JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke// PART 2

Пікірлер: 97

  • @gkay-striker
    @gkay-striker7 ай бұрын

    I love your speech Kapito keep on telling them the fact we have suffered for so long and this is too much now

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm7 күн бұрын

    This man has leadership qualities right away from secondary school days at Mulanje Secondary school . Malawi needs leaders of Kapitos cariber.

  • @phillimonzgambo1663
    @phillimonzgambo16638 ай бұрын

    Mr kapito God bless to open eyes all Malawian I never seen a man like you to openly talking nicely

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx10 күн бұрын

    koma boma ndi ndale zinayandikana kwambir mpake dziko silitukuka ku malawi. thanks mr kapita❤❤❤❤

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk8 ай бұрын

    Truth and powerful talking, proud of you Bwana Kapito, inu ndi mtondo, I salute you, ulemu wanu Bwana 🔥🔥🔥🔥

  • @mussamapira801
    @mussamapira8018 ай бұрын

    Tapangani chipani Chanu inu akapito muwina inu muli kuganiza Kwa u utsogoleri 100% ❤❤❤❤

  • @douglaskabekele7743
    @douglaskabekele77438 ай бұрын

    Mr Kapito ?? Thanks very much for your experience & knowledge Apatu mukulilira dziko lathu deep from your heart ❤ Mulungu..The heaven creator must

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr8 ай бұрын

    Koma Kapito ndi 🔥🔥😝😝🙏🙏❣❣

  • @Marthaphiri-oy4ub
    @Marthaphiri-oy4ub8 ай бұрын

    More power Mr kapita may God bless you you're a true reader mr

  • @McFranklinBanda
    @McFranklinBanda8 ай бұрын

    Properly articulated. God bless and good day

  • @user-hj1qo1nn5d
    @user-hj1qo1nn5d8 ай бұрын

    Powerful message mr kapoto

  • @user-nn9ow8rn8w
    @user-nn9ow8rn8w7 ай бұрын

    One of eye open master... Mr you know what you're saying, God bless you... MCP ibwelere ku opposition kumene Kujadi ndi mbali yawo

  • @atupelejameschalirankhom-yi4df
    @atupelejameschalirankhom-yi4df8 ай бұрын

    what u r saying Mr kapito it's real true we are suffering in many occasions so we need a patriotic leader

  • @PaulKamudya-bf3vx
    @PaulKamudya-bf3vx8 ай бұрын

    Great and true saying Mr kapito

  • @victorkaphaso4663
    @victorkaphaso46638 ай бұрын

    You are a true man of God, Mr Kapito. May the Good Lord, Jesus Christ, bless you and your family

  • @chrischigoma5854
    @chrischigoma585410 күн бұрын

    Mr Kapito tikupempheni mubwere ku UTM muzatiyimilire u president ine ndimafuna munthu wosatila zama Reform ngati inu bwana

  • @edgarzimba1153
    @edgarzimba11538 ай бұрын

    Mr kapito we thank God in everythings ❤

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga7238 ай бұрын

    Thanks Mr kapito telling trueth

  • @raytavares2256
    @raytavares22568 ай бұрын

    Mfiti yayikazi ikulamulira dziko la Malawi ndiye walodza aliyense kudwala manthong'o😢 mu ndale za nyasalande.

  • @TichezeChitukula-zn5xh

    @TichezeChitukula-zn5xh

    8 ай бұрын

    😂😂😂. Mfiti yayikazi ndiyowoopsaa kwambiri

  • @user-oh9bh1cl3b
    @user-oh9bh1cl3b20 күн бұрын

    That's talking mr kapito, tell them n open the eyes for Malawians ❤

  • @user-oq7hi3hd4p
    @user-oq7hi3hd4p2 ай бұрын

    You deserve my credit.

  • @AngellaMaja-pg3op
    @AngellaMaja-pg3op8 ай бұрын

    Awa ndiakatudu 🎉🎉🎉🎉

  • @MosesNgozo-nf9gr
    @MosesNgozo-nf9gr8 ай бұрын

    Thank you very much bro chakwera alibe zeru ndi BULUTU wachabechabe ndi Chilima wakeyo

  • @IshmaelNesta-rb8dx
    @IshmaelNesta-rb8dx8 ай бұрын

    You have a big word Mr Man....I really wish we have dozen like you.... Malawi can change so far

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt8 ай бұрын

    True what you're saying Mr kapito

  • @user-kp1zc6su3k
    @user-kp1zc6su3k8 ай бұрын

    Keep it up to mr kapito ❤

  • @jonas-xh4hz
    @jonas-xh4hz7 күн бұрын

    iam agree with you big kapito you are talking truely but dpp was tried than this

  • @user-jk8zt2oq4w
    @user-jk8zt2oq4w7 ай бұрын

    Proud of you Mr kapito

  • @MikaNamwada
    @MikaNamwada21 күн бұрын

    Well said kapito 🔥🔥🔥🔥

  • @user-kr6ng3zp7v
    @user-kr6ng3zp7v8 ай бұрын

    Kapito thank you for opening our minds

  • @KenesiDaitoni-ob5st
    @KenesiDaitoni-ob5st8 ай бұрын

    kapito ndimunthu oziwa zasogolo komaso ndimuthu waluntha kwambili

  • @ArnoldBinali

    @ArnoldBinali

    19 күн бұрын

    Ndipo kwambili

  • @mijerimasiye7310
    @mijerimasiye73108 ай бұрын

    Mr kapito mwakambatu za nzeru kwambiri

  • @JimmyMawanga
    @JimmyMawanga21 күн бұрын

    Dont provoke DPP, we hate them earlier, and chose to change, DPP remain silents for us to taste and enjoy our choice.

  • @Dakamacdonald-sl4rk
    @Dakamacdonald-sl4rk13 күн бұрын

    True son of malawi kapito

  • @petermasenti2084
    @petermasenti20848 ай бұрын

    Mr kapito inuyo ndi a bodza nthawi ya dpp mumapanga ma demo Koma pano zinthu zikulakwikwa mwangokhala chete chifukwa Mukudya nawo ndalama, chotsani kaye chisoso chili diso lanu musanayambwe mwawona chili mwa zanu

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm7 күн бұрын

    Nthawi imeneyi dpp imalamula otsutsa amatsutsa zimene iwowo akhoza kukonza zinthu koma zinthu sizinasithe ndiye lero kuti dpp azitsutsa a mcp akhoza kumati munali m'boma momwemu mumatani ndiye izi ndi zandale zozuta kumalawi bas

  • @winstonpchilonga6712
    @winstonpchilonga67128 ай бұрын

    I saw the whole interview, Walakhula zilungamo zenizeni

  • @achithoko1981
    @achithoko19818 ай бұрын

    Nyau yalira mokweza pk kutukwana😅😅

  • @user-zj2dr2rp1e
    @user-zj2dr2rp1e8 ай бұрын

    Chikhulupililo chatha Brian pa boma la Chakwera, eish! Kaya tilowere kuti a Malawi. 😢

  • @PetroMatias
    @PetroMatias10 күн бұрын

    Mmakwana inuo mulibho

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga23 күн бұрын

    Akapito mukuyakulazoozake muntuamenesamafunakulagizidwaamaonogeka achakwela akupezamavutochifukwachosavela mulungu awatadize kwabili

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn8 ай бұрын

    Malawi watelekedwa pamoto pano ,kwende nayo tilikumastand kuno tione zomwe Mulungu atichitile amphawife

  • @raytavares2256
    @raytavares22568 ай бұрын

    Dpp ikudwala adverse reaction yotchedwa covid 2024🎉❤🎉😮

  • @user-hu8vp4wt7j
    @user-hu8vp4wt7j8 ай бұрын

    Kodi Mr kapito mukulakhula bwino kwambiri ngat big man bingu anakusilani zeru asanamwalire or bwanji

  • @user-kp1zc6su3k
    @user-kp1zc6su3k8 ай бұрын

    Our president chakwera , He was thinking to rules world is easy 😂😂😂

  • @JossumPhiri-qx9jx
    @JossumPhiri-qx9jx8 ай бұрын

    See the real malawian citizen 💯

  • @Syakinongwa
    @Syakinongwa21 күн бұрын

    CS wachisawawa ngati ameneyu

  • @fysonbilly4123
    @fysonbilly41237 ай бұрын

    You Said Chakwera doesn't have experience simply mean he cannot run the government,,,

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc8 ай бұрын

    Maso phenya yanga ine mr simbi phiri koma apo biii malawi never come alright never

  • @SheenahMwalabu-iz3pr

    @SheenahMwalabu-iz3pr

    8 ай бұрын

    Ndipo zoona zake ❤

  • @user-mc8gk4xv3f
    @user-mc8gk4xv3f8 ай бұрын

    Komadi a kapito ndiinu ofonikira mutakhala president wa dziko

  • @rachelbanda2131
    @rachelbanda21318 ай бұрын

    😂😂😂it's sizibwera pa manja koma wakaaaaa😂😂😂zalowa ku account

  • @louismlanga2230
    @louismlanga22308 ай бұрын

    Komandekulakhula mosaopa eeeehe

  • @frankkasenda9252
    @frankkasenda92528 ай бұрын

    Malawi lawi la moto

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d8 ай бұрын

    Eeeh ok hp u r saying the fact , kma ndie zosaenda , apa nkhani yakula anthu azindilambila pa chifukwa choti ine ndi wankulu than enawa zavuta. Vuto ndi lomweri nsogoleri wadyela osakonda ziko lake

  • @kejescompany-zi1ft
    @kejescompany-zi1ft7 ай бұрын

    Zaziiiiii Mesa malawi ankauzidwa kuti MCP dizinthu Koma okha Amafuna dala nde mukufuna DPP izitani? Asiyeni a DPP azipuma... Mesa mumati asogoleri aDPP samatha kulankhula nde mukufuna chani?,,, mpando wa u president anausiya mopanda kukangana ndi munthu kuutengaso azatenga mosakangana ndi munthu.... Zomwe mukukamba zikunveka zanzeru Koma musalimbane ndi DPP, am not a politician but,, vuto si DPP or MCP Koma tokha amalawi timafuna kusintha now kusintha takuona.. Then next choice we shall make it with real sense.

  • @preciousdyton910
    @preciousdyton9108 ай бұрын

    Akapito ali ndi nzeru 😮munthu wanzeru amaoneka polankhula

  • @user-fr3ge2hf6s
    @user-fr3ge2hf6s8 ай бұрын

    Mr kapito zikomo tikuziwa zambiri koma amalawi tikuvutika 😱

  • @namberalovemore2056
    @namberalovemore20568 ай бұрын

    😂😂😂 Koma mkulu uyu sapsatira

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o22 күн бұрын

    Koma mwamumva wanena tu kuti a DPP ndi anthu ozikonda a kunama? 😂😂😂😂😂😂😂

  • @stephancommercial580
    @stephancommercial5807 ай бұрын

    Where were you⁉️ here to go

  • @richardbanda9997

    @richardbanda9997

    21 күн бұрын

    A Kapito izi mukanakhala Kuti munayamba chonchi poyamba atakupatsani udindo Ku Cama, bwenzi nditakupangani salute Koma Ai udindo wanu ,mumangodya osaganizira the poor Malawian as poor consumers. SHAME, mukufuna udindo winanso? People have been criticizing you for not assisting them as per your responsibility to Malawians.

  • @user-yk1dt1vj2x
    @user-yk1dt1vj2x8 ай бұрын

    Iwe ndi fisi bakha mbalame Kodi si inu nomwe dpp ikakonza zinthu mumawononga inu nomwe munati achoke osatenga iwe bwanji bomalo ukhale wanzeru kuliratu uku ukumufuma peter kuti abwelere unali kuti anthu amaphwanya sukulu misewu yomangamanga takhalapo bwino nthawi ya Bingu tikukumbukila sizoyenela iwe kutiuza unali kuti iweyo

  • @user-fl5im4us7x
    @user-fl5im4us7x8 ай бұрын

    Chiyembekezo pa chakwela tinasosa

  • @samdiverson9733
    @samdiverson97337 ай бұрын

    vuto ndi nankhumwa he is sleeping sakulankhula kanthu😴

  • @AustinChiyembekezo-cx4mz
    @AustinChiyembekezo-cx4mz8 ай бұрын

    And it's very true why Dpp annoying,ana

  • @rodrickphiri

    @rodrickphiri

    8 ай бұрын

    DPP will never bounce back is dead and the country is moving without opposition this is pathetic

  • @patriciap.bandah3385
    @patriciap.bandah33858 күн бұрын

    Panopa ndawamvesa a DPP chimene amakhalira chete President uyu ndi wamagazi ifeyo tikuziwonela kunja koma anzathuwa akuziwonela pafupi President uyu si munthu wabwino a DPP akhalebe chete mpaka campaign iyambe

  • @samdiverson9733
    @samdiverson97337 ай бұрын

    ngwabodzadi president yu

  • @AkimuKalinde-kx4cn
    @AkimuKalinde-kx4cn8 ай бұрын

    chakwera sinikumuonera kukondwa ta mins watipha

  • @user-my5jj5we5j
    @user-my5jj5we5j3 ай бұрын

    Voti yaimwe yilipo

  • @ChamboChange-pq1hd
    @ChamboChange-pq1hd8 ай бұрын

    Chakwela ndi galu kwabansi tsiku transport moyenda

  • @BwanaGD
    @BwanaGD21 күн бұрын

    Dpp ikamatsutsa zinthu zopusa tikumati kusagwilizana kwakuchipani kwanuko musabweletse kuno

  • @ChomeNgondolo-uh5mu
    @ChomeNgondolo-uh5mu8 ай бұрын

    President wathu akulamulila dziko lonse lapansi osati Malawi yokha 😂😂😂 ndipo ndege ndiye siyikwatopetsa 😂 tsiku ndi tsiku asilikali akuvina pelete ku airport😂😂😂😂

  • @paulpaseli6310

    @paulpaseli6310

    8 ай бұрын

    😂😂😂

  • @SheenahMwalabu-iz3pr

    @SheenahMwalabu-iz3pr

    8 ай бұрын

    😂😂😂😅😅😅

  • @daviemungadetse1222
    @daviemungadetse12228 ай бұрын

    Koma kapito ndi akatundu

  • @user-cg8vg5mr6x
    @user-cg8vg5mr6x8 ай бұрын

    So that the best solution he must step down........pa 11 ma demo alipo omuuza kt atule pansi udindo

  • @phpgeek6259
    @phpgeek62598 ай бұрын

    No direction. No hope

  • @henryhenry6632
    @henryhenry66328 ай бұрын

    Machende ako kapito , panga chipan chako mbuzi ya munthu

  • @omarajibu860

    @omarajibu860

    8 ай бұрын

    Ukumtukwana Kapito chifukwa chani? Are you a beneficiary of this rubbish happening now?

  • @omarajibu860

    @omarajibu860

    8 ай бұрын

    Ngati dziko lisakuyenda bwino it's because of people like you, arrogant.

  • @henryhenry6632

    @henryhenry6632

    8 ай бұрын

    @@omarajibu860 achawa machende anu

  • @amisichiphiri8227

    @amisichiphiri8227

    8 ай бұрын

    Munthu opanda mzeru ongutukwana anthu osalakwa

  • @MuhammadTennes-tx5ti

    @MuhammadTennes-tx5ti

    8 ай бұрын

    Anthu osafuna kudzudzulidwa aja ndi amenewa ,nkhani kutukwana basi,why kumtukwana Kapito? Mfundoyo yamubaya kkkk