mwano wa namadingo

Музыка

lulu vs doc

Пікірлер: 105

  • @zaqueuadelinomoiseskanjaut5284
    @zaqueuadelinomoiseskanjaut5284Ай бұрын

    Lulu ndi dolo ku nkhani za nyimbo ndipo kwa ine Lulu is a legend Namadingo ndi dolo ku nkhani za business komaso nkhani za kunyoza wena koma kukamba zi nyimbo Namadingo akadali kutaaaaali kwambiri.

  • @lithembajujwana5577
    @lithembajujwana5577 Жыл бұрын

    Vuto namadingo anayamba bwino,ndi mtendere komano panopa sitikudxiwa kuti namadingo akuimba gospel or secular,zimandibalalitsa but I like his songs,but to be honest lulu nda achalume💪🏽

  • @vesterkadzani8074
    @vesterkadzani8074 Жыл бұрын

    Chilungamo chimawawa Namadingo he talked facts

  • @misheckkazembe1935
    @misheckkazembe1935 Жыл бұрын

    I like Lulu's personality. He is very very humble guy.

  • @user-gl2tj5nj8d
    @user-gl2tj5nj8d10 ай бұрын

    I love Namadingo lulu ndi mwana

  • @vincentchristopherbanda3748
    @vincentchristopherbanda3748 Жыл бұрын

    Awa awo ndimatama basi kumbali yakuimbayi ndimaona nyimbo imodzi ya mtendele yomwe adayimbako bwino komaso nakaika kuti adalemba yekha nyimbo imene ija. Munthu wakut style yakaimbidwe alibe.

  • @vincentchristopherbanda3748
    @vincentchristopherbanda3748 Жыл бұрын

    Kod naoso awa mukut anamadingowa abwela lit akukukula mtima pano chosecho avinavina nyimbo za lulu. Ine sindikuona chifukwa chomafanizila kape ngat namadingu . Munthu wakut alibe or luso lililose loyimba . Mwinatu mukadamayelekezelako lulu ndi dan luu kapena.

  • @stephenphiri4830

    @stephenphiri4830

    Жыл бұрын

    Ndine Stephen. Waku malawi konko koma ndiri ku South Africa Lulu ndi akatundu ndipo anayamba kuimba bwino amalawi ari mutulo kukana khala kayiko akunja bwezi lulu ari ngati ashina diamond 🤞🤞

  • @stephenphiri4830

    @stephenphiri4830

    Жыл бұрын

    Bolako pamenepo

  • @user-jx5kb8pt1m

    @user-jx5kb8pt1m

    3 ай бұрын

    Kkkkkkkkkk mudaka khala ena bwezi mukuyamika kut mavela nyimbo za namadingo enafe nyimbo za namadingo zimativetsa kukoma iiiiiiiiiii guys 😮😮😮

  • @daviemangenje1224
    @daviemangenje1224 Жыл бұрын

    Lulu anabwadwa oyimba and this man mmmm ndi big namadingo ndi mwana kutali i love lulu

  • @richardlulanga8900
    @richardlulanga8900 Жыл бұрын

    Namadingo Swallow your Pride be humble Respect Others.

  • @martinsambanyanja4473
    @martinsambanyanja4473 Жыл бұрын

    Lulu nayenso ndi legend anthu onse tsangapange zofanana aliyense alindi lusolake namadingo ngati akutero akulakwitsa kwambir coz palinso anthu ena nyimbo zake sazikonda

  • @samanthantutha1957
    @samanthantutha1957 Жыл бұрын

    Lulu my legend namadingo ndi nfana kwambiri

  • @user-jd8oz6mk8k
    @user-jd8oz6mk8k9 ай бұрын

    Lulu no one Namadingo wachepa muzonse

  • @chrismatekenya6084
    @chrismatekenya6084 Жыл бұрын

    LULU He is Legend...Of course time changes and He extremely Humble

  • @thingamabobmalawi5340
    @thingamabobmalawi5340 Жыл бұрын

    Let people talk Not Artist ayiii👌👌👌

  • @chifundonkhoma3642

    @chifundonkhoma3642

    Жыл бұрын

    Achalume lulu kuyankhula mwa u legendary

  • @arnoldthomson1063
    @arnoldthomson1063 Жыл бұрын

    Nyimbo za Namadingo omwe amapanga download ndi 🐐

  • @esthermalekezo
    @esthermalekezo Жыл бұрын

    Lulu is legend ndipo sindyerekeza kumvera nyimbo za namadingo ine aaaa

  • @user-jx5kb8pt1m

    @user-jx5kb8pt1m

    3 ай бұрын

    Zuto si namadingo ayi kom inu athu muli vuto namadingo alibe vuto kom inuyo nd muli vuto

  • @caristarndarama-hn7np
    @caristarndarama-hn7np Жыл бұрын

    Lulu amatha I love lulu ten much nt two klkkk

  • @Ndakonderedwa
    @Ndakonderedwa Жыл бұрын

    Nyimbo nditanthauzo, kuvina ndizotsatila pambuyo pa thanthauzo lanyimbo lulu ndi waluso kwambiri

  • @aubrylinoss5390
    @aubrylinoss5390 Жыл бұрын

    Lulu is humble man love him too much

  • @caphyasibu501
    @caphyasibu501 Жыл бұрын

    Namadingo sangamake pa Lulu, Lulu ndi number one

  • @hamdanmasuku4800
    @hamdanmasuku4800 Жыл бұрын

    Kuyimbà amakuona nd anthu akumvera nyimbo zako km chilungamo namadingo sangafike pa Lulu .

  • @jasmonchidima408

    @jasmonchidima408

    Жыл бұрын

    Lulu ndi namadingo ndikosiyana or mayimbidwe awo ndikosiyana

  • @hamdanmasuku4800

    @hamdanmasuku4800

    Жыл бұрын

    @@jasmonchidima408 so y anamadingo akupanga compare ??

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 Жыл бұрын

    Namadingo sunga mwambo undithetsera banja aise Madam adandiphunzitsa kukonda lulu ndipo ndimachedwa lulu ndi legend and family man sungamake docs Lulu ndipatse ma details umwe juice ndikutchula kenakake Ku mukuru all the way from Alberton

  • @joeffnkhoma9722
    @joeffnkhoma9722 Жыл бұрын

    usazitukwanitse ayise lulu ndinkhani ina iwe or nyimbo imodzi yako ndilibe

  • @judithchitukwi165
    @judithchitukwi165 Жыл бұрын

    Lulu is legend

  • @sumayyahlinosi4645
    @sumayyahlinosi4645 Жыл бұрын

    Namadigo mukuchepera ngati mwanhuka chifukwa munarowa nawo zausataniki musiyeni lulu amativesa kukoma

  • @petergabrielnyirenda3441
    @petergabrielnyirenda3441 Жыл бұрын

    Koma zinazi mmm kamangoyang'ana basi Osamatha mau. Apa Lulu walankhula zanzeru ngakhale fumbi ndiwe mwini, koma zinazi osamalowelera ai mudzachita nyazi ngati Namadingo oimba ngati mlakatulu 🤣😂

  • @jemesmasara1332
    @jemesmasara1332 Жыл бұрын

    Lulu umaziwa kuyimba timakoda kumvela myimbo zanu pitilizani lusolanu 🙏🥰🙏🥰✌️✌️🥰🙏🥰🙏🙏🥰

  • @damianochifuniro5416
    @damianochifuniro5416 Жыл бұрын

    Lulu is best namadingo mwana

  • @ChiccoJelly-wp5wj
    @ChiccoJelly-wp5wj9 ай бұрын

    Lulu is the best than namadingo

  • @danielmwatchipitsa7442
    @danielmwatchipitsa74425 ай бұрын

    Km lulu nyimbo zake ziti kod

  • @user-to9jy9vz6z
    @user-to9jy9vz6z Жыл бұрын

    I like legend Lulu

  • @chifundonkhoma3642
    @chifundonkhoma3642 Жыл бұрын

    Kkkkkkk koma lulu.... Kodi ku music kuli ndaleso eti, lulu akuyankhula ngati Gospel kazako bwanji,koma lulu ndi odzichepetsa kwambiri, koma ndi katundu oti Namadingo sangakwanitse kuseza

  • @emmanuelwakuluernest9372
    @emmanuelwakuluernest9372 Жыл бұрын

    LULU ndi deal ,,,Namadingo amangozichemera koma ndikupe

  • @comedyandpoetinafrica718
    @comedyandpoetinafrica718 Жыл бұрын

    Koma sindinawone chipongwe cha namadingo Mwina inuso mumangomuda

  • @mastermindmanyozo5853
    @mastermindmanyozo5853 Жыл бұрын

    Namadingo matama kuimba satha amakakamiza. Leave Legendary Lulu alone

  • @BrianjIlimusosala-mi7wq
    @BrianjIlimusosala-mi7wq Жыл бұрын

    Namadingo is numb 1

  • @sabinachiwinaawali8599
    @sabinachiwinaawali8599 Жыл бұрын

    Lulu number one 😍😍😍😍😍

  • @alinafechisamba3248
    @alinafechisamba3248 Жыл бұрын

    LULU amatha kuimba koma anaonetsa kuzindikila kwake

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 Жыл бұрын

    Kuyankhula kwa munthu ozindikira komanso ozichepetsa. Osamazichemerera wekha. Namadingo ndi self centered, kuzichekenira kwambiri

  • @emmanuelkhamula9886
    @emmanuelkhamula9886 Жыл бұрын

    Sam ndiwe odanisa kale.....

  • @jumbradoone4164
    @jumbradoone4164 Жыл бұрын

    Anthuwa amacheza just kuitanila ma customer kuti adzabwele ku show, koma zachisoni a Malawi tazitengela pena kufunitsitsa kuti anthuwa adane. Ndichimodzimodzi mmene amanenela a Nkhonya akamawapanga interview.

  • @mosesdyelathu
    @mosesdyelathu Жыл бұрын

    Kungoti amalawi timakula mopusa kod pali mwana Pazomwe anayankhula namdingo apa aaaa ngat mukuvesesa zomwe akuyankhula lulu kumapetoko ndizimene munthu angat akuzipopa nanga zomwe akuyimba iyeyu angamafanizile ndi mess

  • @chifundoalfred14

    @chifundoalfred14

    Жыл бұрын

    Inu ndiye tafanana zoona wayamba ndi Lulu kufusidwa uyo akuyakha bc komatu athu sakuva

  • @osmanayatu8558

    @osmanayatu8558

    Жыл бұрын

    aaaa inu mwatani kodi mesa angopeleka example ya mess yo

  • @danielmwatchipitsa7442
    @danielmwatchipitsa74425 ай бұрын

    Namadingo nd ozindikira

  • @madalitsokazembe9569
    @madalitsokazembe9569 Жыл бұрын

    Sindikuona nyimbo iliyonse pa namadingo yomwe angatukwane nayo Lulu. kunena zoona Lulu ndi amuna.

  • @user-jx5kb8pt1m

    @user-jx5kb8pt1m

    3 ай бұрын

    Ngat sukuwona nyimbo ya bwino iwe uyimbe yako ngat unga fike pa namadingo ine nd mwana phuli phuli umboni oti namadingo ndi bolo zowona zimenezo ❤❤🎉🎉

  • @silencengwenyama6770
    @silencengwenyama6770 Жыл бұрын

    Ukunama lulu ndikatundu ndipo ndiwoyimba woziwa ameneuja

  • @trdoxyyusufu7093
    @trdoxyyusufu7093 Жыл бұрын

    Kwa ineyo Lulu ndi Legend wanga

  • @euniceflash5612
    @euniceflash5612 Жыл бұрын

    Naonso anamadingo adziwa liti kusamba?? Hiyaaa ineso nde nyinbo za namadingo ndimadana nazo kuyambila kale kale. Ndipo sindimayekekeza kumvera🤮🤮🤮🤮🤮🤮🤮

  • @caristarndarama-hn7np
    @caristarndarama-hn7np Жыл бұрын

    Iwe wasamba Liti namadingo aaa kulankhula kwa bwanji?ife lulu ndi one mpaka kare

  • @thobeka.m5138
    @thobeka.m5138 Жыл бұрын

    Namadingo sioyimba.

  • @shareefissah7236
    @shareefissah7236 Жыл бұрын

    Namadingo nyimbo ziti zomwe anganene kut amatha kuposa lulu ?lulu ndi lulu bas osamapanga compaire ndi namadingo ,namadingo size yake ndi dayi busy ,maid cee kutchuka kotchukira nyimbo za eni

  • @josephcliffordmwanyongo6965
    @josephcliffordmwanyongo6965 Жыл бұрын

    Lulu ndi machine amayimb nyimbo zopereka tanthauzo komnso chikoka ziti sizichokanso fashion so namadingo dnt judge ngat ukupang zokupsa

  • @doricamavule5976
    @doricamavule5976 Жыл бұрын

    I like legend Lulu's humble

  • @mrbanda9222
    @mrbanda9222 Жыл бұрын

    Lulu ndi one bas

  • @gigsishmael2907
    @gigsishmael2907 Жыл бұрын

    Lulu sapanga zamuthu coz lulu anamukana kuimba thats why namadingo talk too much 😜😜😜

  • @princematope9289
    @princematope9289 Жыл бұрын

    Lulu Sangafane nd namadingo

  • @stephenphiri4830
    @stephenphiri4830 Жыл бұрын

    Lulu ndi muthu walutso

  • @hanffyamizy2706
    @hanffyamizy2706 Жыл бұрын

    That's true lulu it's not like before

  • @jimmygenesis9829
    @jimmygenesis9829 Жыл бұрын

    Lulu is #1 enawo akhala chotcho

  • @priscatemboh5758
    @priscatemboh5758 Жыл бұрын

    👀👀👀👀👀

  • @kenliwinga7997
    @kenliwinga7997 Жыл бұрын

    You can never compare the two, Lulu ndi wamkulu.

  • @fanuelbanda6288
    @fanuelbanda6288 Жыл бұрын

    Lulu ndi legend

  • @HAWAHANDRWE
    @HAWAHANDRWE Жыл бұрын

    Zikomo kwambili sam malvitha TV ndayionera ndinthu video km poti munthu samadziyamikila yekha ai anthu ndamene amayamikila tinthokoze lulu podzichepesa mu video chifukwa akadakhala kuti akumusatila namadingo mayakhulidwe sidzikanakhala bwino tililimodzi Sam malvitha TV pambuyo panu tasakha kusapota inu zikomo

  • @sammalvitha

    @sammalvitha

    Жыл бұрын

    Thanks so much

  • @HAWAHANDRWE

    @HAWAHANDRWE

    Жыл бұрын

    @@sammalvitha Thack You Sam malvitha TV sangalusi wanthu

  • @penjanchipeta2200
    @penjanchipeta2200 Жыл бұрын

    Me I don't see the problem with namadingo talk

  • @jameskphiri9635
    @jameskphiri9635 Жыл бұрын

    Namadingo sumatha Kuyimba yako ndimatamabasi kusukuta shalamuta namadingo

  • @hamissmuhajir4076
    @hamissmuhajir4076 Жыл бұрын

    Mmakwana Sam

  • @henzilymwenitete4147
    @henzilymwenitete4147 Жыл бұрын

    Just keep to giving us this message

  • @chrismatekenya6084

    @chrismatekenya6084

    Жыл бұрын

    Powerful Speech from Lulu.....Dat means Legend "Humble It's reflector from inside good heart

  • @samuelchimimba2966
    @samuelchimimba2966 Жыл бұрын

    LULU ndi chisul cha njanji, anamadingo takusowani liti? Mukufuna mu muphunzire lulu kimuimba kapena mumusokoneze? Inu Matama anu ndi a chule olumpha popanda zenje iyaaa

  • @azunguauskay4903
    @azunguauskay4903 Жыл бұрын

    Lulu ndi machine

  • @yousufsymon6346
    @yousufsymon6346 Жыл бұрын

    Mmakwana big

  • @YNOTGEORGE8
    @YNOTGEORGE8 Жыл бұрын

    Nkhani izitha

  • @alex-wachimwemwe
    @alex-wachimwemwe Жыл бұрын

    lulu ndiwoyimba weniweni nthawi imene namadingoyo nkayamba kuyimba nkadziwa kuti kuli woyimba lulu. apeleke ulemu chonde sikuti aluza akanthu

  • @petersawerengera8193

    @petersawerengera8193

    Жыл бұрын

    Namadingo amaimba bwino koma ndi savage with that i dont like him

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Жыл бұрын

    Lulu more 🔥

  • @scar9216
    @scar9216 Жыл бұрын

    Akumwa kwambiri mowa Doc

  • @chizzzandazzzi6693
    @chizzzandazzzi6693 Жыл бұрын

    Lulu satha kuyimba ...namadingo sakunama...lulu samatha

  • @meianoitjr

    @meianoitjr

    Жыл бұрын

    Ngakhale Namadingo sadziwa kuyimba. Nyimbo zake zilibe mawu achilendo, kapena ndinene kuti amabweletsa mawu akuchepa kwambili. Mawu ake ndi txuni sagirizana ai.

  • @sammalvitha
    @sammalvitha Жыл бұрын

    Chonde Subscribe 💞❤️ Like 👍 Comment 💗💗

  • @dadaharawa3613
    @dadaharawa3613 Жыл бұрын

    Zoona

  • @isaacrodger
    @isaacrodger Жыл бұрын

    Timafuna mbiri ya lulu

  • @sammalvitha

    @sammalvitha

    Жыл бұрын

    On it..

  • @deborahmtalimanja2952

    @deborahmtalimanja2952

    Жыл бұрын

    Pangani search Cruse 5 amacheza ndi anthu osiyanasiyana and mukapanga Cruse 5 Lulu muyipeza zikomo

  • @ussiorijinal9962
    @ussiorijinal9962 Жыл бұрын

    Lulu amatha kunena chulungamo

  • @lazarousnamakhwa6549
    @lazarousnamakhwa6549 Жыл бұрын

    Amuna sakangana guys Inu

  • @laurankhana9833

    @laurankhana9833

    Жыл бұрын

    Ndipo inu zinthu zake aaaa ndichifukwa chake oyimbawa amaphana nanga kukangana kuyimba aliyese mumene mulungu anamupasira luso lake basi muzikondana osati kumasiyanitsa Ife bola tikumvera tilibe nthawi yoti tiziti uyu Kaya uyu aaa Bola Zanu zikuyenda basi

  • @jcolbeatsmw6348
    @jcolbeatsmw6348 Жыл бұрын

    Kodi mukukhala nazo busy choncho bwanji ngati kuti u a manager wa mmodziwa iwo aaaaaa asiyeni ziwathera okha ife zatikwana

  • @emmanuelnamukhoyo4790

    @emmanuelnamukhoyo4790

    Жыл бұрын

    Lulu ndi achikulire. Namadingo big month

  • @markbagarskale7370
    @markbagarskale7370 Жыл бұрын

    Namadingo ndiwe mfana opusa kwambiri lulu amatha

  • @deniskondani1305

    @deniskondani1305

    Жыл бұрын

    Odzikuza adzasusidwa.... Ozichepesa adzakwezedwa. Namadingo untha ukuona. Mwana opanda mwambo iwe

  • @alfredbatumeyo9191
    @alfredbatumeyo9191 Жыл бұрын

    I like both of them

  • @adamabiyen5079
    @adamabiyen5079 Жыл бұрын

    Namadingo u ae idiot palibe chomwe ukudziwa

Келесі