OKWATILA OPUSA || Part 3
Комедия
Thank you for watching Blenac Videos each and every time that we upload here. To be honest with you guys, you really mean alot to us when you come to watch these videos. We also value those sweet comments you make, We love it when you "LIKE AND SUBSCRIBE" . have you already Liked it this video? How about subscribing?
We have no better way to thank you GOOD PEOPLE, All we can say is that ''May the God almighty cover you and protect you always''
Пікірлер: 31
Juuu ndi mwana wambwino kwambiri amanikondwelesa continue to teach us
Junior ndi mwana wanzeru amandisangalatsa😂😂😂😘😘❤
❤❤❤❤ from lusaka zambia God bless you
This lady is full of drama the way she sit on that chair she even put her legs on top of the table 😂😂😂😂😂😂😂koma Mr blenac you're the 5 star general❤❤❤❤❤🎉🎉🎉
😂😂😂😂KOMA MR BLENAC MUTSEGULIRENI MWANA APHE NAWO NJOKAYO MWATANI KODI
@BlenacAnimations
5 ай бұрын
Ayi aaah, Junior si mwana omulora kulowa mnyumba kkkk
Mr blenac inuyo ndi dolo musazafe muzangosowa ngat Elia, mumatimvesa kukoma tisaname yooh❤
@BlenacAnimations
5 ай бұрын
Wow, ulemu kumwamba
Juuuu ndimwana wabwino komaso wazelu kwambili amakhaulisa njoka zakupha
Machokapo kkkkk😊
keep it up bamboo ❤❤blenac your comedys matipudzitsa zambili kwambili ngati ana ndi akulu amata kutengamo pudzilo lalikulu God bless to those who 😂watch your videos,❤❤❤
@BlenacAnimations
5 ай бұрын
Amen
Timakunyadirani kwambiri aise
Mr blenac mumati imilira
We need Nomia character
Blenan😊😊😊😊
Wakuchenjeletsa grace ulipiratu iwe
Kaka😂❤
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Mr blenac
Mr blenac❤
😂
Umatha
Nomia wasowatu wapita ku nchuti
I am a long time follower I remember all these videos❤❤❤❤
@BlenacAnimations
5 ай бұрын
Ndipo sibodza, mwachoka nafe kutali sister. May God bless you so much. Good night
❤❤
Blenac siabva namadress... jnr must caught you redhanded
Km adad mukapitiliza njoka ikuphan watero ndi juuuuu😅😅😅
@BlenacAnimations
5 ай бұрын
Kkkkk thanks Doreen
😂