Kufuna kutchukila pa miracle chinga zaziiii kufuna kufana ñdi bakili muluzi KZread channel Wagwa mayo kape peza zina zochita
@emosichimphengula86555 ай бұрын
Zopusa ukuti chiyani iwe ndiye kaya aaaa mwatani amwene ntchitoyi siyanu
@user-si7po9sd5i5 ай бұрын
Banja was meant for well matured people,not makanda,if you are not well matured enough,don't force yourself into marriage.
@innocentjagali
5 ай бұрын
Wisdom
@marianyirenda
5 ай бұрын
This is a good point ,your true 🤝
@user-gf7oo9ht4y4 ай бұрын
Nde ngati simukuchidziwa mukuyakhuliranji za m'banja mwa eni!!!!!!!!! Ndinu achitsiruuuuuuu!!!!!!
@FYAHMANNINETENINE-ty4jc5 ай бұрын
Keep Up The Good Work 💪♥️🔥
@Yamikanlajah
2 ай бұрын
😊😊😊😊😊
@user-zw8ns7bk7s5 ай бұрын
Kape iwe ukufuna ukambe kt chani apa ndiye olo itatha ndi mulongo wako aaaaa chitchende chako ndithu
@KettieGwedera
26 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@kelvindickson5 ай бұрын
Komatu simunanene chomwe chathela banjali mogwizana ndi mutu wankhani aaaa madala tafufuzani Kaye mutiuze bwino
@UmaliTama2 ай бұрын
Ndikufuna ndidziwe nkhani yeni yeni yokhuza za grace chinga
@user-tt7eh6bm2j5 ай бұрын
Next time mukadzafuna kuposta nkhani yamunthu mudzafufuze bwinobwino coz palibe chanzelu chomwe mwapangapo
@omarlux34345 ай бұрын
iwe sukukwanisa ndikuza chilungamo sam mavita unja amatha
@edsonnyasulu53945 ай бұрын
Banja sichiñthu chamasewela uli ngati usogoleli umafuna nzeru zakuya poyendesa banja Ndichifukwa chake muzaona zose mu banja zilimo koma limathabe chasowa baja ndi nzeru
@inessmsiyambiri85175 ай бұрын
Aaaaaa koma iwe chukukhudza mchani aaaaa koma anthu ena ndinu makape bwanji aaaaa
Be serious make it professional it's like you don't know what you are talking about please don't West time if you don't know anything about someone chifuwa mulibe information apa kkkk maka mukufuna muyakhule chani man kkkk
@user-kp2jo7gp6t
5 ай бұрын
Ndipo ngat akuyakhulapo zomvekapo apa aaaaa koma chimakhala chan kwenikweni 😂😂😂😂😂😂
@preciousbitson2352
5 ай бұрын
😂😂😂 aaah Ndipo mbwerera zake aaa palibe ndamvapo apa
@leahnyirenda38365 ай бұрын
Koma please guys be serious,find something tangible to do than waste your time and our data on useless things,ayambitsa yekha ndiye akuwuzani kut post that, everyone has issues mmabanja no marriage is perfect and they are neither saints, stop minding other people's businesses this is 2024
@phillipstamaley79015 ай бұрын
Ndiye ife chikutikhudza ndi chani za zimenezi
@pemphokatembe443
5 ай бұрын
Koma ndiponso aaaah
@user-vc7bk2ut6b5 ай бұрын
Aaaaah ndimaona ngatitu akulankhura ndi mamunayo Umboni weniweni tikanaumva kuchokera kwa mwiniwake
@user-zf9mj4jj9w5 ай бұрын
Kweni kweni ukufuna kutiuza kt chan ndangoononga bundle yanga ine
@samuelbrian34095 ай бұрын
Mutu wa nkhani?????? 😮😮😮😮😮 Waisting my data and my time yoooo 😢😢😢
@user-gf7oo9ht4y4 ай бұрын
M'kamwa mwa chilomwe ngati m'menemo ungatiuze chani galu iweeeee!!!!!!!
@victoriakumwenda7673 ай бұрын
Galu wachabechabe tsiyan kubweretsa nkhan zopanda umbon bwanji mufufuze kaye
Mamuna waulula? inu nomweso mukutiso chathesa banja simukuchiziwa?
@user-uv1ub3xz7l5 ай бұрын
Nde iweyo ngat choona chake sukichidziwa nde ukubwelelanji apa mkumayankhula fundoles zakoz zaziiiii
@DavidMontford5 ай бұрын
Koma mwakhonzeka koma sizikunvekatu apa aaah mesa mukuti mwafufuza bwino bwino kuti mutiuze
@MacDonaldkachala-cm5gc11 күн бұрын
You start the news without story
@user-wu8kp7ui5j5 ай бұрын
Kufotokoza kukuvuta ankolo muzipanga Kaye training musanayambe program yanu.
@inessmsiyambiri85175 ай бұрын
Nde ngati choona sukuchidziwa ukudzatani apa apatu amzanu akufuna kutvhukisitsa umufumse zomwe amapanga namadingu akafuna ki akita
@ConfusedAtv-bs4gc5 ай бұрын
Nonse mboliyambambo anu nyini Zamanu musamatinyanse APA anthu Ngati ndookongolanso amene mukutithela madata apawa banja limakhala nyumba osati mafoni zauhule basi iwenso Ngati umamufuna huleyo kapeze wako Ngati sumatha kufunsila olo mbuzi ziliko utheka kumakagonanazo kuyambila lelo me siye kumabwekesa nkhani zamabanja aweni APA nanunso anthu amene muli ndimabanja pasani ulemu banja lanu polisunga nyumba osati pafoni
@GanizaniBalon-ie2oq
5 ай бұрын
Nanuso kahweleni uko zochitsilu
@user-bs7mi3td3f
4 ай бұрын
Komatu mau a Mulungu anakaniza zopereka umboni wa bodza...if you don't know what happened lean to be chete cos mudzayankha nazo mlandu ku mpando wa chifumu wa Mulungu mwini kuweruzaaaaaa ohoooo
@ChipiliroLeadson4 ай бұрын
Ndiwe omvesa chisoni kwambiri
@user-nw6om5sc2n5 ай бұрын
Waweso nde maphwara anu aise bwanj kundithera bundle Yanga mukudziwa kuti zilibe umboni weniweni ndikuyifuna Pompano data Yanga
@humphreychisanu24355 ай бұрын
Inu mngamabodza akulu.
@dorcusmnkhondia72205 ай бұрын
Aaaah koma no sense maine 😢😢😢bundle yanga baya.. Why should they tell. You kkma
@user-nb7bv6zy8c5 ай бұрын
Palibe chomwe mukudziwa kafufuzeniso bwino bwino
@allanchawanda18895 ай бұрын
Iwe ada ndi nyasa hit yakoyi ukafuna kuti anthu apange like zakozi uzibwera ndinkhani zoti ulinazo umboni komanso zizikhala ndi mutu weni weni nkhani zotyakuka bwino bwino , ngati nkhaniyo simukuidziwa sibwino kubwera pa media choncho nkumazatithela madata. Cause inuyo mukamayamba kufotokoza ife timaona ngati odziwawo ndinuyo, koma mmm ata, nde munthu upangapo like nkhani yake itiyo apapa?
@user-cv7ow3vb4w5 ай бұрын
Ukamaika ma headlines uzifotokoza zokhuza mutuwo osat zamkutu ukuyakhulaz zikugwiliza ndimutuwo
Пікірлер: 338
Palibe chadzelu mwayankhula Yamba mwafufudza kaye ngat mufuna kutiudza nkhani
Aaah😂😂😂😂 bambo mwakula inu koma !!😂😂nde inuyo chikukukhudzani ndichani?? Zaziiiiiiii basi
Uyu wasowa kosewera iyaaah😮😮
Mukamalankhula muzikhala mutakonzeka bwinobwino
Asaaaa chilungamo sumukuziwa ingositani kuyakhula iyaaa
Khati mukusowa zochita kumafotokoza zamabaja aena paneti khati ari maluzi ndi zopusa zimenezo zabaja mwako amakurengezera ndindani sitikuyisiwa khani imeneyo olo titapanda kuiva yandinyasa kwambiri pangani ndarama munjira zina osati zopusazo mbuzi
You are doing a great job guys
Amalawife tili ndi kuchikamwa eti,mulengezeso la mwana wanga lathaso
@SimplexWiskes
5 ай бұрын
Umakwana😊😊😊😊!!!!!!!
Kod mukufotokozela amalawi chan kweni kweni chifukwa palibe chomwe mukufotokoza please
Ndiwe galu kwambasi cz sukamba zoveka komaso sudziwa kufotokoza nkhani.ndiwe galu kwambasi utaitsa nthawi anthu
Chamba musizuta bwino Galu iwe Pesa dzina zocheta
My data data 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Mukutinjiiii Inu apa eeee
Nanga poti chooona chenicheni simukuchidziwa mwaudza bwanji anthu zoona musanaponye nkhan zanu mudziyamba mwafufudza zopooira
@user-yj2dz5ej7r
5 ай бұрын
Kufuna kutchukila pa miracle chinga zaziiii kufuna kufana ñdi bakili muluzi KZread channel Wagwa mayo kape peza zina zochita
Zopusa ukuti chiyani iwe ndiye kaya aaaa mwatani amwene ntchitoyi siyanu
Banja was meant for well matured people,not makanda,if you are not well matured enough,don't force yourself into marriage.
@innocentjagali
5 ай бұрын
Wisdom
@marianyirenda
5 ай бұрын
This is a good point ,your true 🤝
Nde ngati simukuchidziwa mukuyakhuliranji za m'banja mwa eni!!!!!!!!! Ndinu achitsiruuuuuuu!!!!!!
Keep Up The Good Work 💪♥️🔥
@Yamikanlajah
2 ай бұрын
😊😊😊😊😊
Kape iwe ukufuna ukambe kt chani apa ndiye olo itatha ndi mulongo wako aaaaa chitchende chako ndithu
@KettieGwedera
26 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Komatu simunanene chomwe chathela banjali mogwizana ndi mutu wankhani aaaa madala tafufuzani Kaye mutiuze bwino
Ndikufuna ndidziwe nkhani yeni yeni yokhuza za grace chinga
Next time mukadzafuna kuposta nkhani yamunthu mudzafufuze bwinobwino coz palibe chanzelu chomwe mwapangapo
iwe sukukwanisa ndikuza chilungamo sam mavita unja amatha
Banja sichiñthu chamasewela uli ngati usogoleli umafuna nzeru zakuya poyendesa banja Ndichifukwa chake muzaona zose mu banja zilimo koma limathabe chasowa baja ndi nzeru
Aaaaaa koma iwe chukukhudza mchani aaaaa koma anthu ena ndinu makape bwanji aaaaa
Km inu mulibe zelu pa dziko lapasi lotse 😊
Guys uyuyu nde amafuna chani? Kusatha kuyankhula, zopanda umboni nkumabwera nazo apa? Mxieww
More💥💥
Be serious make it professional it's like you don't know what you are talking about please don't West time if you don't know anything about someone chifuwa mulibe information apa kkkk maka mukufuna muyakhule chani man kkkk
@user-kp2jo7gp6t
5 ай бұрын
Ndipo ngat akuyakhulapo zomvekapo apa aaaaa koma chimakhala chan kwenikweni 😂😂😂😂😂😂
@preciousbitson2352
5 ай бұрын
😂😂😂 aaah Ndipo mbwerera zake aaa palibe ndamvapo apa
Koma please guys be serious,find something tangible to do than waste your time and our data on useless things,ayambitsa yekha ndiye akuwuzani kut post that, everyone has issues mmabanja no marriage is perfect and they are neither saints, stop minding other people's businesses this is 2024
Ndiye ife chikutikhudza ndi chani za zimenezi
@pemphokatembe443
5 ай бұрын
Koma ndiponso aaaah
Aaaaah ndimaona ngatitu akulankhura ndi mamunayo Umboni weniweni tikanaumva kuchokera kwa mwiniwake
Kweni kweni ukufuna kutiuza kt chan ndangoononga bundle yanga ine
Mutu wa nkhani?????? 😮😮😮😮😮 Waisting my data and my time yoooo 😢😢😢
M'kamwa mwa chilomwe ngati m'menemo ungatiuze chani galu iweeeee!!!!!!!
Galu wachabechabe tsiyan kubweretsa nkhan zopanda umbon bwanji mufufuze kaye
Big up boss
Nanga inuyo chukukhudzani nchiyani inuyo mulibe manyazi mmmmmm inuso ndinu Malawi
Musandinyanse ndimkhan zaponda pakeyi
Osamabwera ndikhani Yopanda umboni
Zazi nanu mwasowa khan ,
Nde ife titani umatha moyo wamunthu banjaso ndikachan end bro mokupepha uzipanga khan zoti tikamva tizitolamo kanthu ine sindimakudziwa ndipo ndilibe nawe vutoo bro end timakufilani coz mumatiziwitsa zambiri koma kumabwela mdi khan zokupsa
@SimplexWiskes
5 ай бұрын
Umakwana iweyoo
Sitikuv zomwe mukunen ankol mulibe nkhan
Adah simumaziwa kulongosola mukumveka ngati mukutafuna pena ngati akuchita kukukakamidzani kuyankhula
Mamuna waulula? inu nomweso mukutiso chathesa banja simukuchiziwa?
Nde iweyo ngat choona chake sukichidziwa nde ukubwelelanji apa mkumayankhula fundoles zakoz zaziiiii
Koma mwakhonzeka koma sizikunvekatu apa aaah mesa mukuti mwafufuza bwino bwino kuti mutiuze
You start the news without story
Kufotokoza kukuvuta ankolo muzipanga Kaye training musanayambe program yanu.
Nde ngati choona sukuchidziwa ukudzatani apa apatu amzanu akufuna kutvhukisitsa umufumse zomwe amapanga namadingu akafuna ki akita
Nonse mboliyambambo anu nyini Zamanu musamatinyanse APA anthu Ngati ndookongolanso amene mukutithela madata apawa banja limakhala nyumba osati mafoni zauhule basi iwenso Ngati umamufuna huleyo kapeze wako Ngati sumatha kufunsila olo mbuzi ziliko utheka kumakagonanazo kuyambila lelo me siye kumabwekesa nkhani zamabanja aweni APA nanunso anthu amene muli ndimabanja pasani ulemu banja lanu polisunga nyumba osati pafoni
@GanizaniBalon-ie2oq
5 ай бұрын
Nanuso kahweleni uko zochitsilu
@user-bs7mi3td3f
4 ай бұрын
Komatu mau a Mulungu anakaniza zopereka umboni wa bodza...if you don't know what happened lean to be chete cos mudzayankha nazo mlandu ku mpando wa chifumu wa Mulungu mwini kuweruzaaaaaa ohoooo
Ndiwe omvesa chisoni kwambiri
Waweso nde maphwara anu aise bwanj kundithera bundle Yanga mukudziwa kuti zilibe umboni weniweni ndikuyifuna Pompano data Yanga
Inu mngamabodza akulu.
Aaaah koma no sense maine 😢😢😢bundle yanga baya.. Why should they tell. You kkma
Palibe chomwe mukudziwa kafufuzeniso bwino bwino
Iwe ada ndi nyasa hit yakoyi ukafuna kuti anthu apange like zakozi uzibwera ndinkhani zoti ulinazo umboni komanso zizikhala ndi mutu weni weni nkhani zotyakuka bwino bwino , ngati nkhaniyo simukuidziwa sibwino kubwera pa media choncho nkumazatithela madata. Cause inuyo mukamayamba kufotokoza ife timaona ngati odziwawo ndinuyo, koma mmm ata, nde munthu upangapo like nkhani yake itiyo apapa?
Ukamaika ma headlines uzifotokoza zokhuza mutuwo osat zamkutu ukuyakhulaz zikugwiliza ndimutuwo
Aaah lilime lanu likunveka chilomwe kwambir 😂 ndie zikunveka mopanda dongosolo
Awatu tifika momangodutsa ma post awo aaa,kungotioningera bundle.
Ndiye ukuti chiyani palibe chomwe walankhula
Man vomerezani simukuziwa chomwemukuchita tonse sitingakhale atolankhani inu ofunika mupeze chochita china
Osapeza Zina Zokambilanaxo bwanj. Zachani zimenezo
Chimene mukuyankhula simukuchidziwa ingosiyani
Yamban kae mwapeza official information yokwanila then kumabwera pa podium Cos palibe chanzeru mwakamba koma kungobwera ndi maboza chabe😂
Kusowa doing.chikwamkhuza mchani anthuwo.ngati loyamba kutha ndiilili mmmmmm
Kusowa zochita palibe ndamvapo apaaa busy ndi banja laeni basi lanulo ndiye likuyenda😅😂
Aluminium ndiwe galu kwabas
Zinaz kumangokhar chete ngat simukudzwapo kanthu
Aaa nkuyankhula komwe mukanika zopanda mfuno nkomwe 😂😂😂
Mwasowa zolamba eti olo litatha vuto mchan
Apapa nde ma like tizipanga izizi sizikumvekatu
Aaaaaa koma madala inu sizikumvekapo apa musatinyase
Baxi munthu kumabwera apa kumazakamba zinthu ulibe umboni okwanira. Ndiwe kape aise!! Za zii!
Palibe chimene chikuvekapo pamenepo
Iwe ndi kape kwambiri
😂😂😂😂😂aaaahhh man inuyo simuli serious
Inuyo amakufufuzani nindani
@pemphokatembe443
5 ай бұрын
Kayatu
Ndiwe opusa kwambili..usazabwerenso ndinkhani yozizira ngati iyi.. mxiew
Inuso ndie ndi denje bwanj mukuyakhula zot mulibe information y can't u keep qyt
Fundoless .... Zaziiiiii
Zaziiiiii zaziiiiii!!!!
Mmmm ndiwe wabodza iwe eeeeee 😂😂😂😂
Gututu iwe eeeti?
Tikuva bwinobwino kwa Jack
Ankolo mukanangopeza zina zochitatu
Umafotokoza zabanja kodi ndilako banjalo? Bwanji osafotokoza banja la amayi ako ndi bambo ako
Kodi mukumufuna inu miracle bwanji mukulowelela mu banja la eni Ake zakukhuzani ndiziti pamenepa
Ndinu anamakhonswe kodi
Kambani zanun mubanja mwanu
Aseee improve, ukusewelesa mu Gold bwanj aaaaaa
Bodza ili wakuzani mndani kuti banja Latha?
Nde mukufuna athu apange subscribe izizi😂😂😂
Kodi mwene mukutiuza zchan kwenikweni
Mudangozolowela mabodza
Nde mutu wankhani wat mamuna waulura wausiru iwe
Palije chazelu apa
Za nkutu zenizeni
Munthu ukamanena bodza umangozungulira osanena mfundo yodziwika, kenako umazangonena bodzalo kumapeto😂.
kkkkkk tsono inuyo ngati simu ku dziwa choona cheni cheni chomwe mwa bweletsela nkhaniyi pa bwalo ndi chani