More Manganya humor and life lessons.
Maganya akuti koma mayi anu inu ❤❤Tikuferanji still Trending
Juzi yokongola ndaivala dele😅😅😅😅😅😅😅
Ndikudutsa munsewumu ndat ndikhwete kuno😂😂😂😂
Plz DR Manganya bring Winiko ...I love you all guys
Ukufuna azikangana 😂
Winiko sali mwakalee..mtayeeni
I like the Chewa flavour... ko Mariteni...nikhwetere uku
😂😂😂
Km winiko .....uja another name Mr Nyooo abwereso puliz😂😂😂😂
Mmmmm zokaikisa😂
Komatu magaye, komaliteni ku nathenje😂, mwatitolatu apa😂
Koma Manga 😂😂😂😂😂....great one....
Very lesson, keep up tikufelanji
Ayi Kani sipiki ingilishi 😂😅
Kkkkkkk akuti anabwera pano kuzagwira ntchito zonse naye ndi munthu kkkkkkk kma akazi
Ayi Kani sipiki iwe ndindani ine ndi jetu 🤣🤣🤣
Kkkkkkkk manganya woyeeee. Ayiyaiyaaaa guys mmabebetsa
Koma kuthamanga kumeneku 😂😂😂🤣we need masikono and winiko back plz
Keep it up tikuferanji team❤
Koma Manganya amathamanga osati masewera😂😂🙌🙌
Ai kani sipiki....afuna ntchitoooo😂😂😂😂
Manganya tikufunaso madam anu ma sikono❤
Akuti manga no 🤣🤣🤣🤣 azimu oyera atero
Naye ndi munthu😂😂😂😂😂
Watching from mwineriwa vg mulanje ❤
Manga😂😂😂😂kuthawaa kumeneko muti nchan😂😂
Komatu Nanyoni umatha ❤
Koma kwachema 😂😂😂 manganya
Tikufelanji is not the same again bring ma sikono and winiko back azukulu anga
Ndipo inu aaah
🤣🤣🤣🤣 this is my house kkkkkk koma Manganya
Kom ma comment Ali apa kuwawelenga ku English translation utha kufa ndkuseka
Kkkkkk manganya ndiye wanthawa
Kkkkk koma manganya wadya gear😂😂😂😂😂
Ntchito iliyonse akhoza kugwira 🤣😂😂
Manganya ndi aviator payekha 😅😅😅😅
😂😂😂😂😂 km Nanyon
first to comment ndikufuna zanga😂❤❤❤
Ine pano ase
Mofaya Mr VP, kkkkkkk masewero musasiye 😅😂
Speed ya Manganya ndiyamoto😂
😂😂😂Koma Maganya muli liwiro Koma abweletseni ma Sikono
Koma manganya eshhhhh 😂😂😂
Mr manganya Ngat zingateke we miss nyooo❤
ATI junzi Yokongola kkkkk km manganya anabwera 😂😂😂😂😂
Ukati usamalike ndikuzizilaku ufa peza chilichonse uvale
Manganya Ali nkuliswatu liwiro😂😂
Manga wabwera ngat coming ❤❤❤
Kom manga ndiphyuutaa kung'ambikako kkkk
Ati ukati usamalike ndikudzidzilaku ufa ndikudzidzila chilichose peza uvale 😂😂👘
Bring back winiko guyz ❤❤❤❤
Mayianu ndawatayira kamtengo Mukuoneka kumasuka mosonyeza kuti mukudzidziwatu . 😂😂
Kukazizila ndimene zimakhalila 🎶❤
Kkkk or kutenga cup osaopa kuyexgesa edzi
Kamanganya kasokoneza banja uku😅😅😅
Ati mukanavulala Lero mai😂😂
Koma,, ,,mangany👌
Manganya kuthawa kokha alibe zake 😂😂😂😂
Koma manganya 😂😂😂😂😂
Kkkkkkk koma vice president momwe akuthamangila 😂😂😂😂uyu sangamuphe olo ndegeyo azichita kuyiposa kuthamanga
Winiko Ali Kuti the DC pangolin
Mwana oopsa kwambiri
Ndipo kukhara ngati akulowesapo ndale
kkkkk avayisi musamusiye nyo winiko
Mumakwana a mr manganya 😂😂
Kodi mwanyamula iPhone a Thumbi? Nde gesture ya manjayo cholinga tione lamya 😂😂😂😂
Kkkkkkkkkkkk manganya ndi makina
Kuthamanga ngati mphepo ya mkuntho Mannga🤣🤣🤣🤣🤣
Kkkk winiko 😂alikut
Nanyoni ndiokonda zinthu 😅😅😅😅
Kkkk koma manganya eeee
Usampatse ndimpatsaaaaaa
speed yamphepo
Ayi Kona anthu mumaakita😅😅😅
Matumbi mulimbe nazo 😂😂😂😂
Nkhweta😂😂😂😂
😂😂😂😂Komanso nanyoni Eeeee ayi akuti sakuopa Mai chisi😂😂😂😂
😂😂 Ma skono asowa
Every test is a new test
Ati olo azikatunga ndi cup kkkkk
Jamani jakuti chiiii🤣🤣🙌
Mr Nyo make Sikono pls
amene mumajambula this video be mindful of the background noise that you make while taking this videos we can hear the footsteps
Manganya giving good vision to young ones
😂😂😂😂 speed ili nd Manga
Kkkkkkkk koma yaa
Abale tulusani Ina mumatimvesa kukoma ife
Kkkkkkk nanyoni😂😂😂😂
Koma manganya adakoza😂😂
Bwelesani winiko
Kwa mariten😂😂😂😂
Nice one
Bosslady chiyao kkkk
Uyuyu akamapanga masewelo amaoneka wa zelu koma ku bomaku zelo pa ten
Kkkkkkk
Ubwino wake salipo ekha m,bomamo alimo ambili or uchite zabwino wina ngat akuyipitsa basitu palibe chilipo nonse muyipa fenkis kumpando 😅
girl is beautiful❤❤❤😂
Kukwapuka kumeneko anduna😅😅
🤣🤣🤣 l can sipiki english for me mumatisangalatsa
Kkkkkkk ananyoni mupole Moto
Munabwera maguyz
Kusowa kwakupita basi hahaaaaa
Koma ndye kuthwatu😂
Aphule liwiro kkkkkk
Kunlango kwaugele.... 😂😂😂😂😂
Kusowa kwakupitaaaa🤣🤣🤣🤣
Kkkkkkkk amanga mumakwana mmmmmm
Manganya kuthamanga ngati nyumba ikupsa
Kkkk koma manga ndi speed link tu kkkk amaliyala liwiro kooopsa
Kkkkkk liwiro apule
Ngani sabo 😂😂
❤
Пікірлер: 214
Maganya akuti koma mayi anu inu ❤❤Tikuferanji still Trending
Juzi yokongola ndaivala dele😅😅😅😅😅😅😅
Ndikudutsa munsewumu ndat ndikhwete kuno😂😂😂😂
Plz DR Manganya bring Winiko ...I love you all guys
@matatiyogameboy568
Ай бұрын
Ukufuna azikangana 😂
@levisomba9017
Ай бұрын
Winiko sali mwakalee..mtayeeni
I like the Chewa flavour... ko Mariteni...nikhwetere uku
@TadalaKachulu
Ай бұрын
😂😂😂
Km winiko .....uja another name Mr Nyooo abwereso puliz😂😂😂😂
@pemphokatembe443
Ай бұрын
Mmmmm zokaikisa😂
Komatu magaye, komaliteni ku nathenje😂, mwatitolatu apa😂
Koma Manga 😂😂😂😂😂....great one....
Very lesson, keep up tikufelanji
Ayi Kani sipiki ingilishi 😂😅
Kkkkkkk akuti anabwera pano kuzagwira ntchito zonse naye ndi munthu kkkkkkk kma akazi
Ayi Kani sipiki iwe ndindani ine ndi jetu 🤣🤣🤣
Kkkkkkkk manganya woyeeee. Ayiyaiyaaaa guys mmabebetsa
Koma kuthamanga kumeneku 😂😂😂🤣we need masikono and winiko back plz
Keep it up tikuferanji team❤
Koma Manganya amathamanga osati masewera😂😂🙌🙌
Ai kani sipiki....afuna ntchitoooo😂😂😂😂
Manganya tikufunaso madam anu ma sikono❤
Akuti manga no 🤣🤣🤣🤣 azimu oyera atero
Naye ndi munthu😂😂😂😂😂
Watching from mwineriwa vg mulanje ❤
Manga😂😂😂😂kuthawaa kumeneko muti nchan😂😂
Komatu Nanyoni umatha ❤
Koma kwachema 😂😂😂 manganya
Tikufelanji is not the same again bring ma sikono and winiko back azukulu anga
@edithchisale3009
11 күн бұрын
Ndipo inu aaah
🤣🤣🤣🤣 this is my house kkkkkk koma Manganya
Kom ma comment Ali apa kuwawelenga ku English translation utha kufa ndkuseka
Kkkkkk manganya ndiye wanthawa
Kkkkk koma manganya wadya gear😂😂😂😂😂
Ntchito iliyonse akhoza kugwira 🤣😂😂
Manganya ndi aviator payekha 😅😅😅😅
😂😂😂😂😂 km Nanyon
first to comment ndikufuna zanga😂❤❤❤
@HishamMalikha
Ай бұрын
Ine pano ase
Mofaya Mr VP, kkkkkkk masewero musasiye 😅😂
Speed ya Manganya ndiyamoto😂
😂😂😂Koma Maganya muli liwiro Koma abweletseni ma Sikono
Koma manganya eshhhhh 😂😂😂
Mr manganya Ngat zingateke we miss nyooo❤
ATI junzi Yokongola kkkkk km manganya anabwera 😂😂😂😂😂
@user-gl7yh8vq2s
6 күн бұрын
Ukati usamalike ndikuzizilaku ufa peza chilichonse uvale
Manganya Ali nkuliswatu liwiro😂😂
Manga wabwera ngat coming ❤❤❤
Kom manga ndiphyuutaa kung'ambikako kkkk
Ati ukati usamalike ndikudzidzilaku ufa ndikudzidzila chilichose peza uvale 😂😂👘
Bring back winiko guyz ❤❤❤❤
Mayianu ndawatayira kamtengo Mukuoneka kumasuka mosonyeza kuti mukudzidziwatu . 😂😂
Kukazizila ndimene zimakhalila 🎶❤
Kkkk or kutenga cup osaopa kuyexgesa edzi
Kamanganya kasokoneza banja uku😅😅😅
Ati mukanavulala Lero mai😂😂
Koma,, ,,mangany👌
Manganya kuthawa kokha alibe zake 😂😂😂😂
Koma manganya 😂😂😂😂😂
Kkkkkkk koma vice president momwe akuthamangila 😂😂😂😂uyu sangamuphe olo ndegeyo azichita kuyiposa kuthamanga
Winiko Ali Kuti the DC pangolin
@inessmsiyambiri8517
Ай бұрын
Mwana oopsa kwambiri
@user-rk5ye2tv9z
Ай бұрын
Ndipo kukhara ngati akulowesapo ndale
kkkkk avayisi musamusiye nyo winiko
Mumakwana a mr manganya 😂😂
Kodi mwanyamula iPhone a Thumbi? Nde gesture ya manjayo cholinga tione lamya 😂😂😂😂
Kkkkkkkkkkkk manganya ndi makina
Kuthamanga ngati mphepo ya mkuntho Mannga🤣🤣🤣🤣🤣
Kkkk winiko 😂alikut
Nanyoni ndiokonda zinthu 😅😅😅😅
Kkkk koma manganya eeee
Usampatse ndimpatsaaaaaa
speed yamphepo
Ayi Kona anthu mumaakita😅😅😅
Matumbi mulimbe nazo 😂😂😂😂
Nkhweta😂😂😂😂
😂😂😂😂Komanso nanyoni Eeeee ayi akuti sakuopa Mai chisi😂😂😂😂
😂😂 Ma skono asowa
Every test is a new test
Ati olo azikatunga ndi cup kkkkk
Jamani jakuti chiiii🤣🤣🙌
Mr Nyo make Sikono pls
amene mumajambula this video be mindful of the background noise that you make while taking this videos we can hear the footsteps
Manganya giving good vision to young ones
😂😂😂😂 speed ili nd Manga
Kkkkkkkk koma yaa
Abale tulusani Ina mumatimvesa kukoma ife
Kkkkkkk nanyoni😂😂😂😂
Koma manganya adakoza😂😂
Bwelesani winiko
Kwa mariten😂😂😂😂
Nice one
Bosslady chiyao kkkk
Uyuyu akamapanga masewelo amaoneka wa zelu koma ku bomaku zelo pa ten
@inessmsiyambiri8517
Ай бұрын
Kkkkkkk
@tadalangozo5167
Ай бұрын
Ubwino wake salipo ekha m,bomamo alimo ambili or uchite zabwino wina ngat akuyipitsa basitu palibe chilipo nonse muyipa fenkis kumpando 😅
girl is beautiful❤❤❤😂
Kukwapuka kumeneko anduna😅😅
🤣🤣🤣 l can sipiki english for me mumatisangalatsa
Kkkkkkk ananyoni mupole Moto
Munabwera maguyz
Kusowa kwakupita basi hahaaaaa
Koma ndye kuthwatu😂
Aphule liwiro kkkkkk
Kunlango kwaugele.... 😂😂😂😂😂
@duniankhoma8215
Ай бұрын
Kusowa kwakupitaaaa🤣🤣🤣🤣
Kkkkkkkk amanga mumakwana mmmmmm
Manganya kuthamanga ngati nyumba ikupsa
Kkkk koma manga ndi speed link tu kkkk amaliyala liwiro kooopsa
Kkkkkk liwiro apule
Ngani sabo 😂😂
❤