Келесі
- 00:28
- 110 МЛН
- 13 күн бұрын
- 00:21
- 88 МЛН
- 24 күн бұрын
- 00:42
- 10 МЛН
- 12 күн бұрын
- 01:00
- 8 МЛН
- 6 күн бұрын
- 32:47
- 43 М.
- 54:00
- 60 М.
- 15:10
- 21 М.
- 17:01
- 45 М.
- 1:03:20
- 230 М.
- 49:16
- 69 М.
- 15:18
- 12 М.
- 0:20
- 4,3 МЛН
- 1:00
- 1,7 МЛН
- 0:11
- 11 МЛН
- 0:17
- 2,2 МЛН
- 0:55
- 3,1 МЛН
- 0:25
- 1,6 МЛН
Пікірлер: 545
Mwaiwala kuthokoza limpopo FM and bakili muluzi tv, ife tinamvera pa limpopo FM and bakili muluzi tv zakumangidwa kwanu , ingondilolan kuti ndithokoze limpopo FM crew yonse mosogoleledwa ndi mtanyiwa, lufeyo walufeyo etc komanso bakili muluzi tv, akugwira ntchito yotamandika kwambiri yomenyela ufulu amalawi , keep it up guys ❤!, ndinu mamfana olimba mtima kwambiri mmalawi muno.
@MusheBree
2 күн бұрын
Ndendende
We need more people like u,big up kalindo
Chinyawu chokha chimene chingamunyoze kalindo koma kuyambira muyao mtumbuka nsena mngoni mlomwe mang'anja ndi mitundu yonse ❤❤❤ amamukonda kalindo
❤❤❤❤ I love mr born kalindo this man is strong man God bless you all the time
Mulungu akusungeni ndi moyo makamaka m,tanyiwa wagwila tchito yaikulu ndipo amalawawi tikanakhala achikondi ngati amalaw festir zikoli sibwezi tikunyoza athu ngati inuyo tchito mukuigwila ndipo okumba zenje lanu agwelemo okha ❤❤😢😢
@EmillitaMluga
2 күн бұрын
Ndipo ntanyiwa waonetsa chikondi
The DC❤ much love and respect
Strong guy 💪💪💪 kalindo long live ❤❤
Ing'aluleni Mr DC, ndimadziwa ine kuti simunamangidwe koma mumakayendera amphawi anzathu kundende, proud of you 👏👏
Kungomva voice yanu bwana kalindo ine kuntimaku mya
Adzanga!!!!..Mwasowatu adzanga. The DC Team is here.
Iweyo ukhare vp WA peter ndiwe munthu olimb mtima kwambiri🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Iweyo ndi bambo wa amphawi zoonadi we continue praying for you Mr Kalindo
Kodi uyu chakwelayu mayi ake alip ngati alipo bwanji sakumukwapul
Welcome back Mr Kalindo you really loved
Zikomo zikomo a Bon kalindo osatopa chilungamo chamawawa
Welcome back the DC. Tinakusowa ng'alula amvetsetse
Osaiwala JB from south bend USA
We need federal government ku Malawi kuno, kumpoto azilamulilako ntumbuka or ntonga , pakati zinyawu zizizilamulira zokha, kummwela kuno wina aliyense atha kulamulira kupatula a chewa, anthu agule kuno ayi. Zikomo
God bless you and protect you the DC
This man is very strong...simunthu wamba.Get his message you politicians.Amayankhula chilungamo.
DC exactly mcp sidzawina and no more rulling this country of Malawi chakwera waononga dziko
@user-mq3mh5md5e
2 күн бұрын
Mcp siizawina kodi mwa vota kale?pajatu muli _(50+1
Respect 🙏 ❤ DC we support you 💯
Ndinu nokha Mr bon kalindo am happy to hear yr voice
Tinakusowani takulandirani Mr DC ❤❤
My father also was like that song ❤❤❤❤❤ ndipo Sunday lathali kuno ku South Africa tinalengeza kutchrch zaubwino wanu ndikukupephelelani mulungu watiyakha
@GeraldChisamba
2 күн бұрын
My father also was like that song 😂😂😂😂 kuma guys kutheba kuli chingerezi
Boooooooooooooooooon Kalindoooooooooooooooooooooo!! The DC
We need people like you to provide checks and balances in the government.
The true son of the soil. God bless you.
Yekhayo oyankhulira a Malawi wosalandila chibanzi, ndi comrade mtanyiwa!! Welcome back bro
The DC OSAOPA,OSATOPA OSAFOOKA ,This is our country and our home
Listening frm Cape town big up Njeza man
Komandiye ndiwathandizeso kuthokoza mwina atopa bwana amwe Madzi antanyiwa kumene Muliko ndigulu lanu lonse landilani ulemu waukuluuuh ndipo muchive mulungu akupaseni moyo wautali tikuthokoza kwabasi tchito mukuigwila NG'alulanibe madala atuluka❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Ati mundikozere nsewu kut mukandimanga ndiziyenda mwachangu 😂😂😂 tinakusowani mmmm
God protect you akalindo
The DC long live pambuyo panu sitikukusiyani tizafela mbendela yathu🇱🇾
Km. Kalindoo wandiseketsaa ati mukamangaso mukamusiyeko ku mpoto
Welcome back continue we will support
The 'DC' back in office...Tiyenazoni 100% pambuyo panu..
The DC samatukwana, amangoyankhula chilungamo.
Born kalindo my president l love god bless all the way ❤❤❤❤❤ mcp manyazi bwa upresident si oopsezera anthu kudziko
I CAN'T TALK TOO MUCH BUT BON KALINDO THE DC 🙏🙏
May the good Lord continue to give you long life
Kkkkk Akuti waphunzira zakbiri 🤣🤣🤣Kuyendela ndende.......Nsewu wa Salima-Dwangwa 😡😡😡😖😡
Iiiii koma uyu sadzatheia😂😂😂😂😂🙌🙌🙌
The troubler of Isreal😂 The truth fears Nothing "Thank you.
Welcome back big boss
I'am happy with you my brother fight for Malawi
Eeeeee mumantha ndakuvulirani chipewa the DC wosamphwekesa, Ambuye akhale nanu nthawi zonse.
Big man awawa sazatheka Big up Aluta continua
That's bon kalindo I know no fear for any 1 truth mst review
M.C.P idzawina Kalindo ndi chitsilu,,,Ndichamitsala.Anthu sakukufuna nkomwe,unaluza wu M.P kwanu
Welcome back my truth the DC❤❤
Welcome back the dc🇲🇼🇲🇼💪
@NovassTambala
2 күн бұрын
Mr born kalindo your number 1
Mwana Owopsa kwambiri THE DC our Pangolin 🔥🔥
DC inundi mwaima pachilungamo ❤❤❤❤
Akut it's a donation........ Big up bon kalindo🎉🎉
comano bon kalindo your number one
Kkkkkkk wabwelaso president wathu timaona ngati akudyetselatu kt bs wasiya kuyankhula 😂😂😂😂😂
Our president 💪💪💪 the DCccccc
Inde achina Kamuzu,Chakwera adzipita sitikufuna galu ameneyu
Osatopa osaopadi tilinanu 😂😂😂😂 ambuye ndiwabwino
Machine atulukira tsopano. Welcome back the DCCCC!
Welcome back to the office Mr DC
Umakwana iwe ndi number one Mr president bon kalindo
May wisdom of God be wlth you
Listening from Bagamoyo
I support the DCs mwana woooopsa kwambiri tili pa mbuyo panu boss
Bwana prezideti bon mwayakhulatu chinyamata pakana ngeto kkkkkkkk mwandisangalasa aprezidet Akalindo
2025 sugar tigula 10000 anthu opanda Chisoni ngat awa sinawone
Welcome back mr ❤❤❤
Big up bwana president
More fire 🔥 Booooon kalindoooo 🔥
Chilungamo sichiopadi kungotuluka basi pompopompo
Our president, Bon Kalindo ❤
Kalindo vote☑ ili ndiife anthu osati iweyo zomwe ukunenazo walephela kapume kumulanje
Angosiya ku mumanga president wathu uyuu😂😂😂 chifukwa amangofayapo nthawi
Welcome back president wa anthu osauka
Tingopanga zomwe anzathu aku Kenya akupanga tosadikilenso kudzavota mu 2025 ayi
@AllihSterCasianuh
2 күн бұрын
Ndipo ndipa 10 pano
Big up b kalindo
Boma ili ndi boma lomvesa chisoni kwambiri.Boma limeneli layiwala kuti linalowa chifukwa cha mademo,kuotcha misewu,kuphwanya ma sitolo komanso ma ofesi aboma pansi pa mlaliki,mtumiki wa Mulungu.Zonsezi zimkachitika iyeyo mlalika wa Mulunguyo alipomwepo.Koma dziwani ukuku ndiye kutha kwa boma la MCP
@louismagongwa
2 күн бұрын
kkk anaiwala kale achakwera ndi malemu chilima anali kupit kumademo lelo akumang athu😅
Limpopo fm muyithokozee mwapadela.. Antanyiwa agwila mtchito kutiziwisa everything
Tili pambuyo panu apule 🔥🔥🔥
Welcome our father tinakusowani Ana anu
Welcome back Sir
The Dangerous child DC❤
Mumakwana inuyo Bwana wa osauka ❤❤❤❤❤❤
Bon Kalindo...... Mr phone Donation😂😂😂
Inu tamangopangani zoti mukawine u MP apa izi zikuchedwetsani
Big up brotherman, kungopha inuyo mcp tidzapha ndi miyala,azaziwa the meaning of democracy/mphavu mu wanthu
King born kalindo respect to him
Umakwana iweyooooo kkkkk takunyadilani
The DC respect to you
Mtakula ndilani bon kalindo ❤❤❤
❤bon kalindo president wathu
Mwana woopya d c well come home
😂😂😂😂koma zinthu zake 👐👐👐Eish koma tinva zinthu ,May Mr Saulos Chilima 's soul and the other 8 pipo continue to be Resting in peace 😭 😭
Wangodzukila pa VN😂😂😂😂😂
Ndipo kwawo kwathadi olo patavuta bwanji sangawine
Ndimakunyadira wakula born kalindo
Akupasa mangolomera the DC timakunyadilani