Mtebe is still suffering as we speak....
😂😂😂😂😂😂inde Patricia, tinamuona Ngozo mwamuna wa discipline muthana nokha koma Mtebe akudutsa muzokhoma zoposa za Habakkuk
Kkkkkkkk koma abale nkhani ija yafikanso kwa Habakuku
😂😂
Kkkkkk km busa iwe chiweruzo chidzakhale chako chokha bas kmso pawekhaso
Aaah but sangie is the biggest deal😂😂😂😂😂😂 the way she said "pitiliza"🔥🔥🔥🔥
Mkazi uyo siwa Albert 🤣🤣😂 stalking imeneyo
😂😂😂ndi mkazi wakedi ameneyo ngat akuuser ma perfume ofananaso😂zogula albert
Hahaaa Ngozo you are the best Munthu sasanzika atathamangitsidwa
😂😂😂 grt works guys...need yo works on TV
Love this...looking forward to the next episode.. love the new characters... Also. Kapasule tomthana naye chonchi...😅
Fire 🔥🔥. Zili bwino kwambiri
You are the best guys, koma kafikeko ka 30 minutes per episode
Ndipo inu,, angotilawitsa zoona
Never stop guys keep it up zilibho kwambiri
You guys never disappoint ❤️😊
Abusa amenyedwapo apa hahahaha.... Iyiyi nde yayaka moto keep it up madolo... Mukutimvetsa kukoma
You guys don't disappoint 🔥🔥🔥🔥 love you
Kkkkkk ❤ km busa ku pita kunyumba kwa a tate kd et mwakwana mwava
Jegedaya afuna ayipitse zinthu😂😂😂koma zamuvuta
Jege ndi OG😂
Sangie and Jedediah best actor....
Anthu a humblefe mudzisamala nafe kkkkkkkkk ndi ka short tempered 😂😂😂😂
Kukayaka moto kwa Ngozo shuwa😂😂😂😂 mukumachedwesa ma episode koma ma guy
Osanama, guys, you are doing great
For us who came from Facebook let's enjoy 😂😂😂😂😂
😂
Piksy ukutilimbikitsa ndewu Eit 😂🤣 #brocode... #Piksy umatha✌️
Musamakonde ndeu inu😂😂😂
Hahahhahaha sangie uyo akuthesela banja uzimupewa
Mg1 ndi baby mama aku user perfume mmodzi🤣🤣🤣
Apa nde invigilator asowa kuyumba kopta 🙌🙌🙌🙌now I'm waiting kut adzakumaneso ndi ngouzo😂😂😂😂😂
Ineso ndi munthu, ndikaponda moto ndimapsa🤣🤣🤣
Thebede aaaaaaaaa 😂😅😅😅 Wayamba mqbodza Thebede akufunika makofi 😅 Angauzo mumumenye
Mumatha ma guy🔥🔥🔥 koma nthawi nde tionjezereni please
Apondedwe basi 🔥🔥🔥🔥
Kodi uyuso akufika ndi itit,,,ati mowa my husband, kkkkkk akuonek kut fire 🔥.
😂😂😂😂 zafikapa pakati akufunika kwambiri
This is nice,mupitilixe ndithu
😂😂😂😂😂 the custome Ali bho😂😂😂 my husband this my husband that ...zizungulire nkati..... Wandiwazaaaa
😅😅😅😅😅aaah magaye munabwera🔥,a shado ndi Jebe
U don't disappoint guys
Piksy yur so calm eee ntamuomba mbamatu jededahyo 😂😂😂
Mwana mtonga king of DWAMBAZI
Waiting, km kuchema
Mr ngozo zibwana alibe abusa zawavuta bas 🤣
Ineso ndi munthu nkaponda moto ndimapyaa 😂😂🔥
Ngozo lero mpakana kukwiya kkkkk ayi sorry koma upezenu
Man Pisky mutaionjezera episode yanu idxikhalako yaitali because zikubeba zedi😅 mumatinvetsa kukoma zedi😂
Ndipo fact mmmmm
Ndiyelekeze mwina chomchi aaaaa😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 koma ndasekaa Angozo bwezi atakupondaa iwee
Kkkkk koma abusa eti azimayi achonch😂
Zebedaya apa waponda moto mphwanga....ngozo azakuswa😂😂😂😂😂🎉
“Jedediah, undisamale!”😂😂😂😂
Inenso ndi munthu, ndikaponda moto ndi mapsa😂
Hahahaha kmatu iyiyi nde ndiyokwanila😅😅😅😅
Mtebede athela mwa ngozo🤣🙌🏾
Apapa ukhale sureee😂😂😂😂😂
M'busa akupempha mosweka mtima 😂😂😂😂
Ka mtebe amwene😂
Hahahahaha khaniyi tu nkudziwa kale😂😂😂😂
Jede the rat aka thira kuwiri😂..... koma iwe Sangie sangie🙌
Jedediah azafera manja mwa anthu 😂😂
Kkkkk ma phone avuta😂😂😂
Ka chiunda kodya ndi mafupa omwe a shado kkk
😂Ati umasanzika atakuthamangitsa kkkkkk ngauzo unafika 🔥🔥
Ka m'busa kachinyengo😂😂
ati tikuiziwa ma version awiri osiyana kkkkkk koma ma guy
Hahahahahahaha koma mtebede...😂😂😂😂😂😂
😂Angozo alusatu kubakila bestie Albert
Mtebede zimugwela😂💔🤗🙌
😂😂Ngozo!!!! akunena kuno ka Mtebe👁🗨
Zebedaya 😂😂😂 eti makutu ngati kalulu 😂😂😂😂
😂😂😂 ati ndikupempha mosweka mtima😂😂 ntebe ndi mbala aix
Eti munthu wathamangisidwa akusanzikanso😂😂😂😊
Sangie guys🙌😂😂🔥🔥🔥
Jededaya kusangalala ngati alibe Mavuto 😂😂😂
Ndipo ntebe ndiotopetsa kkkk😅
Ati m'busa uja akupempha mosweka mtima kkkkkk
Y'all can act ehhh🔥 munangotengana
ASE ngati sakunamizilatu
😅😅 ati ndanenera tu nde uzikabwezanso change
Jebedaya asazaphweketse mgwirizano wa ngozo ndi patricia😅
Mukuitha ndisaname❤
Jebedaya tachezetsa eti😂😂😂😂😂😂😂
Kodi ka mkazi kalowa mu shop kaja khalangati ndiwa Albert eeeeti🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂 Jebediah mabodz😅😅😅😅
Za achina Mtebe kikiki
Kkkkk nice 1 Mr ngouzo
guys mumakwana kwambiri ndipo ndimamva kukoma one day ndikukufunani ku bar mumwamwela ija tichezeko wez.
Mdala ameneyu adzathera mmanja mwa anthu
Ngati kuli muthu amene sindimamuopa ndi Aibert
Ma phone etii kkkk anayiwaridwanso
Good work guys
Jededaya tachezetsa heti😂😂
waiting for next
Mwabwera 🔥🔥
Can’t wait oooo eeeish 😢😢😢😢😢
Ntebe😂 apa ndiye zamuvuta
Ngozo amakwana amwene😆kuvuta kumukhala majokes nde sinkhaninso
Iyiyi tizawonera ndeu kutsogoloku😅😅😅😅
Ati iweyo kulowamo ka 4😂😂
Ntebede akufunika kumenyedwa
Ngonzo udzikwiya zenidzeni malo oyenela kukwiya
Patricia wife material😂😂
A piksy ndimakugwirani from Maputo. Ili ngini bhoo nginiii.koma osamachedwetsa
Am waiting ma phone
Pitani nokha abusa mukatenge maphone kwa Albert
Am waiting
Пікірлер: 299
😂😂😂😂😂😂inde Patricia, tinamuona Ngozo mwamuna wa discipline muthana nokha koma Mtebe akudutsa muzokhoma zoposa za Habakkuk
@russellmkawa2237
Жыл бұрын
Kkkkkkkk koma abale nkhani ija yafikanso kwa Habakuku
@STRATADATA-KB
Жыл бұрын
😂😂
Kkkkkk km busa iwe chiweruzo chidzakhale chako chokha bas kmso pawekhaso
Aaah but sangie is the biggest deal😂😂😂😂😂😂 the way she said "pitiliza"🔥🔥🔥🔥
Mkazi uyo siwa Albert 🤣🤣😂 stalking imeneyo
@tonilipenga
Жыл бұрын
😂😂😂ndi mkazi wakedi ameneyo ngat akuuser ma perfume ofananaso😂zogula albert
Hahaaa Ngozo you are the best Munthu sasanzika atathamangitsidwa
😂😂😂 grt works guys...need yo works on TV
Love this...looking forward to the next episode.. love the new characters... Also. Kapasule tomthana naye chonchi...😅
Fire 🔥🔥. Zili bwino kwambiri
You are the best guys, koma kafikeko ka 30 minutes per episode
@taonachisuwo5184
Жыл бұрын
Ndipo inu,, angotilawitsa zoona
Never stop guys keep it up zilibho kwambiri
You guys never disappoint ❤️😊
Abusa amenyedwapo apa hahahaha.... Iyiyi nde yayaka moto keep it up madolo... Mukutimvetsa kukoma
You guys don't disappoint 🔥🔥🔥🔥 love you
Kkkkkk ❤ km busa ku pita kunyumba kwa a tate kd et mwakwana mwava
Jegedaya afuna ayipitse zinthu😂😂😂koma zamuvuta
@manuelnamasani3606
Жыл бұрын
Jege ndi OG😂
Sangie and Jedediah best actor....
Anthu a humblefe mudzisamala nafe kkkkkkkkk ndi ka short tempered 😂😂😂😂
Kukayaka moto kwa Ngozo shuwa😂😂😂😂 mukumachedwesa ma episode koma ma guy
Osanama, guys, you are doing great
For us who came from Facebook let's enjoy 😂😂😂😂😂
@babafamous44
Жыл бұрын
😂
Piksy ukutilimbikitsa ndewu Eit 😂🤣 #brocode... #Piksy umatha✌️
@talandiranyanda8843
11 ай бұрын
Musamakonde ndeu inu😂😂😂
Hahahhahaha sangie uyo akuthesela banja uzimupewa
Mg1 ndi baby mama aku user perfume mmodzi🤣🤣🤣
Apa nde invigilator asowa kuyumba kopta 🙌🙌🙌🙌now I'm waiting kut adzakumaneso ndi ngouzo😂😂😂😂😂
Ineso ndi munthu, ndikaponda moto ndimapsa🤣🤣🤣
Thebede aaaaaaaaa 😂😅😅😅 Wayamba mqbodza Thebede akufunika makofi 😅 Angauzo mumumenye
Mumatha ma guy🔥🔥🔥 koma nthawi nde tionjezereni please
Apondedwe basi 🔥🔥🔥🔥
Kodi uyuso akufika ndi itit,,,ati mowa my husband, kkkkkk akuonek kut fire 🔥.
😂😂😂😂 zafikapa pakati akufunika kwambiri
This is nice,mupitilixe ndithu
😂😂😂😂😂 the custome Ali bho😂😂😂 my husband this my husband that ...zizungulire nkati..... Wandiwazaaaa
😅😅😅😅😅aaah magaye munabwera🔥,a shado ndi Jebe
U don't disappoint guys
Piksy yur so calm eee ntamuomba mbamatu jededahyo 😂😂😂
Mwana mtonga king of DWAMBAZI
Waiting, km kuchema
Mr ngozo zibwana alibe abusa zawavuta bas 🤣
Ineso ndi munthu nkaponda moto ndimapyaa 😂😂🔥
Ngozo lero mpakana kukwiya kkkkk ayi sorry koma upezenu
Man Pisky mutaionjezera episode yanu idxikhalako yaitali because zikubeba zedi😅 mumatinvetsa kukoma zedi😂
@ayaowansongo6436
Жыл бұрын
Ndipo fact mmmmm
Ndiyelekeze mwina chomchi aaaaa😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 koma ndasekaa Angozo bwezi atakupondaa iwee
Kkkkk koma abusa eti azimayi achonch😂
Zebedaya apa waponda moto mphwanga....ngozo azakuswa😂😂😂😂😂🎉
“Jedediah, undisamale!”😂😂😂😂
Inenso ndi munthu, ndikaponda moto ndi mapsa😂
Hahahaha kmatu iyiyi nde ndiyokwanila😅😅😅😅
Mtebede athela mwa ngozo🤣🙌🏾
Apapa ukhale sureee😂😂😂😂😂
M'busa akupempha mosweka mtima 😂😂😂😂
Ka mtebe amwene😂
Hahahahaha khaniyi tu nkudziwa kale😂😂😂😂
Jede the rat aka thira kuwiri😂..... koma iwe Sangie sangie🙌
Jedediah azafera manja mwa anthu 😂😂
Kkkkk ma phone avuta😂😂😂
Ka chiunda kodya ndi mafupa omwe a shado kkk
😂Ati umasanzika atakuthamangitsa kkkkkk ngauzo unafika 🔥🔥
Ka m'busa kachinyengo😂😂
ati tikuiziwa ma version awiri osiyana kkkkkk koma ma guy
Hahahahahahaha koma mtebede...😂😂😂😂😂😂
😂Angozo alusatu kubakila bestie Albert
Mtebede zimugwela😂💔🤗🙌
😂😂Ngozo!!!! akunena kuno ka Mtebe👁🗨
Zebedaya 😂😂😂 eti makutu ngati kalulu 😂😂😂😂
😂😂😂 ati ndikupempha mosweka mtima😂😂 ntebe ndi mbala aix
Eti munthu wathamangisidwa akusanzikanso😂😂😂😊
Sangie guys🙌😂😂🔥🔥🔥
Jededaya kusangalala ngati alibe Mavuto 😂😂😂
Ndipo ntebe ndiotopetsa kkkk😅
Ati m'busa uja akupempha mosweka mtima kkkkkk
Y'all can act ehhh🔥 munangotengana
@lusunguhkayira6924