USAUVER S06E03 ASHADO
Комедия
Introducing Che Nkope
Watch My Other Videos 👇
• Piksy Malawi Music Videos
#Langwani #Piksy #Asauver #Sangie #Music #Malawi #Comedy #Africa #Afro #Trending #Usova #hyphen
Subscribe To My Channel 👇
/ piksymalawi
Watch My Play Usauver 👇👇🔥
• Usauver Episodes
PLEASE NOTE: Unauthorized upload of this video unto any KZread channel is prohibited. (C) 2022. #CCNB.
Пікірлер: 208
Am very happy to see Che nkope and piksy again
Nkope amatha kkkk😂😂😂
Che Nkope ayayayayayayayaya funny dude
Symbol ndi dzungu che' Nkope a shado 😂😂😂
Koma ma guy mumakwana🤗🤗🤗
Che nkope is my favorite nice to see u two again together
Wait! This is hilarious 🤣😆😂😄
🤣🤣🤣🤣🤣🤣koma mwakumanapo pamenepo....this is good acting...flowing naturally...keep it up......
akufuna kuyimilira
Munayamba mwathamangisidwapo pakhomo mutangofika kumene🤣🤣🤣🤣🤣
I miss Malawi. Watching from 🇨🇦 Good work 💪
@maimounaabdulazi4343
Жыл бұрын
Can I know more about Canada 🇨🇦
hyphen akuoneka kuti walezela kale......hahahahaha
Munayamba mwathamangisapo pakhopo mutafika kumene 🤣🤣🤣🤣
You guys mwafika patali hope you get a multi million deal
Koma wandare uyu ndikape🤣🤣🤣
Hyphen nde imukhala ya u driver wa ambulance yo kkkkkk
Ati "gate by gate" osati 'door to door"😂😂 Sangie mwano
Ashado will kill us with laughter 🤣🤣🤣🤣🔥🔥🔥
Hyphen safasa bwino 😂😂😂
Che Nkope😂😂😂
ma guy mwadzaaaa
😂😂😂 Mafilu inuyo mesa
Shadow nzeru alibe bluebook yafika njale isanafike
Ganizan siwamaseweresa
The acting is so natural😂, I love it
@eliaskotopo1870
Жыл бұрын
Ndipo Inu zosakakamizatu
Above all, this episode pokhapo pomuuza Albert kuti azizayendesa ambulance pamandipeza🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ashado muli too much🤣. Naye Gani ndi mzake Nina all fire 🤣🤣
Ma shopkeeper muzikhala ndi ulemu 😂😂😂
Keep the fire burning😄. Koma ashadow🤣🤣🤣🤣ambulance driver
Muyambire pati poyambira simukupawo MP uyu satithandiza😅💯
Che mkopee yomweoo.
Abwera mwa phuma nde apanga balamanthu koma piksy ase 🤣🤣
😂😂😂😂shado
Ashado chidodo😹😹😹😹satithandiza ndukuuzan 🙌a Hyphen a ambulance driver 😹😹💔
Symbol pumpkin 🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣🤣eeeeee koma
Ashado akokele fundo, Alibe fundo zoveka. Bwana sikusinja ali mwala mwala mo fire driver. # usauver ndi mbambande
Entertaining as usual.....ati tidikile maliro enao🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🙌
🤣😂😂😂😂😂😂koma shadow...this is awesome..tikachonga tikakangowona dzungu
Atii Hyphen Azidzayendetsa Galimoto😂😂😂😂PaKhomo Paliponse Nde Kuti amawauza Kuti Mudzakhala ADriver😂😂😂AShadow Sali Serious
Ashado amenewo atithandiza koma 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣.
Che mkope koma 😂😂
ATI dzungu😂😂😂
You guys never disappoint hahahahahahahaah
A Shadow nfundo alibe😂😂🙌
Ndiye mwati fumu iziza yendesa amburasi😀😀😀😀
😄😄😄...eeissh Ashado awawa ayayaya... keep it🔥💯
Haha a shado omweo😅
NZungu lomwelo kt wawawaaah 🔥🔥🔥
Maliro akutsogolo awa ayi🤣🤣🤣🤣
Ashado kutalikitsa nkhani eeeeh😂😂😂😂
Hahahhaha this is nice,mmangoseka ine 🔥🔥
Rewatching basi nanga mkutani zzzzz
Che nkope si munthu wamba muli engine 🤣🤣🤣🤣🤣
Nde mwat Mfumu ili mokayendetsa ambulance yashado 😂😂😂
Kkk ati nde ine ndiabwenze🤣
Penapake ngozo uzitseka bwino kkkkkkkkkk
😂😂😂😂😂😂😂 Usauver just made my day🙌🙌🙌🙌
Ati owo ndizizayendetsa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Makondomu kuvuta kugula 😂😂😂 mpaka kufunsa nazo mafuta anyale
Nice piece....big fan
Mumatha ma dolo keep it up
😂😂😂😂 koma akaka makunga eeeish
😂😂😂 amfumu
Nice nice stuff
ganidzani akufuna nyali ya lamp 😃😃😃😃
Kheze adah 🏃🤣🤣🤣🤣 iweyo u shopkeeper ukukwanira
Kma mayendedwe apa gate apo sinaone bwino mwati zakhala bwanji 😂😂😂😂🤞
ka Shop Keeper kake kachipongwe bwanji. 😂😂😂😂.......#Khezeni
More fire 🔥
Ngozoo sidzatheka sure kkkkkk
Nice one guys
Ganizani😂😂
@albertkamwendo3385
2 жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂..afuna nyali aise
@sylviamachemba1863
2 жыл бұрын
Hahahaha
Akuchimuna a shadow😅😅😅😅
Koma Hyphen akuoneka kuti wathawa mbola pa gate po.....sanaoneke mayendedwe ake
Gan, Nina aaah eeh mssive kkkk makhondomu kkkk
Ashadotu amenyedwa ulele ndi mai sisoko, nanga kukakamila kumeneko zoti ndi wa karate akudziwa
mumakwana a Ngozo mix Hyphen along side Chenkope.
🤣🤣🤣🤣🤣 Anthu muli nd chipongwee
Ashado🤣😂🤣
Anakupezani mukudya pleasure nkusokoneza zinthu
😂😂😂😂😂Nice one
Aah aah aah 🤣🤣🤣 ashado
Manifesto 😂🙌
fire mwana makombora kkkk
Hypen oyendesa ambulance amayine 🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣koma a shadow ake!
BP yanga imakhala yakwera ndikamachokera Ku ngongole🤣🤣🤣🤣mmakwana Mamie......komanso ganizani ayi shuwa🙌🙌
@daviemindozo2933
2 жыл бұрын
amakhala serious mamie tu 🤣🤣
Zoona anzanu kungowachita balamanthu hahaha
Nice one
Gani amatha😂😂😂😂😂
Ambulance iyendetsedwe basii
Bwana sikusinja kkkkkk
Kkkk galimoto yomwe sinabwereyo
Black mina my favourite
Kkkk😂 the best
Sangie is a good Actress
Ganizani😂😂😂
Ganizani aaaaa
🤣🤣🤣🤣🤣ah ah koma ganizani