Milandu Ya chilima Yatha | Kaliati Ndi khwimbi La UTM kusangalala ''Athyola dance''

Patricia Kaliati Ndi khwimbi La UTM kusangalala ''Athyola dance''

Пікірлер: 37

  • @GetrudeMkandawire2
    @GetrudeMkandawire2Ай бұрын

    SKC Boma motooo buuu 🔥🔥🔥🔥

  • @HassanTayubu-li3tm
    @HassanTayubu-li3tmАй бұрын

    Amazing inu mulibe nzelu kwambili

  • @KaipaEmanuel
    @KaipaEmanuelАй бұрын

    Chilima keep it up bwana

  • @temwamfunejere
    @temwamfunejereАй бұрын

    SKC🎉🎉🎉❤❤

  • @WalikoMsutu
    @WalikoMsutuАй бұрын

    Zikakunyasa uwone zochita UTM 🔥🔥🔥

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9oАй бұрын

    Wakwiya ndi mfiti SKC 2025 BOMA ❤❤❤❤❤

  • @user-ve7rx7vj1g
    @user-ve7rx7vj1gАй бұрын

    Muyambeso kutinamiza...kulakwatu uku aMalawi

  • @Dorah-zl9uf
    @Dorah-zl9ufАй бұрын

    Kkkk koma kaliyati sazatheka😂😂

  • @user-dd9yq9qk1k
    @user-dd9yq9qk1kАй бұрын

    Mwaiwala kale a Malawi ayi zikomo

  • @user-ro1pl7rv7z
    @user-ro1pl7rv7zАй бұрын

    Basi tu a zimayi 😂kumadikura 😅

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711Ай бұрын

    Aaaa agalu nokha nokha ndi ndi MCP yanuyo okuba okha okha zauchitsilu mene wathelano malawi pano kumanyadila idzi thembelelo chiyani amalawi

  • @QueenNhlema-sc3nh
    @QueenNhlema-sc3nhАй бұрын

    SKC my vote❤❤❤❤

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lpАй бұрын

    Ukukup sakokakoka kukala ngamti opandazelu kusangalila chakumba chilima ndi mbusi chkwera palukundu pao iya yausilu uweiyai chatap

  • @user-qj3db4lu7c
    @user-qj3db4lu7cАй бұрын

    anthu amene akuononga dziko ndi azimayi amangokondwera zilizonse,Koma pamapeto pake amayambaso kulira ndiyiwowo

  • @HassanTayubu-li3tm
    @HassanTayubu-li3tmАй бұрын

    Anthony inu mukungovomeleza zosalongosoka mukafika kunyubako mukukangona ndi njala

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cnАй бұрын

    Komatu aMalawi kumachilapa chilima ndi chakwera nzawo ndi zimodz pls kumaganiza mwakuya popanga chisakho chanu mutipwetekesaq

  • @user-kr8th5oh7b
    @user-kr8th5oh7bАй бұрын

    Kusangalarila Muthu okuba a Malawi amaganiza mopeoera

  • @user-le9su3mt7r

    @user-le9su3mt7r

    Ай бұрын

    Bola loho chakwera mbava

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489Ай бұрын

    A dpp akuwona nyekhwe kaye ku bagamoyo nyekhwe inatembenukira😂😂😂

  • @manasemaposa
    @manasemaposaАй бұрын

    Bravo

  • @jahmanmakwinja-ef7zn
    @jahmanmakwinja-ef7znАй бұрын

    UTM yabwera kudzakhala,, take it or leave it, afune asafune. Next government ndi UTM led by SKC

  • @ChifundoChiwanda-ru3pg
    @ChifundoChiwanda-ru3pgАй бұрын

    🔥🔥🔥🥳

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711Ай бұрын

    Inu munawona okuba okha okha akumangana uchisilu mudzalowabe mundende bola moyo

  • @ThomNkhoma-no5rt
    @ThomNkhoma-no5rtАй бұрын

    🔥🔥🔥

  • @Abdul-xk8dq
    @Abdul-xk8dqАй бұрын

    Koma mukusowa zochita chosecho maluzi alitho

  • @hopembendela
    @hopembendelaАй бұрын

    Panyapanu agalu

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214Ай бұрын

    Ayi zikomo anthu inu koma ndi chani???

  • @KaipaEmanuel
    @KaipaEmanuelАй бұрын

    Asowa nazo kolowa kd .?

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489Ай бұрын

    MCP amatelo inu muli ku kenani anzanu kuwasiya kwa pilato zaka zonsezi, ulendo onyamukira limodzi.

  • @eliaskhofielias8152
    @eliaskhofielias8152Ай бұрын

    Ndikamaona anthu akumasapotabe chilima ndi tonse alliance ndimangot amalawife tilindivuto lalikulu.koma zoona anthu amenewa atipusisa kale 5 years for nothing still kumawaomberabe manja.agalu amenewa 2019 amabwebwetuka kut anzawo anali olephera lero iwo alowa mkat zero kwa 10 lero anthu akutengekabe nawobenso.amalawi ndife ofa kuzimu ndithu ndi thupi lomwe ndife osaganiza timangooneka ochenjera koma tulo lilindife Mmmm zosaoneka.timatengeka ndizazing'ono kwambili even tishirt imene sitichedwa kuiwala ndife agalu eni eni.atipusisenso kachikena makapewanso tiwaikenso pampando for 5 yrs again zoona?iwo alibwalo akulephera kumenya mpila pomwe ama bulema anzawo kumati olephera.timilomo tawoti tinabwebwetuka kwambili mu 2020 muja apatayambanso kunamiza anthu 😂😂😂😂 mayo I cry for my mother land Kaya nabadwilanji kumalawi ine ambuye tikhululukileni ndithu sitidziwa chomwe timatsatila ndife akhungu mmalawi muno.and sitidziwa chomwe timafuna ife pokavota timangopangila kupsa ntima basi osalingalira zamawa.

  • @Hlehle719
    @Hlehle719Ай бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7eАй бұрын

    Masanje eni,,eni,,kulephera kuimba njaratu imeneyo😢😅

  • @eliffagondewe8214

    @eliffagondewe8214

    Ай бұрын

    😂😂😂😂

  • @louisbonongwe8537
    @louisbonongwe8537Ай бұрын

    Koma campaign iyaka

  • @umalimaganga
    @umalimagangaАй бұрын

    CHIPANI musachichepetse ichi nchamoto

  • @CHAKUWALOMKANDAWIRE
    @CHAKUWALOMKANDAWIREАй бұрын

    Nice

Келесі