Episode 14 My clean crush l Q&A, in this episode Mada and Linda answered your questions
Комедия
To support the channel
everything podcast and comedy: linktr.ee/madalinda
membership:
contact us +265983705090
join our support group chat.whatsapp.com/CG7PfAu9eJL...
Meet the team
Hosts: Mada and Linda
Guest: Isaac the duke
camera: Paul Da-Teacher Manda & Mac-hour multimedia
sound: Mac-Hour multimedia
graphics designer: Dunamis +265 994 68 29 62
to book mac-hour multimedia:
Don't forget to Like, share and subscribe
#madalinda #malawi #comedy
Пікірлер: 28
Inu mumandisangalatsa kwambiri, keep up girls, uhv bright future
Ur the stars madalinda
Mumata alowe anzanga inu❤❤ ndimafuna titakumana
Koma nde ine ndaphuzilapo kathu mulungu akudalisen azanga inu.
Mwantchenatu atsikana l love uuu❤❤
Ana mawila, olo kwathu kuchiyao ndi chocho.
Izi ndiye zimene ndimaziwa asikana akumalawi simumamasuka kulongosola zimene mumakonda mu relationshp. is high time now you should be free to explain what you love in a man so that we should be able to judge ourselves before approaching you. At your ages if you don't know what you want in a man you'll end up with a wrong man ndikumalilira kuwusi nthawi ndikumapita.
Nice girls 😂
a anamayela ndaziwa nawo kkkkkkkk
Inuyo mumatha mafana❤
I envy you for you speak the language I love
kkkkkkkk kma ndaseka asa u guys mabebesa
Kkkk koma inuyo you’re so funny
vishin amatsiwa sekeseke kkkkkk linda iwe
❤
Mwabweera
@Benja2000min
6 ай бұрын
Ndife onyadira
Akhwaka mwatchena
Nice girl 😂😂
Inuyo mumutha
Kodi muli ndi zaka zingati nanga nditati ndakufunani ndingakwatere nonse ?
nice
Iiii koma atsikana inuyo haa ndi one
Mumandisangalsa ndi nkhanizanu girls..kodi masut anuwa munagula osokasoka??enao ndizakusokereni ineyo
Mimba jeee gaiwa uponya kuti❤
Ndiyaluka🤣🤣🤣
no more cathdraws my sister's chifukwa papa wanu waonetsa uchitsilu dziko lonse lapansi