M’busa anayankhula izi pa imfa ya Chilima ndipo wamangidwa zomweso a Kamlepo anamangidwila

Пікірлер: 73

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole5 күн бұрын

    Azibusa ambiri adzuka tsono mumanga ambiri kmso kupalamura mkwiyo wa mulungu.

  • @augustMag
    @augustMag4 күн бұрын

    Man of God do not give up go ahead ngakhale mwamangidwa kuno kudziko musataye mtima ku umzimu ndinu omasulidwa 🙏

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d5 күн бұрын

    Kaya Chakwera alamulira moyo wake onse koma chilungamo mchakuti wapha Chilima wapha munthu amene anamuthandiza kukhala president 💔💔💔💔

  • @Hong_sing

    @Hong_sing

    4 күн бұрын

    Exactly osamati adziwa ndi mulungu yenkha chilichonse ai ifeso anthu timadxiwa timaopa kumagwidwa kapena 2025 kukamvotela ku maula ndinthu 😅😅😅

  • @MosesNyalugwe-ll8hh

    @MosesNyalugwe-ll8hh

    3 күн бұрын

    Osayiwaranxo miya

  • @MosesNyalugwe-ll8hh

    @MosesNyalugwe-ll8hh

    3 күн бұрын

    Osayiwaranxo miya

  • @henryibrahimsailes4638
    @henryibrahimsailes46385 күн бұрын

    Aaa inu apolice ndi zitsiru kwambiri mumanga bwanji munthu osalakwa,kodi mukutenga ngati dziko ndi malamulo ali mmanja mwanu bwanji,kodi satana wanu chakwera akukupatsani zingati kuti muzikazunza anthu chonchi mukubwereza ulamuliro wachipani chimodzi wa kamuzu komatu ulendo zofuna zanu sizitheka chifukwa anthu tinatseguka mmaso ndipo izi mukupangazi malipiro ake nanu muwaona sikalenso ayi anthu opusa inu muphe ndi kumanga amalawi tonse if you can evils 😈

  • @cynthiakananji1608

    @cynthiakananji1608

    5 күн бұрын

    A police ndi abale anthu,Koma akupangidwa force kut azigwira ntchito yausatanayi

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z5 күн бұрын

    Choonadi chimamasula anthu sachifuna chilungamo God is with you pastor nanga akatolika aja .uja adati mwagawana zovala zake.zazii.apolice alibe zochita Haas mcp woyeer 2025

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w5 күн бұрын

    Chakwera akungopitiliza kupeleka mkwiyo kwa a Malawi, anthu ndi okwiya kale ndi ulamuliro wa MCP ndi chakwera. Asamange anthu chonchi.

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1e5 күн бұрын

    Chowamangila anthuwocho,nde kuti zoona wapha ndiye.akanakhala kuti sanaphe ndiye akanangokhala chete ndikuuza ntundu wa a malawi zoona zeni zeni

  • @Imtiyazkalikodole
    @Imtiyazkalikodole5 күн бұрын

    Anakati aziyakhura Chichewa kapena English

  • @ulemujumbe8501
    @ulemujumbe85015 күн бұрын

    Tsono watukwana ndani kuti mpaka amumange ????

  • @meeksonmkhala
    @meeksonmkhala5 күн бұрын

    This makes sense Sir, why MCP police???? Siku lina tizakuukiran muzathawa

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo5 күн бұрын

    Apolice nanuso ndinu zitsiru ,,,,chakwera chilima unamupha ndiweyo

  • @babranzima8120
    @babranzima81205 күн бұрын

    Good voice

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr5 күн бұрын

    Khaniyiyi or ayipinda kaya kuopseza anthu zoona zake ndizoti athu aja ana chita kuphedwa Ngati sizoona akumangilanji anthu

  • @user-nv3rf7bl7r

    @user-nv3rf7bl7r

    5 күн бұрын

    Akuwamanga kuti akapelekele umboni mesa iwo alinawo

  • @fostersimbi8820
    @fostersimbi88205 күн бұрын

    Nothing but the truth was spoken here

  • @GreshamKadzembe-tn8cq

    @GreshamKadzembe-tn8cq

    5 күн бұрын

    Chilungamo chomwe wanenacho nkana amutenga kuti akaperekere ku police umboniwo, ndi umboni okwanira

  • @emmakamwana9724
    @emmakamwana97244 күн бұрын

    This audio is for Kamlepo kalua can you share the audio of the pastor

  • @user-wd5tw1mz8h
    @user-wd5tw1mz8h4 күн бұрын

    Mumakwana big pamoza ndi DC tili pambuyo panu

  • @user-jj3oo6jh1l
    @user-jj3oo6jh1l5 күн бұрын

    Chilungamo mchimenecho palibe nkhani yowamangira akunena zimene akudziwa km panja ukankhala olakwa umafuna umboni udzibisika anthu atopa nanu anthu 9 pakamodzi ai mudaonjenza tulanidi pansi udindo bwanji kd anthu amamwalira ochuluka pa ulamuliro onkhaonkha wa mcp ena ifanzo zimankhala kt?

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala14933 күн бұрын

    prophet liabunya wanena kuti chakwera ali crean sakukhusidwa ndi imfa ya chilima. n wanena kuti 2025 azawinaso . mnya alomwe mwauponda

  • @ulemujumbe8501
    @ulemujumbe85015 күн бұрын

    All of us are angry 😡😡😡😡😡😡😡😡😡😡😡

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj5 күн бұрын

    Kodi mukufuna muzinamiza anthu Mesa imeneyo ndi voice ya kamulepu ndiye inu mukuti ya M'busa

  • @GraceBanda-t4r
    @GraceBanda-t4r3 күн бұрын

    😮sorry a Malawi ino indiyo nthawi yosiliza okamba choonandi sazapeza mtendere ndi dziko lapatsi bible ikutelo

  • @BlessingsNyirenda-ru7ss
    @BlessingsNyirenda-ru7ss5 күн бұрын

    This is not a bad voice

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w5 күн бұрын

    Jipangeni respect mwekha kuyowoya nge wana yayi, wana wasambizgeni makola

  • @user-nt4fr2le3f

    @user-nt4fr2le3f

    4 күн бұрын

    Iwe ndiwe ukulemba nge ndiwe mwana,chifukwa icho walemba uchimanya yay

  • @user-ms8tm3yf7d

    @user-ms8tm3yf7d

    3 күн бұрын

    Imwe namwe ndiwe wachindere munthu waleke kuyowoya uwo mbunenesyo kupusa kwako iwe mumalenge mosi nthena na Boma ili mukuona yayi likukoma wanthu mwe mukopha

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy5 күн бұрын

    Ndingomva ngat nditukwane mwina mtima undiphwa chakwera asandiyakhulise pa mbali

  • @EdwardMukholi
    @EdwardMukholi4 күн бұрын

    Mr chakwera sinu amuyaya PA zomwe mukuchita

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d4 күн бұрын

    Ndipo chakwela waputa m,kwiyo wa mulungu kumanga azibusa ndiwe otembeleledwa ndi nduna zako

  • @user-xo8ms5wh2s
    @user-xo8ms5wh2s4 күн бұрын

    Achakwera mizimu yakwiya olo mutawamanga onse amene akulakhulawa koma akasiya anthu wa kulakhula Mlungu adzutsa myala kuti ilakhule za imfa ya Chilima

  • @SabitSamohgruva
    @SabitSamohgruva5 күн бұрын

    Kodi zikukhala bwanji voice imeneyi ndiyomweso anamangidwa nayoso Akamlepo Kalua ,? Ndiye koma atumbuka onse samangidwa

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo4 күн бұрын

    Nanunso apolice mwasowa zochita, mumangatu ndye amalawi onse hiyaaa osangozitsiya bwanji? Akukulipirani ma million angati?

  • @user-kl5fo1rb5z
    @user-kl5fo1rb5z4 күн бұрын

    Wayankhula chizungu chakumpoto amvana okhaokha

  • @user-gg6uh2wo4x
    @user-gg6uh2wo4x5 күн бұрын

    Choti muziwe dziko lino ndi la demokilase mphamvu ZOMWE muli manasozo tsiku lina sizatha ndie NDI pamene musalimve dziko kununkha agalu anu

  • @user-it5zv2nz7f
    @user-it5zv2nz7f5 күн бұрын

    Remember Bingu atakangana ndi Synod ,mkumanga anthu akupeleka maganizo awo inuyo ngat muli ndi umbon tiwuzen,munthu mwamuchita tintin Chakwera wopusa kwambiri

  • @kajawejawadu7844
    @kajawejawadu78443 күн бұрын

    Kwachema akutapa.

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu68904 күн бұрын

    Boma likupindukanji pomanga anthu amene AKULIRA MOBANGULA ?

  • @jamesgama5489
    @jamesgama54894 күн бұрын

    Tonse alliance osawopa logo

  • @BlessingsNyirenda-ru7ss
    @BlessingsNyirenda-ru7ss5 күн бұрын

    Police sono yanyanyisa esh there is no reason kut amumange uyuyu

  • @LeendaDeborah2005
    @LeendaDeborah20055 күн бұрын

    Komatu nde mumanga ndi azungu omwe. Cos enanso akuyankhula zokuti ndegeyi mudaipangila plan kuti igwe

  • @ceciliathole
    @ceciliathole5 күн бұрын

    Mulungu si analume for tipemphele kuti mutuluke abusa chilungamo chimamasula

  • @user-ig9qk6gi6g
    @user-ig9qk6gi6g5 күн бұрын

    This pastor was saying the truth. Why mu kumumanga?

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri68735 күн бұрын

    Ine pamene ndavera audio ya busa anga cholakwa sindikuchiona. Ngati aboma or kalaya mayi yolamu akuti ndege inafika ku mzuzu apereke umboni kuti tipeze ngati abusa ndiwolakwa ndege kusowa 10 o'clock kufufuza kuziwisa 4 o'clock mmm ndiye muzimanga anthu wu police munaphuzira kuti wopanda nawo zeru

  • @dysonmsamba5778
    @dysonmsamba57784 күн бұрын

    KOMA NGATI MULI NDI INFORMATION INA YAKE MUKAWAUZE A POLICE KAPENA ANY EMBASSY THAN KU POSITA IZI CHOMWE MUNGADZIWE MUKHOZA KUYAMBA KUMENYANA OPANDA CHIFUKWA CHENICHENI NONSE MUUPEZE MNTIMA

  • @CHIWSABINYAMBOSE
    @CHIWSABINYAMBOSE5 күн бұрын

    Chapha chilima chachakwerachi mfiti

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz4 күн бұрын

    Kwacha Kwacha basi😂

  • @HsjsmzmHsjsnsjaja
    @HsjsmzmHsjsnsjaja5 күн бұрын

    Ndiye mumanga angati

  • @BlessMnyenyembe
    @BlessMnyenyembe5 күн бұрын

    Mulimosemo kumeneko chilungamo chioneke

  • @jomochirwa
    @jomochirwa5 күн бұрын

    Njee wamangidwa chonchi basi ?

  • @RhodneyBwa3
    @RhodneyBwa34 күн бұрын

    Angomuttulusa mwaulemu

  • @SamuelMthengo
    @SamuelMthengo5 күн бұрын

    Kodi ufulu omwe timaukondwelera uja uli kuti?why are we still moving backward?

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p5 күн бұрын

    Chakwera anapha chilima

  • @isaacchirwa9518
    @isaacchirwa95185 күн бұрын

    Thanks you for arresting him, akanene bwino komanso akapereke dzina la police yemwe anamuuza kuti palivi zoti ndege ya vice president ikubwera ku mzuzu

  • @user-nw6ie3xx8b
    @user-nw6ie3xx8b5 күн бұрын

    Aaaaaa that's why kuzolozolo wanambembe muchalitchi

  • @user-nv3rf7bl7r

    @user-nv3rf7bl7r

    5 күн бұрын

    😅😅😅😅😅 imwe mwaneneska ka mubusa nayo vikamukhuza nivi va ndege

  • @user-rm2xv8ys1i
    @user-rm2xv8ys1i5 күн бұрын

    Ineso ninamva same thing abusa anthu muwatuluse pls

  • @sinoiajamu9484
    @sinoiajamu94845 күн бұрын

    Same thing is Wrong ndiboma, pamalilo people are free to say what ever they fell why arresting them government did you do anything on SKC if not stop this nonsense,MCP don't bring Kamuzu lifestyle to us

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem5 күн бұрын

    Police yakumalawi kupusa ndchifukwa mukumafa muli amphawi shit

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d5 күн бұрын

    Sorry abusa chakwera azafa chagada

  • @ChimwemweJuwao
    @ChimwemweJuwao5 күн бұрын

    M c p chimpani cha magazi

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1p5 күн бұрын

    Mlw so bad

  • @Kilocssreaction
    @Kilocssreaction5 күн бұрын

    Palije apo chifukwa chakumangira mnthu mmalo mwakuti mlimbane namasuzgo ayo yali mumalawi imwe bizy wa mcp kukoma wanthu mwezi uno pera mwakoma wanthu 10 nakuyamba kukaka wanthu pala wamuzuzulani mapoli mose mlije no zeru yyi vimavi vinu this is no one party system this is democracy" how many people u need to kill?

  • @user-nv3rf7bl7r

    @user-nv3rf7bl7r

    5 күн бұрын

    Imwe namwe zeru mulije mukuwa nga ndimwe wachewa kutinangila mutundu chaa ise wanthu wala wslikufwa kwithu ku mzuzu wakawa wa mcp

  • @user-nv3rf7bl7r

    @user-nv3rf7bl7r

    5 күн бұрын

    Iye muliska va ndege vikamukhuza niviii ndiwo wakuwa waliska waboza awa wanyawo wakuwa busy kupemphelela malawi kuti muwe mutende iyo walibusy namilandu nawanthu wachita makola kumumanga wakayowoye chilungamo

Келесі