Wansembe wamkulu wa katolika anayankhula zonyoza boma zayambaso kuzungulira dzina ndi Fr Tamani

Пікірлер: 75

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p6 күн бұрын

    This is good massage

  • @augustMag
    @augustMag6 күн бұрын

    He is saying truth message he is advice the Government sananyoze kapena kutukwana ai❤

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg6 күн бұрын

    Sananyoze koma amalakhula zona zokha zokha komasotu wanenelatu kuti zochezatu sono chomusakila nchani ndye akunama

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba2 күн бұрын

    Mwalalikazi mwatenga book liti lamulungu, kusochera ndikusocheresa uku, aneneri onyenga

  • @festonphiri
    @festonphiri3 күн бұрын

    Good message fr

  • @scoobymatola8314
    @scoobymatola83146 күн бұрын

    Sakunyoza You can't run a government without knowing economics

  • @adammadi8248
    @adammadi82486 күн бұрын

    To speak the truth sikunyoza ,therefore tisiye mukalidwe woyika anzatu pamoto.

  • @MassPastor-bn8ck
    @MassPastor-bn8ck6 күн бұрын

    Sindikuona chomwe Mkuluyu akuyankhula zonyoza boma koma kuti ambiri mwa ife timakondwa tikamalambalala chilungamo,koma chifukwa choti chilungamo chima pweteka ndichifukwa chake zikuveka ngati kunyoza kama ayi ndithu akukamba zona zake munthuyu. I wish if we can learn to stand for the truth like this Father..........

  • @erasmopedrombewe8842
    @erasmopedrombewe88424 күн бұрын

    Esse padre falou a verdade, não é desprezo

  • @Maliko-bp1xn
    @Maliko-bp1xn6 күн бұрын

    Moyo wa munthu pali thupi ndi nzimu choncho thupi ngati likumana ndi mavuto akuyenera kulankhulapo kumene ,nkhristu ngati ali ndi njala angamve bwanji mau zikufunika zonse ziyende limodzi

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft6 күн бұрын

    Very good and short speech

  • @sankhwe
    @sankhwe5 күн бұрын

    Good one

  • @chrismezalumo5698
    @chrismezalumo56986 күн бұрын

    Very profound 🔥🔥🔥

  • @samuelazumah1050
    @samuelazumah10506 күн бұрын

    Sananyoze koma chilungamo

  • @isaacpaulrabson2099
    @isaacpaulrabson20996 күн бұрын

    Good point farther

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e6 күн бұрын

    This is great massages to the Malawi government if they have knowledge they have to change the direction

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki6 күн бұрын

    Father you are number one! Chakwera is a big failure. Indeed we made big mistake to put chakwera as a president.

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w6 күн бұрын

    Wakamba zoona wansembe amenei chakwera n boma lake sakuzaununkhanso mpando 2025 muzandivoera✋

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y6 күн бұрын

    Good Messnge Chakwela walephela you mast go

  • @uzaleuzale8603
    @uzaleuzale86036 күн бұрын

    Ndiye kunyozako kuli pat

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif95566 күн бұрын

    Very true

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu83843 күн бұрын

    Amen

  • @BeatGondwa
    @BeatGondwa6 күн бұрын

    Good good

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda98306 күн бұрын

    Kwacha yagwa kumene ndipo akuti Chakwera ndi ophunzira koma akulephera kuyendetsa dziko

  • @mtimatrading790
    @mtimatrading7906 күн бұрын

    Ameneyu saopa anayamba kupalamula nthawi ya Bingu, anamupuputitsa mkulu wina wake magilasi a mmaso pa msonkhano.

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl6 күн бұрын

    🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @MelvinVanRooyen
    @MelvinVanRooyen6 күн бұрын

    aaaa kunyoza kwake..kulipati pamenepo akuyakhula chilungamo

  • @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
    @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb6 күн бұрын

    Ulaliki wa kale uwu siwa pa 3 July 2024

  • @user-lj8ug5lq8c
    @user-lj8ug5lq8c6 күн бұрын

    Kaya ndizaliti koma he is saying the truth

  • @user-wp9js5vu6s
    @user-wp9js5vu6s6 күн бұрын

    True mssg

  • @andyjames2050
    @andyjames20506 күн бұрын

    Pali kunyoza apa ichi ndi chilungamo cheni cheni

  • @comradechimbayo3167
    @comradechimbayo31676 күн бұрын

    Powerful

  • @wilisonbornface4282
    @wilisonbornface42825 күн бұрын

    Zoona kwambiri sikuwonapo cholakwika

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba54376 күн бұрын

    Osati kuti wayankhula zonyoza anayankhula chilungamo osamadana ndikuuzidwa chilungamo ayi

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni6 күн бұрын

    🤗🤗🤗🤗

  • @WisdomMaseko-fi5sv
    @WisdomMaseko-fi5sv6 күн бұрын

    Andale ampingo

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg6 күн бұрын

    Sananyoz akunena chilungam uyu

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona6 күн бұрын

    Kunena zoona munthu wa mulungu sanafotokoze monyoza ayi ngati mukufuna kumutapa mkamwa mungomutapa mkamwa sindikuona chifukwa ayi.

  • @FavourKadzembe-sg1yf
    @FavourKadzembe-sg1yf6 күн бұрын

    another Dc

  • @GraceMakoka-v2k
    @GraceMakoka-v2k6 күн бұрын

    Koma akunena chilungamo

  • @user-ui4ux5kc8d
    @user-ui4ux5kc8d6 күн бұрын

    Ineyo sindikupeza vutoo and Chakwera alibenso mzotheka mchifukwa kumakhala cabinet members ntchito yawo kumuuza presedent pomwe sipakuyenda bwino ndipo amamva ndi munthu osamangoti presedent ali ndi vutoo vutoo ndaammbaliwa tere basi

  • @ThomsonNyirenda-df9io
    @ThomsonNyirenda-df9io6 күн бұрын

    Nothing wrong good

  • @RaphaelKweve
    @RaphaelKweve6 күн бұрын

    Palibe kunyoza apa ,,,,

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience22836 күн бұрын

    MCPigs ndi ufiti

  • @GreshamKadzembe-tn8cq
    @GreshamKadzembe-tn8cq6 күн бұрын

    Kodi inu mesa ndi amene munalemba chikalata 1993 kuti mukufuna madipaty, ndiye mukuletsa chani zimenedzo ndiye ndarezo kuba basi onse akhara a kulowa aja ndi okuba ngakhare iweyo ukulankhula we kuti ukhare pampando utha kuba so

  • @adammadi8248
    @adammadi82486 күн бұрын

    Kodi povhota mumasanga kuti awa ndi abusa asavhote? Yet kufnyika and them there are experiencing the heat.

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w6 күн бұрын

    Kuswa kuswa, Chakwera ndi boma lake la MCP kumene aliko mutu waima, zoona zokha zokha, ndipo latikwana boma limeneli.

  • @corretabanda7685
    @corretabanda76856 күн бұрын

    Kunyoza boma ndie kuti chaani? Kudana ndichilungamo kapena?

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona6 күн бұрын

    Uthenga wa bwino zikomo

  • @lazaruschitsamba8394
    @lazaruschitsamba83946 күн бұрын

    koma bwanji kunyoza wosatandiza maganizo

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d6 күн бұрын

    Nanuso musamakokomeze kuti zonyoza boma cholinga amangedwe akunena zoona aliyese pamene zafikapa olo mwana akudziwa kuti dzikoli sili bwino athu akufa ndi njala mwezi uno Kodi nangytifikile January athu akhala motani dzikoli lafika powawa tayendani m,mizimu athu afika pongomupepha mulungu kuti angowatenga chokhalilaso ndi moyo sakuchiona chifukwa Cha mavuto

  • @GanieAlidih-gu7no
    @GanieAlidih-gu7no6 күн бұрын

    Palibe kunyoza apa km kunenachilungamo

  • @user-ev4or2kg4z
    @user-ev4or2kg4z6 күн бұрын

    Uthenga wabwino chifukwa anthu mukuwalikiralawo ali pamavuto mu dziko lawo

  • @rhodrickmpumila1820
    @rhodrickmpumila18206 күн бұрын

    Ndi cadet wa DPP uyu ndikumudziwa bwino

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela6 күн бұрын

    Chilungamo kkkkk

  • @jameschibwana2751
    @jameschibwana27516 күн бұрын

    Vuto anthu mumadana ndi chilungamo, wanyoza chiyani pamenepa?

  • @AllanaChiphazi
    @AllanaChiphazi6 күн бұрын

    Ulaliki musamaphatikize ndizadziko pls

  • @simeonbanda4240

    @simeonbanda4240

    6 күн бұрын

    Rad the Book of Prophet Isaiah! He denounced the oppression of the poor and the injustices of the government. So its the responsibility of the pastors to denounce the envils of the government. Moreover the church has contributed significantly to the development of the country so it has a say where things go wrong

  • @abdukarimmponda5698
    @abdukarimmponda56986 күн бұрын

    Zimakutuzo amalawi kumataegula..anakuuzan ndani kut kutimikira mulungu nde kut azionelera zopusa zikuchitika aba ndalama za anthu zamisonkho kubako siusatana? Nde ena akalankhula alakwitsa...munthu wachinyamata mmutu mukadali ndale za 1990 zachisoniiio,👺🤔

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel29766 күн бұрын

    Pali kunyoza apa? Chilungamo ich

  • @owenmoses9434
    @owenmoses94346 күн бұрын

    Zonyoza??? In what way??? Nananuso mwayambae???

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w6 күн бұрын

    Stop politics, mwayiwara ntchito yanu

  • @user-wt7ve3el5o

    @user-wt7ve3el5o

    6 күн бұрын

    Where is the politics in this speech?? Learn to accept when things went wrong.

  • @Jfphiri-w7b
    @Jfphiri-w7b6 күн бұрын

    Rev....mwasokonela a Revrend yambani ndale...mwakanika inu kuthana ndi Santana Zaka zonsez....musatchukile pa ndale ..simudziwanso kulalika inu

  • @user-wt7ve3el5o

    @user-wt7ve3el5o

    6 күн бұрын

    Osamangosusa zilizonse akulu ngati inu mukumwa tea daily si onse amene akumwa tea ngati inu. Choncho ndi udindo wake ngati m'busa kulangiza nkhosa zake zammene dziko likuyendera. Palibepo za ndale apa nchirungamo chokhachokha

  • @Jfphiri-w7b

    @Jfphiri-w7b

    6 күн бұрын

    Its global...go to Zambia Kenya Haiti Amerika.....homeless...no tea r there....everyone must use his head to make things move urside

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s6 күн бұрын

    Kodi athu awa simadziwa,muve ndi toque yomweyo angakambe zabwino za mtundu wina?amafunana wokhawokha mtundu umeneu_

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe6 күн бұрын

    Kkkk koma politics yo sikuba. Sattargate @Cashgate @Achairs vashgate ..

  • @AllanaChiphazi

    @AllanaChiphazi

    6 күн бұрын

    Tidzangomvotera iyeyo, amalekeranji kukawadzudzula pamaso pa abomawo, lilipo boma lomwe linayamikiridwa ndi anthu amenewa? Popeza bolili lonse amalipezera zifukwa, zilalikani zoti anthu asiye kupanga ntchimo tiziopa tsiku lachimaliziro. Zamavote munayambitsa ndinu nomwe

  • @AllanaChiphazi
    @AllanaChiphazi6 күн бұрын

    Ulaliki musamaphatikize ndizadziko pls

  • @FrancisDay-br7xb

    @FrancisDay-br7xb

    6 күн бұрын

    Iwe kumeneko sikusaniza ndale ndi mpingo koma kuzuzula zoipa za boma

  • @user-wt7ve3el5o

    @user-wt7ve3el5o

    6 күн бұрын

    Lalikani wanu tiumvere

  • @GiftSnoxy

    @GiftSnoxy

    6 күн бұрын

    Nyani iwe wamva ukudziwa chan

Келесі