MCP Change How You Treat SKC - Rwara

On Nyasa VoiceBox, a self declared card carrying member is appealing to members of the Malawi Congress Party (MCP) to show some respect to the Vice President Dr Saulos Klaus Chilima.
Ku Nyasa VoiceBox, chikalata chodzitcha kuti ndi membala wa chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chikupempha kuti apereke ulemu kwa wachiwiri kwa Purezidenti Dr Saulos Klaus Chilima.
#malawi

Пікірлер: 158

  • @langsfieldmwahimba8334
    @langsfieldmwahimba83344 ай бұрын

    You are very right brother. Chilima akuzunzika but he remains humble to to the president. God should see him through. If he was given a chance to implement the reforms, this Government would have been the best ever. Chilima, continue being humble.

  • @robertmwinjilo5331
    @robertmwinjilo53314 ай бұрын

    I never thought I would hear a reasonable, fair voice.

  • @user-iq5xk6ju7y
    @user-iq5xk6ju7y4 ай бұрын

    Tifune tisafune Chilima will remain the genius whether him ruling Malawi or not. It's only Chilima who can change Malawi even the MCP gurus knows. He is a big threat to MCP not APM as it is put on the ground

  • @PhilomenaChikabadwa-dt6vy

    @PhilomenaChikabadwa-dt6vy

    4 ай бұрын

    God save Malawi.

  • @shadreckphiri1799
    @shadreckphiri17994 ай бұрын

    Mr Rwara is a reasonable Malawian who is fair and just. Chilima has been mistreated by mcp

  • @StevenTembo-mb7rm
    @StevenTembo-mb7rm4 ай бұрын

    Malawi lacks citizens who understand issues like the way you do. Big up i like the way you have voiced it out

  • @LearnsMussa

    @LearnsMussa

    4 ай бұрын

    . P

  • @PhilomenaChikabadwa-dt6vy
    @PhilomenaChikabadwa-dt6vy4 ай бұрын

    I am happy with your advice mr Rwara.

  • @danieltisekenawo6723
    @danieltisekenawo67234 ай бұрын

    Well said. Paja chilungamo ndi mwano eti pa Malawi 😂😂❤❤

  • @user-nj4ob8jw6y
    @user-nj4ob8jw6y4 ай бұрын

    A'm a staunch supporter of MCP, but plz make sure, we must give SKC the presidency. He deserves it, whether one like it or not. Anzathu a kumpoto chonde nthawi zonse mumayambitsa zinthu zoti patsogolo timabvutika nazo. Musayiwale kuti ndinu amene munapanga kuti Kamuzu Banda akhale life president, so plz people from the North, stop being stupid by endorsing useless things.

  • @johnsimko2941

    @johnsimko2941

    4 ай бұрын

    North people are not stupid my friend, never been before. Remember they voted for chilima than any other region.

  • @StevenTembo-mb7rm

    @StevenTembo-mb7rm

    4 ай бұрын

    That's true we as the northerners we don't favour useless and stupid politicians. Timavotera munthu wanzeru posatengera chigawo chomwe munthuyo akuchokera bola akhale mMalawi

  • @user-wy2tx2cj6v
    @user-wy2tx2cj6v4 ай бұрын

    Eeeya you are saying the truth. MCP ikukathera ku Convention.

  • @user-ks3uw8gj8h
    @user-ks3uw8gj8h3 ай бұрын

    Well said, from a well Matured person

  • @user-re8fh1yh5z
    @user-re8fh1yh5z4 ай бұрын

    Njoka yofatsa imalumira kumchila chilima is brilliant guy muzamulira atatulusa joka pamapeto pokuti Inu zose mwaika pa ground chifukwa Cha kulubwalubwa

  • @SAIKINGFRIDAY
    @SAIKINGFRIDAY4 ай бұрын

    Chilima ndi pangolini or ku mcp ko imadziwabwino za chilima

  • @SamsonSenzoNyika-tx1sd
    @SamsonSenzoNyika-tx1sd4 ай бұрын

    congrats to Mr vice President for the patience and owning to mcp members For they Bad actions Show to UTM president......

  • @zondwasekhonje3235
    @zondwasekhonje32354 ай бұрын

    You have spoken very well

  • @user-nj4ob8jw6y
    @user-nj4ob8jw6y4 ай бұрын

    A'm from Dedza, the home of MCP, no one can question about that, my uncle managed to keep this party called MCP, even when stupid Bakili Muluzi tried to destroy it, its not negotiable, let us give it to Saulos Chilima. aChewa, chonde tisapange nsanje, munthu uyu adapanga kuti MCP idzuke kwa kufa, chonde pasapezeke m'chewa omunyoza Chilima, ndapota nanu. Musayiwale kuti Muluzi adalimbilira kuti mpaka adzalowe m'manda, adzawonetsetsa kuti MCP isadzalowenso m'boma.

  • @mosesnyirenda5010
    @mosesnyirenda50104 ай бұрын

    Chilima will be president 2025

  • @sweeneykamwendo6251

    @sweeneykamwendo6251

    4 ай бұрын

    Mcp will not allow Chilima to be a torchbearer in 2025 believe me or not

  • @AmusedDimSum-hd5yp

    @AmusedDimSum-hd5yp

    4 ай бұрын

    which country

  • @richardbanda9997
    @richardbanda99974 ай бұрын

    Osamva asamve munthu wayankhula zothandiza chipani uyu, koma poti timasankha kutseka makutu, tiziona.

  • @user-gd2kl1fx1q
    @user-gd2kl1fx1q4 ай бұрын

    Mcp yatha iyi chilima simunthu oti angamutaye chonchi n kumunyoza honestly 2025 I see him winning his good reasoning n humbleness will bring joy to malawians

  • @andrewkalawazawo7600
    @andrewkalawazawo76004 ай бұрын

    ALwara akunena zoona kupanda chilima anthu sakanavotera mcp

  • @JohnMjojo-if1sw
    @JohnMjojo-if1sw4 ай бұрын

    Respect the Vice president as per your advice. MCP if you loose Chilima you will fall by the nose.

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito11094 ай бұрын

    Thats true voice, mcp must not put bhind chilima he is your position fighter.

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg4 ай бұрын

    Koma choti muziwe chilima mukamuswaya mcp sangawine

  • @phillipdorrex3826
    @phillipdorrex38264 ай бұрын

    Mr Lwara zimene mukulakhula ndi zoona BOMA lilipoli ndi la zipani zingapo zimene zinapangisa kuti Chakwera nd a Chilima tiwavotere koma vuto la MCP akadalibe ndi moyo wa one party system akanakhala Ena a MCP bwenzi pano akuwona zili pa Ground Chilima ma corner wose akukondedwa ndi anthu ndipo ngati akususana ndi mugwirizano ndiye kuti sanawina chifukwa sakulemekeza mu gwirizano umene ulipo and a Chakwera asataya chikhirisitu chawo chifukwa cha anthu amene akufuma kugwesa dziko la Malawi chifukwa chosafunira Malawi za bwino go ku Tanzania zinthu zikuvuta koma dziko zitukuko zikuwoneka koma ku Malawi ma family amene akusangalala ndiwokhawo ali close to president izi ndi zapa dziko la pansi tizisiya musamupange chipongwe lero Chilima otherwise muthera mu njira a MCP

  • @frazerfrazer8902
    @frazerfrazer89024 ай бұрын

    Pangano linadulisa mutu wa yohane , MCP must know where the coming from ,Chilima must be respected he put the in power and He can take it back.

  • @henrykapinga1433
    @henrykapinga14334 ай бұрын

    Very good speech

  • @NathanielNthala
    @NathanielNthala3 ай бұрын

    Mr Rwara is saying the truth.

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano4734 ай бұрын

    The words without aparch mau Mau auzeni chilungamo MR AChirwa

  • @Michael-yf1tq
    @Michael-yf1tq4 ай бұрын

    Zoona brother

  • @blacksontrisshavieli6976
    @blacksontrisshavieli69763 ай бұрын

    Chikondi ndi chabwino MCP isayiwale komwe achoka Chilima akuyenela Kulamulila basi

  • @user-om2nj5ul4h
    @user-om2nj5ul4h4 ай бұрын

    Exactly coz every knows that without Chilima mcp could fall down according to our vote percentage btwn tonse alliance and dpp

  • @user-hq2io8nk7s
    @user-hq2io8nk7s4 ай бұрын

    A MCP yakula ndi nsanje ndi Dr Saulosi Chilima. Akuyiwala kut a pambane anagwira ntchito ndi Dr Saulosi Chilima. Kusiya kuzitenga bwino ife a Malawi sitingakuloleni ndipo mukuwonga chipanidi.

  • @user-dh5wf3mr1o
    @user-dh5wf3mr1o4 ай бұрын

    Anthu a mcp ngati akunyoza chilima kuwona ngati awoloka sazapitilira 2025 and mcp ikuzaluza ndi kuntha komweko

  • @user-nb2zz9ih1v
    @user-nb2zz9ih1v4 ай бұрын

    Voice of the voice viva

  • @MonicatimanyeShaba
    @MonicatimanyeShaba4 ай бұрын

    Zoona zake MCP saziwa chomwe akuchita aziwona kusogoloko komwe tikurowelaku angolawawo atulukaso AWA chilima NDI solo

  • @user-hd7wq2yc6m
    @user-hd7wq2yc6m4 ай бұрын

    AKezzie Msukwa wakuvimanya yayi ivi wakuchita suzgo la ise kuno ku mpoto tikugwiritsidwa waka ntchito pala vyakukhumba vyawo vyafiskika mbwenu tikutayika waka ngati chiseru chakumala tikusambirapo kanthu yayi

  • @kennedybanda
    @kennedybanda4 ай бұрын

    Yes paja munthu akakhala kuti ndiwozindikira amadana naye.

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa21934 ай бұрын

    Chilima ndi president wamasomphenya Koma zimene akuchita a MCP ndi zoyipa economic yagwa mumene chakwela alipampando

  • @PhilomenaChikabadwa-dt6vy
    @PhilomenaChikabadwa-dt6vy4 ай бұрын

    Amalawi tiyeni tiphunzire kulankhula mwaulemu,maka inu anzathu andale.Tikapita pamsonkhano ,timafuna kumamva zothandiza,anthu pamabvuto omwe tikukumana nawo,Osati mau onyozana.Ana athuwa tikuwapatsa chitsanzo chotani.Apresident analankhulapo kuti pali anthu omwe akufuna kumaso koneza pakati pa iwo nda Vice president,chonde ngati mulipodi,Mulungu akupatseni mtima wabwino wachikondi.A vice president ndi munthudi wopirira.Pitilizani khalidwe lanu la ulemu kwa president,Mulungu amadziwa zonse.

  • @johnw.posomanchanel4023
    @johnw.posomanchanel40234 ай бұрын

    No one needs chakwera

  • @user-rr5xh3wn9q
    @user-rr5xh3wn9q4 ай бұрын

    Mukunena zoona Mr Rwara asiyeni a MCP akudzikumbila manda

  • @richardbanda9997
    @richardbanda99974 ай бұрын

    Osataya kabudula wakale chifukwa mwagula wanyuwani, tsiku lina mudzafuna kuumba njerwa. Tread carefully.

  • @usherkays4379
    @usherkays43794 ай бұрын

    Cape town streaming you live

  • @khumbochinemba
    @khumbochinemba3 ай бұрын

    Enough is enough mcp God will rescue Chilima one day. But know kuti mwathera pompo

  • @kasambalastuart185
    @kasambalastuart1854 ай бұрын

    There is need for power sharing deal not coalition in Malawi.

  • @user-sz3xk3mw5v
    @user-sz3xk3mw5v4 ай бұрын

    Chakwera will regret ,,, taking chilima for granted

  • @SwswWilson-cl7de
    @SwswWilson-cl7de4 ай бұрын

    ❤❤❤❤ ya ndizoona

  • @JohnMjojo-if1sw
    @JohnMjojo-if1sw4 ай бұрын

    Mega farms, civil servants salariies, reform in civil service and soldiers new houses it's UTM / Chilima manifesto.😊😊

  • @isaacchagwa2917
    @isaacchagwa29174 ай бұрын

    How do you attack north in this.That is not building our beloved mother land.We are one people,nomatter what

  • @user-cm7zw6pk6d
    @user-cm7zw6pk6d4 ай бұрын

    Chilungamo chokhachokha . MCP yakwera pamsana pa njobvu yaiwala kuti kunjaku kuli mame .

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d4 ай бұрын

    Ife amalawi ndi opusa kwambiri tikumayiwala bwanji za MCP

  • @user-lr2df7hy2q
    @user-lr2df7hy2q4 ай бұрын

    Mukuyankhula zowona zokha zokha chilima sakulemekezedwa

  • @chisomoMsiska-cr8cz
    @chisomoMsiska-cr8cz4 ай бұрын

    Mau mau. Chikondi chitsogole pakat pa azitsogoleri anthu.....

  • @jahmiel3169
    @jahmiel31693 ай бұрын

    Mwawuze asankhe chilima a mcp president

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j4 ай бұрын

    Achilima ndi munthu okhwima maganizo paja amati kufasa kumaonesa maso ankhono

  • @NathanielNthala
    @NathanielNthala3 ай бұрын

    Of course Mr Rwara is saying the truth. Dr Saulos Klause Chilima did a great job during 2020 campaign.

  • @Donnex-gn2sf
    @Donnex-gn2sf3 ай бұрын

    No more Alliance this time chilima must go alone ku election we MCP we're not afraid anything this time around

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v4 ай бұрын

    That is true what you saying bro

  • @NathanielNthala
    @NathanielNthala3 ай бұрын

    Mr Lwara is right.

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l2 ай бұрын

    MCP members plus mr Lazarus don't forget about chilima nfi yimodzi anakuwolotsani bwato

  • @gracechiumia7103
    @gracechiumia71034 ай бұрын

    Mcp izaonazosaona muchaka. Chaka cha2025 ikuzagwa

  • @AusmanBenthu
    @AusmanBenthu4 ай бұрын

    Awo akulu akulu a chipani cha MCP asazathamangileso ku chipani china

  • @Catherinembowe
    @Catherinembowe3 ай бұрын

    Truth prevails

  • @moyo77777
    @moyo777774 ай бұрын

    Ndizona chipanda chiliima sakanalowa palibe amafuna Mcp

  • @noelkalewa1745
    @noelkalewa17454 ай бұрын

    Iweyo ndiwe wq chipani chanji chirwa??

  • @asharvinkabondo
    @asharvinkabondo4 ай бұрын

    Mcp as political party has right to have convention disregarding that it is in partnership with other parties hence being party has its constitution , on what you have highlighted concerning what Kezzie Msukwa stated on interview that no one will contest against Chakwera that's obviously, if you may recall that was the similar Scenario with DPP party the time they are in government . Mr Chirwa you are true citizen of Malawi and really you are indeed a member of MCP . I love Dr Chilima very much and 2025 surely he will be our president, Chilima and Chakwera are not fools they know what to do come 2025 , Chakwera being MCP party president will endorse Chilima at last minute believe me those guys are playing underground games

  • @user-fs1ox7ou1b
    @user-fs1ox7ou1b3 ай бұрын

    Ndipo iyeyo muti chakwera sangawine

  • @frankiejackzy9862
    @frankiejackzy98623 ай бұрын

    Big Up

  • @user-cd6db5qb4l
    @user-cd6db5qb4l4 ай бұрын

    Koditu akulu akulu achipani cha mcp ndianthu osazidikila

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp4 ай бұрын

    Abambo inuyo mukanakhala nduna mwina Bwez mukumuuza kapena mukumuzuzula pano mbola Koma ndimulungu kufuna kutizwitsa Ife amalawi Kuti lazalo timudzwe

  • @alicemalika677
    @alicemalika6773 ай бұрын

    In the Bible there is a prodigal son who asked his father to given him his share and went away after using what he was given he went to ask for a job looking after nkhumba and eat together with nkhumba but after thinking wisely he decided to go back to the father and tell the father that I am not wealthy before you but the father prepared a feast for him . Why not Chilima go back to the father and say here I am😂😂

  • @Donnex-gn2sf
    @Donnex-gn2sf3 ай бұрын

    Ukunama yiwe pa ground pake party ngati anthu akumufuna chilima bwanji wosawinako mpando ku kalonga cadet wachabechabe

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk4 ай бұрын

    Very true munthu wankulu

  • @HarryTambala
    @HarryTambala4 ай бұрын

    Jealous Too Much Anthuwa !!! Chilima Arindi Moral Palipose

  • @MpasulavisaSonjo
    @MpasulavisaSonjo3 ай бұрын

    I guess the decision towards political alliance was genuine but lacked credibility. Remember whatever was agreed between the two does not rule out constitutions of the two parties. Unless otherwise there is an inclusion of such a clause in the constitutions validating powers of parties constitutions

  • @IsaacSinkileya
    @IsaacSinkileya4 ай бұрын

    Achakwera adaiwala koma ili ndi dziko

  • @user-oh4yd4dj5p
    @user-oh4yd4dj5p4 ай бұрын

    Sure mcp change mis treating SCK

  • @BeatriceMANDEVUGONDWE-iv4gr
    @BeatriceMANDEVUGONDWE-iv4grАй бұрын

    Akumkhomelera chilima a mcp akudziwa kuti chilima amawaposa dzeru agaluwo

  • @user-fs1ox7ou1b
    @user-fs1ox7ou1b3 ай бұрын

    Izo mukulankhurazo zili choncho MCP sitikuyifunanso boma lakupha

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu4 ай бұрын

    Mkuulu uyu amalankhula zoona zokhazokha

  • @LasimaChatsika
    @LasimaChatsika3 ай бұрын

    Ukunama,owe si wa Mcp,usatinamize apa mmmmmmm

  • @user-mk7np1zt4i
    @user-mk7np1zt4i4 ай бұрын

    Pangolin skc

  • @user-ry6nv8yl9w
    @user-ry6nv8yl9w4 ай бұрын

    There's no one who can speak for chilima

  • @LasimaChatsika
    @LasimaChatsika3 ай бұрын

    Chilima ndi vice president Basi,whether you like or not, Mcp 2030 wooooo,tisapusitsane apa

  • @user-lj3dx7wz9t
    @user-lj3dx7wz9t4 ай бұрын

    Umakwana zoona zenizeni

  • @jahmiel3169
    @jahmiel31693 ай бұрын

    Kuti zinthu zawo zayendele bwinu kupanda apo awona zokhomà achekwela

  • @AusmanBenthu
    @AusmanBenthu4 ай бұрын

    What we're waiting is the agreement that they did at the first time Olemekezeka aChakwera nthawi yao ikutha pompano aziwilethu

  • @CliftonGondwe
    @CliftonGondwe3 ай бұрын

    Zoona zokhazikha.

  • @user-so2ny8jh2w
    @user-so2ny8jh2w4 ай бұрын

    True

  • @user-tt4jb6nr3w
    @user-tt4jb6nr3w3 ай бұрын

    Facts

  • @victormpila4000
    @victormpila40003 ай бұрын

    SKC 2025 boma.MCP take care behave like you have all your sense.

  • @user-gh9ww5xp7p
    @user-gh9ww5xp7p4 ай бұрын

    😢

  • @user-lj3jb6hf9f
    @user-lj3jb6hf9f4 ай бұрын

    He knows that what he feels in himself is more great that what MCP is doing.hyna is a hyna.

  • @kennedybanda
    @kennedybanda4 ай бұрын

    2025 kuli kanthu.

  • @user-wl3nb1mq9t
    @user-wl3nb1mq9t4 ай бұрын

    Mawu mawu mawu

  • @MalumeDubeSaid
    @MalumeDubeSaid3 ай бұрын

    Zoona chilima akunyozedwa

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r4 ай бұрын

    Chilima boma 2025

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu4 ай бұрын

    Zinduna ziwili izi zikuiwala kuti analowa bwanji m'boma

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l2 ай бұрын

    Bwato lija simunakwere nokha kuti muwoloke njanja ya Malawi

  • @HafizahHarack-bn3bf
    @HafizahHarack-bn3bf4 ай бұрын

    A kudziwa chimene a kupanga a Malawi wosagona imeneyo ndi ndale

  • @user-gx5ht9gm3z
    @user-gx5ht9gm3z4 ай бұрын

    NO PAIN NO GAIN NGAN YAVEKA BWIN BWIN BIG

Келесі