Келесі
- 1:00:36
- 32 М.
- 00:15
- 4,6 МЛН
- 7 күн бұрын
- 22:22
- 610 М.
- 5 күн бұрын
- 00:50
- 17 МЛН
- 14 күн бұрын
- 21:37
- 399 М.
- 2 күн бұрын
- 26:03
- 12 М.
- 8:37
- 37 М.
- 14:17
- 78 М.
- 1:43:49
- 43 М.
- 3:52
- 4,3 М.
- 2:53
- 3,4 МЛН
- 2:51
- 1,4 МЛН
- 3:24
- 109 М.
- 3:19
- 884 М.
- 2:13
- 2,5 МЛН
- 3:08
- 477 М.
- 2:48
- 55 МЛН
Пікірлер: 49
Am very proud of you sir
That is what we want,, we are tired of chakwera's government,, big up bro!!! Tikufuna athu olimba mtima like the kaluwa's,,,not adyera omwe alipo mubonamu!
Bon kalindo adanenaponso izi amalawi galamukani
MCP singabere chisankho idzawitsa idzawina ndipo MCP idzawina ndi mavote ambiri kamlepo kaluwa adapenga misala kaleke nrb ndi votes regesration it's deference.
@thokofodya1583
14 күн бұрын
Forget about that
Mcp ikuwinani mukuona maso ndipo munya dpp sikuifuna
Powerful 💪💪💪
Akufuna ndalama galu uyu
Mcp akangobera ndiyekut diyamanja bas tatopanawi
Ukakhala kuti iwe mnyumba mwako sukuifuna mcp , ndiweyo basi koma ife ndi MCP yomweyo ndipo iweyo kufuna or osafuna koma mcp 2025 mpaka 2060 wooo!!!!!
Akaluwa sakudziwa kuti mpando wawowo 2025 akuutenga wa mcp. Ngakhale kwawo anthu anazindikira kuti akamlepu kaluws bongo unazixora.
Amadla awethu💪💪💪💪
Kumeneko ndeye kubwela asogoleli
Namalira uyu
Zaboza zimenezo
@charlesmuwanya7845
20 күн бұрын
The use of the National 😢Citizen Identification of the Republic of Malawi ( ID) for voter registration is not in the constitution of the republic. Political parties in the opposition should not allow this. If 2025 elections are to be free,fair,credible & peaceful, then the normal traditional voter registration requirements used in the past elections must be adhered to i.e use of a passport , driver's licence,letter of identification from the chief etc. I humbley ask opposition parties to seek legal intervention from our Courts.
Well known results
Aaaa chakwela ndi MCP alephela thas why ukufuna kubela otsusa boma ngati mukufuna kuti boma lidzacheke onsadzalole nkhani ya ID kuphatikudza ndilembela wa vote chifukwa otsekonedza dala za ID cholinga azabeledi titsadzalole kutudza kuti opanda ma ID sakavota tsisadzayimve dziwonetselo dziko lotse paka adzichita dzotii apa kulembetsa ID ndikupitaso pena polembesela vote akadzatelo tidzamvola kukupemph monga akaluwa achihana amuthalika atupele mayi Patelo ndi ena ambili kupotsela ndachulawa kuti tikalolela kuti mcp idzitiudza zochita amalawi 2025 tidzalila ndimamvuto bolani pano akutipangila pa passport yakaton kkkkkk koma chakwela ndi chilima inu agalu kwabasi
Ok bwana kamulepo timenyeleni nkhondo ife Amalawi tasuzika chomene
Vakale ivyo kkkkk
MCP chipani cholephera tired with this regime
Sidzidzatheka,ndipo adikile zomwe tidzawapange.
Mcp ndiofoyila bwana angotizuza
Tithananayo mcp mwajira iliyose
Zakusowani zochita
Ulemu
Chakwer watitopesa washoke
Mtikuku dalilani bwana sobelaso sisiteka
Tilipambuyo panu bwana.
Mau amphanvu 👊
Zavuta Ku MCP
Mbava Za MCP tatopa nazo
Kulira kwa mbuzi kalua
@Zelinakhisswell
21 күн бұрын
😂😂😂 mbuzi yaikulu ndiwe 2025 gule kwao abwelere kudambwe
@SameKaposa
21 күн бұрын
Osangotinso yaikulu koma yopanda nyanga😂😂😂😂
Hahahaha propaganda mwayamakale kunjenjemeratu
Satana wa chipani mcp and chakwera ulendo uno chisika
Nonsense, cries of a dying horse.
Good message Kamulepo
Mulungu si Lazaro kumwamba kuli mulungu akuva kulila kwathu
mukuopa chani dpp sinabepo mukuopa
Zabodza izi
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
21 күн бұрын
MCP sikuwinanso 2025 tipange Betchi
Tili pambuyo panu bwana.
ife sitilora kuti MCP yitengeso boma ndipo sitikuyifuna yatizuza kwambiri ndipo ndizigawenga mbamva zopanda zeru
Poor MCP bamva zokhazokha anthu analibe olo nsapato yosinthira koma Pano akusintha ndikuchimbudzi komwe agalu kwabasi
Kumeneko ndeye kubwela asogoleli
Kumeneko ndeye kubwela asogoleli