onerani asanadilite azungu video iyi

Пікірлер: 29

  • @MwenyeCheNsoma-gb2yz
    @MwenyeCheNsoma-gb2yz20 күн бұрын

    Ndukaika ngati Iran angayikwanitse

  • @YusufJmakanjira66
    @YusufJmakanjira6613 күн бұрын

    Nde Pali mbuzi zina zimangogomera azunguwa chosecho chilungamo akuchiziwa🎉😢😢

  • @user-fb7ki3hc7y
    @user-fb7ki3hc7yАй бұрын

    Malawian cameras ❤

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283Ай бұрын

    Azungu omwewo mukumawapempha. Ayi zikomo.

  • @chrischelewani
    @chrischelewani2 ай бұрын

    Those countries have got minerals ndi ma mineral amenewo atha kutukuka nkumaziimilira pa wokha and it can be a danger for them to rule Africa and Asia bcoz they have soldiers in those countries Sinanga asiya kuwapempha u super power wawo ukhala pa chiophyezo

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    2 ай бұрын

    1000% apapa mwalasa amkolo

  • @Bonisiwentamo
    @Bonisiwentamo24 күн бұрын

    Amanyi

  • @user-yg9rs7tp2x
    @user-yg9rs7tp2x3 ай бұрын

    zungu ndi Santana weniweni

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    3 ай бұрын

    Eeeee kwambiri

  • @hastennyanda-fo7jc
    @hastennyanda-fo7jc3 ай бұрын

    Rasta teachings gonna make us free

  • @CeciliaMphili
    @CeciliaMphili10 күн бұрын

    Koma ine ndikamaliza xool ma video ako uyambe mchizungu coz khala ndaphuzira zose😂

  • @user-nh1xh4mc7u
    @user-nh1xh4mc7u2 ай бұрын

    Azungu ana asatana

  • @MacmillanMakombe-sz4iy
    @MacmillanMakombe-sz4iy3 ай бұрын

    Wabwera

  • @user-ql1ig3cv5j
    @user-ql1ig3cv5j3 ай бұрын

    Azungu Nd joka

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    3 ай бұрын

    Ndipo ndi asatana

  • @AbdulkareemSharif-mr1gx
    @AbdulkareemSharif-mr1gx3 ай бұрын

    Ndiye muziti asilamu ndi amtopola

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    3 ай бұрын

    Eti eti koma maikowo akuphulitsa okha

  • @user-mh8ji1wd7f
    @user-mh8ji1wd7f3 ай бұрын

    Eeeeh koma nde zoona

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    3 ай бұрын

    Anthu oipa kwambiri

  • @user-ve4sd5fp1y
    @user-ve4sd5fp1y3 ай бұрын

    Boss pali zambiri chifukwa chake ndanda wa maikowo ayenera kuphwasulidwa if you search that info maso anu aseguka amelika singopanga zinthuzi.

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    3 ай бұрын

    Wesley Clark atafusa kuti why? Zomwe anamuyankhazo nde zifukwa zake zimenezo

  • @user-on3yu7wt9o
    @user-on3yu7wt9o3 ай бұрын

    Muli nd nkhani n info yabho km mungozitolela on narrative stills

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    3 ай бұрын

    Alright thanks broh I really appreciate your support and feedback 🙏🙏

  • @AronAlfazema
    @AronAlfazema23 күн бұрын

    Iwe program ako ndiopanda Thandauzo

  • @AlickMacsando

    @AlickMacsando

    18 күн бұрын

    Pangano yako yothandiza

  • @alickmustafa

    @alickmustafa

    18 күн бұрын

    Osatuluka bwanji

Келесі