eish...Tamvani izi Amalawi

Tamvani izi Amalawi

Пікірлер: 44

  • @ChakhaMacaulayRajab-rl2vf
    @ChakhaMacaulayRajab-rl2vf5 ай бұрын

    Very nice mumayika khani zabwino kwambili

  • @Resterzambasa
    @Resterzambasa5 ай бұрын

    Mumabwelesa nkhani yabwino nthawi zambiri koma ngati mchitidwe obela anthu kapena kupangidwa chipongwe mumafuna kuti anthu tiziwe kuti mwina anthu Ena asabeledweso zimafunika kuti musamabise maina a anthu wo kuti akaziwika ena akamuziwa asapitekoso apulumuke so plz musamabise maina wo

  • @giftchale672
    @giftchale6724 ай бұрын

    I know that movie billionaires club Nigerian movie, zabodza zonsenzi

  • @user-mc6uv9gm5s
    @user-mc6uv9gm5s4 ай бұрын

    Ngat alipo tigayileni number nafeso tikhale ndi ndalama

  • @PililaniChipendo
    @PililaniChipendo21 күн бұрын

    Ine nthawi ikadzakwana mulungu wanga adzasitha nyengo zanga ,koma zinazi mmmm ai over my dead body

  • @user-ip6pt3rw7f
    @user-ip6pt3rw7f23 күн бұрын

    tiyeni tizidalila mulungu zinazi ungopenga nazo

  • @user-le8jh3st8b
    @user-le8jh3st8b5 ай бұрын

    Kupeza chuma ndi chisomo chamulungu koma zamankwala umango pezanazo mavuto kapena kupenga nazo misala ngati mulungu mulungu

  • @user-cn8qh8vo8u
    @user-cn8qh8vo8u4 ай бұрын

    😂Abraham Malo mopepher busy kutumiza mbale wake kwa sing'anga 😢😢

  • @user-dx4zu1wv4q
    @user-dx4zu1wv4q5 ай бұрын

    Kkkkk koma kulemera ndi chisomo chamulung basi

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga73445 ай бұрын

    Tapeza chophera chilima ndi chakwera so pano asanduke ndondocha chakwera

  • @chigokhalid9420

    @chigokhalid9420

    5 ай бұрын

    😂😂😂 hahahaha

  • @user-le8jh3st8b
    @user-le8jh3st8b5 ай бұрын

    Kupeza chuma ndi chisomo chamulungu koma zama

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q11 күн бұрын

    Anthu awa amamuchosa munthu mafupakukhara munofuokha okha

  • @BeatGondwa
    @BeatGondwa2 ай бұрын

    😢😢

  • @user-fq3wz5dd2s
    @user-fq3wz5dd2s5 ай бұрын

    Uzidalira Jehova

  • @user-ij3wu3if5v
    @user-ij3wu3if5v4 ай бұрын

    Yooh this world 😢

  • @stevemalata627
    @stevemalata6275 ай бұрын

    Mulungu yekha ndi wamkulu

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw5 ай бұрын

    Ndietu yathela panjira

  • @user-qu9iu7hs8k
    @user-qu9iu7hs8k5 ай бұрын

    Uziyika tittle

  • @christopherbadson699
    @christopherbadson6995 ай бұрын

    Palibe chifukwa chotidziwitsa ngati mukubitsa dzina lake, its usless information,

  • @user-bn5ed4ky6q

    @user-bn5ed4ky6q

    4 ай бұрын

    Ndipo live

  • @LastonBeyard
    @LastonBeyard2 ай бұрын

    Nice

  • @KennethKambatata-sr2qu
    @KennethKambatata-sr2qu4 ай бұрын

    Koma yeah

  • @noahtsamdoka1172
    @noahtsamdoka11724 ай бұрын

    😂😂😂😂😂 kulemela mkulimba mtima amatanthauza izi eeti 😢😢

  • @Ulard-vc6hs
    @Ulard-vc6hs5 ай бұрын

    😢

  • @user-vy7bm6dg8s
    @user-vy7bm6dg8s5 ай бұрын

    Nde yathelaso panjila bwanji

  • @danielmaganiza
    @danielmaganiza4 ай бұрын

    Ndipaseni mapu or # pilizi

  • @NkambusyeYusufu-eq5hy
    @NkambusyeYusufu-eq5hy5 ай бұрын

    Koma yaa

  • @rhodahjere8747
    @rhodahjere87474 ай бұрын

    Please trust God😭😭

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q11 күн бұрын

    Guys uyu munthu akunena zoonadi anthu akukalonga chitipa nianthu owophwa kwambiri ndipo nianthu oziwazisamba osati masewera ndipo amaopanaokha okha

  • @user-ci6zw3mj6t
    @user-ci6zw3mj6t3 ай бұрын

    😮😮😮😮😂😂

  • @user-cm8ji7im1h
    @user-cm8ji7im1h5 ай бұрын

    Patseni map inee mpite 😂😂😂😂

  • @user-ze2og2mm2r
    @user-ze2og2mm2r4 ай бұрын

    Tipatsen number tipiteko

  • @user-kb7yn5yy6y
    @user-kb7yn5yy6y5 ай бұрын

    Ife ndife achakume aponye number take ameneyo tipiteko bas

  • @user-kb7yn5yy6y

    @user-kb7yn5yy6y

    4 ай бұрын

    Ok

  • @AbdullahBullah-jj6bm
    @AbdullahBullah-jj6bm5 ай бұрын

    good work

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9i5 ай бұрын

    Whichcraft at its peak!

  • @user-kb7yn5yy6y
    @user-kb7yn5yy6y5 ай бұрын

    Tihkoza kukwanitsa ife zimenezo tipatsen number yakeyo

  • @BeatriceMitayi-wt3js

    @BeatriceMitayi-wt3js

    4 ай бұрын

    😂😂😂😂😂akakupatsa undigayire

  • @checkyokwey1772
    @checkyokwey17725 ай бұрын

    Number yamunthu yi bwanji tikamupepherere

  • @agnessjuttah7491

    @agnessjuttah7491

    3 ай бұрын

    Kkkkkk mumapemphelera anthu

  • @ashikalam8616
    @ashikalam86165 ай бұрын

    Address please ❤

  • @FlyingSquadz-nz5cl

    @FlyingSquadz-nz5cl

    5 ай бұрын

    😅😅😅😅😅🎉