LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA USIKU wathawu

Ойын-сауық

Пікірлер: 83

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika678413 күн бұрын

    Mr Chikangawa Chakwera Bp yakwera kale kuti muulura chani 😅😅😅😂😂😂😂yomweyo galu iwe

  • @MikeKanyaza-bm5tp
    @MikeKanyaza-bm5tp13 күн бұрын

    Osamasowa antanyiwa please 😊

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana13 күн бұрын

    Koma ndaseka ngati zabwino 😂😂😂 athu onsewo akaphedwa nde iwo adzawina zisakho Kom hahahaaaaa chakwera akunama kwambiri kumwamba kukanena kuti kwatha ndi kwatha basi paribeso zoti apha muthu wina a ntanyiwa dzikoli silachakwera ndalama sizingamupindulire komaso paribe zoti anga gure chipani paribe yemwe afuna achoke komaso akaliyati sangalore mudzina layesu ndikuti patibe zoti muthu anga gure chipani awo akalandira ndalama ndizawo za kunyumba kwao and olo apatse ndalama kakiyati olo adzalandira koma chilungamo chisitha chimakhalabe chilungamo ndinaonera esau ndi abere choipa chitsata mwini MLUNGU WATHU SALEPHERA

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm13 күн бұрын

    I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you all the time.

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj13 күн бұрын

    ose amene ankufunna kuphedwa mulungu salolla mashall Allah bless you always

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw13 күн бұрын

    Sitiopa wokupha thupi koma timaopa mulungu amene amapha thupi ndi mzimu. Ondikumbila dzenje agwelamo yekha. Mulungu wa Daniel, shadreck, mishel and abdenego will protect onse amene mayina awo Ali pa list.

  • @VaseleMsiska
    @VaseleMsiska13 күн бұрын

    Koma kukhala anthu Ku Malawi. Koma chakwelà azatha ngati ma curtain.

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb13 күн бұрын

    We are here already comrade ✌️

  • @MaxwellumbiriLumbiri

    @MaxwellumbiriLumbiri

    13 күн бұрын

    Zakwanitsa tate akuona zonse

  • @MaxwellumbiriLumbiri

    @MaxwellumbiriLumbiri

    13 күн бұрын

    Yehova akuona chilichonse afa yekha

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika678413 күн бұрын

    Good morning, welcome back tinakusowani tinayamba kudandaura

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl13 күн бұрын

    Ndikamava kanyimboko ndiye ndimasangarara ndimazdziwa kuti chirungamo chirimunjira

  • @user-ul1fb4yn5o
    @user-ul1fb4yn5o12 күн бұрын

    I salute Comrade ntanyiwa,, ndiye titani Comrade amalawi tiyen titengen gawo tipemphere kwambiri

  • @amoschataika7440
    @amoschataika744013 күн бұрын

    The best Radio station in the world. Big up Comrade

  • @user-pl2lj6mh1z
    @user-pl2lj6mh1z13 күн бұрын

    Koma dziko lathu tinalozedwa bas zoona kumuopa chakwela kamuthu kamodzi tiyen tipange ngat ku Kenya please zausilu zikuchitikazi

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli9 күн бұрын

    Loud n clear from Johannesburg

  • @user-ht7vs3dp2u
    @user-ht7vs3dp2u13 күн бұрын

    Pemphelo rathu ndichida chomwe timangonjesera adani zenje akuwakumbira athu onseo agweramo onse akupereka mayina awathu osarakwa imfa akunenayo atamwalire ndiwo 2025 isanafike mulungu akuona

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg13 күн бұрын

    Ntanyiwa wadzuka bwanji kumeneko ifetu tilibwino ndithu tiye nazoni

  • @DaitonKabila
    @DaitonKabila13 күн бұрын

    Comrade am 100% support u always ing'alure fadah

  • @modestamhango7737
    @modestamhango773713 күн бұрын

    Angozinamiza anthu onsewa Mulungu sangalore kuti aphedwe.

  • @simonpaul6567
    @simonpaul656713 күн бұрын

    I ❤ this program

  • @SydneySibande-z6k
    @SydneySibande-z6k13 күн бұрын

    Long liveNtanyiwa

  • @user-ul1fb4yn5o
    @user-ul1fb4yn5o12 күн бұрын

    Muzina la yesu christu achakwera kungopha modzi muziona ndithuuu😭😭😭😭

  • @AnusaNkhoma
    @AnusaNkhoma13 күн бұрын

    Waying'alura kuno mtanyiwa

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg13 күн бұрын

    Oh Lord have mercy on us Malawians Tipulumutseni ambuyeeeee ............Mbuzi ikakondwa kwambiriiii amalonda alipafupi la 40 likudzaaaaaaaa list mwayikayo ikhala yanuuuuu anthu akupha amagazi m'manja inu

  • @MustafaAbdullah-pb5zv
    @MustafaAbdullah-pb5zv13 күн бұрын

    Amalawi kumudziko tadzukani mumchotse chakwelayo......dziko silake

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon342913 күн бұрын

    Atchela kumawa nkhangazaona anyanayo

  • @AbdullahBnp-l8m
    @AbdullahBnp-l8m13 күн бұрын

    long live Mtanyiwa here in capetown i support you❤

  • @JamesDaud-jz7uq
    @JamesDaud-jz7uq13 күн бұрын

    You are our head lamp Mr Mntanyinya tipempha mayiko ena atithandize kuchotsa president okuphayu

  • @louismagongwa
    @louismagongwa12 күн бұрын

    😂😂😂😂😂 nde mcp itsala yokhatu nanga anthu osewo akawapha ku opposition kudzakhala ndan mcp muzitenge bwino zithuzi vuto mwakhalitsa padzuwa muli kotsutsa😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @PetroMatias
    @PetroMatias13 күн бұрын

    Antanyiwa nlipo abale osamasowa chonchi

  • @sulleahmnyimbili1362
    @sulleahmnyimbili136213 күн бұрын

    Lord have Mercy

  • @CharlesmakveliNyirenda
    @CharlesmakveliNyirenda13 күн бұрын

    Iwe chakwela Mano kuyipa ngati nyemba ya pa nyini ya Monica wako uyo usatibowe ife

  • @LouisKanje
    @LouisKanje13 күн бұрын

    Okhesa mwazi yehova sakondwera naye olo nyama ikatero Mulungu amapereka Chicano paizo

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj13 күн бұрын

    Mtanyiwwa ulemu wanuw mulungu adalise wina aliyese astaguffllal yha Allah thallah brother

  • @user-iv4dj1pi3b
    @user-iv4dj1pi3b13 күн бұрын

    Comrade ntanyiwa ..great man ft kalindooooo

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja13 күн бұрын

    Achakwera ku state house atawako posachedwapa

  • @user-zr7wk4oq2x
    @user-zr7wk4oq2x13 күн бұрын

    We're always with you buddy Ntanyiwa.♥️🔥🔥

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda13 күн бұрын

    We love you comrade ..tell us more

  • @MerryWayson
    @MerryWayson13 күн бұрын

    Timakunyadilani Mr Mtanyiwa koma za anthu ogwidwa pa Bedbrig Ili pat naosotu akanapita Maliro kwao kumalawi iya

  • @user-wl4nd7ic1s
    @user-wl4nd7ic1s13 күн бұрын

    GOD bress u Mr mtanyiwahhh!!

  • @user-hg5oj3ko1o
    @user-hg5oj3ko1o13 күн бұрын

    Iiiii ndiye atipha tonsetu

  • @originalblack100
    @originalblack10012 күн бұрын

    aziwombere yekha lazalo wa ku kasiya ndi a zinzake onse, kuyambila zikhale, chimwendo kukunyu ndi agututu a thakati onse a congress. BRR brrrrr pha pha pha, comarde mumakwana boss.🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @kondwaniwhite2871
    @kondwaniwhite287113 күн бұрын

    Nice 👍 nndinakusowani

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl13 күн бұрын

    Amtanyiwa bwanji Kodi odio sikumveka bwinotu

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma10 күн бұрын

    Koma mulipo a Ntanyiwa, mulibwanji kumeneko

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi889713 күн бұрын

    My gracious heavenly Father have mercy on Malawians

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali13 күн бұрын

    Ndipo galu ameneyo siomuchula kuti mr iyayi chakwera akufuna amalawi atani 😂😂😂

  • @mathewsmdzanja3276
    @mathewsmdzanja327613 күн бұрын

    I salute you comrade!

  • @leonardjika2100
    @leonardjika210013 күн бұрын

    WHEN YOU ARE PLAYING THE MUSIC OR OTHER VOICES WE CAN NOT HEAR CLEAR PLS TELL YOUR TEACHINIAN

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember13 күн бұрын

    Mukamachedwa kupanga post timakhala ndi nkhawa Kut chachitika chan

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji160813 күн бұрын

    Muwamve Mai kaliyati mmene anayankhulira kumaliro a LUCIUS BANDA kumuyamikira president kut ankamuthandiza Lucius,pomwe Lucius wavutika kwambiri mmoyowu.i will never trust politicians.kulira konsekuja,lero akufuna alemerere pa imfa ya chilima.Amai awawa apapa ndiye azionongera mbiri .Akufuna awanamize aMalawi.

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus13 күн бұрын

    Am just a Malawian but my president is Traore..on my DP😅😅😅

  • @AminahMussah
    @AminahMussah13 күн бұрын

    anthu onsewo awakwanitsa koma Mulungu wake waliyenseyu aaaa

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk13 күн бұрын

    Mmmmmmm ayi zagawana ku mitunduzo ayi....usatinamize ingonena zoooyenera kunenazo....timakutsat Ra mwachidwi...km zotigawanisazo sitilora...tonse nda Malawi ndipo palibe adzatigawanisa

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d13 күн бұрын

    Mr Chakwera pamtumbo panu ndinthu

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy13 күн бұрын

    Nsembe yomwe inapelekedwa zaka zapitazo ya ufulu chakwera waipangisa expire akufuna mwazi wina otchuluka

  • @kamwazabonomali825
    @kamwazabonomali82513 күн бұрын

    Komatu kulimbana ndi aNtanyiwa kuzipusisa ndithu. Awa ndi akatundu omangidwa ndizitsulo. Mbambande.

  • @user-ny3it3jp9l
    @user-ny3it3jp9l12 күн бұрын

    Lipopo ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤ ❤❤❤❤

  • @user-yu4np2wq4s
    @user-yu4np2wq4s13 күн бұрын

    Zosatheka athu APHA Aja sanakwane BaiBulo Linati okumba zenje agwelemo yekha ndiiiiiiithu amene watenga gawo lokupha athu amenewa agweramo okhaaaaa ambuye invani simunawalenge athu Kuti azuzike paziko pano inu mukule Ife tichepe

  • @user-ny3it3jp9l
    @user-ny3it3jp9l12 күн бұрын

    Lipopo support ❤ 💙

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk13 күн бұрын

    Apa bet bridge aja awafinye especially waku MALAWI athane naye ndi opusa

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z13 күн бұрын

    Palibe so kuphedwa apa Inu ambuye akukutetezerani a ntanyiwa ndi azinzanu onse timakuikizani mmapephero

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg13 күн бұрын

    💥💥💥💥

  • @user-wo2kh4xe8q
    @user-wo2kh4xe8q13 күн бұрын

    futi yomwe akufuna aphere azawo apita ndi iwoo mulungu simunthu

  • 13 күн бұрын

    Okupha nayeso azafa... palibe kuopa mcp ndi azitsogoreli ikagwere

  • @AminAbbass-xc4qk
    @AminAbbass-xc4qk13 күн бұрын

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @PetroMatias
    @PetroMatias13 күн бұрын

    👍👍👍👍🤝🤝🤝🤝👍

  • @PatrickMtira
    @PatrickMtira13 күн бұрын

    Tinakusowani Boss

  • @VanessaGwangwa
    @VanessaGwangwa13 күн бұрын

    ❤❤

  • @user-hj5oq5jm9v
    @user-hj5oq5jm9v13 күн бұрын

    Ing'alureni fadah

  • @edmorswalley6663
    @edmorswalley666313 күн бұрын

    Mulungu sichejemu auzeni

  • @user-bw2cv9sd7x
    @user-bw2cv9sd7x13 күн бұрын

    a comrade yobu 13;13 yakhulani mosaopa

  • @user-mv8vy3ht3n
    @user-mv8vy3ht3n13 күн бұрын

    God is able

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q13 күн бұрын

    Zosatheka osewo kafu olo atalimbikila bwanji

  • @ChiefJustin-cl8jl
    @ChiefJustin-cl8jl13 күн бұрын

    Nthatha za njaladi

  • @ArnoldBinali
    @ArnoldBinali13 күн бұрын

    Koma chakwela eeee

  • @LouisKanje
    @LouisKanje13 күн бұрын

    Chilango

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember13 күн бұрын

    Koma Chakwera zoti kuli Court la ICC lomwe limathana ndi ma President aku Africa akuziziwa Mr President becareful kunali ma President a mphavu kunjaku koma anaphedwa enaso anali okondedwa ndi anthu awo osati inu

  • @Uncle_B265
    @Uncle_B26513 күн бұрын

    Komatuu tili pa ululu eeeeee

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda871113 күн бұрын

    MCP or chakwela si mulungu agalu amenewa atikwana dzene 2025 kwatalika dzedi asanephe anthu ofunika MOTI PAKANGOFA MUNTHU WINATSO CHILIMA NDI ANTHU 8 AJA AKWANA chifukwa ife amalawi sitimakhulupila kuti MCP yokupha timati yakele yija iyi ya wong"ono ung'onu KOMA PANO ALIYETSE WAWONA YEKHA KUTI MCP YAMAGADZI NDINTHU

  • @mipeacemakermw9501
    @mipeacemakermw950113 күн бұрын

    Wina watukwana chakwera uku 😂😂kzread.info/dash/bejne/iYZ4zbNxo8KZZM4.htmlsi=r_3Qm9tNpQwXfR0D

Келесі