"Bwato satsitsirana pakati pa nyanja" Dr Michael Usi kusambwadza MCP pa mwambo okumbukira Kamuzu.

Пікірлер: 58

  • @moosamapira9182
    @moosamapira91822 жыл бұрын

    ali ndi makhutu afe good speech DR USI 100%

  • @paulbanda9638
    @paulbanda963816 күн бұрын

    A Michael Usi mwamugulisa mzano, mwaphesa chilima ndinu

  • @Seche204
    @Seche2042 жыл бұрын

    Malawi 🇲🇼 akufunika anthu ngati awa osangoti yes yes zili zonse

  • @JMB804
    @JMB80414 күн бұрын

    Awa zowayenera nzomwe zija ku masewero not izi ayi adzingopeleka azinzao nchimbuli mbuli

  • @pansigaleta3438
    @pansigaleta34382 жыл бұрын

    Kod zoti yona anamutsitsila pakat pa nyanja sanawelengeko

  • @lucymanjolo9288
    @lucymanjolo92882 жыл бұрын

    A usi mwaiwala chimodzi muzikumbukira nkhani ya Yona muchombo muja zinthu zikavuta sitimasankha katundu oponya mmadzi ai muziwe zimenezo Hon USI

  • @user-ws1ov4se5u
    @user-ws1ov4se5u5 ай бұрын

    Wandale ndi munthu omuyamikila, ndiye utsiluwo Kodi a Malawi mudzachangamuka liti???? Anthu olilitsa inu😭😭😭😭

  • @andersonmaster8055
    @andersonmaster80552 жыл бұрын

    Well said

  • @mathewsmbaluko8522
    @mathewsmbaluko85222 жыл бұрын

    Ausi mumatiimilila kumauzadi zowona anyozele okha achakelawo akazaluza azakhale okha chifukwa chosamva kwao 👍

  • @leonardjika2100
    @leonardjika21002 жыл бұрын

    A NEW VERSION WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD WE WILL END ALL NONSENSE GARBAGE FOOLISHNESS HAPPENING TO OUR LAND

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6yАй бұрын

    Good Message ❤

  • @simonpaul6567
    @simonpaul65672 жыл бұрын

    michael usi you have to be our president ,cause you know exactly what malawians want

  • @nananambela5525
    @nananambela55252 жыл бұрын

    Yaaa neeee Mr usi

  • @hamischikalimba6626
    @hamischikalimba66264 ай бұрын

    Mau abwino okonza dziko Dr Michael Usi

  • @CholapitsaSamson
    @CholapitsaSamson9 ай бұрын

    Good speech

  • @williammhoni5729
    @williammhoni57292 жыл бұрын

    a usi kumeneko ndiko kulankhula kwamphavu takunyadilani more fire 😂😂

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y3 ай бұрын

    Goog Message

  • @enockthomasloyidi4914
    @enockthomasloyidi49142 жыл бұрын

    👍👍

  • @frstyhavoc6678
    @frstyhavoc66782 жыл бұрын

    Yona komatu anamutsitsa zitavuta apatu zinthu zavuta 😀😀😀😀

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y3 ай бұрын

    Zoona ❤

  • @charlesgunda1873
    @charlesgunda18732 жыл бұрын

    This is true

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f7 ай бұрын

    Amakoma asanalowe udindo koma akasakhidwa amasitha

  • @frankkamunde4575
    @frankkamunde45752 жыл бұрын

    yes bwana yes bwana cholinga kufuna kuononga dzina lanu

  • @chekiamaabdul5083
    @chekiamaabdul50832 жыл бұрын

    Allah knows best

  • @mcpreciousnyangulu1501
    @mcpreciousnyangulu15012 жыл бұрын

    100% my president

  • @janenkhoma6447
    @janenkhoma64472 жыл бұрын

    Lelo asiya kuyankhula kut muboma muli mbuz zokha zokha kkkk ndale icant follow

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lpАй бұрын

    Kuswa kuswa basi kkkkk

  • @PaulKaunda-lj8vr
    @PaulKaunda-lj8vrАй бұрын

    Siku lachigawenga muchizungu amati chigawenga day

  • @user-db2xl7zw9l
    @user-db2xl7zw9l5 ай бұрын

    Anayakhula koma osamanamizana chekwera anazivera okhatu apa

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience22832 жыл бұрын

    Bwato likamamira sitimaona chotsitsa. Mwambi otsutsana nawo

  • @hassammaulana4529
    @hassammaulana45292 жыл бұрын

    Dr usi amanveka motelomo

  • @kamwendoderek6567
    @kamwendoderek65672 жыл бұрын

    NDIMAONA NGATI THABWALA AKULU MUNASIYATU KKKKKKKKKKKK AYI NDITHU ,ITS NOT ALL UNITY THAT STAND WHICH IS OUT SIDE THE TRUTH OR JESUS CHRIST

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 Жыл бұрын

    Makape awa

  • @griphinmtonga411
    @griphinmtonga4112 жыл бұрын

    No comment yet

  • @mbirinyirenda176
    @mbirinyirenda1762 жыл бұрын

    Amenentchito sakugwira achosedwedi akuyipisa mbiri chakwera wanuyo

  • @josuahkachali1489
    @josuahkachali14892 жыл бұрын

    Kkkkk true

  • @henrymbalame222
    @henrymbalame2222 жыл бұрын

    Zanveka ndithudi munthu wankulu ndithudi!,,,

  • @cosmasnkanda8193
    @cosmasnkanda8193 Жыл бұрын

    Koma malawi walero ndi nyatwa!😆

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy17492 жыл бұрын

    Zoona zake manganya muuze Chakwerayo mbuzi yamunthu

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733Ай бұрын

    Kkkk usi mukukana kusika bwato? Kkkk mumila limodzitu chifukwa ndie APM akulowanso mwatinamiza tinakuvotelani kwatha amalawi anachenjela sitingamvelenso bodza lanuli bola ki Egypt than ku bagamoyo

  • @ziwani3682
    @ziwani36822 жыл бұрын

    Chilungamo ndi chimenechi

  • @nditumenichagunda4192
    @nditumenichagunda419210 ай бұрын

    Zopepela zanuzo osamagwilisa ntchito baibulo

  • @geoffreymgundo5322
    @geoffreymgundo53222 жыл бұрын

    Kkkk mawu mawu abwino kwambili

  • @jimmysingano799
    @jimmysingano7992 жыл бұрын

    Ndipo musayelekeze kutsika. Mumira.

  • @hassanyahayatahirotahiro1126
    @hassanyahayatahirotahiro11262 жыл бұрын

    Kumeneko ndiye kulangula

  • @RajabWhite
    @RajabWhite7 ай бұрын

    Koma Mkulu uyu 😂😂😂😂😂

  • @muhammaddaimon5294
    @muhammaddaimon52942 жыл бұрын

    Iwe mbuzi munthu wopanda nzeru iwe chitsilu boma lake liti lakuthaithalo

  • @kassimjummah3018
    @kassimjummah30182 жыл бұрын

    Zonazake mbwiyache

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda95542 жыл бұрын

    Kamuzu wakupha anthu uja

  • @isabelmartin4299
    @isabelmartin42992 жыл бұрын

    Madzi achita katondo 😂😂😂

  • @reubenbambe9101
    @reubenbambe91012 жыл бұрын

    Chili Ndi mutu muli dzeru

  • @KozekaniNowa
    @KozekaniNowa11 күн бұрын

    Ngalu

  • @mrr.a.l.s752
    @mrr.a.l.s752 Жыл бұрын

    😂😂😂😂

  • @harrisonmwanga9812
    @harrisonmwanga9812 Жыл бұрын

    If ndiye timasitsila pakati popo iyaaa asambila ngati satha aona plan

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y2 ай бұрын

    Good Message ❤