Apolice ausilu awa anapha mwana nde Trapence akufuna athane nawo osawasiyasiya ayi

Пікірлер: 25

  • @AndrewMachemba-g5y
    @AndrewMachemba-g5y18 күн бұрын

    Anthu oyipa amenewo Migwanya yabomayo alonda amangokhalangat sazafa agalu

  • @JamesKamanja
    @JamesKamanja18 күн бұрын

    Very good amangidweso

  • @Nomsa77
    @Nomsa7719 күн бұрын

    Sakupanga za ntchito yawo manso awo Ali PA ndalama asanduka zigawenga mumalo mowona mavuto awanthu

  • @LouisChipanda-ux9dz
    @LouisChipanda-ux9dz17 күн бұрын

    Ngati bambo akuba mwana atani zayambila kuntundako😢😢😢

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi19 күн бұрын

    Zitsiru za police

  • @thondoyaenterprise3795
    @thondoyaenterprise379518 күн бұрын

    Human rights 😂😂 , im sure they know what is driver's license.

  • @user-dt4ud7gh2n
    @user-dt4ud7gh2n18 күн бұрын

    Manyi and apolisi ankhanza inu kupha mwana

  • @thondoyaenterprise3795
    @thondoyaenterprise379518 күн бұрын

    Apolisi amagwira ntchito yawo. By law ," u need a driver's license to drive a car". What the family and police officers, should have done was to call the ambulance to take the patient to the hospital. MALAWI lets not creat chinam'balala. Lets not destroy out country

  • @user-rn7wv8ze3v
    @user-rn7wv8ze3v17 күн бұрын

    Nkhaza apolice

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph816118 күн бұрын

    A police opusa machende awo

  • @ClementKhomba
    @ClementKhomba18 күн бұрын

    Kupusa kwambiri apolice amazitenga ngati ndiokhawo odziwa malamulo panyopawo ndithu!

  • @chifundochasweka-kv8fw
    @chifundochasweka-kv8fw19 күн бұрын

    Boma lokupha ili

  • @isaaczuze
    @isaaczuze18 күн бұрын

    Gift trapence ndichisilu kwambili mbuzi ya munthu .....gift trapence ndiooepela kale ndi kale ...anagudwa kalekale akufuna atiuze chiyani apa ....anthu akuvutika mmalawi muno iye Ali chete ...mbuzi ya munthu

  • @AliceMbewe-yi1pw
    @AliceMbewe-yi1pw18 күн бұрын

    A police amangofunika mbama yadzidzi basi kukonda ndalama

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o18 күн бұрын

    Nkhani iyi ipondeledzedwa co's Trapence ndi wa MCP uyu

  • @RebeccaNvenya
    @RebeccaNvenya18 күн бұрын

    Muthanedi nawo agalu amenewo amaonjeza ndipo alibe umunthu ai

  • @AndrewInnocent-he8gs
    @AndrewInnocent-he8gs18 күн бұрын

    Khani Siya mcp koma apolice umuthu analibe adyela ndi ndrama

  • @JamesMaduka-wk8xi
    @JamesMaduka-wk8xi18 күн бұрын

    Amafuna ndalama ntimawawumfiti osapelekampatakutimwanayo apitenaye kuchipatala milandu ya licence pambuyo ntimaopandachikondi please apolec khalanindumunthu tosefendiwanthu ifeso tomwe sitigwila tchitokupolec moyosotimawufuna momwe mumaziwonelainumo tose ndichimozimozi samalani ambuye alipo kimwambaku zikomo

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v18 күн бұрын

    President akakhala wa usilu nthambi za boma zonse zimakhala zausilu

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus18 күн бұрын

    Trapenz ndi opusa Ndamene anaika malawi pa moto

  • @sarahmphande6108
    @sarahmphande610816 күн бұрын

    Nfit zachabe

  • @kettiemkweu4528
    @kettiemkweu452819 күн бұрын

    Ndipo muchite nawo a police amenewo Anthu onvetsa chisoni mbuli za anthu. A police aku Malawi adzakhala osawuka ozunzika mpaka kale kale. Ma savage.. 😢

  • @henleysabiya6859
    @henleysabiya685918 күн бұрын

    Koma boma ili tiona zinthu

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience228319 күн бұрын

    MCPigs kupha ndikudya kwanu.

  • @Nomsa77
    @Nomsa7719 күн бұрын

    A human rights pls tiwomboleni Police dziko lonse anagulidwa

Келесі