Skeffa Chimoto -'' Ine Si wa sataniki'' kuchoka kogulisa zipewa Pano Ndi Billionare
Kupatula kuyimba, Skeffa amapangano ma business. Iyeyu ali ndi MAGalimoto ambiri omwe amanyamula katundu . Mu kanthawi kena, anayamba kutchuka ndi mbiri yosakhala bwino yoti iyeyu ndi mmodzi wa anthu a Satanic ndziko lino.
kuchoka kogulisa zipewa Pano Ndi mponda matiki
from sellingTsotsi Hat to a multi-millionaire
the story of skeffa chimoto
Пікірлер: 79
Vuto la ife amalawi munthu akatukuka timayamba kupeka nkhani. Skeffa wavutika pamoyo wake. Pano mulungu wamuona anthu mwayamba kukamba zambili.
@estoriasikwewa1893
Жыл бұрын
Inu amalawi sazatheka samafuna kuti. Azawo alemele
Watching live & direct from zambia , chipata , kasenegwa district - John Ngoma..skefa chimoto my blessing
Asikefa kodi kalata anasiya chinga sipanatuluke zina lanu kumbukilani kalata imeneyi mboni ndi grace chinga anasiya kalata dziko lonse likuziwa ndithu
Watching from Port Elizabeth South Africa,,
Watching from UK
I like chimoto so much
Watching from Cape town
I lke that guy n he is so humble from thyolo
Watching from Namibia
Watching live from United States
Sikefa chimoto Amadidalitsa ndi nyimbozake
watching from kenya
Musatinamizepo apa it's only God who knows everything
Ndichifukwa chake amatilimbikisa kwambiri munyimbo zake
Muthuyu ndi luso lake Koma Muthu akatchuka kapena kulemela anthu amamukamba Koma skeffa usaoke ndithawi yako nyimbo zako Ife dzinatisitha
@macdonaldkorea2928
Жыл бұрын
Amalawi tili ndi bvuto mchifukwa ambiri tili osauka mpaka panopo komano kusaukaku ndi kwammutu mwathu, tikadzalemera mmutu pamaganizidwe tidzayamba kutukulana tokha tokha like Indians...... Ukatukuka akuti walowa satanic, ukasauka akuti anasemphanitsa chizimba, umphawi udzatipha kwabasi.....sinthani maganizidwe potero kuti Mulungu atisinthe nafe
Amalawi tidzitha kuyamika mzathu akachita bwino.Uyu ndi mmalawi akuyimba ku malawi akutukula malawi.Chonde tiphunzire kuyamika zimene wina wachita.
Jealous people always loose
Nthawi yotsiliza ino Satana akugwira nthito kwambiri ndi anthu omwe mukuti ndi alusowo, Tamawelengani za kutha kwa nthawi ya pansi pano , komanso mudzisegula ma website ena mudzaseguka m'mitu mwanu, Inenso ndinkamukonda koma zomwe ndinapeza ku ma website ena zinandipangitssa kufuta nyimbo zake zonse komanso si yenkhayo ayi, alipo kagulu moti ena amati ndi a gospel koma akutumikila satana kuseli , inu simukuziwa komanso mwini wakeyo sangavomere ayi. Chomwe mukuona inu ndi nyimbo basi
Wa was wa akulu akulu!
I like Driemo cfkwa sapanga nao
Bambo ngati kalankhulidwe kanu mumaganiza kuti ndikachikoka aaaaaiiii ndithu sinthani kalankhulidweko thats my opinion
@napsjnr3776
Жыл бұрын
Mbuzi ya munthu iyi kkkkk
@SamPhiri-ru8dc
Ай бұрын
zowonadi man
Sikefa kaya ndiwa sitac zilibe kanthu ine nyimbo zake zimandisintha
Suziwa kumasulila nkhani ataaaa
@manuelmakonda2324
Жыл бұрын
I think better mukanapanga zanu tione, than kuti mukhale wazelu pazomwe wina wachita,
@ConcleyManeya
10 ай бұрын
Osamadana ndi anthu olimbika pogwila ntchito .
Ndimakukondani achimuene
Komaso alibe Galimoto registered number skeffa 1
Vuto a Malawi munthu akayiphula amati ndiwa satanic
Palibe chomwe mudziwa inu za skeffa aaaaaaaa dzina lake lenileni ndi joviara moti simuzidzuwaso
watching from jamaica
@jabumohammednyanganya4435
Жыл бұрын
Sk
@NumbDee
4 ай бұрын
Kodi iwe Hanifa sungamayakhule bwino bwino ine amanditopetsa kwabasi
ooohhhh
Inu taziyankhulani bwino bwino apa.
Skeffa is a blessing love from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Akutameni
Nthawi zambiri chifukwa cha kulephera kapena kufooka kwa munthu mapeto ake wina amayamba kuda anthu ena posafuna kuvomeredza kulephera kwake
Koma tone ya voice mukanasitha please news zanu sizikubeba zuoneka ngati kukakamiza zithu kumangolakhula voice yanu bwanji😂
Sangavomeredze olo ali wasatanik kma akudzuza ndi mulungu ekha basi
🙉🙉🙉🙉
Vuto lakwathu kuno ku Malawi timadana ndi wolimbika ndipo wolimbikayo akalemera amampatsa nickname yotchedwa satanic.
Munthu ndi olimbikira uyu
Komatu zoti ndi Billionaire mukumulakwira inde ali ndi kanthu koma zoti ndi Billionaire mukuzitenga kuti? Mu list yama Billionaires m'Malawi muno iyeyo mulibemo
Ndiwe dolo
Palibe chilipo pamenepo guys
Amalawi nzanu asachite bwino ndekuti ndi wa satanic inuyo mumayankhula chonchonu mumafuna kusauka mulinakoko ngati ndi wa satanic Inu mukulekelanji kukalowa kuti nanunso mulemele tamango kandani anthu opanda tsogolonu
Munipatseko nambar achimoto skef
A Malawi ambiri mukutiopsa kwambiri mwasintha modabwitsa koma Bible imati mwini nyumba akadadziwa kuti mbala ldza boola nyumba si bwenzi ata gona koma akadadikirira kuti mbala lsa boole 'koma a Malawi mwataya chamoyo mwatola chakufa
Ndi n'daliso wake basi
You are the best skeffa not this guys gwambizo fukolo man
Ai ndiwasataniki skefa yo guys
@rainfordisaacs6789
Жыл бұрын
Muli ndi umboni inuyo?
@victormsika1538
6 ай бұрын
Wasatanic yo ndi iweyo ka. Ukhalilanji ndi nsanje ngt siiwe wa satana. Mfiti yachabechabe
Vuto anthufe sitikufuna kuyesa zinthi kuti tiziwe mataleti athu mara muzati in ineso Wa Sataniki koma tikuyambila apa movutikira 👉aaronnemarere TV watch muone mmene timavutikila kuyamba zinthu
Oyimba ambiri akwathu ose awonongeka ndi usatanic vuto asogoleri nde akakuwuza kut ulowe Umarowa u satanic kwathuko sakubisa kharidwe lonyasa
@graciousrobertrobert6928
Жыл бұрын
Its true hé is thé satanic one
@ipyanamwanyongo4169
Жыл бұрын
you're speaking the truth my brother all of them Malawian musician alowa usatanic, chifukwa anampha uyimba but we need to pray for Malawi that God most delivered this country from powers of darkness,
@christopherbadson699
Жыл бұрын
Inu mumati angavomere kuti iye ndi wa satanic?
@alexbanda4982
Жыл бұрын
Kaya abale Inu
@ishmaelchiponda7806
Жыл бұрын
Koma ndinu omvetsa chisoni, satanic kulibeko ku malawi...
🤣🤣🤣🤣 koma adolo inu nde mmadziwa kulongosola nkhan eti
@samuelbartolomeusadia1219
Жыл бұрын
Tenho uma ttt
@thebulonathaniel1772
Жыл бұрын
Hie
God bless you mr
Ndi wa satanic uyu luso lake ija anakagulitsa kwa satana pano saimbanso bwino Mumuuze mmaso mwake skeffa yo
@truthtellerlastonk.m.p4985
Жыл бұрын
Prove it sir
@paramountcommodities3236
Жыл бұрын
Bring relevant information big,,it seems you know each other
@jumbradoone4164
Жыл бұрын
Aliyese ophula pa Malawi paja ndi wa Satanic
@nenanimayinga716
Жыл бұрын
Kkkkkkk km nkhan zakeso
@estoriasikwewa1893
Жыл бұрын
Don't judge anyone please musiyileni mulungu yekha