Analakwanji chilima ? Kulila kwa achinyamata

Пікірлер: 11

  • @tingo3155
    @tingo31557 күн бұрын

    Jealous ndi ufiti zoona, Chakwera and mcp is evil to the core

  • @GabrielMzich
    @GabrielMzich5 күн бұрын

    CHAKWERA KUPHA ANTHU BASI KOMA AKUTI ANALI ABUSA KOMA KUMWAMBAKU AMBUYE AWAYENDERE ACHAKWERA

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py12 күн бұрын

    Ndipo CHAKWERA wationesa amcp ndi oipa kwambiri ,Chilima amalakwa chiyani ndiy mfutso lathu daily mupephero lathu mulungu atiyakhe zatikhuza KWAMBILI tikulira kupha anthu 9 what is meaning of this? Ndale zophana zabwanji ? Achakwera MULIBE Muthu inu Santana iwe Chilima kukuikan Paule inu kubweza chipongwe chonchi AI mwaphadi tikuona APA ndipo YEHOVA sakhalat chete inuso mupita

  • @emilynthite6545
    @emilynthite65455 күн бұрын

    Chakwera zimuvuta yakwiya ndimizimu

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq13 күн бұрын

    Iwe uli ku soth Africa upite ukavote osamango kamba ayi dzoputsa basi utm yachani ife tili ku mbuyo kwa dpp basi chifukwa tikudziwa kuti ndiyachitukuko anawa ayi akuba anachoka ku dpp anapita ku mcp akubanawoso kumeneko uladi ndiena otele dpp motooooooooooooookutibuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuu2025 bomaaaaaaaaaaaaaaassaaaa

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v13 күн бұрын

    Chakwera abwerere Ku Church galu ameneyi

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y13 күн бұрын

    Chakwela you mast go

  • @KellyHart-pi4hd
    @KellyHart-pi4hd13 күн бұрын

    Nanuso munayamba bwino Koma zovotera nyamatazo ndiye ndimbwelera Nanu mukubaralika dziko ramalawi likufunika APM azayikonze then tizizasankha nyamatano otsati panopaso tibweletse ophunzira ayi kumeneko ndiye kukhara kuwononga dziko chifukwa or poyambira nyamatayo sangapawone

  • @user-qp8kh2hj9o

    @user-qp8kh2hj9o

    12 күн бұрын

    Aaaa inu ngati mukufuna APM nde mukuona ngati aliyense angakonde zokonda inuyo??? How???

  • @user-gg6uh2wo4x
    @user-gg6uh2wo4x13 күн бұрын

    Gud news

  • @KellyHart-pi4hd

    @KellyHart-pi4hd

    12 күн бұрын

    Abwana Ndikufuna Ndikuwuzeni dziko ra Malawi sitikufunika mtsogoleli wanyowani chifukwa dziko likakhara ndi atsogoleli ambili wopuma silimayenda bwino ,Coz atsogoleli wonse amarandirabe ndarama zaboma ndiye muganize Kuti tili kale ndi awili Chakwera Akhara wachitatu dziko lizayenda bwanji ?mayiko anzathu mtsogoleli wopuma amamutsakirq zufukwa amumange cholinga asamamulipile kuwopa kuwononga ndarama zaboma, ndiye chikufunika apa tibwelele Ku Dpp Ngati ayi basi timutsiye Chakwera Apange zofuna zake