A Shadow ati ubale wa u kazembe...eish YONECO!!!! 🗣🗣
@rashiddeula571511 ай бұрын
Ntebe hahaha....ati ndamponda Albert hahaha ati Koma Ngozo amathamanga. Eish.....komaaa. Ndiye ayambapo kutsonya? Usauver ndi massive. Great work team. Missed Patricia though
@AjayAgape-no4qh11 ай бұрын
Piksy zugwirizana bwanji ndi za zakeyo 😂😂😂😂
@pemphelobendela537511 ай бұрын
Ntebe alibe mtendere🤣🙌Hyphen ur the best adha
@Mahalia3111 ай бұрын
Pepan zatha alllaaaaaaqq😂😂🙌 the real mtebede
@jacksonmaster228811 ай бұрын
Iyiyi ndi moto eeeeee😂😂😂 mtebede eti 😂😂
@SundayScovaАй бұрын
😅😅Koma a chee nkhope 😂😂 Mpaka ukazembe wa dziko kapena chani
Пікірлер: 545
Hyphen is a good actor as well
Is there anything else better than Usauver so far?😂😂😂😂😂
@westonfunan137
11 ай бұрын
Dyangu
@ephraimmonche6246
11 ай бұрын
@@westonfunan137 Dyangu is behind
@BlessingsBanda-qn7xr
11 ай бұрын
Mfumu kauzi
@harrisonmkandawire1510
11 ай бұрын
Try Mfumukazi
@Manishamalenga
11 ай бұрын
Mfumu nkazi and mdyangu😂
Bar man uyu ndamufila heavy. Mukuitha ma guy❤
Kkkk Amazing...zoti amaphikilidwa ndi alabat..ayamba kupsa ndi tea
Chikhala zmatheka kupanga like ka 20 thousand nkanapangatu
Zayamba kubeba😂 Mtebe ndi Berita are something else 🔥
Ndimakhalilatu😂😂😂mtebe akukhalilatu belita si munthu wamba
Koma hyphen ndi ofatsa za abnormal. Sungacheze naye mtebe that way opanda makofi ayi 😂😂😂😂aaah
Ndimenye ndimakhaliratu 😂😂😂 berita 🙌🏾
Komasotu a Edo 🤣🤣🤣 and ntebe ati mene ndamumenyera Albert ngozo nde wathawa amatha kuthamanga😂😂😂😂😂😂
Okay Ntebe and Belita ndi fire 😂😂😂😂🔥🔥
Ntebe nd belita 😂team mabonyo🤣🙌
Komatu abuse akuonjeza😂😂😂 azamenyedwa siku lina maka izi zopephelela anazi😂😂😂😂😂❤
Patricia amafunika azioneka episode iliyose guys ❤
Ati ndimakhaliratu hahahahah u guys r too funny, u made my day😜
Koma usauver ili ndima good characters....mtebede 😂😂
Koma Mtebe ndi chitsiru. Ati, "ka moyo kakubatu aka" 😂😂😂
😭😂😂Mtebe can lie,,, ati ndamuonetsa Koma zinthu zake 🤣🤣😂abhudulanapo
Kma Ntebe legendary😂😂😂
Mtebe wankuntha Albert ngozo wathawa zedi😂😂😂😂
Belita + Ntebe scenes🔥🔥🔥🔥
Love it .... Guys zikubhebhea zinthuzi... Thanks for this... Looking forward to the next episode.
😂😂😂😂😂😂koma ntebe can lie for africa😂😂😂😂
@lindankhoma9092
11 ай бұрын
😂😂😂😂😂
Eddoh adha🔥🔥 a scene without him sindimanva bwino😂😂.. ati "ntebe mwandiyandikira?"😂😂😂😂
Osamandigwira shatapu😂😂
Komano Edou Yu ndiwa mabodza and very observant eeeeee 🙌 🔥🔥 he's good... Ntebede watethedwa kwabasi 😆😆😆
@blessingsmimu
11 ай бұрын
😂😂koma wayitha si thebe wapeza mafoni ake aja
THE LAST PART😂🔥
Kkkkk hhhhhh emotion damage 😅😅😅 simachidalitsa kale pamenepaa😅😅
Banja ili 😂😂😂 Belita and Mtebe
Komaso abusawa kuwoneka ngat ndibusa wachinyengo 😂😂😂😂😂😂
Keep the fire burning guys 🥰🔥
Komatu a eddo akuti gwiranani chanza 😂😂😂😂😂
Komatu Mtebede, ohkay chabwino 😂😂😂😂
😂😂! Kwachemelatu!! Ati inenso si galutu😂
Hahaha ati ammenya Albert uja ukuuuu 😂😂😂😂😂😂
A Shadow ati ubale wa u kazembe...eish YONECO!!!! 🗣🗣
Ntebe hahaha....ati ndamponda Albert hahaha ati Koma Ngozo amathamanga. Eish.....komaaa. Ndiye ayambapo kutsonya? Usauver ndi massive. Great work team. Missed Patricia though
Piksy zugwirizana bwanji ndi za zakeyo 😂😂😂😂
Ntebe alibe mtendere🤣🙌Hyphen ur the best adha
Pepan zatha alllaaaaaaqq😂😂🙌 the real mtebede
Iyiyi ndi moto eeeeee😂😂😂 mtebede eti 😂😂
😅😅Koma a chee nkhope 😂😂 Mpaka ukazembe wa dziko kapena chani
Kkkkkk mtebe wayamba mabodza akut ngozo muli liwilo simasewela
Koma mtebe ndi m,busa waziwanda 😂😂😂
waiting for what will happen next.keep up guys
Mtebe mabodza, ka busa ka chinyengo in Patricia's voice
Mtebe 😂😂😂😂ati pepani chabwino alaaaaaa😂😂😂😂😂😂😂😂😂 this is funny
Abusa maboza 😂😂😂akut albert ndamuponda
Kufuna kutamika ati Ngozo wathawa 😂😂😂 Mtebe simunthu iii
I like that guy okalamba mmutuyu,,he's good
Kamoyo kokuba ka Albert😂😂😂 Ntebe 🔥
@khumbochihana7038
11 ай бұрын
That part😂😂😂
@ManessChilemba
2 ай бұрын
😂😂😂😂
Mkaz mumuvesa bwanji sakukhuta kubed akutero kkkkk😂😂😂😂😂😂
Last part was nothing but genuine😂😂😂 impressive!!!!
Aedo ndi galu😅😅😅😅
🤣🤣🤣yomweyo achina Belita
😂😂that ndimakhalilatu word 🙌
Kkkkkkkkkk😂😂😂 kma abusa ndi berita😂😂😂😂
Ubale wa ukazembe 😂😂... Ntebe wayamba mabodza kuposa Patricia
Nyimboyo ilimwala🔥... Koma hyphen aaaaa osantizimula mtebe bwanji
Belita ndi mtebe🔥🔥🔥🔥...muphana😂😂🙌
Last part iri bho 😂😂😂ineso sigalutu
Koma mbusa uyu 😂😂😂🤣 si munthu eti belita
Belita and Ntebe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Ubale waukazembe bar man on point
ati ndimakhalilatu😅😅😅😅
The last part you😂😂😂
eee! anakhala ngati kuti ine ndi mkazi wake sitimayenda bwino🤣🤣🤣Sinnasowe, sindine mzimu...Mtebe sadzatheka.
Been waiting for this
😂😂😂Ntebe ndi OG🔥🔥
Timafunso ndi ti ma comment ta Edo 😂😂😂😂 I love Usauver, keep the fire burning guys🔥🔥
Kkkkkkk koma abusa ati amumenya Albert zabodza basi
😂😂😂 ati ngozoh ndiye amathamanga mmmm kma m'busa uyu sazatheka ndithu ndagoma naye
Belita ndi ntebe kuzaphana iiiiish😅😅😅😅😅
kkk km mtebe wamenya albart next part plz
Ati ndimakhaliratu😂😂😂😂 laughed so hard😂😂😂😂😂
Mtebede nayesoooo kkkkkkkkll😅😅😅😅😅
Aaaaaaaaa kma M'busa mtendere ali nd bodza guys 🤣🤣🤣🤣🤣, Ati wamenya Albert
Chikumukhuza ndi chani zakeyu😂 in ngozo,s voice😂 Nae bar man eeeeee 😂akuipasa moto
Wooow ! everything on point💯
😂ashadow😅😅😅 ati akufuna ubale waukazembe😂😂
😂😂😂 eeeh koma yalero inali yokungana mtebe mpaka ku counter 😂
ati sutudziwa kuti tinganene kuti mkazi wandani🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ndimakhaliratu😂😂😂😂🔥🔥🔥
Abusa 😂😂😂😂 mpaka ati atibula achina ngozo
😂😂😂😂😂 Ntebe ndi wabodza kkkk
Ntebe ndi belits💙
Mumatimvetsa kukoma guyz 🔥🔥🔥🔥🔥 best characters ever ❤
The last part😂😂😂😂 ❤
Koma mtebe can lie iiiii😂😂😂😂😂🙌
😂😂😂😂😂akukhalaso ndi awa eeeemm abaya Albert pa mtima
Mtebe kumenya munthu kkkkkkkk koma ulindiboza😂😂😂
23minutes yonse ikanakhala ya scene yakumapeto bola🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ndimenye uone ndimakhaliratu 😂😂😂 Berita udyayo mkawawa
🤣🤣🤣🔥 cant wait for the next one
Bar man was at it❤
@zahraphoya
11 ай бұрын
He wants to hear it in details
@malawimoto1951
11 ай бұрын
@@zahraphoyandipo akufuna kumva kalikonse
Ngozo osangopereka wekha bwanji foniyo?? Mmmmmm😂😂😂😂 Zipongwe basi!!
Che Nkope zayamba kumuthekera haaahaha.... ali m'chikondi🤣🤣🤣🤣🤣
Makwana angauzo
Jebedaya yu akufunika matheche wallahi ine apa,Alaabati achitepo kanthu😂😂😂😂😂😂😂
Ntebe 🙌🙌