Mkangano wa Chimwendo ndi Chakwera; Anamanga ndi Geoffrey Colby osati Kamuzu.

Пікірлер: 163

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7qАй бұрын

    ❤❤❤kumbuyoku zimavuta koma sikuti zimavuta kufika paka apapa

  • @powercharios2087
    @powercharios2087Ай бұрын

    We love you brother you always bring true story. MCP mbuzi izi palibe momwe akudziwa kamuzu palibe chomwe adapanga kupambana kupha wathu

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zsАй бұрын

    Best bakili muluzi tv chilungamo number one watching from Mozambique 🇲🇿

  • @patriciacraiton-sf5vu
    @patriciacraiton-sf5vuАй бұрын

    😂😂😂😂😂😂. He says who's that 😂😂 I love you Bakili muluzi channel

  • @jeuzywandasigner4908
    @jeuzywandasigner4908Ай бұрын

    Iwe ndi number 1 and no one can stop what God bless may God protect you 🙏🏾❤️ Malawi 🇲🇼

  • @user-ce6hy6tp7e
    @user-ce6hy6tp7eАй бұрын

    Man inuyo musadzafe mudzangosowa bakili muluzi TV timakukondan inuyo ❤❤❤

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395Ай бұрын

    Thanks boss this is very interesting analysis

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6yАй бұрын

    Good message Bakili Tv ❤

  • @innocentchirombo2073
    @innocentchirombo2073Ай бұрын

    Ipondeni fadah ❤❤❤

  • @MonicamakwembaKunika
    @MonicamakwembaKunikaАй бұрын

    King of history bakili muluzi tv

  • @salafinamhone-rd1ku
    @salafinamhone-rd1kuАй бұрын

    Let's annoying eachother, time of being nice to each other is gone.thanks bafo for playing your part by exposing these thieves

  • @JoelJoe-uq9of
    @JoelJoe-uq9ofАй бұрын

    Let's look forward zonyodzana tichedwa nadzo Tisayang,ane ndale zokha pachitukuko cha dzikoli

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214Ай бұрын

    Kkkkkkk kupusa amafuna adziwoneka wochenjera mbuzi🔥🔥🔥🔥

  • @user-gg6uh2wo4x
    @user-gg6uh2wo4xАй бұрын

    Your respect brother

  • @alexanderntephea8706
    @alexanderntephea870612 күн бұрын

    Fupa lokakamiza silichedwa kuswa mphika....Chakwela must go & he must go now. . or face the Rage of the pipo & it shall end in tears. ...simumadzitha lekani

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7wАй бұрын

    Kkkkkkk koma bakili tv mbambande ❤❤

  • @samsonmtumbati4855
    @samsonmtumbati4855Ай бұрын

    You're true son of Malawian ❤❤❤

  • @user-mz4tk1pw3f
    @user-mz4tk1pw3fАй бұрын

    Sakuziwa chimene akupanga Ulemu wanu big❤❤

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791Ай бұрын

    Ufumu wanu watha!!!!😂😂😂😂😂 Apm 2025❤❤❤❤

  • @user-ok7bq9es3y
    @user-ok7bq9es3yАй бұрын

    Apiteso Ku Thyolo mulanje, akatero I will support him, koma Only central region? Aaaaaa watumidwa uwu

  • @LuckyKhonyongwa-pt7ck
    @LuckyKhonyongwa-pt7ckАй бұрын

    Chimwendo akungolankhula pofuna kusangalasa fanz koma stadium anamanga ndi Sir Cobe chipatala Queen herself mubas Kanyama chiumye chimene tingaloze kuti kamuzu anapanga ndi kuzemberana ndimkazi uja Cicilia

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dxАй бұрын

    Kodi chimwendo wabadwa litiro kuti akadziwe ma history a Malawi atisokeretsatu

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6yАй бұрын

    Peter number one ❤

  • @JohnGavinara
    @JohnGavinaraАй бұрын

    I love bakili muluzi tv❤❤❤

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2xАй бұрын

    😂😂😂MCP ndiyosadziwa kanthu ndithu chipani cha anthu osaphunzira ndinkana a Malawi tikudzudzika😂😂😂😂😂 Koma MCP eishiiiiii 😂😂

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2duАй бұрын

    Sham chakwera 😢😢😢akuti muchoke

  • @user-cg4ci3wj4h
    @user-cg4ci3wj4hАй бұрын

    Asiyen awa big akuchedwetsani

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996Ай бұрын

    For real brother man!!

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891Ай бұрын

    Senior minister kukanika kudziwa mbiri yadziko lake kkkkkkkk, komaaaaaa

  • @user-cy7gd1go6y
    @user-cy7gd1go6yАй бұрын

    Best tv mumakwana fada

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wxАй бұрын

    Athile moto makape amenewa mbuli chimwendo mulomowo ngati kwambuzi mulomwe ndi muyawo ndiye aeni ake a ulamuliro osati makapewa

  • @JannatuyaseenmwangaMwanga
    @JannatuyaseenmwangaMwangaАй бұрын

    Ulemu wanu big ❤

  • @wilsonwildshemarion8641
    @wilsonwildshemarion8641Ай бұрын

    I was watching a briefing today pa Zodiac ndangomva zoti ukusakidwa ndi MCP anapitaso kwa former president Bakili Muluzi kukafufuza za sambali koma sanapeze kalikose,, ndipamene ndaziwira kuti iwe ukumanenadi chulungamo ndipo anthu aja chikumawa baya😂

  • @AngellahPhiri-wy6xl
    @AngellahPhiri-wy6xlАй бұрын

    Ine ndikawona post ya bakili ndimamva kukoma hvy ndimamphuziramo zambiri mix school mayazi ngt chimwendo banda

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873Ай бұрын

    Chimwemdo sakuziwa history yamalawi vuto mcp kuphangira no 1 kuti alowe muboma anapanga ndewo

  • @user-zh9kb2sj2i
    @user-zh9kb2sj2iАй бұрын

    Akudwala awa dzikolawavuta

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141Ай бұрын

    Chakwela akuziwa history koma nduna zake mavuto kwambilri

  • @user-et3yo6re6v
    @user-et3yo6re6vАй бұрын

    Dzitsilu inu dzimukudziwa amene Anamanga sitedum dzimangokavinan nyau kudambo inu mbudzi dza anthu

  • @user-nr2gs3qy6v
    @user-nr2gs3qy6vАй бұрын

    😂😂😂😂😂😂 ufumu wanu wathaaaa

  • @Pangolinimw
    @PangolinimwАй бұрын

    Kkkkkk my best tv

  • @alexchatambalala9796
    @alexchatambalala9796Ай бұрын

    Ukomera kwake ufumuwo udayambila ND wakekuthako😅😅😅😅😅

  • @shideshidex5679
    @shideshidex5679Ай бұрын

    Dpp Ndi Deal Km Izi Aaaah

  • @giftevans2957
    @giftevans2957Ай бұрын

    Yes 🙌🙌

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8eАй бұрын

    Chimwendo ndibosaphunzilatu paja ndibmbulibsaziwa za history ya Malawi mbuli yeniyeni

  • @matembamadadada8291
    @matembamadadada8291Ай бұрын

    ulemu captain

  • @user-dd1qq5xq1k
    @user-dd1qq5xq1kАй бұрын

    Awa Atichimwisa pali chomwe akudziwa,Akungodzubza a malawi.

  • @SteaveChin-mg8yg
    @SteaveChin-mg8ygАй бұрын

    Bmtv moyo ulibwanji kumeneko abwana ineso mmodzi amene ndimakonda history zomwe mumafotikozela mtundu wa Malawi ndingokulimbikisani osafooka tilinanu angakhale tamva kuti mukuopyezedwa ndi boma likulamulidwa ndi mbuzi za wanthu zi tkupempha mulungu akudaliseni komaso akutalikiseni ndi adani abwela kumeneko wo mulungu awalange koma Ngati mungathekele ndimafuna mbiri ya malemu john chibadula waku Zimbabwe zikomo ambuye akuyang a,nileni nthawi zinse zikomo

  • @user-cp7hu6xu8h
    @user-cp7hu6xu8hАй бұрын

    Ameneyi ndiye mbuli chifukwa zimene amanena chilowe ndi za boza zokazokha

  • @PaulKaunda-lj8vr
    @PaulKaunda-lj8vrАй бұрын

    Nduna dzachamba palibe chanzeru kamuzu chinali chigawenga chimunthu chakupha anthu Nduna mphuno ngati nkhumba😂😂😂

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7gАй бұрын

    Nduna yantuthu koma osadziwa history

  • @SharifahWillardChampionn-rn8cm
    @SharifahWillardChampionn-rn8cmАй бұрын

    Umakwana bro

  • @user-zd9js7qx1i
    @user-zd9js7qx1iАй бұрын

    Panopa history ya Malawi timaitsata tsopano chifukwa cha channel iyi, panopa palibe amene angatinamize kamuzu chiliza chake chija ofunika kugwetsa

  • @user-dx4zu1wv4q
    @user-dx4zu1wv4qАй бұрын

    Timakunyadila man kwambiri anthu awa ndi agalu anyani awa

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wxАй бұрын

    Athile moto makape amenewa mbuli chimwendo mulomowo ngati kwambuzi

  • @TonyBanda-zh2rd
    @TonyBanda-zh2rdАй бұрын

    Kkkkkkk dziko lino tikunamizidwa

  • @RabiaNotes-ql8cf
    @RabiaNotes-ql8cfАй бұрын

    Chimwendoyi tu ....ndionama kwambiri😂

  • @noordeenmsamu6652
    @noordeenmsamu6652Ай бұрын

    History major💪...

  • @NephanNyirenda-jg2ze

    @NephanNyirenda-jg2ze

    Ай бұрын

    Ndakuona major

  • @user-mw8dq4is6k
    @user-mw8dq4is6kАй бұрын

    😂😂😂😂kanganya ameneyu ndiwabodza ndipo ankayankhula ngat kut adzachita zaphindu.😢😢

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6sАй бұрын

    Tathokoza bg the Bakili muluzi Tv mbambande

  • @user-xy4hq6sx7v
    @user-xy4hq6sx7vАй бұрын

    😂😂😂 amisala awa timakunyadilani big

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1eАй бұрын

    😂😂😂 auzeni br kuti zosezo kamuzu mulibemo

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8mАй бұрын

    asiyeni sakudziwa chimene akupanga angonkhala nduna

  • @user-qp4gk5gx8j
    @user-qp4gk5gx8jАй бұрын

    Umakwana bro Be safe pls

  • @WitnessKambwiri
    @WitnessKambwiriАй бұрын

    Awa alemphera kuyendesa dziko malo moti azikamba zomwe apanga koma busy kusitha zitukuko anapanga anthu ena kale

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cnАй бұрын

    😂😂😂😂 uyu amatisegula mmaso ,

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232Ай бұрын

    Did these people knows the history of malawi 🇲🇼 those projects r not for Kamuzu guys open ur eyes

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWOАй бұрын

    Pano anthu atopa ndimene zinthu zikuyendera muno muziko mwathu

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489Ай бұрын

    Chimwendo koma za gule wankulu nde akhoza kukufotokozerani bwino bwino

  • @christophergibson72
    @christophergibson72Ай бұрын

    Eeeeeee nde simugona dairy kumangoona zofooka basi zopusa

  • @user-oy2bu8vm4t
    @user-oy2bu8vm4tАй бұрын

    Best tv

  • @KingjwaYao
    @KingjwaYaoАй бұрын

    Best TV

  • @user-kl1vk1gx2q
    @user-kl1vk1gx2qАй бұрын

    Km khunena chulungamo chimwendo mbanda Ali ndi chimuntu

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780Ай бұрын

    fadahzi's choke kumene mbudzi zimenezi

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8bАй бұрын

    Chakwera chimwendo simwamva history ya stadium ndi queen 's omwe anamanga ? Si zamowa zomwe mukufotodza chakwera ndi chimwendo komanso mumvesese mu stadiam momwe akukuwizani akuti chakwera achoke ndiye ukamati ulamulira mpaka 2030 dziko lake liti ukalamulira munsalu mwa ma .😂😂😂😂

  • @user-yb1nt9te7f
    @user-yb1nt9te7fАй бұрын

    It's true please tell them tell them I don't know anything

  • @SteaveChin-mg8yg
    @SteaveChin-mg8ygАй бұрын

    Sorry I forgot I love you ❤️ bmtv

  • @AusmanBenthu
    @AusmanBenthuАй бұрын

    Anthu akulu akulu pakuba mu dziko lathu lamalawi

  • @user-jw5rx9ze8k
    @user-jw5rx9ze8kАй бұрын

    Mbuzi ya munthu chimwendo milomo ngati ....... Zankhumba.

  • @user-ko1lk3br4r
    @user-ko1lk3br4rАй бұрын

    Iweyotu ulila ulila ulila and kudana ndi kamuzu ukugwa pasi 2kubwelela ku DPP ndikukuuzan boma lose lipita ku mwela anthu awawa ndi oyipa atsankhu agawa zigawo

  • @kennedychinguwo1640
    @kennedychinguwo1640Ай бұрын

    Kodi guys,komwe anthu akuti 'Chakwera a choke' kunali ku Kamuzu stadium koma Chakwera amapangisa Msonkhano kuja?

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089Ай бұрын

    Anthu awa adziwe kuti adzamangidwa amene akulowayo

  • @user-qx3dd7xt9c
    @user-qx3dd7xt9cАй бұрын

    ,,😂😂😂Koma kuli ntchito

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWOАй бұрын

    😂😂😂😂 koma timanamizidwa chifukwa chani

  • @charlesmangani3174
    @charlesmangani3174Ай бұрын

    Iwe ndiwe galu kwabasi. Kudana ndi Kaumuzu kumeneko ??

  • @user-dj5hd4ys3n
    @user-dj5hd4ys3nАй бұрын

    Awa ndimakape bwanji kkkkkk

  • @user-cj2bo4lf7c
    @user-cj2bo4lf7cАй бұрын

    Kumalawi kulibe truth

  • @user-ob1wx4gf2h
    @user-ob1wx4gf2hАй бұрын

    Kkkkkkkk koma ziliko😂😂

  • @alexchatambalala9796
    @alexchatambalala9796Ай бұрын

    Nanuso man musatisokeze peter Yu tidathana naye kale ...inuwo tiuzen kut tipeze munthu wabwino osati mwavawiliwa ai

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7npАй бұрын

    Kkkk zomvetsa chisoni kwambili

  • @KenesiDaitoni-ob5st
    @KenesiDaitoni-ob5stАй бұрын

    Kod relo simutulusa

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lqАй бұрын

    Mcp ndiyononga basi dziko lamalawi madolo ndi dpp padzipani dzosedzalamula malawi ine nda badwila ku lilongwe ndakulila kulilongwe ina ngobwela dpp lilongwe inasitha ndiposo aliyese amene makhala kulilongwe sangakane ayi mcp machendanu nose makamaka chakwela ni chilima

  • @HusseinKassim-od9uy
    @HusseinKassim-od9uyАй бұрын

    Amapiano

  • @user-kv1ik8tj6k
    @user-kv1ik8tj6kАй бұрын

    Chimwendo banda kupepela mboriyakeso samazindikila

  • @tisamulangala5570
    @tisamulangala5570Ай бұрын

    alilatu alira 😂

  • @OZIELBLESSINGS
    @OZIELBLESSINGSАй бұрын

    Mitengo ya mazira yakwelaso monyanya ku mzuzu kuno mpaka dzila limodzi k270 from k150 and tray yamazila mpaka 8 thousand this is too much coz students rely on egg ngat ndiwo zopezekelatu

  • @user-ru5xg9qw4x

    @user-ru5xg9qw4x

    Ай бұрын

    Ku Blantyre ndi 300

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3wАй бұрын

    Boma la mbutuma sakudziwa history , achoke basi

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheemАй бұрын

    Kma Mbuzi iyi

  • @christophersmunthali5348
    @christophersmunthali5348Ай бұрын

    Watengera boza la atate wake achakwera

  • @zastroprecords5329
    @zastroprecords5329Ай бұрын

    Nduna za boma zonse ndizosaziwa kamuzu akumulemekeza ndi zinthu zopanga ena

  • @sandimizeka3199
    @sandimizeka3199Ай бұрын

    Anthu akuba inu