Ati wa Bakili Muluzi ampeza ku Ticktock 😂 komatu Ma duet enenawa mumangidwa nao

Пікірлер: 212

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hiАй бұрын

    Bakili muluzi TV channel never arrested that guy we are together this is home land🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼✊️✊️✊️✊️✊️✊️

  • @stanleychipyela5275
    @stanleychipyela5275Ай бұрын

    Even here in Zambia we love this man may the Lord GOD protect him for brings the truth 🙏🙏🙏🇿🇲🇿🇲🇿🇲

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3wАй бұрын

    Eyah! Iwe ndiwe mtola nkhani no.1 mu Malawi, sitilola kuti tibwelere ku 1 party system, no! Palibe zimenezo , ndiye tiphedwatonse.

  • @powercharios2087
    @powercharios2087Ай бұрын

    Good Job brother you always talking the truth, MCP Mudangozolowela moyo wausilu ngati wambuyanu kamuzu kumapha athu akanena chilungamo MCP nonsense Government iwe Chakwera Basopo

  • @OfenFrank-je3ci
    @OfenFrank-je3ciАй бұрын

    Munthu wankulu inuyo sinu munthu wamba nkhani zomwe mukuwulutsa inu big, ndi nkhani zoti ngakhale ntola nkhani wachipani chotsutsa sangawulule kutiwuza chowonadi anthufe poyera ngati mmene mukuchitilamumu chifukwa amaopa kumangidwa ndiolamula boma. Koma chomwe tinganene ife ndi chakuti chilungamo chimamasula the truth will set you free mulungu a kusunge ndi moyo komaso akutetezere where ever you go kulikonse komwe mupite may God protect you brother in jesus name amen.

  • @George-zd5le
    @George-zd5leАй бұрын

    When I head this program song I feel impressive, good Job

  • @manzyhetekele8697

    @manzyhetekele8697

    Ай бұрын

    Great job this is true I love this guy

  • @user-jw5rx9ze8k
    @user-jw5rx9ze8kАй бұрын

    Eeeee koma amenewa, simunthu wamba may God protect you broz.

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892Ай бұрын

    Kukhala ndi atolankhani 10 ngati amenewa mdziko muno corruption ikhoza kusika koma aaa atolankhani anawa kukonda mabazi

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4bАй бұрын

    Well well our brother I patse moto may God protect you our brother wherever you will gooooo❤

  • @user-qn2nu4xs9i
    @user-qn2nu4xs9iАй бұрын

    Kkkkkk....ulendo ulipo asakaikire😂😂😂😂😂

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6yАй бұрын

    Big man Bakili Tv ❤

  • @georgemponda
    @georgempondaАй бұрын

    Hahahahaha sameneyo anya akhawula samupeza 😅😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @patriciacraiton-sf5vu

    @patriciacraiton-sf5vu

    Ай бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @HannahNtenda

    @HannahNtenda

    Ай бұрын

    😅😅😅😅

  • @HolickLemajomo
    @HolickLemajomoАй бұрын

    Muzingoyenda mosamala ndi mene zilimu koma ambuye ndi wabwino akusamalireni kumene muliko anthu oipawa asakupezeni

  • @user-pn7cj9hb3t

    @user-pn7cj9hb3t

    Ай бұрын

    Man ndinu amatha simungateteze ana anu m'nyumba be a man asa.

  • @MwayiNyilongo
    @MwayiNyilongo22 күн бұрын

    Chisiru China pano chiziti mcp Moto🔥🔥 ndikangochiona sichiliona la mawu

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwaniАй бұрын

    Mdima umadana ndi Kuwunika...Bakili Muluzi TV for ever more

  • @user-mf5ce9wj4m
    @user-mf5ce9wj4m14 күн бұрын

    No stone unturned the truth must be told.Chakwela is getting too comfortable.come on Malawi let's fight fight for out freedom.

  • @augustMag
    @augustMagАй бұрын

    Go ahead brother GOD almighty continue to guide and protect you always you are standing the truth ❤❤

  • @janenkhoma6447
    @janenkhoma6447Ай бұрын

    Aise uja kumugwila wamba ndakaika and ujayi dolo aise and I'm proud of that chanel

  • @roonmasterchindamb
    @roonmasterchindambАй бұрын

    Big man good job Allah bless you bra

  • @user-im3gn6bp4e
    @user-im3gn6bp4eАй бұрын

    Even here China we love this mn

  • @Resterzambasa
    @ResterzambasaАй бұрын

    Stay safe big boss kulikose komwe muliko gwilani ntcthito basi we wish you all the best

  • @user-it5zv2nz7f
    @user-it5zv2nz7fАй бұрын

    Mwandikumbutsa my jnr literature at secondary "" in the field by Edison Mpina" big up bwana

  • @Amgwagwa
    @AmgwagwaАй бұрын

    Wachita bwino adzikuona nkhope kkkkkk❤

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vnАй бұрын

    This guy opened people's eyes and no one must touch him because he's the Malawian Eyes

  • @phidopatrick6021
    @phidopatrick6021Ай бұрын

    We always feel good and we learn a lot from you ,, we will follow you forever, ndinu big

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085Ай бұрын

    Amayenda ndi mdaliso uyu .may God keep blessing u bro

  • @BysonMakalani
    @BysonMakalaniАй бұрын

    Mbambande .. freedom of speech

  • @user-mw8dq4is6k
    @user-mw8dq4is6kАй бұрын

    Ambuye akutetezeleni nthawi zonse chifukwa anthuwa akupanga za Inu bigy tili pambuyo panu🔥🔥🔥God is our protector.

  • @aaronguwechakwira
    @aaronguwechakwiraАй бұрын

    Well done my guy . Keep on going my guy .

  • @user-ce6hy6tp7e
    @user-ce6hy6tp7eАй бұрын

    Inuyo akulu ndnu wanu amene akufuna kumanga inuyo bola amange anthu tonse amene timatsatira bakili muluzi chakwera ndwe galu kwabas umadana ndi chilungamo bwanji ndi achina chithyola moses agalu inu musiyen munthu azitiuza ma history hiyaaaa

  • @NicoleneTony
    @NicoleneTonyАй бұрын

    Mumakwanila palibeso ulemuwanu Big man❤❤🔥🔥🔥

  • @ArnoldMakwewo
    @ArnoldMakwewoАй бұрын

    This man is number one to us Malawian timamukonda

  • @user-uc1pd1tc2x

    @user-uc1pd1tc2x

    Ай бұрын

    Ndipo koopsa Zedi

  • @AwaliJames-wi3jz
    @AwaliJames-wi3jz22 күн бұрын

    Never give up big we follow you for ever❤❤

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3wАй бұрын

    Kkkkkkkkk koma boma ili mmmmm litha ngati ma ketone

  • @antiepogba1534
    @antiepogba153421 күн бұрын

    Watching from south africa 🇿🇦 in Port Elizabeth

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2xАй бұрын

    Bakili TV it's my best ever tv I love ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosiАй бұрын

    Bakili muluzi TV iponden mn

  • @peternashyo9850
    @peternashyo9850Ай бұрын

    I salute you

  • @shideshidex5679
    @shideshidex5679Ай бұрын

    Amene Uja Ndidolo😅 Or Mai Ake Sakumudziwa

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hiАй бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂 boma njenje bakili muluzi TV KZread channel here

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    Ай бұрын

    🤣🤣🤣

  • @JohnConar-kq4hi

    @JohnConar-kq4hi

    Ай бұрын

    @@MalawianCamera akumaga😂😂😂😂😂

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473Ай бұрын

    Kutha kwa chipani chakhaza akukulondola ni chifukwa auzeni ziphaliwali kikikiikiki atakudziwani BAKILI MULUZI CHANNEL 😅❤🎉❤Kozani Dziko osati kulimbina ndi Ma JOURNALIST.

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e.Ай бұрын

    Great one🎉🎉🎉

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jvАй бұрын

    Kkkk boma la malawi zitselekwete zokhazokha ndithu aaaasaaa

  • @user-re5ki2cp4b
    @user-re5ki2cp4bАй бұрын

    Ine ndiye I proud of you

  • @richardstambuli7649
    @richardstambuli7649Ай бұрын

    Zafikapa zitha kutheka kuti ma subscribe ambiri ndi apolice😅, ndi Aboma😂😂 wish to see you one day! Ntolakhani number 1

  • @AfredMbeta-pk1cn
    @AfredMbeta-pk1cnАй бұрын

    Allah protect you all the way

  • @alickkachepa3801
    @alickkachepa3801Ай бұрын

    All the best brother.......

  • @gizzykondwani865
    @gizzykondwani865Ай бұрын

    Keep up the good job boss

  • @JerryChain-cz8ru
    @JerryChain-cz8ruАй бұрын

    Umatiyimila osati, Ben longwe

  • @InnohLukah.1998
    @InnohLukah.1998Ай бұрын

    Ngati akufuna kuzafera ku South kuno abwere basi...

  • @user-vi5ug5to1q
    @user-vi5ug5to1qАй бұрын

    Atolankhani ngati awa ndi mbande❤

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo13 күн бұрын

    Ana achepa, sangakupeze Agalu amenewo😂😂😂

  • @daviemungadetse1222
    @daviemungadetse1222Ай бұрын

    Shame on this government so called tonse alliance may the almighty God bless and protect this man

  • @websterkausiwa8919
    @websterkausiwa8919Ай бұрын

    Ndie awaa mmene akuliramo ati asisatiza zomwe amayankhulaa wa Bakili Muluzi yoo?? Aaah wasowa zochitaa uyu....

  • @user-wd5tw1mz8h
    @user-wd5tw1mz8hАй бұрын

    Olo atatan chakwela akuchoka mbuzi yamunthu

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd

    @JohnmarkNazombe-hi9xd

    Ай бұрын

    Exactly!!!

  • @JamesbhekiGama-gt5oe
    @JamesbhekiGama-gt5oeАй бұрын

    Syabonga Bhutia nomusebeni emuhle

  • @AllieMilazi-do3xv
    @AllieMilazi-do3xvАй бұрын

    😂😂 km boma lanjenjemela ndi bakili muluzi TV 😂😂😂

  • @user-zk5nu5fh6l
    @user-zk5nu5fh6lАй бұрын

    Never lose hope ❤❤❤

  • @Razarusmbavachakwera
    @RazarusmbavachakweraАй бұрын

    Mumuwuze Kunkuyuyo zoti apolisiakewo zoti akangoyelekeza kuponda ku south Africa kuno tiwaphera konkuno

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1bАй бұрын

    Apaso amanama kukhotakota kuti azilima katatu pa chaka km chimunthu banda adakoza ndi zake chakwera yo kkkkkkk anya manyi amenewo sanati agwapewo kkkkk

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1iАй бұрын

    Koma awa ndi machine oziwa kusanthura nkhani ulemu wanu biggy

  • @LamieTiger
    @LamieTigerАй бұрын

    😂😂😂😂achoka ndithud

  • @EvertonMvula-of1um
    @EvertonMvula-of1um20 күн бұрын

    Keep up the good work bro 😂😂😂😂

  • @juniortsegula3847
    @juniortsegula3847Ай бұрын

    Tv #1 in malawi

  • @user-xm3zl5cg6x
    @user-xm3zl5cg6xАй бұрын

    BBali muLuzi tv umakwanila❤

  • @johnkatapeh7182
    @johnkatapeh7182Ай бұрын

    Big up fadah

  • @SalimUthman
    @SalimUthmanАй бұрын

    I like this guy

  • @Pangolinimw
    @PangolinimwАй бұрын

    😂😂😂😂😂 boma rabalalika ndi bakili mulusi 😂😂😂😂

  • @MwenyeCheNsoma-gb2yz
    @MwenyeCheNsoma-gb2yzАй бұрын

    Let tonse alliance learn something from this channel please. I believe Mr. President is a statesman

  • @rexphiri7242
    @rexphiri7242Ай бұрын

    Osafooka inu Nd munthu wankulu💪💪💪

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088Ай бұрын

    long live king💪

  • @AndrewWyson
    @AndrewWysonАй бұрын

    Agalu amenewa akuononga kwambili chumma tisiya kudula msokho aone kkkkkkk. Mbalame

  • @user-dx4zu1wv4q
    @user-dx4zu1wv4qАй бұрын

    Respect man

  • @TonyBanda-zh2rd
    @TonyBanda-zh2rdАй бұрын

    Koma yaaaaa koma ndi emweyu kkkkkkkk kapena mwangofuna kutchuka

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8bАй бұрын

    Katundu wathu ana amuna osati Ben longwe chisiru mphawi n'kunkha panyo Ben iweyo siomenyera ufulu waanthu koma omenyera ufulu wachakwera wathu ndi ameneyu ndi bon kalindo komanso uyu sangampedze chakwera simulungu panyo pako chakwera

  • @moseskathekeni8848
    @moseskathekeni8848Ай бұрын

    Umakwana brother, Mulungu apitilize kukusamalira & kukuteteza

  • @isaaczuze
    @isaaczuzeАй бұрын

    Ngati chakwera angakamile mmalawi muno mukhala nkhondo yachiweniweni .....chakwera ife sitikumufuna ayi

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinjeАй бұрын

    Your are number one

  • @user-dy4gc2hr5e
    @user-dy4gc2hr5e18 күн бұрын

    Big man mumatha timamva zambiri kuchokera kwa inu pitilizani musafooke tili pambuyo panu

  • @jameschibisa1433
    @jameschibisa1433Ай бұрын

    Kkkkkk koma ma duet awawa mumangidwa za eni komabe aliyense amapanga mmene wachimvera ngati amakuwaza umayenera kutero mbambande

  • @susansoko6600
    @susansoko6600Ай бұрын

    MCP Ili ndi chi ntchito chosakasaka big man koma athamanga sanati💪🤸🏾🔥

  • @MuhammadInack
    @MuhammadInackАй бұрын

    Kkkkk a kunama sameneyo afela zaenitu uyu

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
    @AbdulmajeedJbanda-oz3jvАй бұрын

    Even atampeza sangakhalekho 2days alinkathi muzaona nyekwe yinu ndimmene amalawi amankondela

  • @DickisonyusufChiwalo2
    @DickisonyusufChiwalo2Ай бұрын

    My Allah protect you

  • @CharlesKazembe-yf4ff
    @CharlesKazembe-yf4ff26 күн бұрын

    Si uyu mumuone pakamwapo zikusemphana😂😂😂😂

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024Ай бұрын

    😂😂😂😂kom malawi eshiiii sazantheka kukanatu chilungamo bas

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    Ай бұрын

    🤣

  • @IsaiahBanda-gt5qz
    @IsaiahBanda-gt5qzАй бұрын

    Fear no evil brother.❤

  • @ApatsaNgalu-qr7fw
    @ApatsaNgalu-qr7fwАй бұрын

    God must always protect you untill we move them out on 2025 we have fed up ndi mbava you dj nyantaniwa and others mukugwira ntchito yotamandika amalawi akumva zonsezi

  • @MosesMvula-te2nf
    @MosesMvula-te2nfАй бұрын

    Khalangat ndyeyodi tu kkkkk

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomoleАй бұрын

    big boss ❤❤❤

  • @calvinjamal7117
    @calvinjamal7117Ай бұрын

    The best Tv

  • @SolomonShaibuh
    @SolomonShaibuhАй бұрын

    Kkkkk uyu ndkatundu

  • @user-km5cl9xt2p
    @user-km5cl9xt2pАй бұрын

    Utakhar president uli booo

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1qАй бұрын

    Ben longwe za ziiiiiiiiii zeni zeni uyu nde ndi one

  • @ZambukanaBanda
    @ZambukanaBandaАй бұрын

    M'dima ukachuluka kwatsala pang'ono kucha.or atamumanga ena adzabela wina ngati ameneyo.

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732Ай бұрын

    Kudana ndi chilungamo. So sad. Ambuye awayendere mwapaderadera.

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6dАй бұрын

    Mulungu akupatseni moyo wautali komaso ambuye azikuteteza thawi zose tsiku lina kudzacha ndithu

  • @user-cy7gd1go6y
    @user-cy7gd1go6yАй бұрын

    Bm tv ndi za power 💪

  • @BrightonBanda-zc3hc
    @BrightonBanda-zc3hcАй бұрын

    Mnyamata ameneyi amatidziwitsa nkhani zobisika zam,boma mulungu amuyang,anile

  • @CharliePaulelic
    @CharliePaulelicАй бұрын

    Without bakili Muluzi tv KZread is boring