CRUISE 5 WITH ETHEL KAMWENDO BANDA
Follow the truly inspirational story of Ethel Kamwendo who was born of humble parents, struggled with her mother through childhood, never excelled in school but managed to get her breakthrough after making it in music. Ethel is now arguably the leading female gospel singer in Malawi, mesmerizing audiences with her wonderful stage work and amazing voice.
As a born again Christian and Pastor, she says she owes all her success to God who rescued her from a potentially dangerous life style.
Пікірлер: 91
2024 watching this video God bless Ethel Kamwendo Banda you're my favourite 🇲🇼🇿🇦 watching from capetown RSA
Amen kulowelera ndi mtima aunt Ethel ndadutsamo menemo ..anthu amakuona ngati iweo ukulowelera koma saziwa kuti ifeo amakhala ali mamvuto ....mwandikumbutsa nyengo zanga mukatchansomo amai aphikamo ma bar tagwiramo oona kumaona ngati uhule mmmmhh amane mumaweludza moteronu ndimakudandaulani .osatiweludza koma kutifunsa Mulungu ndi mulungu ositha zinthu Amen aunt Ethel...
Ethel, you are blessed, determined and intelligent. I have liked the interview and have come understand that you are more than we know about you. You are an inspiration to a lot of people. Keep going and God should continue blessing you.
Mulungu ndiwowopsyadi. This lady is a true testimony
Baba Frank be professional.. .Dont laugh anyhow...Aunt Ethel keep up the good work.kudos
Proud of you Dr Ethel Banda Stay blessed
Ethel kamwendo Banda you are one of my sheroes (heroes) of today I look up to you. May God give you more grace to continue encouraging us. Deborah from Zambia
This is most best interview in Cruise 5 , gwila Yesu ukhale ndi moyo
Amai Kamwendo mumandilimbikitsa. I like how your music is based on the true word and wisdom of the bible. You don’t compromise. May God give you strength to preach and save more souls through your music.
Nice dressing ethel, your really woman of God osati enawa ovala mowonetsa Matupiwa. God bless you more and more
😢 Dr Ethel kamwendo Banda,,, u r my favourite gospel singers
Thanks joab it was nice keep it up brother
Joab you are a worshipper, that's why you feel like you will cry and you feel goosebumps due to the presence of the Holy Spirit.
I'm proud of you Dr Ethel Kamwendo Banda, God bless you ❤❤
Ive liked this Ethel kamwendo Banda ndiwe umboni
I❤ethel😊😊
God bless you sister Ethel kamwwndo Banda. Ndi kuonera kuno Kuwait 🇰🇼
Joan Frank chakhaza keep it up God bless you
She is real! The interview was awesome, God is good! Amem
You are strong Ethel may God cntinue to bless you and your family
Wat a testimony!!.... Thx Ethel, tadalitsika.
Athu olankhula chilungamo ngati iwesazapezekaso achulukawa ndatonkhwe tonkhwe ozichekenela may God grant you
You are always a blessing mama Ethel kamwendo banda
Aaaaa ndiye mwachoka kutalitu mai kamwendo
mama m'mandi mvesa kukoma nyimbo zanu big up
Koma panopa mwanenepa bwino sister.... Wishing you all the best mama!
Go my daughter,, God bless ur mother
Umboni wanu Chemwali Ethel wandisangalasa, kuvutika kwanu kunali ndi cholinga pa moyo ndi pa banja lanu, Yehova alemekezeke.
Sorry for the loss Ethel. May the soul of Beatrice rest in piece.
This is beautiful
Jacob timasangalala ndi program yako Koma uyesese kupanga Kuti pezara nyimbo zose zakare Monga katawa singers Ethel she is so great
Watching today on 09/12/2023
Ethel is my favorite
Ndipo Mtendere wakumwamba ndi winawinadi
Ethel your strong women ,may God father bless you
Mumandidalitsa mama keep it up
Ethel is a legend!
Thanks mai Banda mwandilimbikisa
Ndipo interview iyi yandikhudza mtima kwambiri, sister mwandipatsa chiyembekezo.
First Viewer! first comment! Sakukalambatu!
Ndakunyadirani mayi. Ambuye ndiwo sintha nyengo.
Mayi nkhulu
Ethel uli ndtinkhan tokoma😅
Umatha
Dziko lathu ndi lopondelereza boma losafuna kuteteza anthu oyimba, mmalo moti apange mwa anthu akungoti azionera, eish boma la malawi liri ngati mwana wamasiye, atsogoleri ogona, atsogolera opepera.
Umatha kucheza mayi
Ndimadalisika ndinyimbo zanu ccter mulungu apitilize kukugwilisirani ntchito
Mama wathu mama 🇲🇼 Malawi
Ndizotheka Joab kukulira pa nkhomo poti pamaphikidwa mowa iwe nkukhala osamwa mowa komanso kukhala ndi makhalidwe abwino. Zitsanzo zilipo zambiri. Moyo ulibe Formula.
So intersting background Big AMEN ❤
alibo
Mama umandimvesa kukoma eeeee kukalamba mkufuna cc
That's nice program Umandisangalatsa Joab
Nic
Dr, Pastor, Evangelist zonsezo ntchito yake ndi chani why cant you just be a gospel singer as youre successful. Maulemu enawo asiyeni Mayi. You're blessed with your talent.
@naomijere1560
3 жыл бұрын
Wats wrong with the name's?
@chesterphiri7523
3 жыл бұрын
@@naomijere1560 Maulemu a Dziko just be a Servant of the Lord
@naomijere1560
3 жыл бұрын
Don't you know even in bible pipo had title apostles Baptist evengalists
@chesterphiri7523
3 жыл бұрын
@@naomijere1560 is there one in Bible who is addressed Dr Pastor Evangelist???? Even the Major Prophets like Moses for example who was trained or educated in the Royal Family in Egypt was he at any point addressed that way??? What about Paul who used to be Saul the educated one? Why? Because the Kingdom of God is about meekness & humbleness. Sister Ethel is one of the most gifted & blessed people nobody can't take that away from her but as an Ambassador of the Gospel of our Lord Jesus Christ, she doesn't need all those titles she can be an Evangelist or a Pastor plus her doctorrate not a chain of titles that's my opinion but it doesn't mean that she must do as I think no. It's up to her to do as she likes.
@giftkazembe3721
Жыл бұрын
Thus jerous .whats wrong with titles. God can give you maitanidwe angapo.or mphatso zingapo but u dont need to hide.
kkkkkkk wati anazakumenya ndichitseko? interesting stories
@rafficsainet8545
4 жыл бұрын
Ndimakunyadilani Mama maka panyimbo dzani dzimatipasa chilimbikiso mwaimodzi yake ndiiyi pamene waimapo osachoke inandipasa chilimbikiso paka nyengo dzanga dzinasitha pano ndikumva kukoma Mama
where is Allan tata's interview
Mulungu simunthu,,,,,
Joab Frank Chakhaza
Zilibho hvy
😂😂😂 koma mai athu ndiochenjera timakundani mai
Joabu uzikhala serious usamaseke moonjeza be professional plz
Kani
Joab if u know Ethel b4 it's not our business, what l want to say is" respect is needed no matter what! Be professional u c't ask Ethel in iwe iwe way why umawalemekedza ena?
@thokom7697
5 жыл бұрын
Culture yathu timalekezana. Even sister Ethel looks disturbed coz of the way the interviewer is addressing her.
@jonathanbanda4082
5 жыл бұрын
simukunaman wakulu ndamudabwa joab
@janetkarim124
5 жыл бұрын
Evidence Bandulo True. Familiarity breeds contempt.
@liversonbandah6352
5 жыл бұрын
Ndizoonadi Koma anayenera kumalemekeza wosati momwe wapangila apapamu kulingati kunyoza kwakukulu
@joelmkandawire954
5 жыл бұрын
The gay seems not to be professional, he is rude to a certain extent, I don't know why.
Wataya mimba zambiri, kkkk koma abwana awa,,,, Ethel Kamwendo umandidalitsa kwambiri ndi mavalidwe ako ukamapanga za mulungu,,,, I just wish kuti uzipanga ndikunja komwe chifukwa ndiwe mtengo wa azimai auzimu,,, komanso utasiya kumanga ma fake hair umamangawo
@beautybero8368
4 жыл бұрын
Fake hair ikugwilizana chani?? Mwasowa nkani
@chisonimponda363
Жыл бұрын
Ndiposo aaa nanga poti akupanga za Mulungu ndiye anane
Koma Cruise5 imafuna anthu otchukha okhaokha choncho si bwino kumayendako ndi anthu ena osatchukawa omwe ali ndi business kuti muwamve maganizo awo ndithu
this guy Frank Chakhaza, why does he have to laugh annoyingly at the people he is interviewing?? Seriously, most of his laughing moments are not even funny at all. Sometimes the guest is trying to explain a point and he is busy laughing. Dont get me wrong there are moments when the host and guest have some fun moments but this guy can be a bit irritating. please be professional and do your job right.
@magclair854
5 жыл бұрын
eric benlazer13 that's true I noticed that too👍🏽
Ndikukumbukira tikuonera Amen Amen song pa music splash on around 2003 and 2004 shaaa And ndinailoweza yonse, kuphatikiza apo ndinaisaka nyimbo ya Amen ndipo ndili nayo imandikumbutsa old good days nsaname
After 3 years, iam here again God is great.
Mum Ethel mumandilimbikisa
@grittersuzy7294
4 жыл бұрын
Amen
Ethel is our mother The first female artist I came to Kno from my childhood age. I love her unique voice