Piksy - Nzanga [Video Lyrics]

Музыка

Verse 1
Nzanga uli bwanji
Zikuyenda bwanji, how is your family
Business ikuyenda bwanji, poti dzikoli nde lavuta kwambiri
Ona daily tikuluza fanz
Kaya chaka chino zitithera bwanji
Every day kugwada pansi
Mulungu akhulukire dziko lapansi
Please hold on my friend
Stay strong it's gonna be a bumpy road
I have hope my friend we gonna be alright
Chorus
Koma pompano tikumana
Tiyese kudzisamala
Posachedwa kuwala
Mwina tingodzisamala
Osaopa nzanga
Poti kukondwa ndi mawa
Pompano kuwala we gonna dream of these days
Verse 2
I miss those trips to the lake
Zima boat drive uku tikusekelera
Achina Dj Klipps on the deck
Tikuvina ndi makapu tikumwemwelera
Koma wapita pita pita pita
Tingosamalira mwina tidzawina
Aii iia iaa
Tingosamalira mwina tidzawina
Chorus
Koma pompano tikumana
Tiyese kudzisamala
Posachedwa kuwala
Mwina tingodzisamala
Osaopa nzanga
Poti kukondwa ndi mawa
Pompano kuwala we gonna dream of these days
Yes I miss church
I miss family
I miss being in the gym I miss hiking
I miss those shows I miss you all
Please stay safe my friend
#piksy#Nzanga#piksy2021

Пікірлер: 7

  • @mandamoses1
    @mandamoses12 жыл бұрын

    Wow! How come I hadn't listened to this genius piece? Big up Piksy.

  • @doloamaphusha8105
    @doloamaphusha81053 жыл бұрын

    Respect big 💙

  • @tammie-rosechimbenje1790
    @tammie-rosechimbenje17902 жыл бұрын

    Beautiful! Just beautiful!!!

  • @wickmanmanzie2886
    @wickmanmanzie28863 жыл бұрын

    This guy is a genius

  • @haddijahhaji7938
    @haddijahhaji79382 жыл бұрын

    who's here 2022 🤗2020 was eeee nono💘

  • @judithmajid9679
    @judithmajid9679 Жыл бұрын

    Piksy it's me William Majid my Nick name SpiKy l like you piksy since when I was child but what I really need to you is kukuwona face to face umatha piksy sindikukumana bt mmene umayimbira ase eeee ayi man

  • @immamhango6357
    @immamhango63572 жыл бұрын

    🥰

Келесі