KAMLEPO KALUWA BOMA ZOMWE MUKUFUNA KUPANGA NDIKUDZIWA

Пікірлер: 49

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe20 күн бұрын

    Uku mkuchikweza amputa olakwika, voice imeneyo ikumveka mwa simple koma ili fire😊

  • @user-ux8bc6wy1i
    @user-ux8bc6wy1i20 күн бұрын

    Even neba ku Zambia they know that we don't have president in Malawi

  • @wittinessnkhokwe
    @wittinessnkhokwe20 күн бұрын

    Inu a mcp nenani kuti tonse amalawi tichokemo tifune kolowela muone kuti mudzilanulira ndani?

  • @TwalikiWisiki
    @TwalikiWisiki20 күн бұрын

    Mr Kaluwa i appreciate you,,,you a true gentleman a hero,, if it takes you to go back to your past to resolve this chakwera issue so it be,,

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w20 күн бұрын

    You have to take this Government to court for this damage.

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly20 күн бұрын

    Guys Kamlepo ndi One of True democrat ku Malawi kuno tsopano kodi kuzunza mukumuzuza munthu wobweretsa democracy koma kokoliko ndalama zamisonkho yamphawi zakomadi

  • @luuu22mwanjabala79
    @luuu22mwanjabala7920 күн бұрын

    Wise man from the North side

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma20 күн бұрын

    Bora ilili tikachotsa chakwera a police ambili akuyenera kuchotsedwa tchito

  • @amoschataika7440
    @amoschataika744020 күн бұрын

    Well said, loud and clear

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl20 күн бұрын

    Wise man mr kamulepo ❤❤❤❤❤

  • @user-zy2nh4lj4h
    @user-zy2nh4lj4h20 күн бұрын

    Zinazo muzipanga koma za artist fredokiss mukangoesera 😮 malawi tiyatsa mukangopha fredo achinyamata tifafaniza state house

  • @JamayakoJamayako-rv2he
    @JamayakoJamayako-rv2he20 күн бұрын

    Am agreed with you Pipo shud open their eyes Wise man

  • @brendamakokola7498
    @brendamakokola749820 күн бұрын

    Politics is dirty game

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr20 күн бұрын

    Chomwe wachiona wankulu atakhala pansi, mwana olo atakwera mumtengo sangachione. Welcome Big

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w20 күн бұрын

    Ndikatundu ameneyu aboma musamutengele masewelo zomwewakambazo ndizoona ndithu

  • @chipilirokalison1334
    @chipilirokalison133420 күн бұрын

    Sizitheka mulungu alipo kumwamba osamara

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b20 күн бұрын

    Amenewo ndie mawu amphamvu mbuzi za police zogwilisidwa ntchito ndi chikangawazo makape amenewo akuti agulidwa ndi mcp gvrt Makamaka mai yolamu nayeso chipawa chosamukhala mutu chija mbuzi ya munthu aziwona makape amenewo mu 2025 wonsewo akathela ku mawulapalibeso kuwakhululukila inshaAllah

  • @JameChome
    @JameChome20 күн бұрын

    Ask Bakii Muluzi anamtangwanitsa kooopya 😂😂😂😂😂

  • @NescotNyamwela
    @NescotNyamwela20 күн бұрын

    Ine president wanga ndi Dad Bingu wa mutharika kwa ine sanafe i can see kuti anapanga chani. Kma mbuz zinaz zimangozuza amalawi osalakwa anyway sindili ku malawi kma home is best mbuziyi izaziwa kazachopa pamwambapo

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr20 күн бұрын

    Boma iliri azitsogoleri mitu sikuyenda bwino why still keeping cellphones of Born kalindo and kamlepo why why Malawi President and the Police why can you please change your decisions why.

  • @temwarachaelkhonje3733
    @temwarachaelkhonje373320 күн бұрын

    Aputa olakwika tu....

  • @GeraldChisokeza-er5cf
    @GeraldChisokeza-er5cf20 күн бұрын

    Oh no osat Fredo ayi.Komano kukhetsa Mwazi chifukwa Cha mpamdo Kaya Mulungu amaona amakantha

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b20 күн бұрын

    Apolice yakhani kuti umuyaya uja udakalipobe kapena ai?

  • @raytavares2256
    @raytavares225620 күн бұрын

    Collect your phone via the attorneys and high court on releasing it without prejudice and bias. We are praying for you. Ndine kuno ku Great Britain. Yes the late dad Green Ng'oma used to w for Southern Bottles even when they lived in Mzimba before moving to Zingwangwa Blantyre and after ZINGWANGWA THEY MOVED TO ALIMAUNDE AREA 25 LILONGWE. We must all pray for each other and the countries experiencing the political tarmoils.

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o20 күн бұрын

    Pambuyo panu bwana..iponden

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma20 күн бұрын

    Mcp ikuyenera kuchoka basi ikuzuza athu osarakwa chakwera wakupha ayende basi

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn19 күн бұрын

    Yooo zilichonchoso 😢

  • @mbewemisoyaanenenji1908
    @mbewemisoyaanenenji190820 күн бұрын

    You fought ngwazi , who are these dogs to fear .

  • @IdahNyasulu
    @IdahNyasulu20 күн бұрын

    Deal with them bwana kalua

  • @zelliachamboto5744
    @zelliachamboto574418 күн бұрын

    Kulibedi wamuyaya

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa847620 күн бұрын

    Pena pache MCP tu , mukuonjeza eti!!?? Is this what we wanted? Why why why??

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw20 күн бұрын

    Zosaesanda

  • @babranzima8120
    @babranzima812020 күн бұрын

    Athu akupha abusa wokopha kodi eeeeee athu akumpoto mwasiye mutha ndinu achakwera ndi azanu wood

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri20 күн бұрын

    Amen Amen...

  • @CharlesKachipanda-jz9jv
    @CharlesKachipanda-jz9jv20 күн бұрын

    Awuzeni makapewa adziwe kuti inu madala madala

  • @user-ss9bj5eh6b
    @user-ss9bj5eh6b20 күн бұрын

    chonde bwelerani muzakale bwana tithane nawo anthu oipawa

  • @ShorayChimera
    @ShorayChimera20 күн бұрын

    I feel ur pain father 💔

  • @victorauwana7258
    @victorauwana725820 күн бұрын

    Good 👍

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto20 күн бұрын

    😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @AgnessMzengo
    @AgnessMzengo20 күн бұрын

    Iponden fadah,,,,,

  • @user-kp7le2pu7h
    @user-kp7le2pu7h20 күн бұрын

    Wise man❤❤❤

  • @user-fq4kv8dj4t
    @user-fq4kv8dj4t20 күн бұрын

    Mwaonjeza English enafe sitimva nde izizo muzilankhulako chichewa chifukwa nzatonse amalawi kuti timve

  • @Standwell78
    @Standwell7820 күн бұрын

    Chana?? Ayesele

  • @MagaLassi-tg7lj
    @MagaLassi-tg7lj20 күн бұрын

    🆓✊

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp20 күн бұрын

    Akupa mcp

  • @MilacleSankhani
    @MilacleSankhani20 күн бұрын

    Ask late kamazu about u

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc20 күн бұрын

    Wise man

Келесі