Times Exclusive featuring John Kapito - 7 October 2023
Times Exclusive’s Brian Banda engages Consumers Association of Malawi Executive Director Mr. John Kapito on the fuel situation and economic crisis in the country.
Times Exclusive’s Brian Banda engages Consumers Association of Malawi Executive Director Mr. John Kapito on the fuel situation and economic crisis in the country.
Пікірлер: 89
This is the best Exclusive interview so far in 2023 done by Brian Banda.
@Mphamdala
9 ай бұрын
You haven't watched the one with Dalitso Kabambe
Your indeed a freedom fighter Mr Kapito❤
Kapito in Christ do what you want bwana mavuto ochuluka skubwela chifkwa chosowa usogoleri wabwno know mwauze aboma amvere kapito
The best 2023 interview on TTV
I Like this man ndipo apuleo akuyenela azinvele zimenezi ziapweteke chifukwa chilungamo chimawawatu
This interview is an eye opener 🔥🔥🔥
Very insightful Mr Kapito
Chakwera ndi Munthu omva zake zokha uja Izek adanena kale kuti ndiwe Galu kwabasi,,,,,,Brian Banda iwe ndi 1
Am here because of the DC
This guy deserves to come back I really like chilungamo chake
A Brian muzibweretsa nkuruyu nthawi ndi nthawi .Akapito always speach the truth since 2011
@juneprice5879
9 ай бұрын
0
@juneprice5879
9 ай бұрын
😢😂🎉😅😮❤😢
@SheenahMwalabu-iz3pr
8 ай бұрын
Daily ndipo samandikwana a kapito ndi mbambande ❤❤😂😂
This is the best medicine Malawi needs inorder to cure the deadly disease we are suffering from
Kuyakhula mwa zeru Malawi munoso muli athu azeru chochi
I like the guy for he can talk wisely and he seems to know more about running the government and lead him to link with born kalindo for they are talking the same thing lastly I like the way brian is paying attention
Kapito and Kalindo our only freedim fighters
This guy makes sense
Kodi Mr chakwera amaonera Times TV?
I love the confidence this man portrays. This is amazing and wonderful.
Now Mr Kapito is talking, but is he talking this. Out of love of Malawians, or he is not able to eat together with this government as he did with past government. I like that though.
Hamayo!!!!!!!!!pali ngamot apa simasewela........mr mulungu akudalisen ndithu.....I LIKE U MR
@jeffulejames3550
9 ай бұрын
❤❤❤
Akapito tayimirani inu tikuvoterani
The best interview ever
Ngati uzingomvetsela.pano ndikumvetsela kachitatu
Big up kapito chakwera ndi munthu osava indeed
Bwana kapita ndinu munthu okondadi dziko lanu ndipo kukakhala kusatenga maganizo anu angokhala anthu owuma mitima ndithu
MR kapito one of best citizen
Mbuzi ndi mbuzi zimzmva kathu.ndiye chakwera
We want people like this one in Malawi, even here in Zambia.❤❤❤❤❤
Awa amayankhula zoona kwambiri. ❤
@mikekaponya6016
9 ай бұрын
😊😊😊
Powerful massage osayang'ana mbali
adhawa akuoneka ngati ali serious'tu
❤❤❤ brilliant 🎉
The best interview of 2023, insightful
A WISE THINKER WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD
The guy is genius ...he knows what is saying
Kapito is real freedom fighter
Za nzeru bwana, kuyankhula Koma kumeneku
Hello Malawi
Kachilungamo kowawa
Kuyankhula zolungama zenizeni
Umakwanila Big Kapito
I think chakwera agopanga rising watikwana zeedi
Apo mkuyooya chilungamo
Machine 🙌🔥👏
Our prayer is that Kapito shud continue to unfold the stupidity that the Govt does😊
Tizayangana track record yomweyo john😊
This man is great
Boma la akhutukumve ndlimeneli ndipo palibe chomwe akusonyeza kut amvere malangizo ayi boma la zitsilu
John kapito ndi kumtunda amwene!!
I like kapito
chimene ndachiona ine palibe chingachitike chifukwa ndalama okuyika nthumba mwawo ife basi khani ndi iyi basi😢😢😢😢
Zoona big man ❤
❤
Komatu uncle a Kapito ndimbambande eee the way amalankhuliratu zachilungamo zokhazokha osaona mbal, dzina olo chipani. ❤❤😂😂
Zake zokha kuphiri la ndalapa
Ndipo achakwera adzayankhura zoti chani ? Nthawi yakampeni.pazomwe akupangazi.
Dziko ndi anthu
Dziko likufunika anthu a economics osat aliyese
Nkuluyi NDI wanzeru
inetu ndikuona ngati namkumwa ndiwa mcp
@enockdaisi1306
9 ай бұрын
Yes namkhumwa Siwa dpp no
@Razzaq2010
9 ай бұрын
Musaone ngati, akumuyuza a tonse
@Yabwata
9 ай бұрын
Osati kuwona koma nakhumwa ndi wa mcp galu ujaa , bola peter basi ..osati mcp
@razackadan7120
9 ай бұрын
Mr. Kapito is a brave man. He never side with any government. He offered constructive criticism on UDF, DPP and now MCP regimes. Unfortunately they don't listen instead they brand him as merely an opposer.
Tag Mr president
Kapito the boy, he is ready 😅
Aa achapondawa kwapasa mpando onona awa sangayankhure zimenezi, analipo anzao
Koma Kapito yu...amalankhula.eeeehh😂😂😂😂😂😂
😭😭😭
Kapito 2025 vice President of Malawi😅😅😅
Kulankhulankoma uku Kothandiza kusintha dziko apo biii aaaaa mavuto okhaokha ndiatsogoleri osadziwa zochita zachuma sazidziwa dziko Liye da bwanji?
Big man
Inu kapito lowani mutenge usogolel ine vot yanu
panakambidwa zinthu
Koloviko
vuto achakwera sakudziwa kuti alikuti akuwona ngati anakalibe ku church akumbutsen ndikupemphela kuti mulungu alange achakwera pamodzi ndi igwira nawo ntchito atuluke mabala kusana lalikulu
Chakwera ndi bulutu
Kapito kapito kulongola too much. Tazayesaniko u president please
Ok kunena zoona dziko likufunika chilima ili
@welcempira2910
9 ай бұрын
Ndipo serious. Vice wake Kapito 😂😂
@charlessakwata7319
9 ай бұрын
Chifukwa tawonani since chilima ananena zama reform anthu amadana naye
The best interview ever
Za nzeru bwana, kuyankhula Koma kumeneku