CRUISE 5 WITH GEORGE THINDWA

George Thindwa is a curious man. He is the Executive Director of the Association for Secular Humanism in Malawi and a confessed atheist. He says he has not set his foot in church, and doesn't see any need to. He does not believe in the existence of God or even the Devil. He is a well-accomplished Economist and once headed the Economics Association of Malawi - ECAMA.
Follow this program and hear more about his background, family and his arguments on how he thinks the world came into being.

Пікірлер: 76

  • @ThumbikoChipofya-gq7sd
    @ThumbikoChipofya-gq7sd Жыл бұрын

    Ndiyambe ndikuthokoza aChakhaza pocheza ndi mkuluyu, poyamba background yake ( childhood development ) Ku mbali ya chipempedzo sinali bwino .Chinanso nchakut sakufunika kumuweruza koma kumupemphelera kuti apulumutsidwe ndi Ambuye Yesu khristu pot malemba akut mu nthawi yakusadziwa Mulungu analekelera ,nkhan siyongopita Ku mpingo koma kumdziwa womtumikira monga zinachitikira pa machitidwe atumwi9 ( nkhan ya mayitanidwe amtumwi Paulo).Kuonjezera apo Mr Thindwa choti mudziwenso nchakuti maphunziro ngakhale Ali ofunika simayankho amavuto onse amoyo uno ndikupatsani chitsanzo cha nkhani ya m' bible mu buku LA machitdwe atumwi chapter16:16-40 pa nkhani yomwe anamangitsa Paulo ndi Sila.Mutha kuona kut chayambi cha matenda awobwebwetuka uja monga luka ( wolemba bukuli) akufotokozera sichimene adotolo amatenda amisala angafotokoze .Akatswiri azachuma sangafotokozenso out chinsinsi cha kuchita bwino kwa omwe amapindula ndi zimezi ndi chiyan? Komanso gwero lakuvutika kwa wodwala uja? Palinso nkhani zawomenyera ufulu anthu kuyambira wodwalayo,Atumwi aja ngakhale amene anabesa chuma chawo kudzera mzomwe zimachitikazi palibe chomwe angachite munyengo ngati izi.Akupatsan funso mwadwala chipatala chalephera wina atakupempheleran nkuchira mu dzina LA Yesu Khristu mwayankha mododomatu? Mwinanso titakamba za Vuto la uhule anthu alangizidwa kuyipa kwa vutoli kupasidwa ndalama out apeze zochita koma osasintha enanso ndalamazo nkukhala Nazi koma osasintha Alonso ophunzira taonani pano Dziko likupereka ufulu kwa achinyamata kutenga njira zolera chikhalirecho zambiri sizawateteza kumatenda opatsirananapogonan KO'd akuchuluka otenga matendawa mdzina LA ufulu tinene kut zikuyenda ?mutha kuona kut Chifukwa chakuti chiwanda chili mkat mwa munthu uja sichinachotsedwe vuto lizingozungulira Muli ndi maphunziro abwino pezan zochita zabwino moyo wanu uli mdzanja la Yehova yang'aniran mathero ake Hebrews9:27 komanso Ku Genesis 3 akut unapangidwa Ku nthaka komwekonso udzabwelera bwanji maphunziro alibe yankho Ku vuto la imfa? Ndibwelenso Ku machitidwe 16 chimene chinapangitsa Paulo kuzindikira gwero la vuto lija ndiye mphamvu ya mzimu woyera( Mzimu wa chidziwitso ) Yemwe mungampeze mutalapa ndikuvomereza Khristu Yesu ngat mpulumutsi wa moyo wanu ( machitidwe2:38) nkhoswe imene Ambuye Yesu anawauza ophunzira akekudzawatumizira ndikuwatsogolera mu choonadi komanso kuvumbulutsa zinsinsi zochekera kwa Mulungu kudzera mwa mwana wake Yesu Khristu.Chiuta wawe namwe zuwa liweme.

  • @blessingsnkhwazi273
    @blessingsnkhwazi2735 жыл бұрын

    Well educated man koma omvetsa chison eeeeeee ayi, anthu anga akuonongeka chifukwa cha kusadziwa.

  • @mosessemuh9681
    @mosessemuh9681Ай бұрын

    Nthidwa ndi Genious, His brain is superpower.....! You're not alone Mr.

  • @martiusgeorge6514
    @martiusgeorge65145 жыл бұрын

    Powerful God always with him that's why he like Rabecca Malope songs because in doing that he is praying

  • @andreamillar9896

    @andreamillar9896

    5 жыл бұрын

    Kuyipa kwa Makolo athu potsatengera Ana athu ku Church ndizimenezo a Bambo awu Satanic. Teach a child to know God while he is still young.

  • @mayababy1877
    @mayababy18775 жыл бұрын

    Uphawi umapangitsa uchimo.izi akupanga pofuna ndalama.the songs he likes are highly spiritual. God loves you mumbuli wanuwo

  • @mwaibanda5877

    @mwaibanda5877

    Ай бұрын

    Unfortunately he is not as poor as you think.

  • @AngungaThatcherNgoma

    @AngungaThatcherNgoma

    Ай бұрын

    Yes

  • @alfredkhogolo1715
    @alfredkhogolo1715Ай бұрын

    These are nothing but the facts

  • @kunsichilazarus9212
    @kunsichilazarus92125 жыл бұрын

    And chimene chidakusangalatsani kuti muzikonda nyimbo za Rabecca ndi umulunguwo please musabisale bambo

  • @RodgersChikumbutso-jr7fh
    @RodgersChikumbutso-jr7fh15 күн бұрын

    Akufunika kumupemphemphelela

  • @aishachisale4267
    @aishachisale42673 жыл бұрын

    Koma zikomo🙌🙌 eeee

  • @blessingskakusa7836
    @blessingskakusa783611 ай бұрын

    Long live George

  • @gloriakamanga7329
    @gloriakamanga73295 жыл бұрын

    A Thindwa Rabecca amaimba gospel nde mumapempheranso.

  • @SimeonKamwana
    @SimeonKamwanaАй бұрын

    Kodi National Anthem ija amayimba nawo kapena amaiwona kuti ndiyolakwika?

  • @DivineSyntaxMw
    @DivineSyntaxMw2 жыл бұрын

    Ati Mulungu kulibe, kuyankhula kwa zitsiru.😏

  • @aishachisale4267
    @aishachisale42673 жыл бұрын

    Akuluwa a Eliya aposatu😆😆

  • @glorydelezah9629
    @glorydelezah96295 жыл бұрын

    Thanks for the enlightenment, this is absolutely awesome

  • @stephenlupanga1970
    @stephenlupanga19705 жыл бұрын

    Joab ndi #1 kkkkk wampanikizatu munthuyu

  • @Littlefair7
    @Littlefair74 жыл бұрын

    Titha kuphunzira kwambiri koma nkukhalabe opanda nzeru ngati akuluwa, ndi Mulungu Amene amapereka mphepoyo kutidziwitsa kuti mmadzi simuli bwino ndiye wina kupanga ignore that plain warning.

  • @Omwale
    @OmwaleАй бұрын

    this guy

  • @kingstonchawinga3869
    @kingstonchawinga38695 жыл бұрын

    Eiiiish ambuye akukhululukireni

  • @kassimjuma8822
    @kassimjuma88223 жыл бұрын

    Dzimene mukuyankhula madala ndizopanda nzelu

  • @DennnisGogoda
    @DennnisGogoda7 ай бұрын

    Bible limati, “ Chisilu chimati kulibe Mulungu “ I guess the man so just so ……Let me save my word.

  • @frankmaluwa2749
    @frankmaluwa27495 жыл бұрын

    Humble man friendly person, I'm very sorry for that papa about being arrested for the mcp government by Dr Banda

  • @edwardbanda5469
    @edwardbanda54695 жыл бұрын

    God is calling him, that is why he loves Rabecca malope. God Himself will make way to bring this man to Himself. He is God of mercy.

  • @nchessie
    @nchessie5 жыл бұрын

    Adzakumane ndi wa njoka ujaface to face adzakambilane bwino

  • @christopherchimbetete2196
    @christopherchimbetete2196 Жыл бұрын

    Chamba

  • @joelmkandawire954
    @joelmkandawire9545 жыл бұрын

    That is according to him, (he doesn't believe in God) not you and me, so leave him alone. It's not up to us to judge him.

  • @ralphhenderson5312

    @ralphhenderson5312

    5 жыл бұрын

    sizoona ngati munthu akutayika akonzedwe akusokoneza life is too short usakhale mbuli

  • @truthtellerlastonk.m.p4985

    @truthtellerlastonk.m.p4985

    3 жыл бұрын

    @@ralphhenderson5312 who told you kuti akutaika????

  • @RedsonRichard
    @RedsonRichardАй бұрын

    Nanu munyanya mwakumana ndi wen wen Satanists

  • @johnsong2118
    @johnsong21185 жыл бұрын

    komadi madala awa sangangokhalakhala,akuyenela amadya chamba

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri75235 жыл бұрын

    Poor soul, just being intelligent as he is explaining it's God's blessing.

  • @ellenfumuyiliko1390
    @ellenfumuyiliko1390 Жыл бұрын

    Bola a Eliya aja amadziwa kuti Mulungu aliko osati phwephwa izi

  • @aubreywallo1987
    @aubreywallo19875 жыл бұрын

    God forgive him!

  • @joechimba742
    @joechimba7422 жыл бұрын

    Inde mdala

  • @geee7672
    @geee76725 жыл бұрын

    But Rebecca Malope is a Gospel artist

  • @ralphhenderson5312

    @ralphhenderson5312

    5 жыл бұрын

    Nchifukwa chake tikuti ndimbuli sakudziwa chomwe akupanga Mulungu amukhudze

  • @kassimjuma8822
    @kassimjuma88223 жыл бұрын

    Mulungu adzikukhululukilani madala

  • @truthtellerlastonk.m.p4985

    @truthtellerlastonk.m.p4985

    3 жыл бұрын

    Apanga tchimo lanji???

  • @user-hc6rc7yr8y
    @user-hc6rc7yr8yАй бұрын

    Satana uja ndamuona ndi maso lero😮

  • @peterbanda5425
    @peterbanda54255 жыл бұрын

    Akuluwa mutu ukugwila koma

  • @Chikomukomu
    @Chikomukomu5 жыл бұрын

    All am seeing is confusion from this guy. He was contradicting himself during the chat

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9gАй бұрын

    Drange kwambir kapen fodya Wa chamba😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @yankhomtonga6325
    @yankhomtonga63255 жыл бұрын

    Looking at the comments it clearly shows how ignorant the so called christians are: Calling the non believer osazindikira. you guys need enlightment for sure dont just believe for the sake of believing

  • @georgesiwale8127

    @georgesiwale8127

    Ай бұрын

    Yes, I am wondering too. We need to wise up

  • @simonabraham7241

    @simonabraham7241

    Ай бұрын

    For sure, these so-called christians are something else 😂😂😂

  • @Littlefair7
    @Littlefair74 жыл бұрын

    Ndi omvetsa chisoni, infact he is worse than the devil himself. The devil doesn't dispute the existence of God, according to the book of Isaiah and Ezekiel, the devil wants to be like God the most high. This old man is totally out of his mind.

  • @CatherinePhiri-bw7wm
    @CatherinePhiri-bw7wmАй бұрын

    Bible linanenakale kuti the fool say there is no God, ndiye mukamawona anthu atelewa wosamadwabwayi p

  • @basharkhan8933
    @basharkhan89335 жыл бұрын

    Ngati chili chamba chikugwira ntchito

  • @duncanchizizi6543
    @duncanchizizi65433 жыл бұрын

    Kkkkkkkkkkkkkk

  • @medsonboti1984
    @medsonboti19845 жыл бұрын

    The holy spirit gives one the ability to sense the presence of God. If the spirit is not in you then there is no sense.

  • @youmad9087

    @youmad9087

    3 жыл бұрын

    What spirit is that?

  • @aminbwanali3954

    @aminbwanali3954

    2 жыл бұрын

    This man is the brother of falawo he deserved to be panished

  • @rashidjackson7085
    @rashidjackson70853 жыл бұрын

    Mkuluyu wangokura koma nzeru mulibemo. Google mwini wache ndi muthu osati mulungu ndipo nthawi zina siigwira network

  • @manzykawika8988
    @manzykawika89885 жыл бұрын

    Muziwerenga Bible Mr thindwa

  • @apatsamuula4676

    @apatsamuula4676

    2 жыл бұрын

    Alibe thawi yowerenga bake akuyakhula xoduka mutu

  • @kunsichilazarus9212
    @kunsichilazarus92125 жыл бұрын

    Kkkkkkkk koma Joab umakumana nazo inetu abambo awo komwe akulowa sindikudziwako.

  • @ellengwazanga6350
    @ellengwazanga63505 жыл бұрын

    Bambowa ndi chiwanda, akufunika mapephero.

  • @truthtellerlastonk.m.p4985

    @truthtellerlastonk.m.p4985

    3 жыл бұрын

    Zaziiii zenizeni 🚮🚮🚮 mapemphero achani??

  • @mussahswallehchimisa5348
    @mussahswallehchimisa53485 жыл бұрын

    koma abale mmmmm zodabwisa kwabasi munthu wankulu ngati ameneyu?? 😯😯😯

  • @weruzanicustom4954
    @weruzanicustom49542 жыл бұрын

    This atheist akungofunika maumboni amachilitso. Funso lakuchipatala lamuyimitsa mutu mpaka wavomera kuti akhoza kukhulupilira kkkkkkkkkkkkkk

  • @ndipo1
    @ndipo15 жыл бұрын

    aaaah kumvets chisoni you dont believe in God- you missing out on a lot hey.

  • @youmad9087

    @youmad9087

    3 жыл бұрын

    Omvetsa chisoni ndi iweyo

  • @Littlefair7
    @Littlefair74 жыл бұрын

    According to the Bible Mr. George Thindwa ndi achitsiru, that's it and i can prove it and he has proven it himself kuti, he is a fool.

  • @ellenfumuyiliko1390
    @ellenfumuyiliko1390 Жыл бұрын

    Anangokula nzeru alibe🚮

  • @simonabraham7241

    @simonabraham7241

    Ай бұрын

    Ndiye mumlalikira bwanji ndi mau onyozawo?