No video

Limpopo APM akuthilidwa poizoni ku mangochi masanawa Ntanyiwa akuulura anthu omwe akukapanga izi

Пікірлер: 81

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xoАй бұрын

    Oh ALLAH tithandizeni malawi tikuvutika mutetezeni peter

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatopeАй бұрын

    Ineyo ndizakhala okondwa ikazangoluza mcp ndimafuna chakwera,,,mwana wake,,, zikhale,,kunkuyu,,mkaka,,,anthu amenewa azagwire life imprisonment osazawapasa bail

  • @lyiemanganjira9708

    @lyiemanganjira9708

    Ай бұрын

    Perfectly said

  • @user-hs4bm2yj8r
    @user-hs4bm2yj8rАй бұрын

    Mulungu kutetezeni akapolo Anu, amene khumbo lawo ndikuombola dziko lathu

  • @FireKajambe
    @FireKajambeАй бұрын

    Pharaoh tried to kill Moses when he was young but later pharaoh died before Moses . Eksodus 16

  • @OusmanBen-f4o
    @OusmanBen-f4oАй бұрын

    Utsogoleri wabwino sukhala wamphamvu ndi kukhetsela mwanzi ayi,koma kukhala ndi mphamvu kwa anthu ochuluka okondwela ndi utsogoleri wakowo.Anthu pano sakondwela ndiutsogoleri wa Chakwela ayi nde asapange 4c anthu kut amukonde akulephela zambiri pa utsogoleri wake,achoke!achoke! achoke basi anzake alamulire mpandowu

  • @user-gg2qn7zf4m

    @user-gg2qn7zf4m

    Ай бұрын

    Koma kodi amalawi inu chikuchitika ndi chani mungosekelela zopusa ngati zimenezo muziwe kuti mulungu akulanfani chifuka palibe wa muyaya pa zikomo pano muziwe zimenezo

  • @ModesterKaphwitiKunkhe-yc7oh
    @ModesterKaphwitiKunkhe-yc7ohАй бұрын

    Comrade pls muomboreni Mutharika..........muimbiren fon ya direct

  • @LetweebZwewe
    @LetweebZweweАй бұрын

    Amuphe ife chakwelayo tizamupha ndimanja ngati galu wachiwewe

  • @JumaGadaff
    @JumaGadaffАй бұрын

    Dzanja lanu mulungu wamakamu tetezani moyo wa peter langani onse oipayo

  • @lillynhlema9656

    @lillynhlema9656

    Ай бұрын

    Amen

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708Ай бұрын

    Mulungu alowelerepo ndithu,,, ndikuteteza Ana a Malawi

  • @TechnicalSupport-lk9im
    @TechnicalSupport-lk9imАй бұрын

    Yomweyo galu iwe ulula Thanyuwa agalu amenewa ayaluke

  • @user-ty1vq9lq6w
    @user-ty1vq9lq6wАй бұрын

    Palibe chobitsika pansi panthaka, kwa oipa kulibe mtendere, palibe tchimo lomwe lizabweretse mtendere pa umoyo wa munthu ndiponso zilibwino poti zaululika sapanga abwelerako amenewo

  • @SolomonBewula
    @SolomonBewulaАй бұрын

    Amuthanyiwa tangowaimbilani ku dpp ko muwauze chonde ndinu akuluakulu nonkhanokha 😢

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wtАй бұрын

    Angoyelekezaa

  • @GiftNasila
    @GiftNasilaАй бұрын

    Mata Nkhanga Zaino ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4bАй бұрын

    Eeeee koma abale Mcp eishhhhhh mukamachita zanuzo dziwani kuti kunja kuno kuli Mulungu our God in heaven may you protect Peter muntharika in Jesus name Mulungu musalore chititsani manyazi satana

  • @PeterThomas-o9k
    @PeterThomas-o9kАй бұрын

    Ukhale nalo dziko uzikonda wekha satana iwe watopesa chakwera your not right stress yakoyo usawaphe azako Otsalakwa uzimve muntimamo koma kulibe chamuyaya

  • @GiftNasila
    @GiftNasilaАй бұрын

    Limpopo FM ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @LindaTebulo-k4w
    @LindaTebulo-k4wАй бұрын

    Just pray for Malawi may God help us

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaonaАй бұрын

    Indeeeeee Mr Nkhanga zomwezo timakunyadirani mukuyimirira Amalawi Ambiri. Mulungu wathu wamoyo adzikhala Ku Mbali yanu Mr NTANYIWA osayiwalanso Mchimwene uko ku Bakili Muluzi TV Dzanja la Mbuye lidzikutetezani.

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4iАй бұрын

    Komatu achakwela zomwe mukupangazi mulungu akuwona siku ndilimozi chomanphela ana ayini ndichani kapena mukupeleka sembe kwazanu akunyanjawo mukamakhala muziziwa kuti nanuso makasu akudikila kukakumba zenje lanu mizimu yaathu mukuphawa ndiamene akakulandileni pakhomo lopapatiza

  • @lillynhlema9656

    @lillynhlema9656

    Ай бұрын

    Ndipo uyuy he has never been a pastor.....kuubusa kuja ankangobisalako

  • @CathyYassimin
    @CathyYassiminАй бұрын

    Oh ya rabbie tilozeren Muthu wabwino okhulupilira lnu ,lnde kwainu kulibe utsogoreli umenewu

  • @UssenNjirinah
    @UssenNjirinahАй бұрын

    Nde manganyu akutani ku Mcp ku

  • @blacksonpeshes5057
    @blacksonpeshes5057Ай бұрын

    mwadzuka sitafu yonse kumeneko. tikudikila zarelo ka 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaonaАй бұрын

    Malawi Chikangawa Party yadya Chilope Chosavuka nacho. Mpaka kuzapezeka akuwayika pa list anthu omwe anawapha kale Chilope chitalowerera . Koma Mr Lazarus its too much hmmmm

  • @NizigiyimanaChantal-c2p
    @NizigiyimanaChantal-c2pАй бұрын

    Kudziwike kut mumatha Ambuye

  • @user-ss9bj5eh6b
    @user-ss9bj5eh6bАй бұрын

    Angoyelekeza awone dziko liwaukile tatopanawo ife

  • @clalesschisale3792
    @clalesschisale3792Ай бұрын

    Ndale zomwe akupanga a Mcp zikanakhala kuti nayo DPP OR UDF kapena utm imapanga zomwezi sibwenzi MCP itabwelelaso mu Boma chomwe akulimbirana ndi anzawo ndi chani kwenikweni kodi kukhala ochokela zigawo zosiyana ndikolakwika ?😢😢😢😢😢

  • @user-gg2qn7zf4m

    @user-gg2qn7zf4m

    Ай бұрын

    Kodi chakwera iye akuyesa kuti ndi wa muyaya?kudya kuno kuli mulungu

  • @HendrinaNyirenda
    @HendrinaNyirendaАй бұрын

    Ndie mwati hug yaku nsepe ija inali ya Judas Iscariot? Ndile zophana ndizachikape😢

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9jАй бұрын

    Chikangawa chakwera koma zooona eeeeish ukalibe ukhuta nyama za malemu atisiya popano popano

  • @SolomonBewula
    @SolomonBewulaАй бұрын

    Ayelekeze aone zosaona

  • @LuciusMakupe
    @LuciusMakupeАй бұрын

    DPP guys don't take for granted Samalani bas

  • @user-xt2gu9yt9q
    @user-xt2gu9yt9qАй бұрын

    Imeneyo nde mcp kaya poti enanu mukuionela chilendo koma ife tachoka nayo pakatali nanu muidziwe

  • @JosephMichael-x7v

    @JosephMichael-x7v

    Ай бұрын

    Kkkkk

  • @DysonNakhaphe-bo4dl
    @DysonNakhaphe-bo4dlАй бұрын

    😢😢tiudzeni mene zathela

  • @PhilmonBanda-dm7nj
    @PhilmonBanda-dm7njАй бұрын

    Zophanazo nde zachibwanatu

  • @ShakilahMbwanaa
    @ShakilahMbwanaaАй бұрын

    Please dpp be careful this is getting worse to us all malawian their crying a lot so be careful then listen to Tanyiwa what him saying please

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891Ай бұрын

    Zigandanga zaku ruanda and Israel zizipita mmakwawo, sitikuzifunanso mmalawi muno except those innocent ruandaniz

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425Ай бұрын

    Iwe opusa kwambili....

  • @RajaboGostihno
    @RajaboGostihnoАй бұрын

    Comrade let's build up our nation...all the corners of the nation 4:44 4:44 4:44 4:44 Durban south....

  • @BrianJoe-z7u
    @BrianJoe-z7uАй бұрын

    Uthenga waurere thanyiwa

  • @Jasper-xk9iv
    @Jasper-xk9ivАй бұрын

    Mcp yathapo palibe angaivotere

  • @EdnaSiyan
    @EdnaSiyanАй бұрын

    Chipani chanji chongokhalira ku khetsa mwazi. A Mbuye ayendereni onse ali ndi maganizo oipa

  • @JoyceJJames-kj7tg
    @JoyceJJames-kj7tgАй бұрын

    Zovuta kwambili ambuye andithandize

  • @wisekanyinji5377
    @wisekanyinji5377Ай бұрын

    Sakunamatu, mcp njakupha kuyambila kale, ndie sitikudabwa kuti nchito zawo nzamwazi

  • @MarthaWemba
    @MarthaWembaАй бұрын

    Noted

  • @user-wp9js5vu6s
    @user-wp9js5vu6sАй бұрын

    Kuli mulungu kumwambaku 🤝

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3wsАй бұрын

    Ngati Ku DPP kuli achinyamata ovuta kwambili aja amadziyakhula ma social media kuti iwowo ndi anamandwa iyi ndithawi yawo kuti athane nadzo zigewengadzo,,zikufunika kuti onsewo mawa apedzeke kuti onse ndi wankulu wawo ndi mitembo zigandanga zatchabe chabe

  • @ModesterKaphwitiKunkhe-yc7oh
    @ModesterKaphwitiKunkhe-yc7ohАй бұрын

    Aimbireni fon ya direct a DPP

  • @RashidSaid-lk6bb
    @RashidSaid-lk6bbАй бұрын

    Mulungu tetezani azitsogoleri ofunila zabwino Malawi amen

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vnАй бұрын

    Ngati anthuwo ndi aku Rwanda bwanji interview monga kuyankhulana nawo m'modzi m'modzi pomwe akulowa

  • @MosesKalenge
    @MosesKalengeАй бұрын

    Moto kut buuuu❤📺💪💪💪💪💪✊✊✊✊🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @RashidSaid-lk6bb
    @RashidSaid-lk6bbАй бұрын

    Zikomo Limpopo FM radio station %

  • @MaryJefry
    @MaryJefryАй бұрын

    Adadi athu okhawo utisiile

  • @Amgwagwa
    @AmgwagwaАй бұрын

    Sikusinja kkkk

  • @DavieMoyo-pe8vn
    @DavieMoyo-pe8vnАй бұрын

    Umakwana iweyo

  • @thokogwebe2337
    @thokogwebe2337Ай бұрын

    May God protect him

  • @modestermalunga
    @modestermalungaАй бұрын

    😢

  • @MathpeterLemon-ls1ns
    @MathpeterLemon-ls1nsАй бұрын

    Kodi page iyi ili pa whatsapp

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9lyАй бұрын

    Mcp Thambani Thambani chipani cha magazi magazi mwazi mwazi

  • @FloLuhanga
    @FloLuhangaАй бұрын

    Please adziwitseni a DPP awo adziwe tatopa kulira

  • @user-wb9ji3oe5o
    @user-wb9ji3oe5oАй бұрын

    Mudzakhala nkhondo ya chiweni went mtsogolo muno

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dxАй бұрын

    Kukakhala security yokwanila

  • @JozzyNthinda
    @JozzyNthindaАй бұрын

    Limpopo imakwana

  • @MartinNyirenda-w7s
    @MartinNyirenda-w7sАй бұрын

    Dziko likupita kuti ili?😮

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972Ай бұрын

    Mulungu akuyendele ndi mabodza akowo

  • @swintonchirwa1897
    @swintonchirwa1897Ай бұрын

    Atinkenawo ndi amene akakamila

  • @Malani41
    @Malani41Ай бұрын

    Chamba

  • @ChikumbutsochantzMakumba
    @ChikumbutsochantzMakumbaАй бұрын

    Amanyengeza

  • @user-fh5yn8xk2k
    @user-fh5yn8xk2kАй бұрын

    Muyelekeze

  • @ModesterKaphwitiKunkhe-yc7oh
    @ModesterKaphwitiKunkhe-yc7ohАй бұрын

    Aimbireni a DPP

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyoАй бұрын

    Wabodza iwe galu

  • @mikesandali8425

    @mikesandali8425

    Ай бұрын

    Mbuzi iyi yaboza

  • @mashallahleonard2793

    @mashallahleonard2793

    Ай бұрын

    Galu ndiweyo wachipan chokuphacho

  • @IssacMateyo

    @IssacMateyo

    Ай бұрын

    Kodi mesa amay ako ndakazako aja ndamene adavota chipani chakuphacho chikhale boma kulibetu chipani chosapha usanadzinamize galu mbuzi iwe

  • @user-rx4ck9ze1j
    @user-rx4ck9ze1jАй бұрын

    Kutelo ndiye ikhala yazikwanje sure

  • @user-hs4bm2yj8r

    @user-hs4bm2yj8r

    Ай бұрын

    Kufadi ambiri galuyu watikwana