Azavotela dpp uyu akungofunako ndalama matumbi ndikumuziwa ndiine bwino bwino tyolo boy uyu ndi dolo
@user-cy7gd1go6yАй бұрын
anthu a mcp ndiwosagwila mitu kumati talandila munthu nde munthu wake matupi mene mumamuwonela matupi mutu wake umagwila koma mcp ndimanyakad
@user-qp4gk5gx8jАй бұрын
It's time to eat money while u know the truth that zinthu sizilibhoo
@HafizahHarack-bn3bfАй бұрын
Zithu Zina zoseketsa😂😂😂
@Blessings-td4crАй бұрын
Afuna pothera awa,,aonako chani? Ngati liri dyera APA watherapo basi.
@SolomonNjolomoleАй бұрын
Zabooka ndalama nanga mkutani pavutira pamalawi katafuneni misonkhoyatuyo km one day to remember.
@user-bp9ot1zo6zАй бұрын
Aliyose ndi ufulu wake kuluwa chipani chomwe akufuna nde democracy imeneyo palibeso nkhani pamenepo
@user-gp9ik2qv7uАй бұрын
Koma malawi ikuvesa chisoni muthu osa phuzila zandare kumu landila akanena chani ku nyumba yamalamulo kachasu watha mumutu matumbi
@binalidjeyshabahzombamalawiАй бұрын
Wathu ndi Dan lu
@PeterPhiri-nd6opАй бұрын
Koma ife athu osa mavuto akafika ndife timavutika koma apa timasekelela nchirichotse eshii
@tasmania527Ай бұрын
Keep making a grating noise for the love of your beloved APM and DPP, but you'll never as DPP, rule Malawi again. Matumbi has made a wise decision and haters keep barking.
@jafaliwotchlovethissongfro1606Ай бұрын
Kkkkkkkkk koma 2 mbi ndi wanjara kkkkkk
@user-fl7br3dw4hАй бұрын
Nayeso ndi munthu basi adye nawo koma malume alibe ameneyo komaso wapitila ma phindu ake aononge nawo dziko anyamata adyela
@MisheckAseloАй бұрын
Amalawi sitidzatheka tizakhala akapolo mpaka kale, chakwera ndi mbava iyi
@AleksaWilliams-qc6cnАй бұрын
Chilima ndie oyenera kuzutsa apule wo,zamkutu
@PeterThawi-jc7zlАй бұрын
How can u compare zambia to malawi ....thats fucking bullshit😂😂😂😂
Пікірлер: 73
Pa ndale uyu ndi ndaninso and olo ku DPP ko amapanga contribute chani LAUGHABLE INDEED 😂😂😂
Matumbi njala ndi yomwe yamupangitsa akudziwakuti ku mcp ndalama zapweka maluzi matumbi
Kutha kwa dolo 😂😂😂😂 Even Ku music 🎵 industry wathelatu😅😅😅😂
Ndinadabwa kanzungu kaja kuti awa njala yawapha kkkkk umphawi ndintchimo ndithudi
Matumbi bwanjiso amwene ?
Mmmmm man thumbi mboratu apa
Kazitape sanalowe mcp with full body ai
Aliyense ali ndiufulu musamunene, ndiufuluwake kulowa chipani chomwe akufuna.
Apite si ndalama zaphweka
Kodi munthu amangolowa chipani kungofikira ku likulu zosayambira ku branch? Zikumatani masiku ano.
Anne matupi ndi munthu otii kumanena kt ndapeza muthu ku chipani komatso matumbi sioyimba koma wandakatulo
Panyapako matumbi osamangoimba bwanji
Kkkkkkk 😂😂 kodi anematumbi wasowa kolower Kkkkkkk mwachita bwino kumutenga kuyimba mulibe mwina kumeneko apedzako ndalama
Njara ndi kukwera kwa fertilizer ndi zinthu zina
Zafika pomangolandira zili zonse
Mbuzi yamuthu chakwela
Azavotela dpp uyu akungofunako ndalama matumbi ndikumuziwa ndiine bwino bwino tyolo boy uyu ndi dolo
anthu a mcp ndiwosagwila mitu kumati talandila munthu nde munthu wake matupi mene mumamuwonela matupi mutu wake umagwila koma mcp ndimanyakad
It's time to eat money while u know the truth that zinthu sizilibhoo
Zithu Zina zoseketsa😂😂😂
Afuna pothera awa,,aonako chani? Ngati liri dyera APA watherapo basi.
Zabooka ndalama nanga mkutani pavutira pamalawi katafuneni misonkhoyatuyo km one day to remember.
Aliyose ndi ufulu wake kuluwa chipani chomwe akufuna nde democracy imeneyo palibeso nkhani pamenepo
Koma malawi ikuvesa chisoni muthu osa phuzila zandare kumu landila akanena chani ku nyumba yamalamulo kachasu watha mumutu matumbi
Wathu ndi Dan lu
Koma ife athu osa mavuto akafika ndife timavutika koma apa timasekelela nchirichotse eshii
Keep making a grating noise for the love of your beloved APM and DPP, but you'll never as DPP, rule Malawi again. Matumbi has made a wise decision and haters keep barking.
Kkkkkkkkk koma 2 mbi ndi wanjara kkkkkk
Nayeso ndi munthu basi adye nawo koma malume alibe ameneyo komaso wapitila ma phindu ake aononge nawo dziko anyamata adyela
Amalawi sitidzatheka tizakhala akapolo mpaka kale, chakwera ndi mbava iyi
Chilima ndie oyenera kuzutsa apule wo,zamkutu
How can u compare zambia to malawi ....thats fucking bullshit😂😂😂😂
Matumbi apangako chani kumeneko akukalowa azake qkutuluka boma kkkkkk
Umphawi a matumbi...😂😂😂😂😂
Matumbi upangekotu zakupsya kumeneko
Anthuena amangochulukisa gulu apite
Kodi Matumbi naye ndiwadyera chonchi kamangoonekadi koma😂
Kkkkkkkkkkk maludzi kape😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkk koma abare nkhani zake mcp zoti ikuchoka mboma mukuwona ngat boza et muzithaima zirowani
Man thumbi mwasakha molakwika
Amatumbi sadale
😂😂😂😂😂 Amatumbi ife timaziwa chifukwa cho imba koma wosati
Deluded Matumbi...has no love for Malawians but has love for money... After all you are just an infant in political circles...
Kkkkkkk kutha ma plan awa
Kodi matumbi anali ndani ku dpp
Mwayambapo kuondatu uchimo kunzuza!
Malawi mungafanidzile ndi zambia hhhhhhhh
Matumbi anatha😂😂😂😂😂
Zinasisopanda selu
Matumbi kkkkkkkkkk wata maplan yet
Madala thumbi zoona 😂😂
Zichedwani inuyo
Amatumbi mwathela patambala wokuda hhhhh
Amatumbi sanaganize bwino
Ndidani kwaife
Joker ndi chilima
Anthu okuba awa eeeeee
Walowa kolakwika chipani bola DPP or UTM 🔥🔥
@user-ky4ce9gb6j
Ай бұрын
Ndipo kwambiri
Kkkkk kampeni kod
Maluzi afikapo
che 2mbi njala chani
Amayenda pasi kuti atope
@PaulKaunda-lj8vr
Ай бұрын
Matumbi wangobwela kuti adzapeze nyimbo yoti adzaimbe
Maluzi amukunga uyu
@user-ky4ce9gb6j
Ай бұрын
Kkk
Ose amene akuombela manjamu ndimene akudya misongo ya aMalawi ongolitsa 🍅 mulungu akuyendani , chakalawacho ndi🐕🦺
@isaacchiwaula731
Ай бұрын
Mmm a dpp ndie sankadya ndalama zamisonkho za amalawizo
@user-oq5rg5mz7q
Ай бұрын
@@isaacchiwaula731 sinati DPP, inuyo nde azisilu ombela manjamo tikuziwa , nthawi ya DPP nthumba lachimanga linali pazingat , nanga fetelaza anali panzingiti , sugar, cookng oil, mwachidule zose it was how much?
Great thinking 2mb go forward not back wads
wellocome chakwera bomaaaaa
Joker ndi chilima