Zodabwitsa Zimayi Uyu Watutumusa Gulu -''AKUMASHANTAH''

sangalore ana ake azivutika galimoto ilipo ngakhale ali nzimai

Пікірлер: 34

  • @JustinSuman-do1ob
    @JustinSuman-do1ob2 ай бұрын

    Osafooka ccter chitsogolo basi mwapeleka chitsanzo kwa azimayi anzanu omwe amaziyang'anila pansi 💪💪💪💪

  • @user-mk8cn2no3o
    @user-mk8cn2no3o2 ай бұрын

    Congratulations God bless you always

  • @EstherMilanzie
    @EstherMilanzieАй бұрын

    Congratulations

  • @AlexSochela-kp5lc
    @AlexSochela-kp5lcАй бұрын

    Money its for everyone as long as value is provided.

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa59812 ай бұрын

    Ulemu wanu sister

  • @Alicekazembe-tu7rz
    @Alicekazembe-tu7rzАй бұрын

    That's great

  • @user-pf1xd3lp2u
    @user-pf1xd3lp2u2 ай бұрын

    Ulemu wanu Mai olimbikira osamaziyang,anila pansi

  • @alomuddin8801
    @alomuddin8801Ай бұрын

    Mayi wa mzelu Kwambiri osafooka ayi mumakwana

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x2 ай бұрын

    Chemwaaa anga your great mother keep it up🙏🏿🙏🏿

  • @CharlesMillion-bt9su
    @CharlesMillion-bt9suАй бұрын

    Sister umakwana.

  • @user-cs5ss4rj7g
    @user-cs5ss4rj7gАй бұрын

    Ulemu wanu

  • @chifunirosaka9077
    @chifunirosaka90772 ай бұрын

    Ambuye azikutsogolelani nthawi zonse

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem2 ай бұрын

    Mkadz olimbikira Allah azimudalitsa

  • @mellipherjohn7158
    @mellipherjohn71582 ай бұрын

    mwaintha kwambili sisita mumakwana💪

  • @mellipherjohn7158
    @mellipherjohn71582 ай бұрын

    mwaintha sisita kumalimbikila 💪

  • @fridaywapheefriday3487
    @fridaywapheefriday3487Ай бұрын

    🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤

  • @johnfikilini3667
    @johnfikilini36672 ай бұрын

    Tabwerani ku LL mudzawapeza azimayi akuntchata

  • @thomchiphwanya3451
    @thomchiphwanya34512 ай бұрын

    Ulemu wanu masiteni Ku Zomba nde alipo Amai ambiri amashanta Chinamwali chinamwali

  • @rostermazengera2800
    @rostermazengera28002 ай бұрын

    I like her

  • @mellipherjohn7158
    @mellipherjohn71582 ай бұрын

    mumakwana sisita 💪

  • @mellipherjohn7158
    @mellipherjohn71582 ай бұрын

    Mumakwana sisita ulemu wanu

  • @user-qh5fq2nh7w
    @user-qh5fq2nh7w2 ай бұрын

    Sister zilibwino azimai tilinako kuthekela nthawi zambili timangodalila a zibambo nawo amafuna kuthandizidwa azimai tiyeni tidzilimbika kumayesa yesa ngati mwayi utapezeka tikudutsa munyengo zambili ndikudziwa ❤❤❤

  • @wabitha9769

    @wabitha9769

    2 ай бұрын

    Azimai tisaziyang"anile pansi tieni titengele phunziro apa zokomatu izi

  • @user-qh5fq2nh7w

    @user-qh5fq2nh7w

    2 ай бұрын

    @@wabitha9769 for sure

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w2 ай бұрын

    Nana waitha manyazi sathandiza

  • @user-xv9en6se4i
    @user-xv9en6se4i2 ай бұрын

    Ulemu wanu amayi

  • @GidionJonas-sr4zr
    @GidionJonas-sr4zr2 ай бұрын

    Nice sister

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy2 ай бұрын

    Ife Ku lilongwe kuno Ku 25 tilinao amayendesa ma min bus

  • @user-mk8cn2no3o
    @user-mk8cn2no3o2 ай бұрын

    Nice

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe10382 ай бұрын

    Zofunika

  • @user-po6ir6eh4z
    @user-po6ir6eh4z2 ай бұрын

    Ulemu wanu sister ndi bwera muzandiphuzise nane galimoto

  • @Fatima-li5rg
    @Fatima-li5rg2 ай бұрын

    Ulemu wanu sister

  • @user-wk1gf1wo3q
    @user-wk1gf1wo3q2 ай бұрын

    Nice sister

  • @Dorah-zl9uf
    @Dorah-zl9uf2 ай бұрын

    Ulemu wanu sister