Nthaw mkachitsiru. Tionana 2025. Zidzakuvoteran nd Ndondocha osat anthu
@LukaAron-el5qh2 ай бұрын
Bambo vumbe mukunena zoona inu
@NgomaRaheem2 ай бұрын
Kuyakhula kopusa ndithu tikumana 2025 ino
@user-cy7gd1go6y2 ай бұрын
Iwe ukuyendela chigoba chimoz chachimanga komaso chigobacho chokakamisa nde kumati chakwera awina chamba eti chifukwa akupasani chitenje panyo panu anyapapi inu nanuso inu adala magalasiwo ndi mutucho pakolo pako
@user-gx8or3yz9u2 ай бұрын
Ndalamazotu tilandila mudzipereka ndithu ife tidzilandila komasikuti tidzakuvoteraninso ai zimenezo muiwale amalawi tatopa Nanu kkkkk mudzalila chaka Cha mawa muli ku mastand tikufuna tione zina
@user-uf4db7im7d2 ай бұрын
Manyi anu
@user-vh9uk1jy7w2 ай бұрын
Mukunama chemwali
@FefieTenisha-du7ge2 ай бұрын
This is very pathetic With this kind of thinking how can we move forward as a country? I can now see clearly why this country will never develop... People are commenting on things they don't really understand.. Democracy will never work in Malawi... The masses are so idiotic that they can't even know how to elect a good leader for them
Пікірлер: 37
Chonsecho agona ndi njala anthu anthu osawona patali😩
Awa ndiye manyiiiiii onunkha
Sakuziwa chomwe akuchita
Athu ovetsa chisoni kwambili
Ndiganiza kuti pansi pa mtimapo mukuziwa kuti mukunama zomwe mukulankhulazo
Dziwani kuti tonsefe sitingakhale ndimaganizo amozi malawi ndi dziko zalazipani zambiri tosefe sitingakonde dpp aliyese ali ndi chisakho chake ndiye adpp mkuchedwa
Kkkkkkkk koma munthu anakonza alibe kalikose akuvutika ndikumatamililabe ng'ona party mbava yachabe chabe chakwela kwamtele
Azimai ovesa chisoni kwambiri pomwe kunyumba kwako kulibe chakudya
@ImraanJafali-dk7rg
2 ай бұрын
Ndiposo inu mwina adyesedwa ma2 pin
@user-hm9nc7lz6e
2 ай бұрын
Zoopsatu anthu amabgidwa papango komaso asekedwA maso sakuona
Pa mtsonkhano wa mcp angayinyoze ndani kuti akadyedwe ndi ng'ona
Iwe ukunena kuti anthu akonzekere, ife tinakonzeka kale zochotsa masanjewa 2025.
Kumalawi kwene umo wathu tikugonela nanjala thena bwenu tikukhumba ku votelaso chakwela mmmmm sata nadi malawi wazingizga nadi eshìii koma
Awa asandichimwise odi mgone
Chala imapele ka usilu
Izi izi ,muchepese ndithu ,kufuna kuutsa mkwiyo wa anthu uku mxeuii
Thawi yanu koma sangalalani komaliza malizitsani thawiyanu yatsala pang.ono
Azibambo ena mzeru zero...sad
Komadi anthu opanda nzeru mulipo, zoona munthu wanzeru mpaka kumasiya kupuma kwawo kupita kunsonkhano wa izizi?
Mdalayu akudwala chakwela wapanga chan😅
Zomvesa chison ndithu mmh
Kodi inu mumamufuna azinena kuti DPP izawina kodi tonse ingakhale ana agogo????
Mbuli za anthu
Munthu Ali PA Laine yokalandila zithu za mcp anganene kuti mcp iluza 2025 mukufuna asalandile kkkkkkkkkk
Anthu enawa ndi agalu awanthu
Ndarama sosi kwapusisa 2000 munduwamay kumanena simeneso mundu wobeleka sovesa chison asimay atu 😭🤔🤔
Nthaw mkachitsiru. Tionana 2025. Zidzakuvoteran nd Ndondocha osat anthu
Bambo vumbe mukunena zoona inu
Kuyakhula kopusa ndithu tikumana 2025 ino
Iwe ukuyendela chigoba chimoz chachimanga komaso chigobacho chokakamisa nde kumati chakwera awina chamba eti chifukwa akupasani chitenje panyo panu anyapapi inu nanuso inu adala magalasiwo ndi mutucho pakolo pako
Ndalamazotu tilandila mudzipereka ndithu ife tidzilandila komasikuti tidzakuvoteraninso ai zimenezo muiwale amalawi tatopa Nanu kkkkk mudzalila chaka Cha mawa muli ku mastand tikufuna tione zina
Manyi anu
Mukunama chemwali
This is very pathetic With this kind of thinking how can we move forward as a country? I can now see clearly why this country will never develop... People are commenting on things they don't really understand.. Democracy will never work in Malawi... The masses are so idiotic that they can't even know how to elect a good leader for them
Anthu akufa awa komanso osapenyanso awa sorry kwabasi
Mcp bomaaaaaa❤❤