Kungoyelekeza Kuti Chilima Ndi Mgelo Enanu Pa Gate Ya Ku Paradizo Akakubwezani - Samuel Lwara

On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara continues to mourn the Vice President saying that, it is not right to praise someone when they are dead instead of when they are alive.
Pa Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara akupitiliza kulira kwa Vice President ponena kuti, sibwino kuyamika munthu atamwalira mmalo momuyamikira ali moyo.
#malawi

Пікірлер: 29

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk17 күн бұрын

    Rwala mwandililisa ine Chilima anali munthu wabwino anthu amangomunda koma kufa kwake sikupita pachabe

  • @BryantLusungu
    @BryantLusungu17 күн бұрын

    Unenesho wakulu,ndilinamwe lumoza

  • @4ourcusworldwide426
    @4ourcusworldwide42617 күн бұрын

    Tilibe masophenya.

  • @alexsumani6823
    @alexsumani682316 күн бұрын

    Thanks for speech fearless comrade,but stop attacking DPP please

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie16 күн бұрын

    N nw what is the result of joining MCP tell me nw?

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira16 күн бұрын

    Utm yambanipo kupanga identify munthu amene angatenge chipani pa tsogolo. Also inu a catholic, you must play a crucial role and decampain mcp. We are heart broken ndi infa ya chilima

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v16 күн бұрын

    A Lwara the court did not say anything about DPP kubela chisankho, put your facts correct otherwise you may lose test. Chilima was not a saint the way you talk about him. Chilima was answering corrupt charges. So while we mourn him but do not speak no sense. Helping people or church using stollen money will not make you to heaven.

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm16 күн бұрын

    Akulu nyati dzoyangula zatha siyani chilima ndi amene anatipereka ife kumavuto brother ndipo iyeyo zovuta amalawi dzimasangalasa kwambiri sanari wabwino brother cz anthu akamuudza kuti atukuke msp amakana amava kukoma anthu akuvutika

  • @user-iu6mr5xu6r
    @user-iu6mr5xu6r16 күн бұрын

    Rwala, Khalidwe lotukwana ndi la aliyense kwathuko. Kumbukira kuti inu ndi anzanu munanyoza Peter kuti mdala opanda mano, lero munyoza Chakwera, MCP anyoza ena panthawi ino. Ndadelera!

  • @CharlesmakveliNyirenda
    @CharlesmakveliNyirenda16 күн бұрын

    Siya zoti Malawi onse adamutukwana inu nokha a MCP cholinga muphe mu2 iwe mboli ya mukazi wako Panya pa chakwela nyemba ya pa nyini first lady Monica chakwela 😊

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI16 күн бұрын

    Mwana oukila makolo ake amavutika paka kufa ...A p m sanamuphe

  • @user-ti2ct8ts8d
    @user-ti2ct8ts8d16 күн бұрын

    Chilima anali kuboma komweko,palibe chomwe akapangako?ndiye akome lelo chifukwa anamwalila?RIP Chilima Koma munatisiya mavuto

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i16 күн бұрын

    Khani yabwino koma amene akulila ndiathu ambili atuluka lelo kuziwonesela chifukwa kumbuyoku ukazowonesa kuti ukusapota UTM kapena DPP ndekuti ndiwe dani waziko lachakwela koma Pano tayuka poyela cz taziwadi kuti mbatata dingasithe kukhala chinangwa MCP ndi MCP koma khani ndiyakuti amalawi titong'ole masoathu kuti achakwela 2025 abwelele kuchipiku olo kuubusa koma chilima ambuye apitilize kusamala mzimuwake kumphatikizaso ndiathu ena 8 ambuye awafungatile koma ifa chilima mmmm zikungokhalanga anapita kwanakwake ndipo😭😭💔 azabwelalaso

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r16 күн бұрын

    Ndi mmene zimakhalila lelo adpp ndi angelo pamarilo achilima abingu anaga ifa yowawa anthu kusangalala ngati kwafa galu koma lelo akuti bingu anali wabwino ndiye mmalawiyo

  • @user-ms8tm3yf7d
    @user-ms8tm3yf7d10 күн бұрын

    Pena pake iweso umapalaso bwanji lero nde palibe chanzeru

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h16 күн бұрын

    DPP idamusiya ndimoyo nanga MCP ng'ona komanso ngati mulibe zonena ingomezani Samuel

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r16 күн бұрын

    Lelo mwalalikila ndipo msanyozeso mulungu walowa mwa inu tilape amalawi or kalindoyo amamtokwana chilima kwambili lelo akuti ndiwabwino koma chakwela azayima mulungu azatetezela bolani chakwela kusiyana ndi agoviw zikomo tiyeni tiirile mafilo tisaphatikize ndale

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira16 күн бұрын

    Palibe munthu angavotere nkhope ya chakwera ndi mcp forget it

  • @augustMag
    @augustMag16 күн бұрын

    Mundaonapo mtembo kapena kuti maliro akutikwanidwa? DPP mukunenayo Sanamuphe anamusiya moyo kuti azipikisana naye pa zisakho kusowa chokamba eti? Ameneyi atchulidwa oyera akukadya nao mphando la kumwamba Hon: Chilima Ndipo Amalawi sasiya kuyankhula za muthu ameneyu

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl16 күн бұрын

    Mumatukanana nokanoka a tonse ndi mcp lero mwayamba kulapa mcp ndi agalu

  • @user-em1qi8kj9h
    @user-em1qi8kj9h16 күн бұрын

    Bola DPP ...inamusiya ndi moyo...nanga kwanu ku MCP Mpaka munachita kumupha....zimenezo ndi ndale...DPP Imango wauza kayambiseni zipani zanu

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm16 күн бұрын

    Ngati zoyangula zatha stop prz

  • @sylviachisama3829
    @sylviachisama382916 күн бұрын

    Neneri salandiridwa kwao. Amakachitidwa appraise ndi anthu akutali.learn from Jesus.

  • @CharlesmakveliNyirenda
    @CharlesmakveliNyirenda16 күн бұрын

    Ndi mwamupha mu2 phindu yanu ndi chani

  • @CharlesmakveliNyirenda
    @CharlesmakveliNyirenda16 күн бұрын

    Iwe panya pako chitsilu iwe panya pako mau kunyasa ngati chule

  • @InnocentMlowoka-ew4lo
    @InnocentMlowoka-ew4lo17 күн бұрын

    Because of stupid politics 😢

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm16 күн бұрын

    And don't talk about DPP prz chilima him was not good for malawian

  • @JamesMalango
    @JamesMalango16 күн бұрын

    Speech yalero ndiye ilibe attractive, aliyense amayamikiridwa akamwalira mukudziwanso inuyo

Келесі