Rev Alexander Kambiri preaching at Sopani ground in Malomo, Ntchisi

It was a sports evangelism campaign

Пікірлер: 1

  • @user-cm8ji7im1h
    @user-cm8ji7im1h2 ай бұрын

    Koma mukuziwaa kuti chipembezo cha mpila chili ngati chipembezo chimozi cholemekeza satana???? Chimene opephela ndi osapephela amasokhana Malo pamodzi ndikumamulemekeza satana kudzela mukusewela mpila??? Kumbukilani abusa Bible limati munthu mmodzi sakuyenela kukhala ndi ambuye awili Nde ngati mpila uli osakondwelesa Mulungu okha kumwamba nde kuti umakondwelesa ndan?????? Ndimatsatila kwambili MA ulaliki anu ndipo inenso ndimazuzulidwa kudzela mma ulaliki Anu Koma Kumbukilani Mulungu wathu ndi wa msanje