WIKISE INTERVIEW - Answering all the controversial Questions plus narrating a very touching story
What happened to him and Konkala| how is he managing his relevance as an artist| what drives him to the music concepts that he does| any plans to shoot his latest song titled MALE|
WATCH AND DONT FORGET TO SUBSCRIBE
#wikise
#interview
#makosana
Пікірлер: 73
Mmandiwaza abusa🎉🎉
🔥🔥🔥🔥
More fyah
More 🔥🔥🔥
when people meet new people
Bravo Mary💥💥👍
more 🔥🔥🔥
Wikise ndiolimbikira I like this guy
Mumakwanira Abusa, Following live from Chikwawa
mkazi uyu ndi best interviewer
@c-kayz1946
Жыл бұрын
Every question ndikufunika kwanji
Great interview
U got good content koma abusa keep pushing....
Bigman 💥💥💥💥🇲🇼🇲🇼🇲🇼
On a 🔥 🔥 fire
Ulemu wake MARY
Wikise umakwana receive your flowers 🎉🎉🎉
Wikise umatiimilila keep up
Mary is good interviewer
Mkazi amatha kufusa uyu
Mary uli bho🔥
Interview inali yotsangalatsa so happy.......
Mary Moyo🔥💥
Wikise 1992 umakwana❤❤
Mwana male
When pple meet new pple,
Chewikise anamvaya guys 🔥🔥
Mary Moyo ndiwe dolo🔥
Keep good work makosana 🔥🔥🔥🔥
@esaukenani3036
Жыл бұрын
Chikamuphulikire komkala🤣🤣
Za Komkalazo ukanazizembako pang'ono, makamaka Paolo pomunena zot wakupanga delay po ummmh ukanabitsapo pang'ono
@liki-likiladies---lilongwe6963
Жыл бұрын
true
Munabwer madala❤
Mafuso ofunika mwana
Umakwana @Wikise
uzayimbeko ndi sir patricks plz plz
ndi zoona ada awa tinkapuzilila lumoz pa kaluluma
Wikise umatha iweyo
Dolo
The questioning koyambilalako
Mary moyo ulem wako mesa
Flow of the questions Next time try to improve. Osapereka mafunso then u be like u are answering wekhanso
Iyo munadyera yoneco😂😂😂
Umatha
Wikise ndimunthu wokoma ntima kwambir. Vuto liri pa anthufe pa zolankhula zanthu
Komkala ndiwausiru🤣🤣🤣
Wikise aise wabwela kuzakhala 😅
Habusa
Akonkala ndiwochepekeledwa nzeru monga munthuyo aliri
Mamakwa mn
Kochokera simunafuse
Kod mu cup mo mumakhala drink yanji😂
Koma mafioso enawa
Muzamufunsenso konkala tizamve kut olakwa ndani
@ElisahGibson
6 ай бұрын
Live
Tiwuzen a che wikise sopano alikuti nkonkala Koma timaku fila ife pano pa jonzi wikise Maka Maka pa nyimbo ya natacha
@franciskameko2586
Жыл бұрын
Amat Natasha not Natacha Aaaah bwanj kod? Kkkkk
@futuremoyo5714
Жыл бұрын
Kkkk mmmmm momwemo iwe waziwa bwanji kt ndimanena kt natasha
Abusa anayakatu🤭🤭🤭🙄
Why unnecessary questions here, pallbe ndatolapo
Forgive your father
Interview iyo ili ngati yofuna ntchito coz timayamba kumufunsa dzina kwawo amatani not momwe mwayambilamo go back to school
Those who are here because of FB lets gather here 😂😂😂🙌
@Young2Dumb
Жыл бұрын
😂😂🙌
@madalitsojere9107
Жыл бұрын
ha😂😂😂ha
Abusa😂
Abusa😂😂😂😂
You don't wash your dirt linen in public. You were supposed to distance yourself from answering much mafunso okhudza Komkala
@GodfreyTonde
11 ай бұрын
Bola wayankha akulu hahahaha
👉 Promo`SM
🔥🔥🔥🔥
Mafuso ofunika mwana
Mafuso ofunika mwana