Chipani cha UTM chalengeza kuti chatuluka mu mgwirizano wa Tonse Alliance

Пікірлер: 246

  • @julietbanda5203
    @julietbanda520321 күн бұрын

    Zakhala bwino kutuluka mumgwirizano, congrants utm and dpp my votes

  • @kelvinchola739
    @kelvinchola73921 күн бұрын

    Mmmm a Malawi chonde tengani Maiwa ngati mtsogoleli wa dziko la Malawi, ali ndi mphatso yaikulu Kambili. Kuchokela ku Zambia 🇿🇲

  • @spargomw
    @spargomw21 күн бұрын

    Ng'ona zizidyana zokhazokha tsopana😂😂😂😂😂😂 Ngat ali Chauta yemwe wakuuzan kut mutuluke, tingoti Alemekezeke Yehova coz ku Tonse mukadatha Psitiiiiiiiii. Atsaleko Manga yekha ku Tonse'ko😂😂😂😂😂

  • @FazackKambwiri-he8xe
    @FazackKambwiri-he8xe21 күн бұрын

    A UTM mwachita bwino kutuluka alliance yanu mmmm inali yakupha

  • @user-ml4bl2ll2g
    @user-ml4bl2ll2g21 күн бұрын

    Mwachita zimene mwini wake wa chipani SKC akadachita akanakhala kuti alipobe Ambuye akudalitseni utm senior leaders

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx21 күн бұрын

    mwachedwa nazo zinthu anthu inu. munawonerera muvi kuti ukuloweni m'maso ndipo lero ndizi chipani ichi sogolo kweni kweni silikuoneka

  • @JamesKadango-qs3ej
    @JamesKadango-qs3ej21 күн бұрын

    Congratulations faz for SKC

  • @willardkajalika-m8g
    @willardkajalika-m8g21 күн бұрын

    I'm just saying all the best mwachita bwino ndithu akhaleko okha akanganyawo

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika678421 күн бұрын

    Job well done 😅😅😅😂😂😂😂atsaleko adzidyana okha okha yomweyo mr Chikangawa 😅😅😅😂😂😂

  • @BlessingsmadalitsoShumba
    @BlessingsmadalitsoShumba21 күн бұрын

    Perfect breaking news 🎉🎉 i love it keep up ❤ utm

  • @GertrudeMakumba
    @GertrudeMakumba21 күн бұрын

    Zosangalatsa kwambiri changa chikunkhala chisoni mmmmm imfa imandiwawa

  • @DonexMajiga-su9yv
    @DonexMajiga-su9yv21 күн бұрын

    Dpp my vote😂😂

  • @joejoman4541
    @joejoman454121 күн бұрын

    ❤nw i can able to go home n start support our country

  • @CharlesChipwere
    @CharlesChipwere21 күн бұрын

    Mai kaliyati mwachita bwino kutuluka allance ndizomwe ndimadilira zikomo ndamva bwino kuchoka Kwa mavaphire sianthu away taonani mmene ikungwera kwacha sangakwanitse kuyendetsa boma

  • @user-ql8nf2vb8s
    @user-ql8nf2vb8s21 күн бұрын

    Very good very good very

  • @Dean-De-Matrex1
    @Dean-De-Matrex121 күн бұрын

    Zikomo UTM pothetha mgwilidzano umeneo ndi anthu akuphawa

  • @alexgweje8610
    @alexgweje861021 күн бұрын

    Mwachedwa inu mukadapanga izi nthawi imene Chilima adakali ndi moyo anthu amkakuuzani kuti mutuluke Alliance koma kusamva inu bwelerani ku Dpp basi

  • @SothinieKanjuchi
    @SothinieKanjuchi21 күн бұрын

    UTM for life ❤

  • @InnocentBanda-u8y
    @InnocentBanda-u8y21 күн бұрын

    Nde ndiwe mtsogoleli nkumawopa kukumana ndi anthu omwe ukuwasogolera pali zabwino pamenepa ndiyankheniko

  • @GracePendame
    @GracePendame21 күн бұрын

    Yomweyo apapa ndiye ziribwino

Келесі