Episode 12 my clean crush l Kwacha devaluation, who cheats more in a relationship?

Комедия

To support the channel
everything podcast and comedy: linktr.ee/madalinda
membership:
/ @madalindacomedy
www.maso-awards.live/category...
Vote for Mada and Linda as best Comedians on maso awards by following the link above
contact us +265983705090
join our support group chat.whatsapp.com/CG7PfAu9eJL...
Meet the team
Hosts: Mada and Linda
camera: Paul Da-Teacher Manda & Mac-hour multimedia
sound: Mac-Hour multimedia
graphics designer: Dunamis +265 994 68 29 62
Don't forget to Like, share and subscribe
#madalinda #malawi #comedy

Пікірлер: 53

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i8 ай бұрын

    This conversation is good komano mada and Linda musamachite makani kwambiri,try kudekha nzanu alankhule amalize kaye,kenako muziyankha

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    Zamveka

  • @PeterChilombo-ou2cd
    @PeterChilombo-ou2cd2 ай бұрын

    ndizoona mahule okwatiwa otiali ndiazimuna ao alipo inuyo simunazione kkk

  • @mphatsomonjeza4371
    @mphatsomonjeza4371Ай бұрын

    Mmmh azimai masiku ano aopsa azimai akufuna ndlama kwambiri dzibwenzi 4muntju mmodzi ndiye akuti kuli ma MG2🙌🏻 ayi Zikomo

  • @AsimenyeMweneungu
    @AsimenyeMweneunguКүн бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂 eee koma guy's mumatha

  • @daudmasikam
    @daudmasikam8 ай бұрын

    I love you my 2 sisters mada and linda big 👆

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o2 ай бұрын

    Ndipo azimbo abwino alio example ndi wanga❤❤❤

  • @AlinafepiliraniMbale-md8en
    @AlinafepiliraniMbale-md8en8 ай бұрын

    Mada and Linda Bwerani Mbali zakuno nzakuonetseni wangayu satchita nawo.

  • @LeviMalanda
    @LeviMalanda18 күн бұрын

    Koma azibambo ali pa top kunama😂

  • @user-yx1te9gi7o
    @user-yx1te9gi7o4 ай бұрын

    Kkkk mumakwana

  • @user-lx8ow6ek6k
    @user-lx8ow6ek6k8 ай бұрын

    😂😂😂 ine ndilipo ndili ndi mkaz modz

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    Zopanda umboni zimenezo

  • @jackiendlovu9564
    @jackiendlovu9564Ай бұрын

    Atsikana inu chomwe munhadziwe ndizakuti nkazi ndiopolila komanso amavomeleza momwe mwamuna wake alili , ndipo amakhazikika pamenepo ndipo amapanga ntchiti akamuone mwamunayo zomwe akupanga komanso nzomai samapanga ntchiti the time amamuonetsetsa kaye akatopa nzimai ndipamene amapangano ntchiti nzomai good day

  • @MemoryLester
    @MemoryLester2 ай бұрын

    Am with u sisters it's better to be single kusiyana ndikumasamala munthu moti sasamala zaiwe

  • @user-qq6lw6yo8y
    @user-qq6lw6yo8y6 ай бұрын

    Linda ndi Mada, amuna odziletsa alipo ndithu ambili, amene amakhutitsidwa ndi mkazi mmodzu

  • @user-hq8yn8tl1h
    @user-hq8yn8tl1h8 ай бұрын

    Nkhaniyo si sayizi yawo😮😮😮😮

  • @ConeriasPhiri
    @ConeriasPhiri2 ай бұрын

    Kulibe mamuna amene Ali okhulupilika

  • @hardworkkayuza6353

    @hardworkkayuza6353

    2 ай бұрын

    Ndpo kwambili,,azimai akakwatila anakhutisidwa😘😘

  • @user-hq8yn8tl1h
    @user-hq8yn8tl1h8 ай бұрын

    Tianato sitidziwa kanthu😅😅😅😅

  • @user-xz5ov7oy4r
    @user-xz5ov7oy4r8 ай бұрын

    Akazi amapanga shirt mowonjeza

  • @alicehananiya
    @alicehananiya8 ай бұрын

    Mada umakwana🎉🎉

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    😘😘😘

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa15568 ай бұрын

    Tili munyengo yasakhulupirirana😂😂

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    Umukhulupilire mwana wa ndani? 😂😂

  • @ThomsonMusowa
    @ThomsonMusowa8 ай бұрын

    Kutaya mimba ndikupha dziwani kuti umoyo wachinthu umayamba pamene wadzindikila kuti uli ndi mimba tsono mumapha munthu yemwe wayamba ulendo. wamoyo.

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    Eish

  • @marygoza1205
    @marygoza12058 ай бұрын

    Ine amuna anga sapanga cheat ndati ndisutse zoti palibe amuna osapanga cheat 😂😂

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    Mulibe umboni iyaa 😂😂😂

  • @yamikanimkanthama4354
    @yamikanimkanthama4354Ай бұрын

    Azmay or mwalusa koma mwachepa

  • @LodrickJamitoni
    @LodrickJamitoni2 ай бұрын

    I can say that now there is a lot of cheating but I agree with him, Milliyam Azimai is the most vulnerable.❤

  • @matembanevermind-po3me
    @matembanevermind-po3me7 ай бұрын

    Kkkkkk

  • @FatimaKananji-kz6yx
    @FatimaKananji-kz6yxАй бұрын

    aliyese pauwili wawo wose alipabanja akuzembela nkazi wake musamanene kt akazi uwule akupanga nkasi nimamuna eyetu

  • @WilsonMwale-yu4js
    @WilsonMwale-yu4js6 ай бұрын

    Inu ndiaboza Gati popo akugonana ndi Amina azake posana pawo

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure8 ай бұрын

    Mada, mada ndi Linda mukunena zoona

  • @JamesMalango
    @JamesMalango8 ай бұрын

    To be honest Mariam akunena zoona

  • @MussahHassan-pj7il
    @MussahHassan-pj7ilАй бұрын

    Umeneo nde uhule kulimbikisa kutamimba anthu

  • @bornface4786
    @bornface47862 ай бұрын

    Alipo azibambo okhulupirika ndithu and ine ndi m,modzi wa iwo

  • @user-kn7pv5wt2r
    @user-kn7pv5wt2r8 ай бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    😂😂😂😂

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283Ай бұрын

    Pa nyini panu nonse

  • @louisgolden
    @louisgolden8 ай бұрын

    Azibambo samapanga zinyengo Ngati nkazi akukanika mnyumba

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    😂😂😂😂😂

  • @FatimaKananji-kz6yx
    @FatimaKananji-kz6yxАй бұрын

    amarriam uwule nditima muone

  • @robertsitifano9021
    @robertsitifano9021Ай бұрын

    Winayo sapato zili kuti?

  • @user-ep9rk2nr8j
    @user-ep9rk2nr8j2 ай бұрын

    Mada and linda try to calm down when someone is talking And palibe chimodzi chomwe mumadziwa chukhuza banja akunena zoona malliam kuti mukwatile koma chimene ndingakuuze its not all man are shirting and nkazi ndimunthu oyipa one tou will reglet what malliam was light

  • @ThomsonMusowa
    @ThomsonMusowa8 ай бұрын

    Mukunamizana azibambo alipo okhulupilika

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    Mubweleseni poyera timuwone

  • @louisgolden
    @louisgolden8 ай бұрын

    Azi bambo tilipo ambiri wokhulupilika

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    😂😂😂

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    Zokayikisa

  • @ThomsonMusowa
    @ThomsonMusowa8 ай бұрын

    Inu mukukambilana. 17:09 zimene muli mubanja?

  • @MadaLindacomedy

    @MadaLindacomedy

    8 ай бұрын

    Mubanja tizikatanimo?

Келесі