • @user-qe2lv3hs8q
    @user-qe2lv3hs8q6 күн бұрын

    ulaliki wazifukwa

  • @TroubleKatsala-jp2li
    @TroubleKatsala-jp2li6 күн бұрын

    Zovuta

  • @OssmanAbubaker-xu7ql
    @OssmanAbubaker-xu7ql6 күн бұрын

    Chilungamo

  • @user-yk5xv4dt7v
    @user-yk5xv4dt7v6 күн бұрын

    Zkm brather

  • @anusahjenala1063
    @anusahjenala10636 күн бұрын

    Zoonadi

  • @prayer-room35
    @prayer-room356 күн бұрын

    Ine sindikuonapo nkhani apa ...oweruza ndi Mulungu ndipo kuweruza kwathu ndikopanda pake , koma chiweruzo cha Mulungu ndicho chokwanira , munthu ndani kuti afufuze za imfa ya munthu kuposera omulenga munthuyo! We're all going to die and wait for judgement, ...! Nthawi yatha iyi kukokana kokana sizipindula kanthu! Ulaliki ogawanitsa Amalawi uwu ...tiyeni tiyankhule zomangilirana monga Ambuye wathu anatimangilira ndi Atate wake! Kodi Mulungu atayamba kutifufuza njira zathu lero ndani amene angapambane pamaso pake!

  • @user-lp8wj3vq4x

    @user-lp8wj3vq4x

    6 күн бұрын

    Ndangokuina kuti ndiwe uvuta kuphunzitsidwa.

  • @prayer-room35

    @prayer-room35

    5 күн бұрын

    @@user-lp8wj3vq4x Kodi zomwe akunenazi sikusiyana chani ndi zomwe zidachitika 2012 pa imfa ya Bingu.. Joyce Banda adalowa Malo a president omwalira asanaikidwe... .. Tayambani mwamukonda Mulungu ndikuchita chifuniro chake ndipo adzakutumani kukatumikila ntchito yake ..Koma zoyankhula za mumaganizo athu ndithu tizamenyanitsa anthu zedi

  • @KingsleeKandiadoh
    @KingsleeKandiadoh5 күн бұрын

    Ambuye akutetezeleni father, chifukwa nkutheka kuti uthenga uwu ukubweletselani mavuto. Ambuye samalilani mzimu wa SKC uziusa mu mtendele