MCP vs DPP Cla$h? What happened at Mbowe, in Lilongwe today, 24 feb 2024

Members of the DPP (Democratic progressive Party) party have accused MCP (Malawi Congress Party) members of attacking them today and destroying their cars and other properties.
In this video, DPP National Deputy Director of Operations Hon. Levi Luwemba and Hon. Victor Musowa explain how alleged MCP thags attecked DPP supporters in Lilongwe today.
SUBSCRIBE here for more videos goo.gl/aYvIXK
Malawi videos in English and Chichewa

Пікірлер: 91

  • @InnocentMlelemba-dr6eg
    @InnocentMlelemba-dr6eg4 ай бұрын

    It's very unfortunate kuona izizi chikuchitika ku Malawi kuno yet pipo are suffering with hunger, economic crisis and the like. God is watching and will rescue His own pipo.

  • @petrosmunthali5562
    @petrosmunthali55624 ай бұрын

    Ine ndikuonga ngati anthu angapange zimenezi eyenera kukhala anthu omutsatira Nankhumwa😢 chifukwa chomuchatsa my chipani cha DPP😢😢😢

  • @user-we4zr2dv9y
    @user-we4zr2dv9y4 ай бұрын

    Siianthu omusatira nankhumwa amenewa?

  • @user-fs5gr8iv5s
    @user-fs5gr8iv5s4 ай бұрын

    Ngati ndinu madolo bwanji osakalanda network yamapassport akuhagolani

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td4 ай бұрын

    Mumaziyamba alomwe pitirizani mwano muona nyenkhewe pitala agura Ina anzanu akukuphani kumangolira muziponyaso Nanu ugaru changamu patawuni

  • @user-bp1gq4io7c
    @user-bp1gq4io7c4 ай бұрын

    Grace Chinga anaulula kaye kuti utsogoleri uwuwu ndi wa mwazi ndi thukuta ndizimenezi Mulungu atithandize

  • @user-jw5rx9ze8k
    @user-jw5rx9ze8k4 ай бұрын

    Ambuye atithandidze, dxiko lathu la mkamka ndi uchi lija😢😢😢😢😢 lasanduka la tsabola ndi njuchi. Yoooo satana ndiolephera. Koma apolice mulikuti? Nanga malawi defence force muli kuti? Adzakhala ali makolo anu kapena akadzi anu, mudzamva bwanji😢😢😢😢

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Kuno ndi ku Lilongwe panyo Mwayiwala ku Zomba

  • @edenngoma8214

    @edenngoma8214

    4 ай бұрын

    Zachamba izi , ayiwala momwe amazuzira anthu nthawi yomwe alimboma , amenyana okhaokha amenewo adanamizire MCP

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe39584 ай бұрын

    Ndizi mene munafuna kubweresa MCP Lero mulimbe nazo koma kumeneko musama temane ayi, koma A polisi akungo yang'ana pamodzi Ndi asirikari m'mawa tu zimenezo ndi Ngozi inuso mukamapita muzi Tenga zikwanje akakupezani muzigwira m'modzi mpakana azau lure Amene wamutuma

  • @user-yo5ff3uh6p
    @user-yo5ff3uh6p4 ай бұрын

    Ana asukulu musalowerele ndale ,ndale nkanyama koipa ,nkasa song

  • @user-re1jh6ko8x
    @user-re1jh6ko8x4 ай бұрын

    Eeeeee zosayenda amatha bwanji kupweteka mnzawo pomwe anthu tikuvutika

  • @user-nk4hd8hl6i
    @user-nk4hd8hl6i4 ай бұрын

    DPP woyeeee

  • @sheila5812
    @sheila58124 ай бұрын

    Zonsezi ndi Chilima ,potiuza tivotere kongiresi

  • @DngAisee

    @DngAisee

    4 ай бұрын

    Zoonadi ndichoncho

  • @user-nx9zx6fv4i
    @user-nx9zx6fv4i4 ай бұрын

    This boma instead of bringing development but chaos you will not going to rule again this country tibweza

  • @user-te8hh2hb8o
    @user-te8hh2hb8o4 ай бұрын

    Malawi😢

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy4 ай бұрын

    Ulamulilo wa mcp ndizimene timkafuna amalawi vote aythu yomwe chahta wakwiya mvula ndimenei ikusowa mudziwe yedu mcp

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Anaziyamba olha ku Zomba

  • @user-fg1me1un8p
    @user-fg1me1un8p4 ай бұрын

    A mcp ndikuchenjezeni dziwani kuti tikamati Malawi Siku Lilongwe kokha. Timaona ngati dziko likulamulilidwa ndi a busa koma ichi mchinyama.achoke😢😢😢😢

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1p4 ай бұрын

    Sorry guys

  • @user-pi3ef7zl4s
    @user-pi3ef7zl4s4 ай бұрын

    This aint fair for mw as acountry, where is this animality coming from?, the conclusion though

  • @EvansPhiri-ug4oz
    @EvansPhiri-ug4oz4 ай бұрын

    I think kufunika kuona was MCP munjila ndiye kumumenya bas zisilu Za anthu

  • @BvaruJoker-bg6zl
    @BvaruJoker-bg6zl4 ай бұрын

    He's the friend of Minangagwa if he wants to make onestate party this is coming from his friend munangagwa

  • @hastingsmdindo627
    @hastingsmdindo6274 ай бұрын

    DPP is very calculative.........

  • @anoldkapolo4493
    @anoldkapolo449314 күн бұрын

    Pitani kadzilimani chifukwatu azanu omwe munawachotsa mchipani aja akuthani. Dont blame mcp ,bodza limeneli

  • @ceptermicray
    @ceptermicray4 ай бұрын

    0:43 don't include me in your nonsense 😂

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l16 күн бұрын

    Mwakhawula mufela zaeni😂😂😂😂

  • @CharlesMateya
    @CharlesMateya4 ай бұрын

    Malawi

  • @pcalvinjere5276
    @pcalvinjere52764 ай бұрын

    Agalu a DPP athireni utsi amenewa

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Sitigawa ma Sweet

  • @user-kc2bv5jk4b
    @user-kc2bv5jk4b4 ай бұрын

    Kom zosayenda yooo 😢😢😢

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q15 күн бұрын

    Iiiiiii chakwera watizuza mokwana inu muone uramuriro wachakwera.nimumene anthu afera nivula zaka zosezi kunaribe kufa ni vula.ayi uwu niuramuriro.wasataniki.chakwera.angofuna magazi.ndipo dpp oyeeeee

  • @patricgama4788
    @patricgama47884 ай бұрын

    Kuno ku south Africa sangapange manyi amenewo ayi kuli futi kuno pipose khomo ndi khomo ndiye basop

  • @user-yh3dw6qu7z
    @user-yh3dw6qu7z4 ай бұрын

    Chilima ndiye adalondolera mavutowa

  • @macdonaldmzale4387
    @macdonaldmzale43874 ай бұрын

    Midipiti yanu mzikapangila Ku Thyolo ndi Ku mangochi konko kwinako muphedwa nazo

  • @user-hs2yi3hc9z
    @user-hs2yi3hc9z4 ай бұрын

    akulila chan mu nthawi Yao anapha banja lose LA tambala ndi petrol bom nde angokhapidwa akudandaula chan

  • @momuumro
    @momuumro4 ай бұрын

    Futsegi

  • @GeorgeNdippo
    @GeorgeNdippo4 ай бұрын

    Izi tichepese zoona nkhondo imayambadi chonchi

  • @user-fg6ff9ex1i
    @user-fg6ff9ex1i4 ай бұрын

    Vuto amalawi mumasatira zinthu zimene simuzawina nazo zipani zosenzo ndizakuba zosathandidza

  • @KaipaEmanuel
    @KaipaEmanuelАй бұрын

    Km izizi mmmm sibwinoai .iiii ndio nkhondo

  • @henryhenry6632
    @henryhenry66324 ай бұрын

    Dzitsilu mitumbo yanu nonse a dpp dzibwana dzimedzo mudzipangila kwanu konko ku mpanyila

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Khope yonyasa

  • @user-gh1yc3mu5r
    @user-gh1yc3mu5r4 ай бұрын

    Very bad

  • @user-qs2tx7wt6g
    @user-qs2tx7wt6g4 ай бұрын

    Koma bwezela kuwawa mene anatimenyelaso DPP thawi yawo inja akukuthani mupangeso muone

  • @user-kg5lf6bd1g
    @user-kg5lf6bd1g4 ай бұрын

    Athu amenewa ayi km

  • @user-mb6ck6gw4j
    @user-mb6ck6gw4j4 ай бұрын

    Honestly mcp yalephera kukonza zinthu kwasala ndikubera anthu zosowetsa information ku immigration mcp ikuziwapo kanthu the aim yawo ndiofuna kuti anthu amene ali maiko ena athamangisidwe 2025 azavote then information izatuluka after vote izi mudziwe a Malawi amzanga,sine wandale koma pankhani iyi yachitika ku Lilongwe its part of the war instead to help poor citizens of Malawi,you send people kukaononga galimoto za anzawo what is that, pastor can't ruling the country that is big mistake,GOD watch this see you bye

  • @patricgama4788
    @patricgama47884 ай бұрын

    A dpp mokhozeke mupangeso mukapangeso musatope

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l16 күн бұрын

    Ufela zaeni, ozavutika nfi ama 😂😂nyamundola I ndi mukazi wako

  • @user-ce6hy6tp7e
    @user-ce6hy6tp7e4 ай бұрын

    Naye ndi president lero chifukwa amapanga kampen yomweyo lero iyeyo akukanisa anzake kupanga kampen komaso akukanisa mademo chifukwa Chan galu wamunthu chimfiti wasatanic uja

  • @patricgama4788
    @patricgama47884 ай бұрын

    SIMATHA AYI KOMA SIMUNAKOZEKE NDIYE NDIZDOVUTA MADALA

  • @user-qs2tx7wt6g
    @user-qs2tx7wt6g4 ай бұрын

    Malangalanga yapeza zochitaa

  • @patricgama4788
    @patricgama47884 ай бұрын

    Komatu zimenezi sikulina adzakumana ndi futi chikwanje nifuti sizinga fane adzvulala

  • @marryphili5419
    @marryphili54194 ай бұрын

    Chakwera shame on you Kodi wunali mu busa wotani Koma wuziwe mulungu si munthu akuwona zosezi atimenyera nkhondo amalawi 😭😭

  • @sharifmbali7240

    @sharifmbali7240

    4 ай бұрын

    kunalibe chakwera ukuinu

  • @user-fs5gr8iv5s
    @user-fs5gr8iv5s4 ай бұрын

    MCP waziputa uzitsirize tibwexa

  • @user-et2ho2wp9k
    @user-et2ho2wp9k4 ай бұрын

    Akuchitabwino

  • @petersoko4283

    @petersoko4283

    4 ай бұрын

    Ukuyala manyi😂😂

  • @bayanimponda8746
    @bayanimponda87464 ай бұрын

    Defamation

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Inuyotu Alomwe ,kuziyamba dala

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Mwayiwala thawi yanu, Shipiti koza Chipani chanu Agalu Inu munya muona

  • @user-fs5gr8iv5s
    @user-fs5gr8iv5s4 ай бұрын

    Tisaope Malawi ndiwatonse Dpp ikuptira kuda phiri kasungu DDP WOYE KODI CHAKWERA ADZAPITA KUMWERA MUGWIRE MAU ANGA

  • @dysonmsamba5778
    @dysonmsamba57784 ай бұрын

    KU MALAWI KULIBE CHIKONDI UDF INKAPANGA ZOMWEZI KUPHA ANTHU NTHAWI YAO, DPP NAYONSO POSACHEDWAPA IMAPHASO ANTHU , NAYONSO MCP IKUYAMBASO ZOMWEZI,VUTO NDI SANJE KU MALAWI ANTHU SAMAKONDWERA KUONA WINA AKUSANGALALA,

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga4 ай бұрын

    Inu mukudzayamba dala mku Lilongwe bwanji osakayambila kwalomwe anzanu komweko

  • @user-qs2tx7wt6g
    @user-qs2tx7wt6g4 ай бұрын

    Mpaka ugula Ina eeeee ilimpogwila etiiii tichixulaso imeneyo

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland92414 ай бұрын

    Mmm nkhopeyotu ikuwonetsa kutupa muridi ready kufa etiii..komatu muzikonzekeranso za umfumu wa kumwamba..chifukwa mukuwonetsa kuti mankhwala simukumwa..pliz mukufunika kumamwa mankhwala kuti mudyelere chipani chanuchi chikawina 2025 ...anga ndi malangizo chabe..

  • @lifayohbenson1994
    @lifayohbenson19944 ай бұрын

    Osawajambula anthu oyipawo bwanji zigawengazo anthu azione.

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Innoyotu ndi Central

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l16 күн бұрын

    Akukhawulisani DPP...... Akanakhapa pamodzi ndi😂😂 madala wanu... Mcp UTM Moto

  • @user-nj5vu8cd5l

    @user-nj5vu8cd5l

    16 күн бұрын

    Ndiakuba muzichenjela pa tauni

  • @AlickChima
    @AlickChima4 ай бұрын

    Koma mpaka kutsegula car breaking pomweposo shaaaa anthu anafasa eeeeeeh., koma yu see mtima umeneu omati tikalowa m'boma kumawapanga nkhaza anzathu ukanachepako chonde a Malawi amzanga, padzana paja DPP ndiyo inali patsogolo ndi nchitibwe wochifwamba oterewu kumawakhapa ma activist kuwagenda miyala kuwaswera galimoto zawo apolisi alipompo koma osapamgapo kanthu . Makolo dating nkhonya yobwezera kuwawa lero ndinu mawa ndi ife. Kodi tikifunapadzafe kaye mzungu kuti mw8na mkup3za polekera

  • @happykadammanja-rz5bc
    @happykadammanja-rz5bc4 ай бұрын

    Kom ndye kunapita ma car breakers2 kkkkkkkkk

  • @mafukenimasangwi5487
    @mafukenimasangwi54874 ай бұрын

    Ndala zimene mwapasidwazo zokwana thumba lachimanga zaiii andalewa siyanthu

  • @walesbanda4959
    @walesbanda49594 ай бұрын

    Kkkkkkk akulu awa kuwaimba mulandu nkulakwa. Anamwa mowa wambiri. Umayankhulawo ndi mowawo

  • @EdwinMabviko
    @EdwinMabviko4 ай бұрын

    Simuli m'boma ndiye Inu mukupanga chani?

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Panyapanu ,tilinanu

  • @DCpangolin
    @DCpangolin4 ай бұрын

    Mmmmmm km MCP ikufuna nkhondo sopano

  • @George-ux7vq
    @George-ux7vq4 ай бұрын

    😂😂😂 anthu opusa inu

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r4 ай бұрын

    Abambo inu zikanakhala zamlulungu beta kuchikamwa kakau mzafela zaziko

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Central mwayidziwa

  • @Fatima-li5rg
    @Fatima-li5rg4 ай бұрын

    Wavuta Malawi Kodi mulephela kumuthirila poison muchakudya

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Munatha jauju

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Alomwe Zitsilu Inu munya muona

  • @VincentAndrew-jz2gf
    @VincentAndrew-jz2gf4 ай бұрын

    Dpp inatha Izo mudziwe

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e4 ай бұрын

    Cakwera akufuna magazi amalawi titha ndithu afuna magazi akapereke kumidima cakwera chakwera cakwera sindife ana ako komanso udzikamwa magazi aana ako muthu oipa mtima ngati iwe sitinamuone chiyambireni mmalawi komaso ukangowina udziwe kuti khondo idzayamba wamva satana

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r4 ай бұрын

    Nkhalamba yili phee kunyumba kwake inu mwa banja lanu inuyo mkafa agogo anuwo azasamalia ana anu koma ndale ndiuchilu mkafa banja lanu lizavutika ndinu zisilu

  • @FunnyBasketball-er3vc
    @FunnyBasketball-er3vc4 ай бұрын

    Very bad

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td4 ай бұрын

    Mumaziyamba alomwe pitirizani mwano muona nyenkhewe pitala agura Ina anzanu akukuphani kumangolira muziponyaso Nanu ugaru changamu patawuni

  • @hendiemailosi7824

    @hendiemailosi7824

    4 ай бұрын

    Mapwala ngati alomwe iwe ndi opusa eti

  • @AckimKachiluwe

    @AckimKachiluwe

    4 ай бұрын

    You guys mufera dziko asiyeni andale azipanga zao khala ngat kumalawi ndinu achilendo bwnji zooona mukuonongesa katundu wanu choncho za ziiiiii aaaaaaaaaaaaa mbava zapezelapo mwai apo

Келесі